BON KALINDO LERO PA 28 JUNE NDETU KULI NKHANI |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 29 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 195

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 3 місяці тому +5

    That's very wonderful massage it's true,tiyeni Malawi tisegule maso

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 3 місяці тому +4

    Ndalama ndi zimenezo koma mzipatala mulibemo mankhwala shame. Bon kalindo Mulungu anasankha inuyo ngati ngelo wamulungu pakati pa dziko amalawi I silute you

  • @EmmanuelThambo
    @EmmanuelThambo 3 місяці тому +21

    Umboni tauwona kuno ku Zomba ma centre ena anatsegulidwa kwa 5 days ajambula kwa masiku awiri masiku enawo amati mafuta anawathera mu magenarators. Keep it up Kalindo we're proud of you.

    • @AmirGeloo
      @AmirGeloo 3 місяці тому +2

      Why translating it English ?

  • @davedavie6211
    @davedavie6211 3 місяці тому +3

    Ukhalise DC Ukutisegula maso

  • @Mpondapromise9
    @Mpondapromise9 3 місяці тому +2

    Big up DC

  • @juntoiman
    @juntoiman 3 місяці тому

    Mr DC timakunyadilani Cox mumatisegula maso and mumaima pachilungamo

  • @ChimwemweWanga
    @ChimwemweWanga 3 місяці тому

    Mumatiimila bro

  • @JoshuaMagodi
    @JoshuaMagodi 3 місяці тому +2

    Umakwana ase

  • @mathewsmhone8953
    @mathewsmhone8953 3 місяці тому

    The last man standing umakwana big man

  • @MacKamanga
    @MacKamanga 3 місяці тому

    Wake up call

  • @FridayMpanga
    @FridayMpanga 3 місяці тому

  • @tariroJinya
    @tariroJinya 3 місяці тому

    Yes tell him he think he is live president

  • @NASP-g7h
    @NASP-g7h 3 місяці тому

    Kom mcp kuwina tizavotaso cz axakhala kuti abela 99

  • @VictorKachulu-y3n
    @VictorKachulu-y3n 3 місяці тому

    Mbuli izi ndi kalindo wanuyo ine ndatulukamo mu DPP ndimaganiza anthu ake ndi a mzeru koma eeeeeeeee kuyambila atsogoleri ndi owatsatila omwe akuyendera magazi a ndale panopa akufesa ndalezo adzakololanso ndale zomwezo

  • @charlesmuwanya7845
    @charlesmuwanya7845 3 місяці тому +9

    Please a Law Society of Malawi ndi zipani za opposition zonse pitani Ku court mukane mfundo yoti opanda National Id asavote.
    Kuchokera pachiyambi timavota polembetsa mu voter register pogwilitsa ntchito passport, driver's licence,Kalata yochokera kwa mfumu etc .
    Every Malawian above the age of 18 is eligible to vote without National ID restrictions.

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember 3 місяці тому +14

    Mwana oopsa kwambiri the DC

  • @AlexPhaloni
    @AlexPhaloni 3 місяці тому +6

    Muthu openga ndiyekhayo angasapote mcp

  • @JosephMichael-x7v
    @JosephMichael-x7v 3 місяці тому +3

    I wish bon kalindo atakhala president ku Malawi

  • @amosphakira7936
    @amosphakira7936 3 місяці тому +2

    Mr kalindo ,mfundo imeneo ndiyoona a kufuna kubela ma vote njira yake imeneo .Ndie ndikofunika kti anthu asavotere through l D chifukwa xisokonexa xithuxi pls.

  • @BhekiMavundla-po2bq
    @BhekiMavundla-po2bq 3 місяці тому +3

    Zonwe akunena Bon Kalindo zokhuza NRB ndivomelezane naye ndithu,kuno Kumangochi zachitika ndipo zikuchitikabe madela ena.Pano anthu ambiri asiyidwa mu masenta olembesela zaunzika kut alephele kukhala ndichipatso chaunzika ndicholinga kut anthu asazavote ambiri kuno kumwela ndipo Ineyo ndimboni ndithu kwa Born Kalindo.Pa anthu okwana 300 pamudzi uliwonse amene alembedwa zaunzika ndi anthu okwana 100 akha basi Kumangochi kuno,ambiri enafe tasiyidwa akuti nthawi yatha sapitiliza koma 2days yokha ndimene akhala akupanga process ya NRB mumasenta onse kumangochi kuno

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 3 місяці тому +4

    Mose atamwalila mulungu anapeleka wina mtsolelli mpaka anakafika ku dziko lamalonjezano ndiye autm msabwelel ayi mulungu atipasa wina tisafooke tisapange mantha tipite chisogolo

