A Chimwendo Banda Mphamvu Zoyakhula Za Report La Biyeni Mwazitenga Kuti? - Sizwe

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 вер 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Sizwe from Ntcheu seems to have a few issues to address with Honourable Richard Chimwendo Banda, Minister of Local Government, Unity, and Culture, regarding his remarks at a political rally about the air crash that claimed the life of the late Vice President Dr. Saulos Klaus Chilima.
    Pa Nyasa Voicebox, Sizwe wa ku Ntcheu akuoneka kuti ali ndi mfundo zingapo zoti akambirane ndi nduna ya maboma ang'ono, mgwirizano, ndi chikhalidwe, a Richard Chimwendo Banda, pa zomwe ananena pa msonkhano wa ndale wokhudza ngozi ya ndege yomwe idapha malemu Vice. President Dr. Saulos Klaus Chilima.

КОМЕНТАРІ • 84

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 20 годин тому +5

    Mwafusa bwin a mfumu adatiphera achilima munthu wosalakwa anthu awa chikangawa mwa ndifusira mfuso la bwino zedi, alira bwanji abiyeni oti anapha yekha chikangawa Mulungu wathu awakatha awa, mfumu zikomo kwambiri Ambuye. Azikusamalani ❤

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 8 годин тому +2

    That's the spirit we need in our warm heart of Malawi 💪💪

  • @peternashyo9850
    @peternashyo9850 20 годин тому +4

    Mau amphamvu, long live Sizwe

  • @LousierBombeya
    @LousierBombeya 7 годин тому +2

    Osaopa osafooka osagonja malawi dzuka rest well SKC

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 20 годин тому +2

    We are with you

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 45 хвилин тому

    Ine ndikusegula radio FM Ku Malawi ndipo dzina la radio yanga ndi CHIKANGAWA RADIO FM❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q 19 годин тому +3

    Imfa ya Biyeni ikundiwawabe mpaka lero honestly speaking ife angoni moyo ukutiwawa za imfa ya Biyeni misozi yathu ikutsikira mimba

  • @JulietLizziePhiri
    @JulietLizziePhiri 21 годину тому +5

    Ndipo nde wafikapotu naye uyu😮

  • @BilalAliyah-k1f
    @BilalAliyah-k1f 20 годин тому +4

    Zikomo kwambili amfumu potiyakhulira

  • @RoseThindwa
    @RoseThindwa 21 годину тому +3

    Zaona Malawians go konko parliament ayamba kutitola anthuwa alibe chisoni

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 20 годин тому +2

    Achimwendo ndigulu kwakupha chilima kupanda chilima anali ndani a MCP aaa amalawi chakwela ndiamena anapha VP uchitsilu wa MCP akuwona amalawi tikadagonabe ngati 1958 aaa ino 2024 tu

  • @emmanuelchirwa3420
    @emmanuelchirwa3420 8 годин тому

    More fire 🔥🔥🔥🔥🔥 big man mkondo wangoni

  • @Laksamupazila
    @Laksamupazila 19 годин тому

    G0d bless Malawi to all Malawians for the voicecall Friday

  • @DavidKanyemba-n2s
    @DavidKanyemba-n2s 19 годин тому +1

    Aluta continua angoni
    Biyeni anatiphera osalakwa😢

  • @isaackinod1256
    @isaackinod1256 19 годин тому +1

    Isvuke madoda 😊

  • @jennyx6914
    @jennyx6914 21 годину тому +2

    chakwera mwina agwidwa ku malawi koma ngati anathawisa prophet bushiri ku south africa anthu onse kuzunfulira mutu ndiye mu malawi kuzabera mavoti akhoza kubera nfati tiputse

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 21 годину тому +2

    ofunika kusalaza zuma zawo akaluza zapiteni ku Zambia sapanga zopusa

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 21 годину тому +4

    Zauchisilu kodi waletsa kuti anthu asamalire or kutengela za ndale pa maliridwe amalirowa iye adakambapo zalipoti anthu enanu ndizisilu kwambiri nkhani imeneyo or pa court chimwendo zangaluze nkhani imeneyo muvetse bwino

