Report La Ndege Ndi Manyaka - Pastor G Shumba

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 10 жов 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Pastor G. Shumba comments on the preliminary report regarding the Chikangawa plane crash, which has been released by the German Federal Bureau of Aircraft Accident Investigation (BFU). He refers to it as "Manyaka."
    Ku Nyasa VoiceBox, abusa a G. Shumba athirira ndemanga pa lipoti loyamba lokhudza ngozi ya ndege ya ku Chikangawa, lomwe latulutsidwa ndi bungwe la Germany Federal Bureau of Aircraft Accident Investigation (BFU). Alitchula kuti "Manyaka."

КОМЕНТАРІ • 78

  • @mariezorgen7735
    @mariezorgen7735 Місяць тому +3

    Lord save your people in malawi please,,with also rosary in hands or necks ,,,they need your support

  • @JonesChilonga
    @JonesChilonga Місяць тому +2

    Ili si report imene amalawi amayembekezera Pali mafunso wochuluka amene amalawi sanayankhidwe report iyi ndi yabodza

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os Місяць тому +4

    Vuto ndi Asilikali athu safuna kuchitapo kanthu

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp Місяць тому +3

    Mtengo udakali chiimile kma anthu onse anafa,it does not make sense

    • @ColetteMalunga
      @ColetteMalunga Місяць тому

      Eti eti? Anthu anavularira muja basi ndege kuphwanyikiratu koma mtengo kungowazika? 😂😂😂😂

  • @MPHATSOKALUWA-lm2uy
    @MPHATSOKALUWA-lm2uy Місяць тому +2

    Ndipo ine dabwi out ndege yinayamba yayendapo pa 4.5m

  • @JonesChilonga
    @JonesChilonga Місяць тому

    That's great pastor Shumba mukugwira ntchito yabwino yomenyera ufulu wa anthu wosauka

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi Місяць тому

    Osamati abusa plzzz muziti andale ife tikukunveserani

  • @JohnFrank-cg1yh
    @JohnFrank-cg1yh Місяць тому

    Vuto ndi lakut moses kumkuyu adanena kut blackbox ilipo ayisunga ndie mu report likuonetsa kut blackbox mudalibe so anthu akhulupilire chati

  • @GilbertFabiano
    @GilbertFabiano Місяць тому

    God will reveal the secret as we believe, there is power in rosary that the vice president hold in his hands.

  • @VanessaAlinafe
    @VanessaAlinafe Місяць тому

    Mvuto ndilakuti timangoyankhula pakamwa anthu akuyeneladi kuchoka chakwera sitkumfuna ngakhale atachoka lero komaso adziwe komwe kunapita azibale anthu nayeso azapitakoko

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi Місяць тому +1

    Akutitola osati masewera zoona lingakale report ilo zoona a Malawi?

  • @MarkGonda-qr4vm
    @MarkGonda-qr4vm Місяць тому +2

    Ndi nduna zake zomwe mbuzi zokhazokha

  • @davidbulla5128
    @davidbulla5128 Місяць тому

    😢A SAULOS 😢😢😢😢😢

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 Місяць тому +1

    Ashumba tagokafufuzani inuyo mutiuze zangwa ndege zingati chaka chino padziko lose lapasi m busa uyu ndimbuzi ya muthu

    • @isaacchiwaula731
      @isaacchiwaula731 Місяць тому +1

      Nanga m'busa wanzeru angamayankhule zimenezi, amene watulutsa report ndi MCP kapena ndianthu aku German? Aaaa

    • @SydneyMwale-u9w
      @SydneyMwale-u9w Місяць тому +2

      Zoipa ziyenera kulankhulidwa ndi aliyese .taganizani bwino kafedwe ka anthu inu kapena muli limodzi ndi chikangawayo .muzingofera kudzenje basi _ tiwopa chani _ zautslu

    • @BensonChilundu
      @BensonChilundu Місяць тому

      Mbuzi ndi iweyo.Kwanu sikudachitike maliro eti?Dziwa ichi,Chakwera wakoyo nonse mudziwona ndipo ndikunenesa mudziwona.Ifetu sitikufunatu MCP ayi ngati mukuganiza kuti mupitilila 2025 mpaka 2030,ng’ooooooo chipani chapita ichi basi takuyesani koma mwalephera

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 Місяць тому

      @@BensonChilundu iweyo upidulapo chyani kod or unene president ngati ulibe ufa ulibe basi or utatukwani dzina Lalo silisitha koma so ndalama ya u president sudzalandilapo or ya u mp ayi limbika tchito alekere omwe amadyera mu ndale palibe pindu lathu apa or tilongolole mwayi Sala Dana chomwe anakoza mulungu iweyo sungasithe gwira tchito uwone kt panga bwanji chaka chikubweracho

  • @MebleNgulinga-hi6rg
    @MebleNgulinga-hi6rg Місяць тому

    Afiti awaaa akunamizira mtengo poti mtengowo sulankhura? Mulungu akuoneneni inuuu onamizira mtengonu

