UTM WHISTLE STOPS LIVE TODAY - FREDOKISS KALUA WAIYAMBA KAMPENI NDIKUSAMBWADZA MCP LERO KU CHILOBWE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 10 лют 2025
  • UTM WHISTLE STOPS LIVE TODAY - FREDOKISS KALUA WAIYAMBA KAMPENI NDIKUSAMBWADZA MCP LERO KU CHILOBWE

КОМЕНТАРІ • 14

  • @HildaMbizi
    @HildaMbizi 4 дні тому

    Mwa utm ndimakondwera

  • @EmmanuelSimthole
    @EmmanuelSimthole 5 днів тому +1

    Maso kunyoza mtima kupepusa utm my vote

  • @MikeChimombo-n6w
    @MikeChimombo-n6w 5 днів тому +2

    A malawi tazuzika ndi dpp and mcp eeish anthu akuba,aboza and ankhaza now we want new goverment and UTM with DK 2025 bomaaaa🔥🔥🔥

  • @JanePhiri-q8n
    @JanePhiri-q8n 5 днів тому +2

    Mmmmm inu ine ndinali komweko pa zioni market po mmm nfundo palibe adad adad adutsa achepa awa

    • @GoodluckVithumbiko
      @GoodluckVithumbiko 19 годин тому

      poti inuyo mrindifundo yanji yimene munapanga panthawi yanu zazii nose mcp ndi inuso tiwone zina

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 19 годин тому

    koma mziwe kuti murungu sataya wake tiwona pa 16. September murungu zimene akupanga amene iweyo ukumusisa ndamene akumukweza ambuye tiyendereni

  • @AcctyhBuno
    @AcctyhBuno 5 днів тому +2

    Chilima sindizamuiwala anali munthu woipa ntima wadyela mavuto onse tikukumananawo panowa ntchifukwa cha chilima wokumbila nzake dzenji amagwelamo yekha

  • @LovelyArcade-gm5hh
    @LovelyArcade-gm5hh 5 днів тому

    Azigogo ayi nzeru zinawathela musaiwale pajatu anachosedwa pampando kamba kowononga,za dad muiwale masansi sadyedwaso

  • @EricNthiramanja-l1i
    @EricNthiramanja-l1i 5 днів тому

    Antchana ndi team ya utm mutiendere kwachesombakusotu

  • @LysonMkomadzinja
    @LysonMkomadzinja 5 днів тому

    Talengezani mwachangu kuti utm,DPP,afford and udf tikufuna inuyo akabambe to be running mate then boma basi only Mawis hope Kabambe

  • @LysonMkomadzinja
    @LysonMkomadzinja 5 днів тому

    Alawi yose palibe chikuyenda olo kukasiya kwenikweniko

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 5 днів тому

    Kulibe mfundo

  • @McdonaldChirwa
    @McdonaldChirwa 5 днів тому

    Drama chabe iyi simungatenge Boma ndi anthu ochepawa