    • @user-zj1xx1ic2m
      @user-zj1xx1ic2m 20 годин тому +1

      Inu palibe mukuchidziwa court amalidziwa ndi MA criminal, iwe firstonder court umalidziwa iwe? Popeza MA judge a Kumalawi ndi a chikangawa party nde nde chimfupi mwendo wakoyo akhoza kuwina, koma MA judge amene analipo mbuyomu chimwendo wakoyo sangalimbe ndiponso ndiwe galu + Mr chikangawa wakoyo mwana wa hule pantumbo pakonso😢😢😢

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 19 годин тому

      @@user-zj1xx1ic2m iweso palibe ukuziwa chifukwa zomwe adalakhura chimwendo sizimezo

    • @wisdomsadyalunda2001
      @wisdomsadyalunda2001 19 годин тому +1

      Chipwili Cha munthu ngati iwe you don't even know what chimwendo said koma busy kulesa.
      Ma bundles opasidwa omwea....

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 10 годин тому

      @@wisdomsadyalunda2001 kulesa chani simunave zomwe adalakhula vuto ndilimenero kulira lirani koma osalowesapo Ndale ndiye Pali vuto palibe ngati muli adolo osapita kumademo bwanji

  • @anifoiuene6301
    @anifoiuene6301 18 годин тому +2

    Sizwe tili nanu limodzi dzikoli ndi lathu ili si la chakwera yekha kapena chimwendo yekha ayi tikakumana konko ku citycenter

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 22 години тому +2

    Ziko ili mwaliwononga mu zaka zochepa .....amalawi tili pamavuto koma mulungu atithandize kuti agalu awa achoke basi anthu osamva zonena za anthu chifukwa cha ndalama zokuba

  • @maxwellmashon4897
    @maxwellmashon4897 19 годин тому +1

    Chimwendo akuzitenga ngati ndiozindikira kwambiri muno mu dziko lathu la Malawi zoti akumatuma anthu kumapha akuona ngati sitikuona

  • @ShukuraniTonex
    @ShukuraniTonex 18 годин тому +1

    ✊️✊️✊️✊️

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 21 годину тому +2

    Apanenidi amenewa kuwapha anzawo ngati dzinyama zamanyazi ndithu

  • @mbelengamavuto2517
    @mbelengamavuto2517 20 годин тому +1

    Zimvele mtolo chimwendo ndizimenezo

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 21 годину тому +2

    Thawi kachitsiru wina alira 😂okutetezani ndiamene akuzakutapani😂

  • @trifoniachilunda6263
    @trifoniachilunda6263 21 годину тому +2

    Afumu mwayañkhula bwino

  • @PetrusTlhokwane
    @PetrusTlhokwane 19 годин тому +1

    Tiyeni tiyeni tonse lachisanulo a Malawi tigwirizane Chakwela ndimunthu oyipa

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 19 годин тому +1

    Sorry about Malawi zovuta kwambili

  • @LeonardChinomba
    @LeonardChinomba 19 годин тому +1

    Chimwendo banda nkhani ndi imeneyo sindisowanso kukuthanthauzila yalankhulidwa mu chichewa komanso momveka bwino ungoyamba kulongezelatu uthawe

  • @wisdomsadyalunda2001
    @wisdomsadyalunda2001 19 годин тому +1

    Inu mukulandira bundle yoti muzikapamba zabwino za athu akuphawa musamale heavy..
    My warning tishala limozi mmakonbo so mwachulusa kuwerewesha vuduka mitu apa anyokopola muchito so...

  • @innocentwingolo8724
    @innocentwingolo8724 19 годин тому +1

    Apapa Angoni ayambapo. Wathuyo sangapite chomcho

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera 20 годин тому +1

    Chimwendo Banda alibe khalidwe.

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 17 годин тому +1

    Chimwendo ndi MCP ndiyakupha

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis 11 хвилин тому

    ARichard chimwendo Banda. Mutu wong'alukawo.

