Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Excellent comedy 👏👏 keep it up 👍 Pastor Mulelemba you're the best , many thanks to everyone in Mdyangu comedy..
Kkkkkkk abussa murerember advanced nzima ozaphembera et njara 🎉
Mukuchulutsa nthawi kwa anthu ena bwanji episode yonse sikuti izitha nd modx modx yemweyo ai much love to mr shokoshoko
Mdyangu ndi More FIRE 🔥.A Mulelemba umbombo mpaka kubisa Nsima 😂😂😂😂😂😂.
Kuli nepman wachibwibwi franko Tifan alikuti mungokakamiza mulelemba sikuti samabhebhesa komabe enawo aganizireni
I like mrs sasoka her heart is so sweet 😘
Kkkkkkk km mulelemb 😂😂😂
Mwamugula mkhwaniyo nde mwamuwelusatu😂😂😂😂😂😂
❤ u guys mukuitha keep it up
Akuti Munda mwa eden munja unaoko nyama........Koma amu mulelemba 😂😂😂😂😂😂😂
Koma Mlelemba mukumupatsa nthawi yochuluka.
You are more than best mmm awesome acting
Iyi yokha sinabebe 😂
Sukunama aaa
Pangan yanu yobebayo tione mxiii😂😂
NDI ZOONA
Mai shokoshoko mumandiwaza heavy😂😂
Onse umu ndima actor ndi ma actress ❤❤
Mlelemba pena muzimuchepetserako nthawi,kkkkklkkk
MUKUCHEPETSA FIRE GUYS , MUZIWILIKIZA ACTIONS NOT DISCURS. MUZIPANGA ZAKUTI ANTHU ONSE A NKOMEDY IMENEYI ONEKA MMALO MOWONETSA ANTHU AMODZIMODZI MOWILIKIZA. MUMAKWANA NDIKUWONERA KUCHOKERA KUNO KU MOZAMBIQUI.
You give mlelemba more time... Chepesaniko..
Amulelemba kusuka km mukuti ndinu apastor😂😂😂😂😂
Mayi shokoshoko mumandiwaza heavy ..banja la sasoka limandisangalatsa heavy..ma Gabi ndi amunawo tsopano kubisa nsima yankhwani 😅😅😅😅😅😅
Mulelemba more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Chikang'a sasoka😂😂😂😂😂
Nsima yamasamba ija munasungabe😂😂😂
😂😂abusa wanji awa
Mulelemba sazatheka akuti ukanankhala ulimi bwedzi mwayamba bwino 😂😂😂
Chepesaniko time Kwa mlelemba amatenga nthawi yayitali plz.
mlelemba palibeso wina mumatisagulusa
Kkkkkkk kma mulelembayo
Sasoka ndi tivane we love 💕 you mix chipwanya Koma wasowa why
Lululuuuuu nkhuyu zokudya gani zakapota nep man gani mutu wakula queen mwana units ndiizo ntchito mulibe mupanga bwanji? Munthu wamulungu kubisa nsima chifukwa chobwera sasoka .
😂😂😂😂 sasoka wathawa Ku barracks 🤣🤣🤣🤣 koma mulelemba wa mwano
Unice koma ndiwabwino akanakhala ma mg1 onse azipanga zimenezo ufiti bwenzi pano kulibe 😂😂😂😂
😂coz amamukonda Gan kwambiri kkkkk
sasoka
Sasoka utijoine basi kumpingo wa Aaron
You are number one
Timakunyadirani koma zomabweleza munthu mmodzi sizisangalasa ai
Sasoka is something else 😂😂😂amazembe chopeleka basi
Ati mmunda mwa Eden wa Adam nd Hava mnaonamo nyama mmene muja 😂😂😂
Sasoka iweyo umakwana I love you Ndi waifi wako❤❤❤❤
Mambo aJu akut mpingo wa Aaron😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Mlelelemba ndi mbambande 😂😂😂😂
Kkkkkkk sasoka mwati mimba zachuluka
Unice waku labour basi yakwana yokha akabelekeno chi elephant ankaneka apongozi ake chija😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Akuti amene mwamugula nkhani amuwelusa. Hahaha
Very nice
Ayi guys mulelemba thawi ikuchuluka chikubeba palibe aaa
chifundo ❤
Beseni ra mwanayo rakuchigayo😂😂
Congratulations guys
Km Mai shokoshoko ndikatundu
Kodi Tiffani yu tiziti akuyamwisa hetiiiii.....