  • @Jasonnyatwa
    @Jasonnyatwa 3 місяці тому +1

    Ayi ndithu tikuyenela kukavota opanda ID chifukwa zimenezi zitiphela maufulu athu,

  • @LeviChakwira
    @LeviChakwira 3 місяці тому +2

    A utm please stand up and be united. We love this party. We are behind you. We thank you Boni kalindo for saying the truth

  • @MaxwellDzaone-ym1vg
    @MaxwellDzaone-ym1vg 3 місяці тому +6

    Big Freedom fighter of Malawi

  • @DafterKhungwa
    @DafterKhungwa 3 місяці тому +6

    Yes,zoonadi tiyeni a Malawi tisagone tulo

  • @SophieKamanga
    @SophieKamanga 3 місяці тому +1

    Zawapengetsadi ndlam ndichifukwa akugula masuti ovala mwana opanda size ndipo olo chigawo chapakati sitikuwafuna achakwela ndi nduna zawo onse amenewo salowaso boma chaka cha 2025

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 3 місяці тому

    Ndiyeno zikusonyeza kuti anthu amene akubwezedwao Sitidzavota? Chonde chinyengo chimenechi tayambatu kale kudandaula.

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 3 місяці тому

    Wanthu azavota ngakhale alibe cha u nzika ngati bungwe lo imirira chisánkho achite zopusa Litha, Chakwera wapha Chilima.aliyense waziwa Ndipo Chakwera pa nyero pa mache

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 3 місяці тому

    😂😂😂😂 a president ndeno mukuzikanda pasaya apo pakuyabwa mumanivesa kukoma inu aboni pangani chipani tizakuvotereni ife anthu osauka chonde

  • @YamieManda
    @YamieManda 3 місяці тому

    Muthu uyu wa dpp,osangobwerela ku dpp bwanji mbuzi yamuthu iwe😊

  • @LawrenceDickens-jk3zx
    @LawrenceDickens-jk3zx 3 місяці тому +5

    End of MCP ndanena ndanena /wetting zachitika ku Kenya basi!!!!

    • @EliasOdala
      @EliasOdala 3 місяці тому +1

      DCcc ndiwe katundu omanga ndi wire always proud of yu

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td 3 місяці тому

      If only your family will vote you can talk that rubbish MCP it's not the way simple you think most MCP members they don't respond rubbish the don't talk nonsense they make sure keep quiet no fight with empty teen wait and see chakwera is not a small boy of Malawi so he is always showing the nation of Malawi that he is full grown up man always is away from the stupid people 2025 be careful

    • @UTHMAN-WAYA
      @UTHMAN-WAYA 3 місяці тому

      ​@@JackMvura-ik2td🤣🤣🤣Inu MCP ikumanga anthu ndemuzit ili Quit aaa🤣🤣💔

    • @LawrenceDickens-jk3zx
      @LawrenceDickens-jk3zx 3 місяці тому

      @@JackMvura-ik2td uziwo ase kapena umadyanawo za chipanizo? Zako zimene asaah.....

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td 3 місяці тому

      @@UTHMAN-WAYA police kapena MCP tell people the truth don't just talk cause you can talk what I need people must go to court tell them MCP is no longer MCP is a police but talking while you're sleeping by house it won't solve the problem

  • @williamdaka79
    @williamdaka79 3 місяці тому

    Anzathu ku Kenya amuonetsa Ruto koma ifeyo a malawi Kaye tinabadwa bwanji?

  • @GustarLafisha
    @GustarLafisha 3 місяці тому

    Nkhani ya azanu nde simukamba ya avice pulesidenti takambani wez

  • @BittonRashid
    @BittonRashid 3 місяці тому

    Pangolini ululani tikavote asinthe zimenezo isagwilentchito.

  • @Centre-m6f
    @Centre-m6f 3 місяці тому

    UTM ingotuluka mwachangu isanafike thawi ya campaign

  • @ZaccheousPetrol
    @ZaccheousPetrol 3 місяці тому

    Iwedi ndikatundu....ine kudabwa kuti opposition mukudikila liti

  • @ELINATengule
    @ELINATengule 3 місяці тому

    Akalindo mulungu azikutsogolerani thawi zose❤

  • @simeonkatema6484
    @simeonkatema6484 3 місяці тому

    Zoona zake DC umakwanira iweyo tikavota bas ooanda cha uzika

  • @JamesTobiasNkhoma
    @JamesTobiasNkhoma 3 місяці тому +1

    Thanks kalindo for the good information.....keep it up am behind u

  • @arthurkayuza
    @arthurkayuza 3 місяці тому

    Neighbour waionera patali game ....this is true !

