A President Ayenela Kukafika Pamene Panagwela Ndege - Samuel Lwara

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 8 вер 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara urges His Excellency the President, Dr. Lazarus McCarthy Chakwera, to visit the site of the plane crash that killed the Right Honourable Saulos Chilima and eight other Malawians while he is touring the northern region for official duties.
    Pa Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara apempha mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus McCarthy Chakwera kuti apite pomwe panachitika ngozi ya ndege yomwe inapha a Saulos Chilima ndi a Malawi ena asanu ndi atatu, pomwe akuyendera chigawo cha kumpoto kukagwira ntchito zina.
    #malawi

КОМЕНТАРІ • 125

  • @mrsmkjb2411
    @mrsmkjb2411 Місяць тому +19

    Indeed! This is the truth. This guy is right…💯! That is the prerogative of the Office of a Head of State! It is expected of him! Everywhere in the world, a huge tragedy such as this one has always been acknowledged by the Head of State! ! This was the Country’s VP! 😢😢😢😢😢😢.

  • @user-ks3uw8gj8h
    @user-ks3uw8gj8h Місяць тому +5

    Very True The President is always acting like he is not in the Country, can we just make a post of, the Lost President in Malawi,out of all the insults and Complaints that our people Has been complaining it's in vain, he cant even come out and address the nation, illiteracy of the most Malawias ikutipweteketsa,Zimafunika muzisonkhanomo asamapezemo Anthu, that's the response that the people are Angry with his conduct, This is the Worst President ever ever that never happened in the History of Malawias,

  • @augustMag
    @augustMag Місяць тому +7

    Mr Samuel mwayankhula zamphamvu Kwambiri Ambuye akusogoleleni ❤❤

  • @JuvenileDebwe-bv8ow
    @JuvenileDebwe-bv8ow Місяць тому +8

    Samuel is a true son of Nyasaland indeed

  • @lightwellsilumbu
    @lightwellsilumbu Місяць тому +8

    Mr Samuel Lwara mwandilankhulilako. pena zinthuzi zimdabwisa?. Bwana athuwa ali ndinkhope ofasa bwino koma zochitikazi pena zimabweresa mafuso.

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa Місяць тому +5

    Zoona brother LWARA your talking truth GOD bless you go ahead

  • @ronaldordinga6537
    @ronaldordinga6537 Місяць тому +3

    Kuyankhura kwabwino kumeneko,,,, dzimenezo nde nzeru lwara big up

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Місяць тому +8

    Chiuta wamutumbikeni a Lwala

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m Місяць тому +2

    Vuto ndimaliona ine azisogoleli anthu timawasankha amankhala odziva olo utawalangiza bwanji osava

  • @NorahSomanje
    @NorahSomanje Місяць тому +5

    Zowonadi choyambilila akanapitadi pamalo angoziwo, koma pakuti umuthu alibe sapitako

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Місяць тому +4

    Amawanyamula anthu mmalole kuti azikanyengana, azimuna opusa amalola azikazi awo azikavinila chakwera,
    Rest in peace Ryton Mangochi you have fight a good fight

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Місяць тому +7

    Anthu akumpoto toiyeni tiwadyele ndalama koma osawavotela, ndalama landilani ndithu, kumachenjela patawuni

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj Місяць тому +1

      Kumangochi anthu amayakhula zimenezo koma mcp idawina komaso izawinaso

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Місяць тому +1

      Chikangawa team 😂😂​@@SaidiMbawa-st6bj

    • @user-ww9rj2wx8d
      @user-ww9rj2wx8d Місяць тому

      Iwe kuno anthu anabeledwa chifukwa anthu akumangochi ndiosaphunzila wamva ku mpoto anthu ndiophunzila wamva​@@SaidiMbawa-st6bj

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 Місяць тому +2

    Si anthu awa ndi mikango

  • @user-hx6jl2jq9j
    @user-hx6jl2jq9j Місяць тому +2

    Chikangawa chakwera zooona nkumachita kumuuza zochita, uku ndiye kusadziwa nchito. Zooona mpaka pano chikangawa akalibe ukaona pamene anagwetsera ndege

  • @user-gd2kl1fx1q
    @user-gd2kl1fx1q Місяць тому +2

    Nice speech lwara, mind u anthu anali mmalore kukavinira chakwera ndiakumíz anakapasidwa ma 2000 achina Harry plus a speaker send those lorries northerners are angry with him and afune asaufe

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses Місяць тому +2

    Ndipo palibe president amene wapanga mbiri yachabe ndikutukwanidwa ngati chakwera.