  • @WysonChilonga
    @WysonChilonga 14 годин тому +1

    Mwayankhula bwino zedi,uyutu atiuze bwino ndithu

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 20 годин тому +2

    Tikakupelekezani

  • @NgeyasjuWadeya
    @NgeyasjuWadeya 21 годину тому +1

    Akuluwatu awuze mtundu wa Malawi amene adawauza kuti ndege yadzadza mulibe Malo ndindani? Kapena amkadziwapo kathu? Adziwe ichi amalawitu siopusa ndipo zoti akusakaza ndalama zathu tikudziwa ndipo munya mukatuluka m'boma atambwali inu

  • @BettieKamija
    @BettieKamija 20 годин тому +1

    Ndipo musawasiye aigiputo amenewa

  • @Miracle-o1k
    @Miracle-o1k 20 годин тому +1

    Chitsiru nachimutu ameneyu

  • @GiftMathewe-fr3kn
    @GiftMathewe-fr3kn 19 годин тому +1

    Osawopa

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere 19 годин тому +1

    Anthu enanu ndinu zisiru pakqganizidwe vuto mulipo ambiri Amene mukutenga maliro aChilima ngati chida chotchukila pandale

  • @LuskaMoses
    @LuskaMoses 20 годин тому +1

    Kachimutuyu amangidwe basi chimwendo banda oipa nkhope yomwe mutu omwe

  • @davidkadyakapita8836
    @davidkadyakapita8836 20 годин тому +1

    Chakwera unya uwona .

  • @AbunthiMtambo
    @AbunthiMtambo 9 годин тому

    Asambeni sonke Friday Sizwe ukhulumile😂

  • @wilhelmellington569
    @wilhelmellington569 18 годин тому +1

    Lewis Maria Allen Karen Martinez Margaret

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i 5 годин тому

    Be strong 💪 guys more fire 🔥 don't give up be strong again 💪 🙏 this president is nonsense 😑 🙄

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb 20 годин тому +1

    Olo galimoto yavuto siyenda pansewu evn number ngati palibe imafusidwa y.what more ndege

  • @JulianaMkonda-k2n
    @JulianaMkonda-k2n 18 годин тому +1

    Kukamwa ngati adya manyi

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb 20 годин тому +1

    Gokomko .komanso anaziwa bwanji kuti yagwera ncthire ndani mzumzu yeseunja .aphe tonse nyero zawo

  • @TottiesJackie
    @TottiesJackie 10 годин тому

    Finye ameneyu Chimwendo watikwana ndi nzake chikangawa,was hoping kupanga ma demo akamabwela ku America azapeze anzake atenga mpando

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 19 годин тому +1

    Kod athu inu tupere zananene kom 2020 ija anakuusatu wosafa

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev 21 годину тому +1

    Ndipo osaloradi tiyeni tigwilane manja sua napankholoyu achokedi

  • @wonganimwase9881
    @wonganimwase9881 4 години тому

    Chakwera wathawira ku UNGA

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere 19 годин тому +1

    Ulindichani kuti Anthu akusake kapolo ngati iwe olakwa ndiyemwe wakupasa phoneyo galu iwe

    • @Yahiya-wm8nd
      @Yahiya-wm8nd 8 годин тому

      chisulu ndi iweyo ine sindine ngoni koma ndiwe opusa kwabasi

  • @user-pe8dh1ks1y
    @user-pe8dh1ks1y 6 годин тому

    Kuyankhula kukufunika nkumeneko , osaiwara kupanga action

  • @YamikanChirwa-s1n
    @YamikanChirwa-s1n 21 годину тому +1

    Gokonko

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal 10 годин тому

    A MCP la 40lakwanila pa chilima mwapha olakwika muziwona ndipo afinyidwe amenewa akutiwona ngati amalawi zitsilu

  • @cynthiandekhakatundu6890
    @cynthiandekhakatundu6890 7 годин тому

    Chimwendo umve uliliko ... Biyeni sanali wakwanu .. 5 days

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 6 годин тому

    Imfa yachilima ikuwawa ndipo Amalawi nose mukulimbikisa kuti chilungamo chidziwike

  • @DanChiwaya
    @DanChiwaya 12 годин тому

    Amva kuwawa amenewatu Friday sikale

  • @EdithDuncan-s7o
    @EdithDuncan-s7o 20 годин тому +1

    .

