Iyi nde munaimba bwino komaso azimai avala maduku kumutu kulemekeza Ambuye. And mavinidwe akeso a simple that's why this song is a blessing to many. Keep up this simplicity stay away from worldly dances
Ndalephera kusankha nyimbo yopambana izake ,,iliyonse ukamvera ngati sunamvereko in short all songs were composed by talented sisters, AMAITHA AZIMAYIWA TISANAME DPP MORE 🔥
Since l come across with this song, am now addicted to it 🤣🤣 l would play and dance the song the whole day bt am Shona and worse l don't even know the meaning of the song still looking from someone from Malawi to translate it to me, l would really appreciate a lot ❤
The day l came across with this song am telling you am like am addicted to it but funny of it l don't know the meaning of the song it because am SHONA . Am appealing to anyone from Malawi who can able to translate to me the meaning of the song 🤣🤣.l would really appriciate a lot ❤❤.
Nyimbo yi anthu akumwera mowa. Ndipo yawathera ndalama😊😊❤❤
Iyi nde munaimba bwino komaso azimai avala maduku kumutu kulemekeza Ambuye. And mavinidwe akeso a simple that's why this song is a blessing to many. Keep up this simplicity stay away from worldly dances
Zoonadi
Nice song l love it
Ine nde sindimadikilanso kuti ayitane katatu, koyamba komweko ndimakhala ndanyamuka kale🔥🔥🔥
Nyimbo ili boh, iyi mwamva , ndipo tinaivina ku Kenya, at Malawian Embassy, Nairobi pa 26 October 2024, Akatolika
CCAP members let's gather here🥰🥰🥰🥰🥰
🎉🎉🎉❤
My Church for life🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
❤❤❤
@@faithmwanga6078exactly ❤
Am SDA church but ndimakonda nyimbo iyi kwambiri
This song is amazing I love it.keep it up Kasungu praise team
This reminds me my time I stayed in kasungu with my parents. This is a hit . kasungu inyamuke... kalondolondo
This song is awe! , may God almighty bless you abundantly for informing, entertaining and educating us🙏🙏🙏.
Proud to be a C.C.A.P member.All the way from Zimbabwe Harare Epworth Mpingo
Praise the Lord ❤
Thanks for watching and supporting KU Praise and Worship Team
Ine dzakwela mwamba ndi Angelo.
My favorite song.
Muzatiitane mukazakhala ndi any function yanu or ya church
I was born and raised in a CCAP christian home, l love this song even though lam now a Catholic woman, God gave me a catholic man😊
Nde Ife titani
Chete ku Synod 🔥🔥🔥
Iiiiiiii na nyimboooo iyiyi mmmmm dope
Powerful song mulungu amene munachotsa chitozo cha Hannah muliyemweyo chitani baba
Kasungu Nice nice ccap
Wonderful song
Powerful message kasungu praise ❤❤
I like this song ambuye apitilize kukupatsani nzeru zopangila nyimbo zina
Ndidzafera mu C.C.A.P kwathu kuli zokoma
Ku Bar tumavina yomweyi🔊
Iwe umati 😂😂
😂😂😂😂
😂😅😂😅inde iwe
Kkkk ndipo sukunama
U dnt kno how blessed I became when listening to this tune😊🔥
Kasungu woyeee😅😅😅...nice song
CCAP❤the mission it to see heaven and be with God
Nice song ❤
This song is so hot in CCAP Zim right now 🇿🇼
Ndalephera kusankha nyimbo yopambana izake ,,iliyonse ukamvera ngati sunamvereko in short all songs were composed by talented sisters, AMAITHA AZIMAYIWA TISANAME DPP MORE 🔥
Since l come across with this song, am now addicted to it 🤣🤣 l would play and dance the song the whole day bt am Shona and worse l don't even know the meaning of the song still looking from someone from Malawi to translate it to me, l would really appreciate a lot ❤
Am Catholic but I love this song soooo much.
