BON KALINDO 24 JULY 2024 KUSWANYA BASI PA WEDNESDAY

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 76

  • @KelvinLaudon
    @KelvinLaudon 2 місяці тому +11

    Kuyankhula ndiye mukuyankhula koma anthuwa kusamva big up kalindo your the genuine the DC

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 2 місяці тому +6

    Ngati inuyo a DPP, UDF AND AFORD simugwizana mutaphe matiparty ndinu mutizunzisa koopsya pamene bolani inuyo muli ni ndalama muzatha kuthawa koma ifeee tizangosowa Ngati mmene zinkachikira mu mcp yapitayo😭😭😭😭😭😭 tikulira kodi kumwera kuno singathe kukhala nigwizano wa zipani kupanga chimozi please akaliyati apm,Atupele choonde choonde pangani chimozi zukani tikutha tonse muno please

  • @AugustineMwamadi
    @AugustineMwamadi 2 місяці тому +7

    Chisankho nthawi zambiri zimatengera amene waimirayo kuti ndi ochuka bwanji kuderalo chisanzo BT wawina wa independent kusonyeza kuti iyeyo ndi amene anali popular mangochi wawina uja ngakhale akanaima pa yekha still akanawina sanabvotere mcp amubvotera munthuyo chimodzi modzi chisankho Cha 2020 anthu anavotera mcp chifukwa Cha chilima namukonda amb

    • @AffectionateGeyser-fm7dl
      @AffectionateGeyser-fm7dl 2 місяці тому

      Zoona ma candidate ena imakhala character siyabwino ndiye anthu savotera the problem is not the party but candidate

  • @BenPhiri-r8j
    @BenPhiri-r8j 2 місяці тому +5

    Next year MCP might win opposition hasn't been active chiloweleni, so voting ndikumudzi ambiri amayenera kupangidwa convince

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 2 місяці тому +1

    Simukunama opposition ikugona, kmanso Madera omwe avotera MCP mitu yawo sigwira kuno ku Thyolo MCP taikana

  • @PromiseBonya
    @PromiseBonya 2 місяці тому +3

    Otsusaw akubowa ndipo akupsesa mtim ochenjeza schenjeze bwanji KT amve anthu away eshiiiii

  • @TanishaLiffa
    @TanishaLiffa 2 місяці тому

    The DC 💪

  • @inamrigala
    @inamrigala 2 місяці тому

    apepetula zisilu izi zitayen bon

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 2 місяці тому

    KALINDO NDIYE AKUYANKHULA KOMA KUSAMVA KWA ANTHU OSUSA AGONA AKUFUNA KUWINA ZASANKHO KOMA ALI NDWIIIIII.NGATI AKUMETESA , AKUFUNA KUMENYEREDWA NKHONDO CHONSECHO ANGOKHALA

  • @BrightNkhoma-xz4bg
    @BrightNkhoma-xz4bg 2 місяці тому

    Bon Kalindo 🇲🇼🙏

  • @FrankMwachande
    @FrankMwachande 2 місяці тому

    😂kkk kukhunuka inuyo a opposition seriously .

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 2 місяці тому

    The DC'S mwana woooopsa kwambiri akhalise Malawi

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 2 місяці тому +5

    Vuto option yikugona kwambiri. Munthu oti akudziwa zoti atha akumenyedwa ndeu, amakonzekera kwambiri, lero ndi izo

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 місяці тому

    The Minister Boni Kanindo, you see yourself how these options their mind is just to tuka each other , so it's not solution, Bon you are a big Minister

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 2 місяці тому +1

    Bon kalindo anayamba kale kuyakula koma position yili ziiii yikutibowaso bwanji😊

  • @FrankMwachande
    @FrankMwachande 2 місяці тому

    True story the DC😢

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 2 місяці тому

    Koma chilima timuliladi mpakamkapa chifukwa ndiyekhayo anakakhala active analidi msikilikali wa anthu osauka a DPP,UDF,AFORD alibe nazo ntchito iwowo bola zawo zilibwino sagona ndinjala koma akupha ife amalawi osawukafe eeeeeh koma achilima munatisiliyanji ifeee😢😢😢😢😢

