Comrade Ntanyiwa On Limpopo FM "Enock Chihana Akusakidwa Ndi Police"

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 27 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 59

  • @MaxwellChaminju
    @MaxwellChaminju 16 днів тому +7

    Bwana wanga watulukiraso 😂❤❤❤much ❤

  • @LeahSimbeye-m3b
    @LeahSimbeye-m3b 16 днів тому +4

    We love you Mtanyiwa

  • @GogoAbigale
    @GogoAbigale 4 дні тому

    I love your audios big up never stop fighting for malawi

  • @PaulDaka-dc3re
    @PaulDaka-dc3re 15 днів тому +1

    We proud of you Mr Ntanyiwa lovely

  • @StoniaMoyo
    @StoniaMoyo 15 днів тому +1

    More fire 🔥 mr comrade ntanyiwa

  • @HenryManda-c4i
    @HenryManda-c4i 14 днів тому

    Koma anyamata kumuswa sound eeeeeeeeh💕💕🔥🔥🔥🔥

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson 15 днів тому +3

    Nyimboyo ndaikonda heavy

  • @ChimwemweSauka
    @ChimwemweSauka 15 днів тому +1

    Welcome antanyiwa we love you brother

  • @AyamiMustafa
    @AyamiMustafa 15 днів тому +1

    😂😂😂 comrade mulungu anaziwadi kuthi tizakala mu nyengo yachikangawa big up my brother

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite 15 днів тому

    We love you mtanyiwa comrade

  • @jamesmsonkho4830
    @jamesmsonkho4830 15 днів тому +1

    Acomrade mufuse athu opephela muchoonadi zokhuza chisakho kuti kumwamba anawawosela chani muzaziwa

  • @AlicePondani
    @AlicePondani 15 днів тому

    Tizafa chifukwaa cha mbendera imeneyiyi,restwell biyeni, ntanyiwa proud of you

  • @FrancisMakina-e6k
    @FrancisMakina-e6k 15 днів тому

    🔥🔥🔥🔥nmtanyiwa

  • @HenryManda-c4i
    @HenryManda-c4i 14 днів тому

    Plz tigairenikoni link ya nyimbo yoo

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 16 днів тому +1

    Welcome back Mr Ntanyiwa.

  • @ElisaNyirongo
    @ElisaNyirongo 15 днів тому

    Smartmatic yadwalika😂😂 imeneyo inali pick two tikudikila jocker😂😂😂😂

  • @HarryMsudzula
    @HarryMsudzula 16 днів тому

    Amtanyiwa can you share me a full song this is so nice

  • @HabiboZimba
    @HabiboZimba 16 днів тому

    ❤❤❤ mtanyiwa yemweyo awuze kaka

  • @Spare-n8l
    @Spare-n8l 16 днів тому +1

    Chiboma ichi ndichoyamwiladi magazi Chi Congress party chakupha chizingomanga A opposition

  • @AdamDawood-h7l
    @AdamDawood-h7l 15 днів тому

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉 tilipano. Kuvelainu. Basi

  • @OwenZimba-b4s
    @OwenZimba-b4s 15 днів тому

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂big up mr comrade

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 16 днів тому

    Comrade nkhani yoti inuo ma activist nonse ndi mabungwe nonse mulembe makalata kusumila MDF komanso MPS pa nkhaza zomwe akucitazi imeneo ndiyomwe tikufuna cifukwa mcp yationjeza tili pambuyo panu osadanda democrancy yathu ikutha. Tikuthokozeni comrade pokamuona gangata bolani mitima yatsikako pomva kuti aliko bwino, mukapitanso kwa a mai awombeledwa dzulo mutiuzanso mmene zilili cifukwa anthu amenewa ndiomwe tikudalira kuti aticotse mmavutowa.Comrade apapa nde mwamalidza yonse ya smart matic imenei mbuzi zimenezi yagwa nayo cifukwa ndiyomwe amadalira cifukwa amadziwa kuti palibe angawavotele.

