Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Nyimba yabwino koma pa kolasi sindikunva, akuti chiya ndithandizeni
Kuchimwa tikungochimwabe odala olapa tchimo ndikulisiya mkuyanjana ndi Yesu Christu Nice song❤❤❤❤
Ndimwana akuyambitsayu koma alindiluso kwambili nice song❤
Nyadani mwayesu anthu amakodwa kumowa or maliro amene kulibwanji za yesu palibe oletsa masukani osaopa pondani satana amvetse inenso kuno nuponda nawo thanks guys
Ilike this song n the dancing style, keep the good work guys❤
I like it zoonadi tiyeni tilape🎉🎉🎉❤❤❤
Girl in pink top eeiish alipa eazy koma alibhooo 🔥🔥🔥
Kuipatsa moto ana zilibwino kwambiri,kumakondwa mwa yesu,yesu yemweyo kt wa wa wa
Thanks alot for the song❤❤
Nde pali ka baby Ako woooooow nice💕💕💕 muzabwereko ku Kapaza CCAP
Mbambande maguys this is real Malawian gospel sound ❤❤🎉🎉🎉
Congratulations 🎉🎉 guys
Mudzabwereko kwathu ku msamba chikho cccp. Mudzatiimbireko nyimbo imeneyo
ndaikonda nyimboyi
Gospel mbambande ❤ mumakwana keep it up
Glory to God Almighty always
Nyimbo anaimbatu iyi eeeh
That small boy is genius 😅😅😅 nice
😂😂😂😂😂😂Yeah that little one is inginious indeed bro😂😂
Yehova mutimveretu ife Ana anufe
Vibes my Friday
Nice song❤❤❤❤
This guys sound akupha
Ineso sndkumva
Nice one guys ❤
Nyimboyi ndimayikonda kwambiri koma pa chorus yimandiphonya akuti chani kwenikweni?
God bless this choir yes yes holy sprit
Nice song,
Jerous down good music
That little boy is another class eishiiii😂😂😂😂😂
Oh, yes ndukuuzan, a good song
nice tune
My choir kukafita nursery choir timakukondanibe
How are you my favorite Tabandilekani pang'ono girl?
Nice sound❤❤❤
Ndagwa nawe muchikondi umatha ase
Nyimbo yabwino
Akuimba bwino kwambiri
Spiritually super
Ati yeleyele a ha sitimamusonyezala
Nice one
Thanks for watching
Nyimbo iyi imandisangalasa mpaka ndinamusaka Timoteo amakambidwayo 1_4 anthu akuiwaladi za mulungu masiku osiliza
Nice song Mmmm Amen
Asasiye anawa akutitsitsimutsa
Sound yabwino keep it up
Every im watching this video 🤣 boy boy eeeee
I need this song, audio.... Where can I get??
Thanks
Amen
Nyimbo ya bwino mu kupha sound
Kod pa chorus akut chani?
Mbambande kupanda kusintha iyiyi ndekuti sudzasinthaso ndiwe okanika
Uthenga wabwino
Mwana ako kavala trouser ya allow kakufunika mphotho
mwana ameneyo ndi dolo
This boy 😂
Amen 🙏
Ku church or ku part
Ku church aliyese ali ndi malo ake osangalalira. Awa awo ndi amenewa asiyeni kulibe kwina koti akasangalalire.. zayesuuuuuu
Choir yakuti iyi ndayikonda
Ndirande Makata CCAP ,, BLANTYRE
❤
Kuimba nde akuimba bwino kma mavinidwe mwaonjeza za mulungu kumazilemekeza kumasiyanitsa ndi za ku dziko
You want kuti azikavina ku bar?
asiyeni ana asangalale
Za yesuuu .. akasangalalira kuti koposera kwa Mulungu..more fire guys