  • @enocklimani1750
    @enocklimani1750 2 місяці тому

    The Dc

  • @AndrewChiponga
    @AndrewChiponga 2 місяці тому

    Ase karindo ndi doro maguys chisakho chizavuta chaka chamawa apapa zaonesa kuberedwa

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 місяці тому

    awa olo apange zonela anthu akumudzi ananaminza zachimanga koma akumangochi anthu opunsa kwabasi musapangeso zimenezo ku mp ndikuwuzeni ine ndiwina ndipo mangochi zizayivutisa tikawina inu mukavotera mcp yanuyo muziwa Malawi musayelekeze mistake ina mulilanayo anthu awa mene tikuvutikira pano inu zowona kwavutera kodi mvuto lanu ndichani inu achiyao mumazichemelera kuti inu ndaya odzindikira apa mwatani ìnu inu munali ndi mvuto lanji inu ❤Dpp UDF ilikoko zowona inu

  • @dinchisale
    @dinchisale 2 місяці тому

    Akugonadi too much chifukwa amafuna mipando ya u Prezident,

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko 2 місяці тому +1

    A opposition ndizisilu zawanthu😅😅

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 2 місяці тому

    A opposition machende awo zoti amalawi akuvutika sakusamala what kinds of opposition parties are these , atikwana kwambiri

  • @GeraldChisokeza-er5cf
    @GeraldChisokeza-er5cf 2 місяці тому

    Auzen adziwe

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    Amalawi apapa a opposition,'wa asatipusise coz dzikoli ndilathu, tiyeni tipange mademo ochosa akhwakhwananda amenewa m'boma mosogozedwa ndi Bon Kalindo, President wathu wa amphawi basii, opposition leaders are scared to be jailed and killed

  • @FWhite-w3l
    @FWhite-w3l 2 місяці тому +1

    Opposition yonse ndiyausilu mwina akuziwana mpatumbo pa opposition

  • @KennedyKanyama-ce8lb
    @KennedyKanyama-ce8lb 2 місяці тому

    Zaoneselatu kuti DPP yatha. Udf yatha. UTM yatha. Afford yatha. Nanga ichi ndichani? Zoona awawa mmene akudzudzira zikoli alipo angawavotere?

  • @YamieManda
    @YamieManda 2 місяці тому

    Wasowa chonena mkulu iwe ,,athu amawona wokha zothandiza osati zopanda tsogolo zanuzo.mcp mpakanampakana bacedwani mkutukwana kwanuko

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    😂😂😂😂😂😂 boma ilooo , mcp oyeeeeeee 😂😂😂😂😂, mumkatitu mukufuna boma la anyamata oganiza Booo kkkkkkkkkkk chakwela mukati ndi m'busa owopa MULUNGU 😂😂😂, lero ndebwa?, muchiwonatu inuu simunati , ife tinaziona kale nkhanza zawo zinatikwana kale mdzaka zimenezooo, mchifukwa chake timasamza evrytime tikangomva za dzina la chikangawa mcp crocodile dancer party 😂😂😂😂😂, ine lero ndiye ndingoti chakwela yemweyoo , kuti waa waa waa 😂😂😂

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi 2 місяці тому

    Tivomeleze kuti ngati osapanga n'gwilizano ndithu sitingaboole PA Chakwera ochenjera PA sosho midiya shiti

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 2 місяці тому

    Koma akudziwa ndalama zomwe chakwela ndi mcp yakeyo awononga chifukwa cha mpando waung'ono ngati umenewu ? Mcp ikufuna anthu aziyesa ngati akukondedwa. Chipani chanzeru sichingaononge ndalama zambilimbili chifukwa cha zinthu zofoila.