Mulelemba is a good actor, Yes. But u r giving him too much time. Tidzingoonera yekhayo 3/4 of the time?
Pajatu amagawa,,iyiyi Ching'aning'ani, Nepman mulibe,inayo awawa sazaoneka azaoneke ndi enawo
@@lingstonenagoli7729 ayi bodza. Timaonera izi every week. Mulelemba amakhalapo full time
Iyi ndye 0%
Komaso unici kulila kumeneko mwanayo mukabelekadi kkkk
@@raymondchisomo3533 komatu drama 🤣🤣🤣🤣
Mulelemba akuonjezadi plz
Mulelemba akumatenga nthawi yaitali part 2,3 and 4 yekha mukutionongera data iyaaaa iyi yokha ndiye mwapala guys
Ife kukanika kugonatu 😂😂😂😂😂Mdyangu 🔥🔥🔥🔥
Kkkkkkkkk koma Mr shokoshoko dothi lake adatenga liti kkkkkk
Ma minutes akuchepa muonjezele
Lelo mwapemphetako bwinotu kkkk
Koma nsimayo idyedwa aaaa😅😅😅😅 mose nulili ulaliki
Kkkkkk km2 mulelemba upole moto
Mdyangu umativesa kukoma 👊👊
Km nep man adha😂
Munthu wa mulungu kubisa chakudya
Welcome guys 🎉
Sasoka kuno dubai umandiwaza 😅
Nepman akuti mimba za anthu ena zikumuvutisa😂😂😂😂
Komamai chokochoko akamati ndiamisara ndizoonadi zikuoneka zochitika
Koma mukumachebwetsa guys
Amulelemba angosiya kupemphela nanga umbombo wake umeneu kkkkkkkkkk
Muleleba#1
Mdyangu ❤ always 😅
Koma sindi ndi amuna ako ayi zikomo ma gabi😂
Abusa a umbombo mlelemba😂😂
sasoka singing 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Sasoka umatha
Sasokaaaaa ndi dolooo
Muli ndi ma actors komanso actresses ambili sizabwino kumapeleka nthawi yambili kwa munthu mmodzi si tonse timakonda iwowo,, you know what I mean balance up please it's getting boring.
Komatu Mlelemba anakonza
Kkkkkkkk koma mai shokoshoko mmmmmm
Eee koma gani matama onse aja athetsa azikazi eeeh mumawon ngt zophweka kusamala akzi a wili?
Kodii mlelemba ndi mpesa??? ..😂
Kkkkk Kwachema
Ndwachedwa or bwanji
Koma sikuveka mawu kapena vuto ni Fon yangayi
Make ju wachepa thupitu bwanji???
Mulelema amaitha
Mai shokosho ni shock zedi
Mulelemba 🔥
Suyaaa mukuchedwetsaa
❤
Moro fire guyz
Kkkkkkkk koma
Kikkkkkkkkk 😂
Mabanja Ali umu anthu ake amavana kwambili
chimphwanya ndi make chiswe eeee
Koma mai shokoshoko mutitsunga
🤣🤣🤣🤣🔥🔥🔥🔥❤️❤️❤️❤️❤️
Love u gyz ❤❤
Mumakwana nose
Guys but way mukumachedwesa
Kkk kama small
Hello guys inuyo ndi one
Mlelemba amatha
Mulelemba umbombo
Nepia
Excellent comedy 👏👏 keep it up 👍 Pastor Mulelemba you're the best , many thanks to everyone in Mdyangu comedy..
Kkkkkkk abussa murerember advanced nzima ozaphembera et njara 🎉
Mukuchulutsa nthawi kwa anthu ena bwanji episode yonse sikuti izitha nd modx modx yemweyo ai much love to mr shokoshoko
Mdyangu ndi More FIRE 🔥.
A Mulelemba umbombo mpaka kubisa Nsima 😂😂😂😂😂😂.
Kuli nepman wachibwibwi franko Tifan alikuti mungokakamiza mulelemba sikuti samabhebhesa komabe enawo aganizireni
I like mrs sasoka her heart is so sweet 😘
Kkkkkkk km mulelemb 😂😂😂
Mwamugula mkhwaniyo nde mwamuwelusatu😂😂😂😂😂😂
❤ u guys mukuitha keep it up
Akuti Munda mwa eden munja unaoko nyama........Koma amu mulelemba 😂😂😂😂😂😂😂
Koma Mlelemba mukumupatsa nthawi yochuluka.