  • @PeterRabson-z3w
    @PeterRabson-z3w 3 місяці тому +5

    Ndipo ñdinu nokha otimenyera ufulu

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 3 місяці тому

    🔥New clear BOM,Bonn Kalindo!

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 3 місяці тому +1

    Tivote ndi ngati kale ma id tilibe

  • @JosephMichael-x7v
    @JosephMichael-x7v 3 місяці тому

    I wish bon kalindo atakhala president ku Malawi

  • @JosephMichael-x7v
    @JosephMichael-x7v 3 місяці тому

    I wish bon kalindo atakhala president ku Malawi

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya 3 місяці тому

    Openga kwambili ndiyemwe angabweleleso ku DPP mutu wake unayima fwetseke zanu ndi kalindo wanu yemweyo mwalandila ndalama kwa gogo wanu opanda mano mkamwayo ndinu zitsilu shupt

    • @MbaulaJames
      @MbaulaJames 3 місяці тому

      Lemekeza atateako ndi amako kut masiku amoyo wako apitilile

  • @AndrewWyson
    @AndrewWyson 3 місяці тому

    Pompano 😅Kenya Kenya game ndizikwanje

  • @IsakyIsak
    @IsakyIsak 3 місяці тому

    Chakwela awukhudzidwa za ifa ya saulo chilima

  • @ShiraKasekaNyirenda
    @ShiraKasekaNyirenda 3 місяці тому

    Timadalira inu bwana DC mumatiyimila amphawi

  • @FrankChingudu-pi8kn
    @FrankChingudu-pi8kn 3 місяці тому

    Muleken mwana wa eni alankhule za kumtima kwake.

  • @AdamChirwa-u3d
    @AdamChirwa-u3d 3 місяці тому

    Ulem wanu mnthu wamkulu kwambili

  • @AdamChirwa-u3d
    @AdamChirwa-u3d 3 місяці тому

    Ulem wanu mnthu wamkulu kwambili

  • @EliasPhiri-yv8gv
    @EliasPhiri-yv8gv 3 місяці тому

    Koma uyu Nde amatokotadi eish

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm 3 місяці тому +2

    Is our president thanks

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 3 місяці тому

    For sure this is State Capture

  • @WilfredYekha
    @WilfredYekha 3 місяці тому

    Mbambande, keep it up

  • @Jasper-xk9iv
    @Jasper-xk9iv 3 місяці тому

    Tili pambuyo pano DC

  • @RodgersChikumbutso-jr7fh
    @RodgersChikumbutso-jr7fh 3 місяці тому

    Ichi chimandisangalatsa

  • @MacleanKwacha
    @MacleanKwacha 3 місяці тому +1

    Ulemu wanu big man,mumatiyimilila

  • @JamesPonds-j9v
    @JamesPonds-j9v 3 місяці тому

    Big up our own DC

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 3 місяці тому

    Zoona big man kalindo

  • @frankjolijo
    @frankjolijo 3 місяці тому +1

    .... Kuswa kuswa....opha mnzake, naye aphedwe

  • @NumeliKambo
    @NumeliKambo 3 місяці тому

    Born kalindo nd Dolo

  • @MercyChavula-qy1my
    @MercyChavula-qy1my 3 місяці тому

    Mumakwana ulem wanu

  • @HamzaMkwanda-bh8dc
    @HamzaMkwanda-bh8dc 3 місяці тому

    Chakwera why are you evil 😈
    Chakwera why are you wicked
    God will punish you soon

  • @Djmsakama-kj3ne
    @Djmsakama-kj3ne 3 місяці тому

    Osamabisila

  • @RhulaniMukasi
    @RhulaniMukasi 3 місяці тому

    Pari galu wina mmenemu waremba masege yonyoza chilungamo cha DC mancgendeake ameneyo mot Malawi mmene akuvutikila ndipo ndikuuzen agalunonse zomwemwaba mukudyazo mukanyera mundende apa sitikusekerelan tatopananu iwenamachende chakwera segula zimakhutuzo uve nthawiyanu yatha

  • @MarkKaliati
    @MarkKaliati 3 місяці тому

    It's fact

  • @MessiahPitros
    @MessiahPitros 3 місяці тому

    It's true

  • @KelvinBAligiza
    @KelvinBAligiza 3 місяці тому

    Bg up Dc

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 3 місяці тому

    DC 🥰

  • @MauriceTayali
    @MauriceTayali 3 місяці тому

    Ndalama za satanic, samalani. AMALAWI amzanga dziko ili laipa satanic yalowa mudziko lathu ili CHAKWERA atipereka kwa satana