  • @ishmaelsiffah9900
    @ishmaelsiffah9900 2 місяці тому

    Amene amaimila ku Mwasa ward pa ticket ya DPP ndimunthu osowa khalidwe anthu sanamuvotele chifukwa chachimenecho,iye uja ndiwaguru la Bam Bam lija limasokoneza pam baluku limamenya anthu lija pomwe uyu anaimila mcp ndimunthu wabwino kwambiri,fact yankhani imenei ndi imeneyo basi,tikamakamba za Bam Bam ndi guru la anthu lomwe linapangidwa kuchokera ku dzina la film ina yake ya anthu osokoneza aku Mexico ena amati B13,anthu amenewa ngati mukukumbukira mmbuyo muja ndi aja anamenya ndikubvula a UTM aja ameneo

  • @sinethembangubo3718
    @sinethembangubo3718 2 місяці тому

    The DC bon kalindo avery dangerous child

  • @NelsonNdeke
    @NelsonNdeke 2 місяці тому

    Opposition is sleeping indeed ali ziiiii!

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 місяці тому

    Or zipani zonse zitasokhana sizingawinen inuyo mcp mmangodananayo chabe ndiye ubwino wake mulungu samakhala kwanu mbuzi inu simunati mulila shupit

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    Opposition leaders osapita kukhoti kukatenga chiletso choti achikangawa akuphwanya malamulo oyendetsela zisankho, nrb sikupanga bwino ndi mabungwe ena ambiri, instead mwangopindilila michila yanuyo mma trouser mwanu , mukufuna kuti amalawi atani komanso mukufuna kuti amalawi awomboledwe kumoto wachikangawu ndindaniiii?

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 2 місяці тому

    Eya zivoterani MCP ikumalizani kuku phani Nonse Wanthu opanda mzeru

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    Opposition leaders osamva malangizo awanthu yamtundu wanji?, eish!, bon Kalindo, mtanyiwa alongside bakili muluzi tv akutivumbulusila zinsinsi zomwe asatanic'wa akuchita pobela zisankho , koma inuyo a opposition mwangoti machende phwii osatengapo action iliyonse y?, i think muli gulu limodzi ndila chikangawa inuu and musamawapusise amalawi agalu 🐕🐕🐕 osusa inu, chikangawa yomweyo galu iwee 🐕🐕🐕

  • @JonaZimpita
    @JonaZimpita 2 місяці тому

    Chistilu uyu More Fare MCP wina afune asafune 2030 walila chokweza B,K

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    Bon Kalindo please, pangani mademo oti tichotse guleyu pampando wa u President, munamulemba ntchito ndinu ndipo wayesedwa mayeso and wapezeka kuti walephela , mabwana akefe tikuti achoke basi , awoposition anamachende 😂😂😂

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 місяці тому

    Ndipo inuyo okonda zotukwananu mukhaula mulimbana ndi ma bgy

  • @MathiasJoseph-xv1hj
    @MathiasJoseph-xv1hj 2 місяці тому

    Uwundiuthenga waukulu ku opposition sure

  • @EusébioLucianoGaiondo
    @EusébioLucianoGaiondo 2 місяці тому +1

    Bon kalindo 🔥🇲🇿

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    Please bon Kalindo, mademo omwe mupangise akhale ochosela chakwela satana ameneyu pampando, atmalizatu amalawife satana ameneyu 👺👹👿☻

  • @PatrickMkonongo
    @PatrickMkonongo 2 місяці тому

    🎉

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 2 місяці тому

    Adad mukugonatu

  • @IshmailiMkoz
    @IshmailiMkoz 2 місяці тому

    Mmera poyamba

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 місяці тому

    Akulu akulu timanena nthawi zonse sosho midia singasinthe kanthu ndale ndi pagiraundi inu mmakhala bze kupeka maboza pano azanu alibze pa galaund mungawine? taonani kularonga anakumenyani 3 zilo koma simabva mukhaula ndipo simunati mcp simungaichose boma

