Ndithokoze UA-cam,FB,tiktok chifukwa timamva zobisika from so many created channels tikamati tidalile ma radio Aku Malawi tikananamizidwa coz alibe chilungamo. Bakili Muluzi TV the best of the best with the number one journalist for all. Uu a brave man announcing without fear we ❤ u
I have listening to this guy for so long, if theres a person to support then its this man, he great acess to almost the evil and secret plans mcp has been doing bwanji tonse timpange support? olo atakhala kut ali ndi side koma he reveals vital information very helpful as a country tonse pliz guys lets support this man
Achewa ndiochepa akuzinamiza amenewo this is new Malawi osati wadzana tipotokola makosi zimenezo nyumba amangazo ndimalodgwo zakwana sisanathezo bs komno nxt yr wautali
History is the best teacher long live BMTV ♥️
Ndithokoze UA-cam,FB,tiktok chifukwa timamva zobisika from so many created channels tikamati tidalile ma radio Aku Malawi tikananamizidwa coz alibe chilungamo. Bakili Muluzi TV the best of the best with the number one journalist for all. Uu a brave man announcing without fear we ❤ u
Ma radio aku Malawi anatha mmmm🙆♀️🙆♀️
😊
😊
The best TV ever
Zooona Mubale wanga Bakili Muluzi Tv ndi Yachilungamo
Komatu akunamizana a chewa generation yake siino ay❤❤❤❤
1😮
Ndikanakonda anthu wofuna kwabwino kut tisale kudya kut mulungu alowelelepo zafikapa zoti amphat tose
Ndagwilizana Nanu kwambili
Pompano MULUNGU aziwonetaera tikupephera
Kudandaula kwa a Malawi mulungu akuwona ndinthu
Bakili muluzi tv mulungu wakumwamba akusunge manja mwake
Bakili Muluzi Tv no 1❤
Akatundu amene akufwanyulura zinsisi momveka bwino. Amene amadana ndi zokamba za akatundu awa ndi ndie kut ali gulu la anthu okupha.
Ndipo kwambiri tu esh
Zoonadi
Awona ngati atimalidza tonse akunama ameneyu God is protector
Best television ndpo iyiyiii ikung'alula zobisika❤
Mulungu was Abraham atimenyera nkhondo ndi wamoyo yesu khristu
I have listening to this guy for so long, if theres a person to support then its this man, he great acess to almost the evil and secret plans mcp has been doing bwanji tonse timpange support? olo atakhala kut ali ndi side koma he reveals vital information very helpful as a country tonse pliz guys lets support this man
Best of Bakili muluzi TV always kung'aluratu❤❤😂
I believe that your the best of the best yimakunyadilani kwambili ❤❤❤❤❤❤❤
Love bakili muluzi TV always
Civil war is around the corner in Malawi. May God bless only true and fearless Bakili Muluzi TV.
This crazy government wants to make Malawi complicated and fighting each other like DRC this is madness and very shameless
We are here for you our own brother keep fighting for the poor and voiceless people
What a whistle brower sent by God, courage Bakili Mulizi TV
God of the mountain is the same God in the valley he will protect us keep up the good work brother 💪
Bakili muluzi TV ndikatundu srs ife timakupempherelani 🙏🙏
big up fadah silute inuyoooooo
Bakili muluzi tv mbambande 🔥 ndipo mulungu atimenyera nkhondo
Bakili Muluzi TV ndi more
The best reporter in our country
Timakala tikunene kuti kumalawi kuyamika good ndimene achakwela akuchitila akugawanisa mithudu
izi ndi zeni zeni, channel ichi Ichi chimakamba zoona zokha zokha. long live boss
Zimawoneka ngati akunama but days later zikumachitika ,Thanks potitsekula maso mpake page iyi ndimayikonda
BM TV, GOOD NEWS MAKWANA 📺📡📡📡📢📢📢📢📢📢
Malawians let’s unite like kenya this guy it’s doing his part wat about us all??