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi Місяць тому +2

    Ndagwilizana nanso 🤝

  • @RanaQari-py4bd
    @RanaQari-py4bd Місяць тому +1

    U good talking very nice

  • @user-fh7sd6gp3f
    @user-fh7sd6gp3f Місяць тому +2

    Anthu amene amapita KU misonkhano ya MCP a kumpoto sanavutike the last 4 years.
    Please northern region wake up Chikangawa is not helping at all

  • @user-um6yo6nc3e
    @user-um6yo6nc3e Місяць тому +1

    Ine Mmati adakawonapo kaletu padagwera ndegepo😢

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko Місяць тому +1

    Aaaaaaaa mr God bless you so much walankhula bwino kwambiri

  • @andreabanda7838
    @andreabanda7838 Місяць тому +1

    Very true. These were very prominent people

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 Місяць тому

    Lwara today you are really talking as a citizen of Malawi

  • @RossanaMitha-tl9in
    @RossanaMitha-tl9in Місяць тому +1

    You are right 👍

  • @user-rd4ft9nd8t
    @user-rd4ft9nd8t Місяць тому +1

    Powerful vbro

  • @DivineMercy-df2pu
    @DivineMercy-df2pu Місяць тому +1

    I second this akafikepo ndithu.

  • @user-vp6fv2mu6i
    @user-vp6fv2mu6i Місяць тому +1

    Alibe respect mr chakwera

  • @user-rz8qp8tj8e
    @user-rz8qp8tj8e Місяць тому +4

    Koma uyu 😂😂😂ai ndilibe mau yoooo

  • @collennyadile8179
    @collennyadile8179 Місяць тому +1

    uku ndiye kuyankhula chilungamo

  • @MEGANABIGAILMNTHALI
    @MEGANABIGAILMNTHALI Місяць тому +1

    We love u

  • @Lingstone-r3z
    @Lingstone-r3z Місяць тому +1

    Really we want to know, for that,, thanks

  • @michaelcharles-p9v
    @michaelcharles-p9v Місяць тому +1

    😢😢😢😢 we are not Happy at all RIP SKC 😭😭😭😭😭

  • @user-rz8qp8tj8e
    @user-rz8qp8tj8e Місяць тому +5

    Anthu ndi amene akususuka becz of money busy kukwera rorry not me i can’t never

  • @vicshyma5644
    @vicshyma5644 Місяць тому

    No this president has absolutely no remorse. Himself Chakwera, it's a " mission accomplished game " umunthu mulibe

  • @user-xb1re8dl3v
    @user-xb1re8dl3v Місяць тому +1

    🎉

  • @frankdomingo1109
    @frankdomingo1109 Місяць тому

    Or he is hoping that this matter will die naturally...and pple will forget about it!!😮

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Місяць тому +2

    Lwawa iwe ndikatundu 😂 tikamalakhura pamafunika school Jeannie wise fuso kodi solomo adalekezera chani Kiri inhale fumu ya zeru ,asiyeni abatokosa mavu pa chisa 😂

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Місяць тому

    Ineyo kupanda kukumverani a Samuel Lwala sindimva bhoo 😂 ndipo mudzindiuza kuti nditumize ya bundle every morning and evining. Ever since l started following this man last year, ndinaona nzeru ndi chilungamo mwainu koma Vuto kusamva atsogoleri athuwa. Moti SKC akanawaturuka a mcp bwenzi pano tili nawo a president athu a Chilima koma sungamutsutse mulungu RIP Saulos Chilima 😢 A Lwala musaope komanso osadzachita dyera ndianthu oipawa

  • @user-kj6qj1md5e
    @user-kj6qj1md5e Місяць тому +2

    Mumakwana bwana tikamati boma ili ndilopepela timanenela zimenezi

  • @paulvimbamvula9508
    @paulvimbamvula9508 Місяць тому

    Kutukwana president ndi umbuli chabe....ku Malawi zikuoneka sazakhalapo mdi president wabwino aliyense ndioipa,....kuseweretsa president.
    Ndiye umafuna dziko lisayende asamalamule dziko kamba ka imfa,or ukutanthauza Vice president asagwile ntchito basi daily kukhale maganizo aimfa

  • @paulvimbamvula9508
    @paulvimbamvula9508 Місяць тому

    Kuwona pa malo pa ngozi president sikukakamiza,mdipo president simunthu woti basi easily apite paliponse popanda programs......

