We need a constructive Malawi with its reservoirs from all sectors of production to the users and benefiters of the product effectively.Thank you elder Kalindo, Malawi needs you too,rebel, rebel, rebel.Big up 🎉
The DC kuwang'alura mosawopa musatopa mopanda mantha MCP ikuziona ngati iyo ndimadolo koma nthawi Ina azaoneka opusa 2025 sipatali masiku akuthera kuchiseko awa the DC Boooon Kalindo president wa aphawi 🔥🔥🔥🔥❤❤❤❤
Andale ena tabadwa ali andale mpaka zaka 40 akungosintha zipani😂 mm safuna kungokhala osadyera amphawi,(Taxi Payers Money),akutipweteka anthu amenewa kwambiri..

This thing of dancing when the President or MP is having a meeting eish, is of old fashion. Wake up my country Malawi 😢😢
Amandipweteketsa mtima n
Amandipweteketsa mtimadi bwanj? Anthu akuwazunza mkuwamavinilanso
Speechless
Ur true DC
Uyu bon kalindo akufuna dpp kuti azizamuthamangisa ndizi kwanje
Amene alowa mcp ndi ufuru wawo wo joina chipani chomwe akuchifuna
Thé Dc Bon kalindo number one ❤
Kalindo your are a hero
The DC
The DC kuwang'alura mosawopa musatopa mopanda mantha MCP ikuziona ngati iyo ndimadolo koma nthawi Ina azaoneka opusa 2025 sipatali masiku akuthera kuchiseko awa the DC Boooon Kalindo president wa aphawi 🔥🔥🔥🔥❤❤❤❤
That's reality speech
Andale ena tabadwa ali andale mpaka zaka 40 akungosintha zipani😂 mm safuna kungokhala osadyera amphawi,(Taxi Payers Money),akutipweteka anthu amenewa kwambiri..
😙😙😙😙😭😭😭😭
Dancing like that, just to get 2pin Mk 😂 silly men and women and children..
The DC Mwana owophsa kwambiri pangolini
Andale ena pafupifupi zipano zonse analowapo
The DC umakwana ...asiye apite basi kunja kuli dzuwa uku
Opposition yowola Sheikh Mtenje mpaka kulowa mcp
A opposition akugona kwambiri DC amanena zoona nthawi zonse
Awawa nd akatundu✊✊✊
Awuzeni kuti zibwanazo kwawo komko
Speech yabh the Dc
Zovina ku nsonkhanozi aaaaaa sindimaziona ubwino ai chifukwa ndikhulupilira ndi malawi amapanga zimenezi.
The Dc
Agalu a MCP tatopa nawo
Pangolin iwe
Komans kut abele sazawina 2025 inshaallah
Kkkk ma computer akalekale
😂😂
The DC