Bwana Ku Army Anyamata Anu Ndi Okwiya Kwambiri - Bon Kalindo

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 вер 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo alleges that all is not well within the Malawi Military Establishment, as junior officers are reportedly unhappy with the reduction of their benefits and remunerations.
    Ku Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo wati zinthu sizili bwino mu gulu la asitikali a Malawi, kamba koti akuluakulu achichepere sakukondwera ndi kuchepetsedwa kwa mapindu ndi malipiro awo.
    #malawi

КОМЕНТАРІ • 32

  • @Richardbanda-hg6pt
    @Richardbanda-hg6pt Місяць тому

    Mr❤kalindo may God bless u all the time in Yesaya41v10,Yesaya54v17,fear not this is Democracy thank u very for reminding the oppositions

  • @BishopMaxwell
    @BishopMaxwell Місяць тому

    M, dani wamkulu ww MCP ndi Mr bakili muluzi tv ❤❤amene uja ndi shasha kuposa akalindo

  • @AufiThera
    @AufiThera Місяць тому

    The DC 💪 always with you 💗

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Місяць тому

    The DC president wa anthu osawuka 💪✊❤

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms Місяць тому

    Inde bwana zoonadi

  • @HassanTmasuku
    @HassanTmasuku Місяць тому +1

    Athanenazo aku army ulemu kwambiri bwana chigawa sanafunetu chibwana nthawi ya kamuzu

    • @zubairsantoschifomboti3604
      @zubairsantoschifomboti3604 Місяць тому

      That's only commander we hard our history genaral manken chigawa he was true lead who sacrifice to us malawians to deal with pioneer

  • @user-id8rr8or6d
    @user-id8rr8or6d Місяць тому

    Ati asaaa

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu8384 Місяць тому

    A kalindo za MDF zilekani Waka ndivizeleza chomene is better iwe ngati ukaya command wa MDF panji ngati viwawa vya muno mu malawi ngati kulinje oloso ngati Dr chilima Andafwe Akalindo chiuta akutumbikani

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw Місяць тому

    The DC 🎉🎉🎉

  • @Uladimbwana-fr9ev
    @Uladimbwana-fr9ev Місяць тому

    Akuti charakwe😂😂😂😂😂😂

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Місяць тому

    ASILIKALIOTU AKUYENERA AZIONE CHIFUKWA NDI ZITSIRU ZA ANTHU KWAMBIRI MENE CHAKWERA AKUCHITIRA PANO WAONONGERA DZIKO AKUBERA NDALAMA ZA BOMA ZOMSEZO ASILIKALI AKUNGOTI NDWIIIII AKANAKHALA MAIKO ENA ATAMUKHAZIKA KALE CHAKWERA PANSI KOMA AWA AMAOMBERA MANJA CHIKANGAWA , NDIYE LERO NDI IZII AKUWALOWERANSO KU BARACKS KUMAKAWAPHA MALO MOONETSA NKWIYO.ALI CHETE AZIONA

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona Місяць тому

    Ndalama adula kumalipiro a Asirikali wo akufuna akagulire zida zokaphera Anthu Ku Chikangawa. Mukutchukatu Chikangawa boys, Kuba Za Amalawi ndi kupha . Anthu opanda Chisoni Komanso opanda manyazi ⚒️👹👹

  • @savinapili7185
    @savinapili7185 Місяць тому

    akalindo kuyesesa ndiye mukuyesesa kulangiza koma mmmmm chakwela ndi galu ndithu

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Місяць тому

    Mumayesa abon kalindo koma anthuwa samava,akhapanaso kubaracks ko kkkkkk

  • @PatrickMulangala-os4by
    @PatrickMulangala-os4by Місяць тому +1

    Ingoyambika bas

  • @GreenBadani
    @GreenBadani Місяць тому

    👍💪💞🇿🇦

  • @Sarahmuskambo
    @Sarahmuskambo Місяць тому

    Yesaya 54:17

  • @AbdullahaziziAmoswalala
    @AbdullahaziziAmoswalala Місяць тому

    😢mavuto alipo ndithu

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Місяць тому

    Kkkk ayambilatso yokakamidza anthu kuti adzipeleka mphatso mowawumilidza iiii koma sidzatheka basi oo

  • @AufiThera
    @AufiThera Місяць тому +1

    Anthuwa Nd a nonsense km

  • @james-zd2nz
    @james-zd2nz Місяць тому +1

    The Dddddddd Ccccccccccc

  • @georgelupiya1313
    @georgelupiya1313 Місяць тому

    za ziiiii

  • @Sarahmuskambo
    @Sarahmuskambo Місяць тому

    Masalimo 118:17:18

  • @IreenChilingulo
    @IreenChilingulo Місяць тому

    Mwina chifukwa analanda futi kona aadula kkkk

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o Місяць тому

    Bwana wathu🎉🎉

  • @SackinaMachemba
    @SackinaMachemba Місяць тому

    Chonena ndiribe

  • @user-ch6pw6mf3l
    @user-ch6pw6mf3l Місяць тому

    DC sazatheka😂😂😂😂😂

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda Місяць тому

    You are lying,

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Місяць тому

    Aaaa chakwela olephela uyu chisilu ndi MCP yakeyo atadzuza amalawi