  • @HastingsNkhoma-q9c
    @HastingsNkhoma-q9c 2 місяці тому

    Zoona a opposition akugona

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 місяці тому

    Ndpo ndi zoona atsogoleri athu akugona kwambiri kupanga masewera mcp ikhoza kutenga boma, ndpo akatenga boma tizavutika kwambiri, kulankhura ndye anthu mukulankhura km atsogoleri sakumva

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 місяці тому

    Koma tipephele mulungu asithe nyengo ya ziko lathu posawelengela kuti zikoli ndi la Chakwela koma mulungu azilemekeze yekha kusitha ziko lathu

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 2 місяці тому

    Mau oti “zinthu sizikuenda” is not a political strategy pitani mukawafunse anzanu ku Zimbabwe 🇿🇼…..ndaletu ndikufikira anthu Pa ground osati Pa social media 🤣🤣mulira simunati

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r 2 місяці тому

      Kuyankhula motumbwa chonchi ndikomwe kudachotsetsa DPP mu boma. President wakoyo is even very far from the ground pomwe ukupanenapo. Mutha kuyankhula motumbwa chonchi chifukwa nzachidziwikile kuti chaka cha mawa mukuzalowa mboma mwachinyengo. Koma choti udziwe nchokuti muzachoka mboma muli ndi nkhope zamanyazi kwambili

    • @ziyamporoma377
      @ziyamporoma377 2 місяці тому

      @@Lee-lee-w1rAnkolo mwanvako olo mfundo imodzi from opposition other than kungoti ‘sizikuenda’?
      Akakhala ma activist ndekumangotukwa daily. Boma ndilomweli basi mufune musafune 🤣

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 місяці тому

    Zomvesa chisoni tu kwambiri esh

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 2 місяці тому

    The D.C. ❤❤❤

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw 2 місяці тому +1

    Mangochi athu ake alibe selu

  • @YoungScott-p7e
    @YoungScott-p7e 2 місяці тому +1

    Anthu aku opposition ndi opusa kwambiri

  • @AlbertMatola-u9r
    @AlbertMatola-u9r 2 місяці тому

    Zosusa zomwezo 😂😂😂

  • @Chiso2019
    @Chiso2019 2 місяці тому

    Ndipo zoona zikunenedwa apa.....ndi mcp woyeeeeeeee .....kugona too much ku opposition

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 2 місяці тому

    Zoona mangochi ndichiani chachika anthunu bwanji nzeru mulibe mukunyengedwa ni deya kodi kumpoto anachita kubera koma inuyo a DPP, UDF, AFORD anthu opanda chikondi chisoni ni wanthu mwandiliza kwambiri mukukonda ndalama osakonda anthu mwatikhumudwitsa kwambiri

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 2 місяці тому

    Zikupwetekesan Mutu izi zitayen

  • @PhilipMatolino
    @PhilipMatolino 2 місяці тому

    The DC zoona ? Apo ndie akubeladi ansaaaa!

  • @chrisgremu740
    @chrisgremu740 2 місяці тому

    Vuto anthunu MCP simuidziwaa

  • @chrisgremu740
    @chrisgremu740 2 місяці тому

    Munyeraaaa

  • @MatthewLameck
    @MatthewLameck 2 місяці тому

    MCP boma ilo 2030 wooooo💃💃💃

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 2 місяці тому +1

      Government less chikangawa Idiot 😡, tikuchotsani b4 2025 asatana akupha inuu👺👹👿☻

    • @DeenesNurudMeke
      @DeenesNurudMeke 2 місяці тому +1

      Palibe zimenezo mukunama

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r 2 місяці тому

      Ndipotu zoti muzawina sizachilendo chifukwa tikudziwa muzapanga chinyengo komatu muzaphana agalu inu

  • @FrancisMakuluni
    @FrancisMakuluni 2 місяці тому

    Ndipo live

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 2 місяці тому

    Abela mcp koma