Asilikali , fell Malawians let do something mantha satithandiza
We Malawians uthink wa btv alibe koma he stand and tell us truth ife wat are we doing?? Basi ma comments bakili tv one en e.t.c let’s wake up guys plz
Exactly
Bakili muluzi Tv is ranked No 1
@@JacksonMoyo-tm8dv exactly
Keep crossing all borders and regions timava zambiri nkuziwaso zina zoti sitikanaziziwa i will follow you for ever BMTV Chanel god bless you
Akunamatu amenewa kuyambika khondo
You are the one in this country pls continue to wise us Malawian ngati anthu amadana nau mmmm simmalawi ameneyo ine ndiye ndinakunyadirani
Mulungu akudaliseni Big man mukutiziwisa zambili zabwino zose
The best tv the all malawi mumakwana Big
I respect you mr big mn kuchokera kwa ine kuchiponde border uko
Only God will protect Malawians. All the best BMTV for your info
Anthuawatu kwiyo wa mulungu wawazugulira ndipo akugwira read butane ndipo choopsya chiwagwera posachedwa sachedwa safulumira pomwe akuziva kuva kukoma kwabili ndipomwe ya hova akuti kwantha adzidzimuka alupanga omwewo akuphana nawo onkha sitikuwopa kuti kwabwera futi ndizophanirana okha zimenezo
We pray for Malawi against civil war ... God bless Malawi.. lov u from Zambia
Inuyo nd 1 a bakili muluz tv
Koma iwe bakili muluzi tv ndiwe Genius.😊😊😊❤❤❤❤❤❤❤
We always appreciate with your true news brother.
Umakwana B TV morefire
Best channel Africa ever had it's bakili muluzi tv
Bakili Muluzi tv is the best TV
Best tv in Malawi
You are best of the best journalism 👏
Best TV at all❤
Eishh
Best TV and Limpopo FM tikuziwa zambiri ndithutu mmm
B.muluzi tv the one
Long live BMTV
Machende awo akapha ndani muyese kupha Peter 😢😢panyapake chakwera
Ndimomwemo bg man ❤❤❤ mwawulule ayamba chibwana
Best TV in Malawi keep updat
Ndip agalu amenewa koma peter muthalika yekhayo atisiile please
Mulungu achititseni manyazi anthu wonse akuphawa musalore satana apambane tichitireni chifundo Mulungu
Go deeper Big Brother, we love you!
Koma yaaaaaah Kupha Chilima lero akufuna aphenso Peter Munthalika ??? Sorry Ululu ndiye simutithayi munamuonelera Mngoni yemweyo ifeee alomwe ndie tizakupha ndimanja nonse a MCP kuyambira Chakwera wanuyo
Mbambande
Best tv for ever
Thanks boss we have been waiting for this continue to give us the best
Good massage, and history is the best teacher
Best TV Mulungu atisogolele ndithu Malawi is not safe.
I proud of you my beloved brother keep to inspire us bru
Mulungu akubise.mmapiko mwake
The best TV in southern Africa
Achewa ndiochepa akuzinamiza amenewo this is new Malawi osati wadzana tipotokola makosi zimenezo nyumba amangazo ndimalodgwo zakwana sisanathezo bs komno nxt yr wautali
Big up bro
Big up brother man!!
Best tv forever
You're the best mr
Good job brother we are frant of you brother 💪💪💪
Chonena chandithera 🙌🙌🙌🙌apa nde kukhala kupha anthu mwachisawawa coz mayufi ndi umbuli sanapite ku school mmmm..
Like from Johannesburg Kempton park
I pray for your protection dear brother am afraid ndi moyowu
Ulemu wanu big God bless you
Brother wanga Mulungu Akutetezere
Best TV 📺
Bakili muluzi tv will trust you all news is coming from the is tru 100%
Army commander 1993 anali ISAAC YOHANE CHIUNGE. MANYAZI MUXIKHALA NAWO MUKAMANAMA
Nkongo waamako
Brother ur best always
Koma tv iyi timayankhula zoona zokhazokha and zikuchitika
Paja a Malawi timafuna tisimikize titalira 😢 kenako tiziti aaaa zinanenedwapo izi,,, tiyeni tisithe kaganizidwe ndikachitidwe kathu pa zithu😢
Keeping bro
Matiimilila blo
Kwachema🙌🏾
Always following sir 🙏 👍
Nde mwati achewa tizisapotana tokha tokha? Rubbish, I'm a Chewa but I can't support that shit
Ambuye akudalitseni kwambili,mukuyankhura sinunuyo ayi koma Ambuye.
Best TV
Ameyu ndigalu ndithu❤
Best tv
Munthu amene sanena zabodza ku mtundu wamalawi ulemu wanu 🙏
Mmatiimilira bro keep it up
Zovuta only GOD will help us
May the vengeance God be with us, kanthani oipao Ambuye
Pakufikano posankhanamitundu chifukwa cha maudindo ngati akufuna iyeyo azizalamulila kulilongwe kwaoko ife ochepafetigwirizane
Iweyo kwa ine ndi one bros i love
Asitikali akumalawi onse ndimbuli zokhazokha sakudziwa kuti mapeto olandidwa dziko ndiomwewa
Live longer mr boss man
Zitsiru sonjas wake-up is your time