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Місяць тому +1

    Apite chakwera akaoneko kumene kunagwera ndege

  • @FlorenceNkhata-f5l
    @FlorenceNkhata-f5l Місяць тому +1

    Kutengeka amalawi

  • @PiusChawinga
    @PiusChawinga Місяць тому +1

    Akudziwako kale

  • @MadalitsoMtambalika
    @MadalitsoMtambalika Місяць тому

    Ndipo kuyambila kamusu kufika lero amene wapanga mbili yoyipa komaso chikhalidwe chonyaza nde ndi wakwela 😂😂😂😂 kufika lero osakaona pomwe anafela chilima uyuyu afa kuwawa sedi 2025 sifukwa ife tinalusa sogoleri wathu wamasomphenya koopsa 😢😢😢😢😢 kuiwala kusanifuta sedi usisiwa iwe wakwela kumene uliko ife monkha makozana omumonda SKC tiona umo sithele

  • @DanielChiumia-v4r
    @DanielChiumia-v4r Місяць тому +1

    Zikomo Lwala mwayankhura bwino koma vuto la Malawi mulibe chilungamo Oro atabwere akafukufuku azabisabe chilungamo

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507 Місяць тому

    You are so brave Samuel

  • @kennethnyaluso7503
    @kennethnyaluso7503 Місяць тому

    Dyera ndiyomwe yakula basi a Malawi.

  • @user-xb1re8dl3v
    @user-xb1re8dl3v Місяць тому +1

    Awuze

  • @paulvimbamvula9508
    @paulvimbamvula9508 Місяць тому

    Ayi akuzilankhulila yekha akamati akumpoto,ndale zosamanga dziko

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam Місяць тому

    Guys chakwelatu ndi muthu wabwino koma amene amuyipitsa ndinduna xake zokupha chilima inali pula I yachakwela ayi koma man nduna xake zamcp amayi somba imodzi ikawola mudengu zonse zimawola guys chilima rip

  • @user-ln3zx6wo4w
    @user-ln3zx6wo4w Місяць тому +2

    Exatly

  • @johnbullyohanittokasikizim7127
    @johnbullyohanittokasikizim7127 Місяць тому

    Nkhalu walije Chakwera

  • @MEGANABIGAILMNTHALI
    @MEGANABIGAILMNTHALI Місяць тому

    Ngati sakukafika kuchikangawa achakwela ndi Bambo asikono komwe ndege inagwera ndiye kuti a kuvomeleza kuti ndege igwe komanso anthu aja aphedwe napangiska ndiyedi.

  • @lizzymotika3895
    @lizzymotika3895 Місяць тому

    Big man ulemu wanu

  • @IanAllstal
    @IanAllstal Місяць тому

    Ndiposo onse omwe anagwesa ndegeo tizikapeza pa Malo angozitu

  • @Aubiekenneth
    @Aubiekenneth Місяць тому

    Akutuma iwe a dpp ulephera

  • @elizabethbalalasdp721
    @elizabethbalalasdp721 Місяць тому

    Zoonadi, inenso ndikudabwa kuti saakukhudzidwa kuti akaone pomwe panatenga moyo wamng'ono wake bwanji? 😢😢😢 Kapena akudziwapo kanthudi that's why he is not interested to visit the place!😢😢😢😢😢😢😢

  • @WillyZuze
    @WillyZuze Місяць тому

    President opanda molaro,ndichifukwa amakatenga anthu kwa nsundwe pa lory kupitanao ku nsonkhano za u savage

  • @zondwasekhonje3235
    @zondwasekhonje3235 Місяць тому +2

    Unenesko

  • @InnocentnMbale-zq8pk
    @InnocentnMbale-zq8pk Місяць тому

    Mwayowoya akulo eti anthu akukakamiza kuti ayankhulepo za ngozi moti iye ndimusogoleli basi sangalankhule wuyu ndi nothing ndithu chikangawa chikangawa

  • @paulvimbamvula9508
    @paulvimbamvula9508 Місяць тому

    Abusa analankhula zolakwika ndipo kumangidwa kwao boma silinalakwe

  • @innocentbanda-zc6zf
    @innocentbanda-zc6zf Місяць тому

    Mbuzi yamunthu iwe palibe chomwe ungapange kapolo iwe

  • @user-xb1re8dl3v
    @user-xb1re8dl3v Місяць тому

    Brother kumayankhula bho

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b Місяць тому

    For sure dear it's true Nothing

  • @tamalangoma2765
    @tamalangoma2765 Місяць тому

    Only God can answer your questions , A chilima anafa pa ngozi ya ndege .

