First things first.....sangie wafunsa a 5years Aja ndi inu??😂😂 Bwanji simunamuyakhe...komanso angozo chidhindo chanu chili kuti uncle amwana......😂😂🙌🙌🙌 Also pakati is the real deal amwene...it's the way he was calling the wetaaaaa!!!! for me evidence mmanja.....mmakwana guys
Mkazi wa Hyphen wayankhila za mzeru tu😂😂😂
Mamuna wachibwezi asamanyoze mamuna waku nyumba 😂😂😂
Zoti mamuna wakoyo akuoneka ngati opepera zinthe
Ife tidyaa, Zobwera Zonso Tidyaa🤣
Nina My Guy🤜🤛
Pakatiyo akupatsani BP mayi😂😂💔mungomunamizira kt amagulitsa chamba amumange😭😂😂💔🔥🔥
Kkkkkkkk komatu
I love mbusa and Gani these guys olo asakukamba ma jokes munthu umaseka wekha. these guys can act Manganya uja akunama.
🔥🔥🔥🔥
Its the way Ngozo stood to Protect his family 🤣🤣🤣🤣♥️♥️♥️
😂😂 Big guy Ngozo
Ife tidya, zinazonso zikabwera tidyanso😂😂😂. Sikut ndi chiphsinjo ahhmm
Gani is underrated actor🔥 he is an icon ithink
Loving this show! Watching from Finland with friends please add subtitles am tired of interpreting while watching 😅
Koma mwati pakatiyu si mfiti 😂😂🤣
He's too much
Mukuyitha kwambiri...we really gaining some lessons from your videos
Koma Black Nina eeeeeish.....🙌🙌🙌
Ndiwe chiyabwe 🤣🤣🤣
Ndipo I'm enjoying it eish keep it up guys 🔥🔥🔥🔥🔥
Eish pakati has proven to be a great obstacle 😂🤣
Simmatopa following you guys 💃💃💃,,,,,I enjoy this
Black Nina 🔥🔥🔥🔥 Abusa ndi Moreee ndi uyu wadanziyu kaya ndi ndani ndi Fire naye
Abusa tsopano 😂😂😂🔥, komaso Pakati penapake 🙌🙌
Every character is unique in this series😘 this series is very addictive Yooooo🥺🥺🥺❤️🔥🔥🔥
Eish I like it 😂
All of you guys mumakomesa kwambiri big up 🔥🔥🔥🔥💪
I like mkazi waneba she got a sweet voice koma achimwene akewo mcholetso😂😂😂😂😂
Thank you Komatu flu inali itanditengetsa day imeneyi...
@@mwaisambani1849 😂😂😂🙌
Pakati koma ndosokoneza eish😂😂and the way angozo stood up to protect his wife eeeee
I can't stop laughing😂😂😂😂😂 @ mzimu woyera wulipaliponse😅😅😅😅...koma pakati ndiwe owonga😂😂😂😂😂
Yu guys mukuyitha koospya!!!! Kip the fire burning....am Lovin this
A man has to protect his family. Safuna zoyambana Ngozo kkkkkk
Ganizani ndi pakati are the real deal🤣🤣🤣🤣
Best ever , l have been following you guys since first day much proud
Kkkkkk ati chikuoneka chopepela🤣🤣 Koma utakhala ndi m'bale wako ngati pakati 😅🤣😅
Pakati ndi ka nuisance 😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂 abusa mpaka Njira yoyamba ungozimangilira😂😂😂😂
Abusa mumayang'ana kwambiri camera, as if you were checking if akujambulabe but you are a very good actor, iweyo umakwana
Koma m'busa ndi katakwe
Akut pali njira ziwiri
Yoyamba ndi kuzimangilira
😂😂😂😂😂😂😂😂langizo lotan ilo🙌🏾🙌🏾🙌🏾
@piksy koma ka blacknina ko ai ndikoonongaaaa 😂😂😂😂🚶♂️
Chikuoneka chopepela.kkkkk more fire
Pakati ndi chi vibe the way he speaks😂 remember evidence😂ngozo ndi sangie my favorite 😂
😂😂😂, pakati is 🔥.. Ati nde inu mungadye, ine osadya?? Mfana wa Evidence😂😂
Pastor Ntebs hahahaah.......Akuti mkatikati mwa ubusamo muli munthu.....
Kwamvuta 🔥🔥🔥🔥🔥 paliponse pakukanika kukhalika kuchoka wa ujauja basi😂😂😂😂😂😂😂
Ife tidya,,, zinazoso zikabwela tidya 😀😂😂😂😂
Gani ndi pat amandisangalatsa nsaname ❤❤❤
🤣🤣🤣🤣pakati kuno wayaka moto 🤣🤣🙌🙌. Achemwali anu mwapanikizatu koma
Nina ur #1.. Evidence beyond reasonable doubt
😂😂🔥🔥🔥
Chaka Chino muli fire 🔥 mukuitha kwambiri koma chonde kazitalikirapo mumatifira
Pakati akuyatsa moto ovuta kuzimitsa🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Komatu pakati akutamika kwambiri kkkkk akumane 😂😂
Mzimu oyela ulipaliponse 😂😂😂😂😂
Wow wow apa nde zafikatu pa crimax
Give Pakati his award😂😂😂😂
You guys need to go international! You are good!