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 7 годин тому

    Ndipo wokoma awa

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 22 години тому +2

    Munthuyi ndichisilu akuti akufuna kusangalasa bwana wake chakwera ......zisilu zokhazokha .....munapha chilima ndipo ndizoona .....boma la zisilu zokhazokha

  • @MveraNambala
    @MveraNambala 11 годин тому

    Ifa ikutipweka ya chilima adafelanji bhiyen.

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g 8 годин тому

    AMALAWI TIYENI TIDZUKE CHILIMA OLO ADALI NGONI KOMA ADALI VP WATHU WAMALAWI AMCP MWAZIPUTATU UWUWU NDIY MOTO UYAKE MALAWI NDIPO NDEGE KUGWA KUMVURA ANTHU ZOMVALA , AAAAAA AI TILI NDIMAFUTSO CHILIMA KUFA KOMA CHAKWERA OLO OSASUTHIKA NGAT MZAKE YEMWE ADAMULOWESA M,BOMA. MCP 31YRS MULI KUNJA KWAM,BOMA ZANU KUKULOWESANI , M,BOMA KOMA ZOONA CHIFUKWA CHAMAUDINDO KUMUPHA ZANU ACHAKWERA , MWAPANGA MISTECK ZEDI. IYIYI YOKHA IKUMVUTISANI MIZIM YAKWIYA EEEEEEH ACHIMWENDO NANU MUTU ULI PHWIIII NGAT FUWA LAPAUKWATI UZIONAT MUTU KUKULA CHONCHO KOMA OPANDA MZERU. NDIPO NO 1 KUFA UKHALE IWEYO WAMUTU NGAT FUWA LAPAUKWATIWE CHIMWENDO ,CHILIMA MUDAMULAKWIRA , ADALAKWANJI?

  • @AngelaMphinji
    @AngelaMphinji 6 годин тому

    Kusakhaledi. Kukulirana. Mitima. Azipani.. Zichepeseni. Gwirizanani. Muwombole. Amalawi. Chonde!!!!!!UTM. Chonde. Zichepeseni. Join. DPP. UDF. AFORD.. Please.!! Mayi. Joice. Banda.and. Your party please. Join. Ngwirizanowu. Ombolani. Malawi

  • @LeoLongwe
    @LeoLongwe 10 годин тому

    Chimwendo mutuwo umamulemela ameneyi

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe 4 години тому

    Koma abalee akuti tisamulirw biyeni koma tilire chilima ?nzoona zimenezo?ambuye amuyendere munthu ameneyu

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 8 годин тому

    Chimwendo Banda ndikanakonda atafufudzidwa bwino bwino apo biii. Tikhala ndi mafunso ambiri osayankhidwa mu mitima yathu. Chinaletsa iye kukwera nawo ndege ija ndani????? Pamene malo analimo ambiri mbiri mu ndeve muja. Mmmmmmmh munatipweteka anthu inu.

  • @MveraNambala
    @MveraNambala 11 годин тому

    Chimwendo chimutu cha chikulucho mutu wopotoka

  • @gladysmanthimba7851
    @gladysmanthimba7851 12 годин тому

    Tili nanu limodzi angoni

  • @JoyceBanda-k8t
    @JoyceBanda-k8t 10 годин тому

    M

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere 19 годин тому +1

    Mwasanduka kukhala zisiru kenako mupenga chifukwa Munthu or Anthu omwe mukulimbana nawowo sakukuynkhani mulibe manyazi? Zisiru inu

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i 21 годину тому +1

    Kwachema tiyeni tose tigwirsne manja

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 6 годин тому

    Mizimu ya anthu 9 songakhale chete
    Akuyankhulatu si anthuwa ai
    Koma mizimu ikulowa mwa anthuwa mkumawayankhulitsa
    Anthu ajatu adaksli.kuchikangawa
    Chomwe akuopela chakwela kukaona kunagwela ndege mchiya???
    ????
    Achakwera asavukatu chaka chake mchino

  • @AyandaPhungula-bg9ql
    @AyandaPhungula-bg9ql 10 годин тому

    Asambeni muwumodzi muli mphanvu Malawi dzuka dzuka osawopa