MOYO NGWABWINO- Pokhala Mtendere By CHITSITSIMUTSO Women Choir (Masintha)

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 25 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 15

  • @misheckkikwanza-jb6hr
    @misheckkikwanza-jb6hr День тому

    Oh there is just piece in listening to gospel songs 🙏🙏

  • @namondwejohn9354
    @namondwejohn9354 12 днів тому

    Ngakhare satana andizuze ine,koma ndimadziwa kuti chitonthozo changa ndinu,amen

  • @judithmingo
    @judithmingo 6 днів тому

    Hear the sweet voices amayi mmatisunthira chifupi ndi Ambuye

  • @yarnmakalani
    @yarnmakalani 6 днів тому

    thanks for the gift of life

  • @benjamingolosi8106
    @benjamingolosi8106 4 дні тому

    Moyowu ndiwabwinondi mwatikokera chifupi ndi mulungu zikomo

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 25 днів тому +1

    Moyo wanga ulitu bwino, Zikomo ambuye pondisungabe ndimoyo🙏🙏

  • @Emmanuel-l6i
    @Emmanuel-l6i 6 днів тому

    Amen Moyo wanga ulitu bwino 🎉🎉🙏🙏

  • @PatriciaKafaniza
    @PatriciaKafaniza 19 днів тому

    Moyoudi mgwabwino, zikomo ambuye pondipatsa moyo

  • @EthelOsman
    @EthelOsman Місяць тому +1

    2018 nditadwala ku South Africa nyimbo iyi linali thandizo langa Zikomo yehovah

  • @ElizaMarko-l1w
    @ElizaMarko-l1w Місяць тому +1

    Moyou ngwabwino ndipo zoona👏👏

  • @AffectionateChocolateBon-gl9rc
    @AffectionateChocolateBon-gl9rc 19 днів тому

    Mumatikokera kufupi ndi chavuta Maka Maka ife tili mmayiko amagazi ano Capetown oyeee

  • @mercykokha2851
    @mercykokha2851 19 днів тому

    It is well with my SOUL!!!!

  • @SaamSaaam-g2n
    @SaamSaaam-g2n 2 місяці тому +2

    It is well indeed with my life ❤❤❤

  • @AskKankakee-wg2sd
    @AskKankakee-wg2sd Місяць тому

    mavuto ndi akuludi .....moyo wanga ulibwino...