  • @SenzoKatopola
    @SenzoKatopola 3 місяці тому

    Umakwana fadah

  • @YammsyZebron
    @YammsyZebron 3 місяці тому

    DC ❤

  • @EviePhiri
    @EviePhiri 3 місяці тому

    Dc

  • @FanizoKawindula
    @FanizoKawindula 3 місяці тому

    Chitsiru ichi

  • @SelinadeniasDenias
    @SelinadeniasDenias 3 місяці тому

    Ulemu wanu

  • @HarlodLemwe
    @HarlodLemwe 3 місяці тому

    kod bwana DC ukamapanga zimenezi umafuna chani kwenikweni ??? anthu andale awa amafuna kumatisokoneza anthu akumidzife mbolatu iyi

  • @MasterHeadson-ki7ji
    @MasterHeadson-ki7ji 3 місяці тому

    📌

  • @AkibuMdala-sr1dy
    @AkibuMdala-sr1dy 3 місяці тому

    ❤❤❤

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 3 місяці тому

    Izi ndizoonadi ku south kuno nrb palibe chikuchitika ife tikudabwa kuti a oppositions Ali kuti??? Nkhani ya ziphatso ikuyenda bwino only central region wat is this after all?? Nrb ikufunika kuyipangira ma demo akuzolowera tsopano kaya adya ndalama azisanza ndithu.

  • @LeviChakwira
    @LeviChakwira 3 місяці тому

    Campaign will be easier for opposition parties. A mcp apha chilima. 90% ya anthu mu Malawi akuziwa kuti mcp ndi amene apha chilima.

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson 3 місяці тому

    Chilombo chachilungamo koma bon kalindo mulungu akutetezele until nkhwandwe itachoka 'l think akufuna tipange ngat anthu akukenya.

  • @LeviChakwira
    @LeviChakwira 3 місяці тому

    Palibe munthu amene angavotere nkhope ya chakwera ndi mcp. Never

  • @sukiemapemba4094
    @sukiemapemba4094 3 місяці тому

    Tizavota zopanda ma ID apo ayi miyala izagwila ntchito kuphanakuphana basi

  • @StevenNathaya
    @StevenNathaya 3 місяці тому

    Bwana Dc mumakwanila hvy ndipo musasye kutimenyel ufulu

  • @VioletMovella
    @VioletMovella 3 місяці тому

    Born kalindo umatiyimilila,,,tili kumbali yako
    Malawi cwa mun2 uyu

  • @GanizaniPhiri-f2i
    @GanizaniPhiri-f2i 3 місяці тому

    Umakwana mr DC tingopita pa nseu basi .mbuzi zimene zatitopesa kwambiri.

  • @johnchitenji4
    @johnchitenji4 3 місяці тому

    Big up born kalindo With powerful message 👍

  • @MartinKapanga-q6m
    @MartinKapanga-q6m 3 місяці тому +1

    ndimakukondani a born kalindo ❤❤❤

  • @GetrudeBanda-sd1yf
    @GetrudeBanda-sd1yf 3 місяці тому +1

    Osafooka go on

  • @AbdikaniDasar
    @AbdikaniDasar 3 місяці тому

    That's powerful message continue to show them the right way to catch this big fish mr nyo

  • @MeliaMichael
    @MeliaMichael 3 місяці тому

    I support the motion
    Pamene anthu akuvota NRB izakhare pomwepo

  • @FrancisDinala
    @FrancisDinala 3 місяці тому

    Ndikungopanga scroll koma ndisanapeze pomwe amunenera zoyipa Bon kalindo more fire

  • @ZephMbeleswa-n8m
    @ZephMbeleswa-n8m 3 місяці тому

    Kkkkkkk akuti ndi president osauka ndiye inu ndi osauka moti daily amakupatsani chakudya

  • @WinerdShadreck
    @WinerdShadreck 3 місяці тому +1

    Aliyese akavota

  • @HarlodLemwe
    @HarlodLemwe 3 місяці тому

    kunali achina mtambo pano kuli ziiiii anadya chimbazi chafuleshi kkkkkkkk

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 3 місяці тому

    Mulungu adalise Born kalindo ndi azake ose otimenyela ufulu

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa 3 місяці тому

    Mumatiyimilira Bwana BORNE KARINDO tilirimodzi osaopa

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 3 місяці тому +1

    Ayaluka akubawo