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka Місяць тому +1

    Zafikapa Amalawi asatiletse kulira 😢😢😢 Chilima anaphedwadi tsutsani lero kulibe Chifunga pa dzana ankati Chifunga hahahaha mwalemba madzi takudziwani

  • @MarkGonda-qr4vm
    @MarkGonda-qr4vm Місяць тому +3

    Kumalawi pano tilibe tsogoleli ndipo chakwela sakudziwaso chimene akuchita kaya mwina mizimu ya anthu aja ikumuzunguza mpake akumangoyendayenda zinthu zopanda pindu

    • @DanielJuwawo
      @DanielJuwawo Місяць тому +1

      Ndimanyazi ndichifukwa chake sakukhala kumalawi kuno iyitu ndietu simalawi wakare wanu uja Ayi umbon tikufuna weniweni

    • @MarkGonda-qr4vm
      @MarkGonda-qr4vm Місяць тому

      @@DanielJuwawo aziona sinthawi yakale ino

    • @SydneyMwale-u9w
      @SydneyMwale-u9w Місяць тому

      Munthu mmpaka ku German ukakwer njinga mizimu ya chilima nd anthu 8 aja afunthadi chikangawa

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 Місяць тому

    Mbusa wakeyo ndiye amowa omwewatu

  • @ImmanuelndagomaKondowe-n1v
    @ImmanuelndagomaKondowe-n1v Місяць тому

    Zpangizo zomwe sizimagwira ntchitozo anawononga mwafka

  • @KondwaniLimbe
    @KondwaniLimbe Місяць тому

    Tulusani report yanu abusa nafe timve

  • @JosephNambazo
    @JosephNambazo Місяць тому

    Alembe lake report nda iwe opusa eti ukuganiza kuti Kufa kwa anthu onsewo ndizosangalatsa mbuzi ya chabe iwe chitsilu iwe

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Місяць тому

    ndizitsiru za mcp zilira sizinati kuja kudacha anthu tidazuka, ndipo musathawe

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl Місяць тому

    Anamachende amcp musaone amalawi kupusa I nu agalu ndi opusa kwambiri mukwanamiza ana

  • @EdwardGeorgeKasabola
    @EdwardGeorgeKasabola Місяць тому

    Nankha ma 4n awanthu onsewo anatengaso ndi mtengo omwewo

  • @KondwaniLimbe
    @KondwaniLimbe Місяць тому

    Inu abusa mumafuna kumva chani zangozi

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda Місяць тому

    Afiti enieni

  • @IbraTaulo
    @IbraTaulo Місяць тому

    Tiyeni tigwilane manja pofna kuthana ndi zigawengazi

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 Місяць тому

    A Shumba anthu angokumenyani komaso mungomagwidwa nazo izizi coz mukuzitenga ngat ndiinu anzeru koma ndiinu opusa kwambiri,,,,,,,i think ndilekere pomwepa koma mufa ndizomwe mukukambazi sure

    • @SydneyMwale-u9w
      @SydneyMwale-u9w Місяць тому +1

      Ndye zinthu zabodza tizikhala cete xopusa basi😊

    • @ConeliousTandwe
      @ConeliousTandwe Місяць тому +1

      Don't silence anybody....freedom of speech....onse anafa mmenemuja kunalibe WA MCP .....UTM ....set up.....but there is God in heaven

    • @ColetteMalunga
      @ColetteMalunga Місяць тому +1

      Anthu amaganizo ngati anuwa akulu mpake dziko lilowa pansi. Mufuna anthu adzisekerera zopusa mudzina lokhala mtumiki? Sitinafike kumwamba, we can't pretend to be fine because we are Christians. Polakwika tidzudzule pomwe tikukonzanso moyo wathu wauzimu podikira kubweranso kwa ambuye wathu

    • @Mphangala
      @Mphangala Місяць тому +1

      Iweyo ukumupyeza Shumbayo uli ndi ufulu omutseka munthu pakamwa kuti alekeletu ndiye Shumba si Malawi alibe ufulu alankhula zakukhosi..........?
      Kodi bwanji anthu mumakonda kupanga support zinthu zopusa, Kodi imakhala dyela kapena chani kweni-kweni Oooooooo! Kusonyeza kuti ufulu wa munthu monga Malawi kulankhulapo pa zochitika za dziko lake ndikulakwitsa.........? Komatu chomwe mungadziwe ndichakuti omwe mukuti ali pa udindowo adalembedwa ntchito ndi a Malawi omwewo omwe mukuti ndi zitsiluwo.
      Tizikumbuka mawu awa kuti Mbalame yowulukitsa idaphonya chisa ndipo ukakwela pamsana pa njovu usamati pansi palibe mame, mlimi wa mzeru sachita choponya khasu pobwelela kumunda pomalizila penipeni kholo la mzeru silinyoza mwana wa ku njila chifukwa cha chuma chopanga nonse zotelezo Yehova Mulungu amalanda ndipo Yehova Mulungu mngwakumva mwansanga kupempha kwa ana amasiye okalamba ndi ovutika kotelo kumasala ndi anthu chifukwa zilango Zina tizaziyamba kuzilandila tili pansi pompano monga adachita Mulungu wathu wa mwambamwaba kwa mfumu Davite polakwila Uliya Muhiti pa ntchimo logonana ndi mkazi wa msilikali wake kotelo Mfumu Davite idalandila chilango pansi pompano kamba kosawugwila mtima ndi kufuna kuti zonse zabwino zikhale zake.

