Sameer Suleman - Kwake kwatha

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 5 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 14

  • @GeofreyMkhala
    @GeofreyMkhala 4 дні тому +1

    Suleman . Msalowese ndale kugozi you guys ndinu malida dziko mkusankha mlibe chibalale mmalo mogwilizana kukhoza dziko basi kukanganda

    • @YamikaniMsosa
      @YamikaniMsosa 3 дні тому

      @@GeofreyMkhala mmmm kod Mesa aboma ndi amene anayamba kuzisara

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 3 дні тому

    Suleman kwake sikunathe ndipo kungopha suleman ziko lisokonekela .....agalu awa komatu achoka ....

  • @EdwardPatel-f1g
    @EdwardPatel-f1g 3 дні тому +1

    Mukusogosa mau onena kut suleman kwake kwatha chifukwa chani? Musamasogose mau a negative. Suleman kwake sikunathe, in Jesus name, Kaya in Allah name kaya

  • @AustinNkhula-j6y
    @AustinNkhula-j6y 4 дні тому +4

    Iwe talembanso ma sms akowo sakumvekatu ndiwe mchewa zoti ife tikuwalila anthu ameneaja

  • @Lamyasmoyo
    @Lamyasmoyo 2 дні тому

    Ndiye nkhani NDI headline zikusiyana bwanji mufuna tive ziti

  • @GeofreyMkhala
    @GeofreyMkhala 4 дні тому +2

    Azibale any akuvutika pamozi ndi amalawi pamodzi mmalo MOTi tipange bwanji basi nkhani imodzimodzi kunyankhula everyday

  • @CrossleySingo
    @CrossleySingo 3 дні тому +1

    UYU NDI MUTHU OLIMBA MTIMA INE NDALE AYI KOMA UYU SAMANENA OLO KUNYOZA MUTHU ZOSE AKUNENA NDI ZOONA

  • @APOSTLEBJ-tc5fp
    @APOSTLEBJ-tc5fp 3 дні тому +1

    Penapake mukamalemba ma headline anuwa chonde muzilemba zomveka bwino.mukati Suleman kwake kwatha mukuphunzitsapo chani anthu?.
    Taziyetsetsani kulemba ngati munapitako ku school

    • @LetshaChirwa
      @LetshaChirwa 3 дні тому

      Ndipo zoona Kaya ndi umbuli ma headlines nthaw zambiri amasephana ndi nkhan

  • @MemoryMteketi
    @MemoryMteketi 4 дні тому

    Chilima wanga ine Ambuye

  • @LukaAfromad
    @LukaAfromad 4 дні тому +1

    Uyu ndie munthu wachilungamo

  • @malcolmmacadam6270
    @malcolmmacadam6270 3 дні тому +1

    Amwene, nkhanzanzo ndiye zili mbali zonse, dpp idapha issa njaunju ndi anthu ambiri, ndiye nonse ndi akupha ngati mukutchula anzanu, komanso ngozi ya ndege ukunama iwe, siifanana ndi ngozi ya galimoto, ngozi ya ndege imakhala ndi impact yaikulu kuposa galimoto, just needs to use common sense basi

    • @BrendaJailosi
      @BrendaJailosi 3 дні тому

      Ok onse ndiakupha km pano zinthu zili worse kuphatikiza pakuphanapo mmmmm Mulungu alowelerepo basi