A Timothy Mtambo Akufuna U President - Country Man & Uncle

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 30 вер 2024
  • On Nyasa VoiceBox, loyal DPP supporters Country Man and Uncle says that the U-turn Honourouble Timothy Mtambo, Former Minister of National Unity has taken on President Chakwera simply means he wants a crack at the presidency himself.

КОМЕНТАРІ • 14

  • @NicksonMoffat
    @NicksonMoffat 5 місяців тому

    Mtambo u president hahahaha....kape ameneyi kapeeeee. Mwina anthu arelo sadziwa kuti kape ndichani??? Cosefera mowa wa masese ..
    Dzina lake ndi kape...ndiye mtabo galu wa Munthu...wobwera

  • @spargomw
    @spargomw 5 місяців тому

    Mtambo u president? Mtambo adasewera game yovuta kwambiri pa Malawi pano so paibe angamufune. Thumba lomwe adalandira ku MCP latha pano akufunaso ife a Malawi kut atipusitseso? Uchitsiru sagawana so usilu wakowo khala nawo wekha😂😂😂

  • @Blessingsseleman-d4x
    @Blessingsseleman-d4x 5 місяців тому

    Vuto ndi ife amalawi kuchemelrla zilizonse monga a nanenela achakwela timangoyamikila olo tikuziwa kuti akutipusisa muona ena akwela ya amtamboyo

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 5 місяців тому

    Mtambo what is that? Alibe nzelu ndipo aziwe kut choipa chisata mwini coz watizunzisa aMalawi mfiti

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 5 місяців тому

    Mtambo angakhale President, asah! Adaika anthu mu mavuto , akagwele uko chitsilu cha munthu.

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 5 місяців тому +1

    Hahahaha 🤣😂🤣 Mtambo sitidzamukhululukira anatigulitsa ife a Malawi m'manja mwa satana relo tikuzunzika kamba kazibwana zake.

  • @fittachipeta2043
    @fittachipeta2043 5 місяців тому

    Zopanda mutu, sanali Mtambo yekha odana ndi dpp koma a Malawi. Ndiye musatinamizepo apa

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 5 місяців тому

    Akhale presented ku family kwawo angomvotere ndani ngalu wamuthu akanyere uko

    • @spargomw
      @spargomw 5 місяців тому

      Koma ndie akanyeredi iyaaa😂

  • @DonaldPonda-p2q
    @DonaldPonda-p2q 5 місяців тому

    Ndinkhani yomveka ntambo tachuluka omudandaulo chifukwa ndi amene ankalimbikisa uchiganga 😂😂😂

  • @JoycieMbaya
    @JoycieMbaya 5 місяців тому

    Koma ndiye kulakalaka kkkkkk!

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 5 місяців тому

    Kkk akuti ndi chigawenga