Pakati pa Usiku😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Eeeeeeeeeee ayayaya
Nina simunthu wamba,,,,amakwana mfanayo.Watching in South Africa
Chuoneka chopepera chi Hyphen 😂😂😂😂😂😂
Akupemphelerana ku Doogles😂😂😂
😆😆🙌🙌
Abusa Amatha eshhh. Amunakowa akuoneka opeperatu.🤣🤣 Hyphen mwamuonjeza.
Keep moving guys zili bwino ndithu
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Koma adah akuti Chikuoneka chopepelatu kkkķkk
Kkkkk akuti Koma nde chikuoneka chopeperatu🤣🤣🤣
Kkkkkkkk eti man 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣 km Ngozo nde kulusatu iih.
Evidence 🙌🙌🙌
Koma Wakuda wangalusa akuwazunza chemwali ake🤣🤣
Pakati is my favourite I tell you 😂😂🤣
And also mahope a Connie why are you ronning 🏃
😂😂 he doesn't want to die
Iiiiiiiiii ngozo serious imeneyo 😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
First things first.....sangie wafunsa a 5years Aja ndi inu??😂😂 Bwanji simunamuyakhe...komanso angozo chidhindo chanu chili kuti uncle amwana......😂😂🙌🙌🙌 Also pakati is the real deal amwene...it's the way he was calling the wetaaaaa!!!! for me evidence mmanja.....mmakwana guys
Camera lero 🔥🔥💥
😂😂😂😂koma guys eeee your killing it for sure
Koma pakati zokhuza umboni
Ndie abutsa mwati hyphen ndiotani kuchitila umboni ndikamamuudza tu. 🤣🤣🤣🤣
Ife tidya zinazoso zikabwela tidya 🤣🤣🤣🤣wakuda wangalusa💪
Thankx guys mukutimvesa kukoma keep it up💥💥💥💥💥💥
Mumakwana guys
Go ahead
Pakati blackmailing your own sister 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Ngozo protection imeneo sikuthawa mlandu wina kumeneko🤣🤣🤣🤣 Nina for me🔥😂😂
😂🤣😂🤣 mpaka ndaonera kawiri blacknina ayi zikomo
😂😂😂😂😂ati chikuoneka chopepera,,walakwa wakongola munthu
Usauver anakonza🤣♥️🤣
Its Black Nina for me hahahahahahaha akuti amuna ena ndinu odala zikabwera tidya izinso tidya 😜😜😜😜😜😜😜😜🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Pakati ndi more😁😁😁😁
Ineso ndikukaika ngat Ganizan zot akulu ameneaja agwila corne ndakaika
HaHahahahaha koma bar imeneyi idzatha kkkkk
Man Gan, ada awowo sangagwiredi Connie ndiaphuma😂😂😂
Best line ever,,😂😂😂😂
Koma pakatiyu ndi Zoba kwabasi eeeish it's a pain in a ass ase. 😂😂😂😂😂
Ati akuoneka opepela mamunayi 🤣🤣🤣🤣🤣
Black Nima 🔥🔥❤❤ iweyotu sichiphingo 😂😂😂
Pakati😂😂😂😂 fire
Pakati wabwera kudzakhala uyuyu🔥🔥🔥🔥 remember evidence 🤣🤣🤣
Kma iweyodi ndi pakati aise abusa achisiya chakudya akuchifuna😂😂😂nde mwati ngozo kulusa odi uko kmatu wakuthawani😂😂😂chidindo😂😂😂
😂😂😂🚶tidya zinazoso zikabwera tidya
Weta!!!!! Hahaha! Pakati ndi evidence yake pheeeeee! Kumastand kudyerela kkkk
Not Ganizani getting catfished💀
Kodi cha KHUMI chikupitilira🙌🙌🤣🤣🤣
Eti muchimwene wako akubwelatu🤣🤣🤣🤣
Kkkk koma Pakati adha....ineso zikabwere ngat zomwezi...Amatha acting nsaname
Black Nina 🤣🤣🤣🤣🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Hahahaha ntebe umatha
"Chikuoneka chopepera
The title😂 musandijambule
Nice one 👍 big up Nina
At moyo ukanakhala galimoto🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 akasika
Ntebede lero wadzaa😂😂😂🙌
Munakumana madolo mukubhebhesa 😃💥💯
Komatu pakati eeeeh apole 😂😂😂😂
Man gani amatiwaza
Kmanso abusa aaaa🤓 at mlongo wako uja ukumudziwa pamutu pake paja sipamayenda
You made my day guys 😂😂😂😂
Pakati is a menace 😂😂😂
A very big threat! Akufunika kumusowesa