  • @GuejendraMk
    @GuejendraMk Місяць тому

    Mbusa ndiwandaletu.

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Місяць тому

    Dziko likuyenda bwino ili, Chakwera mpaka 2030 boma

  • @IbrahimMatola-h4i
    @IbrahimMatola-h4i Місяць тому

    Chakwera achoke mboli yamake

  • @PrinceMzava
    @PrinceMzava Місяць тому

    Koma ndaseka😂😂😂😂

  • @ColetteMalunga
    @ColetteMalunga Місяць тому

    Hahahahaha mukukamba zoona, mpaka ndege kuomba mtengo? Imauluka mmunsi mwake motani? Nde ngati imauluka mmunsi choncho nde anthu onse mkufa atavulala chonchija? Mabodza okhaokha. Amalawi tiyeni ku mademo, izi sizikufunika kusekerera

  • @ImmanuelndagomaKondowe-n1v
    @ImmanuelndagomaKondowe-n1v Місяць тому

    Anawononga mwadala

  • @MandressMbebe.kundwe
    @MandressMbebe.kundwe Місяць тому

    Iwe mesa ndiwe m'busa? Titero kut umenewu ndi ulaliki.Mumanamizila ugali eti yambani ndale akulu.koma mudziwe kut DPP Sidzatenganso BOMA

    • @ColetteMalunga
      @ColetteMalunga Місяць тому

      Aliyense wakhudzika akuku, mafumu, atumiki, akhristu ndi wina aliyense wakhudzika. Kukhala mkristu, mtumiki or mbusa sizikutanthauza kuti asayankhule pazolakwika zochitika mdziko mwawo. Akupanga express ma views awo 😊

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o Місяць тому +1

    Ashumba siyani ubusawo tangokhalani wandale

    • @ThivadoartistDyson
      @ThivadoartistDyson Місяць тому +1

      Iwe galu sumatha kudziwa kt azibuza ndi azitzogoleli athu, mumadana ndichilungamo.

    • @ThokoLungu-tq6pw
      @ThokoLungu-tq6pw Місяць тому +1

      Chifuk akunena za chilima? Ukakhala m'busa ndekuti Suuima achilungamo? Anthu 9 amatiphwetekatu

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g Місяць тому

    Soonadi anduwa akupadi choke agalu wa atikwana

  • @YamieManda
    @YamieManda Місяць тому

    Kodi iweyo ukuyakhulawe osapita kufufuza,,

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga Місяць тому

      Kagwere uko naweso , takasambeni uko. Ma press briefing mmalankhula ndi report parallel nde mufuna anthu asafuse??? Kapena muwaphaso onse

    • @TiyamikeMakande
      @TiyamikeMakande Місяць тому +1

      Kuteleku inu mwakhutitsitsidwa nalo report lo?

    • @YasenYasen-q9g
      @YasenYasen-q9g Місяць тому

      Iwechizilu chamundu galu ifetikulila ifaya chilima

    • @SydneyMwale-u9w
      @SydneyMwale-u9w Місяць тому

      Pany

  • @FaysonChimbalanga
    @FaysonChimbalanga Місяць тому

    Kape wa dpp uyu

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 Місяць тому +1

    Lemba lako report mbusa wa fake iwe lembani lanu

    • @TiyamikeMakande
      @TiyamikeMakande Місяць тому

      Kuteleku inu mwakhutitsidwa nalo report lo?

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 Місяць тому

      @@TiyamikeMakande mesa atulutsa nanga lichokera ku mwamba

    • @YasenYasen-q9g
      @YasenYasen-q9g Місяць тому

      Uligulumo iweyo

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms Місяць тому

      Wa fake ndiwe asayeneni anthu ayakhule naweso ndi wakupha

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 Місяць тому

      @@Eric-gb9ms palibe amene anamupha ameneuja koposa yesu yemwe analola kuti akhoza kufa moteromo

  • @abdulsalammkwepu3321
    @abdulsalammkwepu3321 Місяць тому

    @ndege inaomba mtengo wa tsabola😂😂

  • @MathewpeterLemon
    @MathewpeterLemon Місяць тому

    Koma ndaseka😂😂😂😂