My favorite tune when I was on sick bed, continue the good work
Amen ambuye ndiwabwino
Nice 🔥🔥🔥 Mumatimvetsa kukoma koma Choir iyi ikufunika Support ndithu
This song is a vibe ,ku synod timanjoya
Ambuye ayitana koyamba ndava ayitana kachiwili ayitana ka chitatu ndavomela 🥰🥰 ndikubwera
Duuu mu synod❤
Ndine Muslim but this song ndi hit kudos guys🎉🎉
yes also am muiism 2
Amen. Tizimuyamika Mulungu ndi mitima yokondwera
Nyimbo iyi ikufunika support financially vedio ijambulindweso in high quality, iyi ndi hit
I second dis...........nyimbo aiswa iyi❤
Really it requires fully supports
Ndipo camera was not good at all atachita kabweleza zikhoza kukhala bwino like ana a kaswalipande
It has to start with your support, n then people will follow ❤
Amen apa zilibwino ngat tikupta kumwamba kuchta kukoma 🎉
This is a very good production worthy listening and dancing mudzina la Yesu
Ine phee ku nkhoma❤ love you guys
Thanks Nkasa this is awesome
Singagone nsanamvere nyimboyi....mwamenya magayeeee big up
Gospel stress free beautiful piece of music 🎶
Zikomo kwambiri Kasungu ccap chifukwa cha nyimbo za chitsitsimutso.Pitilizani ntchito yayikulu yabwino.
Kasungu mwayimba bwino nyimbo izi, great voices. Alemekezeke Ambuye🎉🎉🎉🎉❤
I am Catholic but this is beautiful ❤️
This song is a Lovely to my wife DJ JOJO'S repeat
Nyimbo iyiyi siyamasewela. Inakungidwa
This song keeps me going day by day❤
What a hit, iyiyi mwapha guys.... Wooow so anointing
Zokongola kwambr 🥳 ndkbwera bc kalondolondo
This song keeps me going, kundidana kakwamba keniko mbwe ndasoka, wafyaa ulendu💃💃💃🙏🙏
Yimbo ya bwino zedi am Desmond from mzuzu
In love with this song
This is beautiful song and you can listen again and again
Madala aphatikiza kasinod kagule wamkulu,😅😅😅😅😅😅 koma aimba bwino kwabasi keep it up lam blessed.
Powerful song 🙏
A chakulangila ndakuonani kasungu CCAP yathuyathu iyi ❤❤❤❤❤❤
Nyimbo iyiyi indipangitsa kuvala mvano ndisanakonzeke❤Hope mwayamba kuimba m'ma Gospel show
Kumwamba kulandire ulemu
Kuimba kotsitsimutsa moyo❤❤❤
Mwana mkatundu uyu 😊
Nice song Mr Gondwe ndakuonani
Let this be our national anthem
Ndimasiya kudya wina akangoika nyimbo imeneyi.
The day l came across with this song am telling you am like am addicted to it but funny of it l don't know the meaning of the song it because am SHONA . Am appealing to anyone from Malawi who can able to translate to me the meaning of the song 🤣🤣.l would really appriciate a lot ❤❤.
Ambuye ayitana .....
Watching from SA ❤❤
Cant wait ine zakwela mwamba nd angelo
Ilike this song very much
Ambuye akudalitsen ma guy luso ili hvy
Amen im blessed today i as i watch the song
Proud to be a member of synod👏💞💕💥
Ndubwela 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Mbambande song in love with ❤
Beautiful song❤ ine nzakwera mwamba ndangelo 🥰
Iyiyi ndi gospel song of the year ❤
Thiyeeee🥳❤
@Kasungu CCAP this is nice
Inde kalondolondo
Iyiyi mwaimba bwino. Creativity at its best
Ine dzakwela mwamba ndi Angelo 🙏🙏🙏
Pamenepoooo
the way soldiers love this song mmm ❤
Here I'm my Lord,, 🥳🥳🥳🥳🥳
The best of all time
I can't sleep b4 heard this praise and worship song d
Amen and amen 🎉🎉🎉🎉🎉
Reminds me of my late uncle
Malawi Polytechnic team nyimbo yathu iyi
Aitana kachitatu 🎉
nduchoka ku church now😂😂couldnt stop singing this song i had to come here ndiloweze bhobho.....2 days to crossover
Synod woyeeeee 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
si mmene ikumavinikila bwino ku mowamu
Kavinidwe kosangalasa kwambila ❤❤❤❤
What a good song. Amen
Kasungu kuzayaka moto ku buuuuu😂🎉
Ndavomeleza ndubwela
Ndipo nyimbo iyi ndi katundu
My favorite song
Power full message 🎉
Amen
nyimbo iyi ilibwino zedi🎉🎉🎉