ZOMWE WAYANKHULA BON KALINDO LERO KU MA DEMO A KU BLANTYRE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 9 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 79

  • @MussahWilliam-py1ff
    @MussahWilliam-py1ff Місяць тому +6

    Mwana wowopsa kwambili....the Deeeceeee ..Boooooon Kalindo

  • @AubedPhiri-c4c
    @AubedPhiri-c4c Місяць тому

    Booooon Kalindo!!!! Moto kuti buuuuuu

  • @joegibsonzulu2599
    @joegibsonzulu2599 Місяць тому

    Viva my president 👏👏

  • @DanielJulius-y4p
    @DanielJulius-y4p Місяць тому

    Mr DC mumatiimilila zd

  • @PhilbertoChaimah
    @PhilbertoChaimah Місяць тому

    Akamuna awa the DC wanthu

  • @user-pf5hu2pd2b
    @user-pf5hu2pd2b Місяць тому

    Mr Bon kalindo your only the strongest person who can fight for Malawian s, booooon kalindo, the last Man standing.

  • @user-lg6kh2mn7h
    @user-lg6kh2mn7h Місяць тому

    Bon mulungu akudalitsen ndipo akuwongolelen

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Місяць тому

    Zoona analowera mademo Apm atawaphwasula mochitsa manyazi

  • @dboydkatunga5360
    @dboydkatunga5360 Місяць тому

    Bon kalindo DC president WA anthu osauka to much lv man DC❤💪💪

  • @OscarBernard-w5b
    @OscarBernard-w5b Місяць тому

    Ulemuwa wanu mr president wathu osauka

  • @MohammedAriesa-h8s
    @MohammedAriesa-h8s Місяць тому

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ bon kalindo ❤❤❤❤❤❤

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga Місяць тому

    Mwaita a Pulezideti again mumakwana

  • @IanAllstal
    @IanAllstal Місяць тому

    The Deeee Ceeeee kung'alura 💪🔥

  • @BenzoBula
    @BenzoBula Місяць тому

    Zikufunika ndzimenezo

  • @sharifujoe7633
    @sharifujoe7633 Місяць тому

    The Dcccccccc !May Allah protect you like always All the best Mr Kalindo

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o Місяць тому +5

    That. is true

  • @EnetChiomba
    @EnetChiomba Місяць тому

    😂😂😂 Dic bon kalindoooooo pitilizani ndithu kutimenyeta ufulu wa anthu osawuka

  • @PatrickChilinga
    @PatrickChilinga Місяць тому +1

    Kma akuluwa amatikonda

  • @user-oh9bh1cl3b
    @user-oh9bh1cl3b Місяць тому

    Big up tchana kalindo fight for the Malawians, bring that car tidzayike ma speaker pa carrier po pa sonke 🎉🎉, yatsala ya chikangawa

  • @user-zv3cy2xj5p
    @user-zv3cy2xj5p Місяць тому

    Mademo sanabebe chifukwa sanaphwanye zinthu

  • @GerladMakayika-on5rt
    @GerladMakayika-on5rt Місяць тому

    Zoonadi the DC

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Місяць тому

    Urendo wina madem ajila yatanda sitikuwafuna

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Місяць тому

    Mwandisangalasa ,simunawononge zinthu ,Ambuye akudaliseni ,tili kale NDI umphawi wambiri Muno ,Koma simunaphwanye zinthu ,zikomo Mr DC

  • @AlfredFrackson
    @AlfredFrackson Місяць тому

    the DCccccc! mwana owopsya kwambiri I like the calibar of the DC

  • @user-lw9su5om5z
    @user-lw9su5om5z Місяць тому

    Mwayamba bwino musaimenso ay

  • @user-bj7fj2mz8g
    @user-bj7fj2mz8g Місяць тому +2

    Mangochi ife tilibe zopembeza mafano tukukaphwanya kwa a DC tikufunaso kt atiyake za ndalama yomwe amati misokho ija imapita kuti coz as district timaziwa kt ngt tikupeleka misokho azitimangira zithu monga miseu ya bwino zipatara muzikhala makhwara okwana eeetu

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o Місяць тому

    DC mumakwana

  • @RichardKumbambe
    @RichardKumbambe Місяць тому

    B K you are our inspiration. Good work. God be with you.

  • @GiftKalulu-u8v
    @GiftKalulu-u8v Місяць тому

    Koma kunali chigulu cha anthu

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 Місяць тому

    Massive cruise 😅

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i Місяць тому

    The DC mwana wowopsya kwambiri Bon kalindo 😂😂😂

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl Місяць тому

    The DC panchenga🔥🔥🔥

  • @user-zv3cy2xj5p
    @user-zv3cy2xj5p Місяць тому

    Alibe ndi chikoka nkomwe

  • @JessicaManda-zm1ug
    @JessicaManda-zm1ug Місяць тому

    Koma nde mademo ake mhu 😢

  • @MustapherLino
    @MustapherLino Місяць тому +3

    Boooon kalindo mwana opsa

  • @RebeccaNvenya
    @RebeccaNvenya Місяць тому +1

    President wa anthu osauka the Deeeeeceee😂mumatiimilila

  • @AlexanderYovatiKhumalo
    @AlexanderYovatiKhumalo Місяць тому

    Simungathe kuchita zinthu zobweletsa mtendere pakati pa a Malawi? Okonda izizo ndi amene safuna kugwila ntchito yodzipezela zothandiza ma banja awo, Malawi safuna anthu a ulesi oyenda mtauni kuthyola ma shop a anthu anzanu tikulima mbewu m'thilila ku madimba cholinga kudya bwino inu mufuna zongotola ulesi ndi m'tsogoleli uti angapeleke mbale ya ufa khomo lililonse kwa anthu a ulesi ongofuna zosagwilila ntchito?