You are more than best mmm awesome acting
Iyi yokha sinabebe 😂
Sukunama aaa
Pangan yanu yobebayo tione mxiii😂😂
NDI ZOONA
Mai shokoshoko mumandiwaza heavy😂😂
Onse umu ndima actor ndi ma actress ❤❤
Mlelemba pena muzimuchepetserako nthawi,kkkkklkkk
MUKUCHEPETSA FIRE GUYS , MUZIWILIKIZA ACTIONS NOT DISCURS. MUZIPANGA ZAKUTI ANTHU ONSE A NKOMEDY IMENEYI ONEKA MMALO MOWONETSA ANTHU AMODZIMODZI MOWILIKIZA. MUMAKWANA NDIKUWONERA KUCHOKERA KUNO KU MOZAMBIQUI.
You give mlelemba more time... Chepesaniko..
Amulelemba kusuka km mukuti ndinu apastor😂😂😂😂😂
Mayi shokoshoko mumandiwaza heavy ..banja la sasoka limandisangalatsa heavy..ma Gabi ndi amunawo tsopano kubisa nsima yankhwani 😅😅😅😅😅😅
Mulelemba more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Chikang'a sasoka😂😂😂😂😂
Nsima yamasamba ija munasungabe😂😂😂
😂😂abusa wanji awa
Mulelemba sazatheka akuti ukanankhala ulimi bwedzi mwayamba bwino 😂😂😂
Chepesaniko time Kwa mlelemba amatenga nthawi yayitali plz.
mlelemba palibeso wina mumatisagulusa
Kkkkkkk kma mulelembayo
Sasoka ndi tivane we love 💕 you mix chipwanya Koma wasowa why
Lululuuuuu nkhuyu zokudya gani zakapota nep man gani mutu wakula queen mwana units ndiizo ntchito mulibe mupanga bwanji? Munthu wamulungu kubisa nsima chifukwa chobwera sasoka .
😂😂😂😂 sasoka wathawa Ku barracks 🤣🤣🤣🤣 koma mulelemba wa mwano
Unice koma ndiwabwino akanakhala ma mg1 onse azipanga zimenezo ufiti bwenzi pano kulibe 😂😂😂😂
😂coz amamukonda Gan kwambiri kkkkk
sasoka
Sasoka utijoine basi kumpingo wa Aaron
You are number one
Timakunyadirani koma zomabweleza munthu mmodzi sizisangalasa ai
Sasoka is something else 😂😂😂amazembe chopeleka basi
Ati mmunda mwa Eden wa Adam nd Hava mnaonamo nyama mmene muja 😂😂😂
Sasoka iweyo umakwana I love you Ndi waifi wako❤❤❤❤
Mambo aJu akut mpingo wa Aaron😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Mlelelemba ndi mbambande 😂😂😂😂
Kkkkkkk sasoka mwati mimba zachuluka
Unice waku labour basi yakwana yokha akabelekeno chi elephant ankaneka apongozi ake chija😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Akuti amene mwamugula nkhani amuwelusa. Hahaha
Very nice
Ayi guys mulelemba thawi ikuchuluka chikubeba palibe aaa
chifundo ❤
Beseni ra mwanayo rakuchigayo😂😂
Congratulations guys
Km Mai shokoshoko ndikatundu
Kodi Tiffani yu tiziti akuyamwisa hetiiiii.....
Mulelemba is a good actor, Yes. But u r giving him too much time. Tidzingoonera yekhayo 3/4 of the time?
Pajatu amagawa,,iyiyi Ching'aning'ani, Nepman mulibe,inayo awawa sazaoneka azaoneke ndi enawo
@@lingstonenagoli7729 ayi bodza. Timaonera izi every week. Mulelemba amakhalapo full time
Iyi ndye 0%
Komaso unici kulila kumeneko mwanayo mukabelekadi kkkk
@@raymondchisomo3533 komatu drama 🤣🤣🤣🤣
Mulelemba akuonjezadi plz
Mulelemba akumatenga nthawi yaitali part 2,3 and 4 yekha mukutionongera data iyaaaa iyi yokha ndiye mwapala guys
Ife kukanika kugonatu 😂😂😂😂😂
Mdyangu 🔥🔥🔥🔥