  • @WiseJordan-ds6km
    @WiseJordan-ds6km 15 днів тому

    ❤❤❤

  • @JacquereenPereira
    @JacquereenPereira 15 днів тому

    Kkkkkk ulibe pabwino nyanii kkkk Nice song ❤

  • @bhowazpindani7755
    @bhowazpindani7755 16 днів тому +2

    Ntanyiwa ndikawawa ulemu wanu

  • @MubarackKathumba-w9t
    @MubarackKathumba-w9t 15 днів тому

    Yomweyo ntanyiwa iwe

  • @LilianMakweya
    @LilianMakweya 16 днів тому +1

    Antanyiwa ndi mbambande

  • @MphatsoKhwengweya
    @MphatsoKhwengweya 16 днів тому

    Commerade Ntanyiwa koma nyiwa nyimboyo plz ibwerezedwe eeee ilibwino k wambiri iziimbidwa tsiku ndi tsiku.

  • @MemoryMteketi
    @MemoryMteketi 16 днів тому +2

    Ulemu wanu antanyuwa ndimakunyadirani ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @DavieDulani
    @DavieDulani 16 днів тому

    Big man timakupephelani

  • @GiftMatiki-q7s
    @GiftMatiki-q7s 16 днів тому +2

    Ndimakunyadilani atanyiwa mulungu anakutumani ndicholinga mulungu azikutetezani azikudalisani 🙏🙏🙏🙏

  • @MubarackKathumba-w9t
    @MubarackKathumba-w9t 15 днів тому

    Nyimboyo iyambilenso

  • @chikondikandulu7052
    @chikondikandulu7052 15 днів тому

    Makwana

  • @EricKamwendo
    @EricKamwendo 16 днів тому

    Mukunena zoonadi za Ben Longwe tinamutuluka kale kale ndi kape amene uja wa dyera lopoira

  • @BrandonKanseka
    @BrandonKanseka 15 днів тому

    Inuyo ndi 1 basi, ndichifukwa athu ena sakumwa nanu madzi, mwabudulira mmemo

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite 15 днів тому

    Komdwani ndiwopanda mzeru

  • @VincentMagriva
    @VincentMagriva 15 днів тому

    Ndafika sound guy mwaipha heavy kathupi koonda nd ufiti ndiye mutu ngati wasenza batile!?????

  • @InnocentTwalick
    @InnocentTwalick 16 днів тому

    Umakwana ntanyiwa

  • @MathewsChitambe-m6o
    @MathewsChitambe-m6o 15 днів тому

    Wabandulatu nyimbo mfanayu,yakumapetoyo

  • @PaulRice-n1f
    @PaulRice-n1f 16 днів тому

    Kodi boma limeneli akufuna chiyani makamaka
    Akufuna chiyani nkhondo chiyani

  • @Rasheedissa-f3q
    @Rasheedissa-f3q 16 днів тому +2

    I'm the first one to see mtanyiwa imeneyo

  • @InnocentTwalick
    @InnocentTwalick 16 днів тому

    Umakwana koma ife timasangala ndi wailes yako

  • @JonathanLameck-b4s
    @JonathanLameck-b4s 16 днів тому

    Atanyiwa pitilizani kutisekula maso Mulungu azikudalisani ndipo akutetezeni nthawi yose ya moyo wanu

  • @InnocentTwalick
    @InnocentTwalick 16 днів тому

    Unapita ukanapanga likod

  • @DanielJuwawo-s5n
    @DanielJuwawo-s5n 16 днів тому

    Koma boma ili likungodziwa kumanga anthu opanda chifukwa

  • @PaulDaka-dc3re
    @PaulDaka-dc3re 15 днів тому

    Kufoilako peter watani? Kupusa kwambiri

  • @SylvesterSululu
    @SylvesterSululu 15 днів тому

    Mungolamula kt dzikolonselino mwatimangamwe achikangawa usatana wotani womwe mukuwachita anthu.eeeeeeee mulungu wanga ine tiveleni kulila kwathu ife

  • @GrivinSauka
    @GrivinSauka 15 днів тому

    Ngat ku Malawi kuli kape number 1 ndi uyuuuu. Your days are numbered trust me.

  • @PaulDaka-dc3re
    @PaulDaka-dc3re 15 днів тому

    Yomweyo galu iwe kkkkk

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 16 днів тому +1

    Welcome comrade Ntanyiwa🎉🎉🎉

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr 16 днів тому

    Tym is gone mcp l

  • @saidimponda
    @saidimponda 15 днів тому

    We love you mtanyiwa

  • @OwenNyambose
    @OwenNyambose 15 днів тому

    ❤❤❤❤❤