  • @sinethembangubo3718
    @sinethembangubo3718 Місяць тому

    The DC kung'alura osaona nkhooe

  • @user-vu2hh3lw8l
    @user-vu2hh3lw8l Місяць тому

    The DC amakwanila ❤

  • @MohammedAriesa-h8s
    @MohammedAriesa-h8s Місяць тому

    2025 bon kalindo boma

  • @HaruunWalusa
    @HaruunWalusa Місяць тому

    The DC more 🔥 🔥 🔥

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 Місяць тому

    Muziwonetsa video yonse osati kudula .ka half ayi.we are a far from home we want to see exactly what had happened. Please.

  • @Kelvin-hj5qv
    @Kelvin-hj5qv Місяць тому

    Kkkkk 😂😂 mademo akumalawi ndiwoseketsa kwambili

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali Місяць тому

    Boooooon kalindoooooooooo❤❤❤ the DC

  • @user-nu1dj3jh7b
    @user-nu1dj3jh7b Місяць тому +1

    Mademo ngati mukupita ku church 😂😂😂 aaaa... mademo anali kukenya.

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Місяць тому

    The DC chiwanga mliro more fire

  • @JaphetSakala-pq4fl
    @JaphetSakala-pq4fl Місяць тому

    Ndimaganiza kuti mupanga mademo za report la ndege yomwe adalonjeza kuti azalengeza KWA amalawi

  • @danielsulani8689
    @danielsulani8689 Місяць тому

    ❤❤

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala1493 Місяць тому

    kkk mademo or njila ya mtanda kulibe anthu ku BT nanga ku Lilongwe kukakhala bwaaa apa tisanamizanepo zavuta

  • @OsmanMasamba-ck4mo
    @OsmanMasamba-ck4mo Місяць тому

    You deserve to be Malawian president born kalindo

  • @maybingoma8247
    @maybingoma8247 Місяць тому

    Mwana wosaopa, opusa kwambili the deeeeceeee... Boooon Kalindo

  • @NolityKondowe
    @NolityKondowe Місяць тому

    School kids

  • @charlesvenacio9773
    @charlesvenacio9773 Місяць тому

    Umakwana DC

  • @NizigiyimanaChantal-c2p
    @NizigiyimanaChantal-c2p Місяць тому +2

    Azibambo

  • @VeronicaYohane
    @VeronicaYohane Місяць тому

    Chikanhawa amve kuwawa osaopa osafooka osafooka osawopa

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala1493 Місяць тому

    kulibe mnthu opanda ID kuti vote

  • @TIDEscom
    @TIDEscom Місяць тому

    Kkkkk kulowera ma demo kutulukira ma demo

  • @JeanKambala-gm1zr
    @JeanKambala-gm1zr Місяць тому

    Machine bambo😂

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Місяць тому

    Timakunyadirani mr bon kalindo

  • @CellinaNgolingoli
    @CellinaNgolingoli Місяць тому

    Chakwela apume watikwana

  • @EusébioLucianoGaiondo
    @EusébioLucianoGaiondo Місяць тому

    Hu

  • @DauglassNkhoma-dj9lp
    @DauglassNkhoma-dj9lp Місяць тому

    😂😂😂 Malawi yavuta ife tibwela

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Місяць тому

    Ndipo aziwaso mandemo ena akubwera ku zomba mangochi ndi zunzu

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 Місяць тому

    The DC mnyamata oopya kwambiri

  • @JohannesNamale-f6c
    @JohannesNamale-f6c Місяць тому

    Adaphwa msuzi awa

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws Місяць тому

    Kodi matafale anamangila kuti???kodi anali president chakwela???kodi munali kuti pathawi imene ija mwachisoni anamupha evison matafale koma a Bon kalindo kunali ziiiiiiiii chibanzi chikuwagata pakhosi otsayakhulapo,,ngati ku Malawi tinataya oyimba kupotsela oyimba onse malawi nde ndi evison matafale nzimu wake uwutse muntendele

    • @evancesteven9755
      @evancesteven9755 Місяць тому

      🤣🤣🤣🤣 comment ngati mwana wa nursery, was born kalindo that time an activist? Kungolemba zosemphana basi

  • @user-lo8dx9ei7e
    @user-lo8dx9ei7e Місяць тому

    Boni kalindo umatiimilira malawi

  • @FelixAlfled
    @FelixAlfled Місяць тому

    Mbambande

  • @BhekiLithuli
    @BhekiLithuli Місяць тому

    ❤❤❤🎉🎉

  • @user-oy6dl1pv9e
    @user-oy6dl1pv9e Місяць тому

  • @RichardKumbambe
    @RichardKumbambe Місяць тому

    Noooooooo to IDs for voting plz !!!!!

  • @Jasper-xk9iv
    @Jasper-xk9iv Місяць тому

    Ameneo ndie mademo?

  • @zumahmedison9672
    @zumahmedison9672 Місяць тому

    ❤❤❤❤❤❤❤