  • @sanlakedickson6780
    @sanlakedickson6780 Місяць тому +1

    chipedwe mesa anapha chilima

  • @wittinessnkhokwe
    @wittinessnkhokwe Місяць тому

    Chigawenga sichikhala ndi chisoni anthu awa anapangana ndi utsi kuti amuphe nzawo

  • @paulvimbamvula9508
    @paulvimbamvula9508 Місяць тому

    Akulankhula motumbwa,mdipo mwamatama

  • @Aubiekenneth
    @Aubiekenneth Місяць тому

    Kod woyamba kufa ndichilimayo opusa iwe makutu ako

  • @DanielJuwawo
    @DanielJuwawo Місяць тому

    Anthu adatisiya 10 June akupita lero kukatani

  • @user-gg9hw4oj2v
    @user-gg9hw4oj2v Місяць тому

    🔥🔥🔥🔥💪💪💪💪💪

  • @user-nu3rb5fj2i
    @user-nu3rb5fj2i Місяць тому

    Alibedi kalidwe mgalu meneyo

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507 Місяць тому

    Osaopa

  • @RaphaelKweve
    @RaphaelKweve Місяць тому +2

    Luwara yankhulani , kkkkkkk

  • @Chifundokapondodza-f6d
    @Chifundokapondodza-f6d Місяць тому

    Akaone pomwe ndege idagwera kapena akaone malo amene anthu adathedwera

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri Місяць тому

    Mbambande

  • @user-dx4zu1wv4q
    @user-dx4zu1wv4q Місяць тому

    Timakunyadila man kwambiri

  • @user-zv3cy2xj5p
    @user-zv3cy2xj5p Місяць тому

    Alwara mulije zeru bwanji simunanenepo za anthu aja anaphedwa ndi DPP pa 20 july si ukunenapo bwanji? Bring the solution, even president goes there where t he earoplane made an accident is just meaningless because chilima sangadzuke, anafa anafa basi , chitukuko chaboma sichingayime chifukwa chilima afa

    • @UseniMailosi
      @UseniMailosi Місяць тому +2

      Mademo aliyese amasiwa kuti ene mistake mukosa kumwalila

    • @ibrahimchalimba5985
      @ibrahimchalimba5985 Місяць тому +2

      Even a mcp apangako ma demo anthu ndikumwalira then don't compare ma demo ndi chiwembu this is a murder not mademo😢 and ngozi ikachitika even ya nyumba mwanu umapita kukapanga check how it happened then iyeyo sakufuna kupitako why??? And why sakuvomela even akubanja kut akawone pomwe anafela m'bale wawo😢

    • @user-ww9rj2wx8d
      @user-ww9rj2wx8d Місяць тому

      Panyo pako iwe chakwela kupanda chilima bwenzi ali president mbuzi iwe

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r Місяць тому

    Jesus is the only true man not this one and Jesus knows everything than man so Jesus will judge us one day chotsani ndale mungafe muli mu ndale zikomo

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Місяць тому

    Vilekani kuunukila magalimoto wazakawenayo asa

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 Місяць тому

    Hahaha 🤣 .. mukufuna afe ndi bp? Anamugwesa yekha

  • @Yahiya-wm8nd
    @Yahiya-wm8nd Місяць тому

    koma lero mkuluyu walankhula eeeee

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Місяць тому +2

    Komaso pano anthu ambili ndinu ozungulila mutu pali zoyamikila apa uyu umphawi wamupweteka amangolakhula zopanda zelu chisilu uyu mukhaula pagaraund mcp anthu akuyikonda alesinu dzililani musobva

  • @EdwinMbewe-wu9jd
    @EdwinMbewe-wu9jd Місяць тому

    Ndiye akakafikapo wat will change?

    • @user-ol4cf2oh5u
      @user-ol4cf2oh5u Місяць тому +1

      Athu atapita pa lithipe pa natha athu panja mpaka chiliza dii panasitha chani? Khani ndi respect for those pple

    • @user-vp6fv2mu6i
      @user-vp6fv2mu6i Місяць тому +1

      Kuonetsa umunthu wake kaa

  • @lupakishomalangaelix6606
    @lupakishomalangaelix6606 Місяць тому

    Kkkk koma

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Місяць тому

    Koma anthu ena zelu alibe chingapindule ndi chani kupita kukaonako ngati munthu azukaso

  • @ArnoldKamanga-r6k
    @ArnoldKamanga-r6k Місяць тому

    Basi akudusa pa nthungwa ali phe kusekelela, wakanakhala kuti anafa ndi chakwera first thing chilima akanayima paja asanafike ku mzuzu, anthu tinabwadwa mosiyana

  • @RaphaelHara-tr9iy
    @RaphaelHara-tr9iy Місяць тому +1

    Kape iwe usamanene zinthu mwachibwana bwana tithokoze ziko lakwanthu ndilosauka koma lamutendere ifa ya vp ndiyowawa komaso anthu onse aja koma koma chachikulu kafukufuku uyende wachilungamo kumbari yachakwera ndibwi ndipo kukhara chete chifukwa ukakhara wawonesa mukwiyo you are chief in comander haif population yamalawi anthu antha kumalira khara opusa koma useve zika zamalawi ndi simple kunene koma ?

    • @ibrahimchalimba5985
      @ibrahimchalimba5985 Місяць тому +1

      Tayakhulani bwino Inu tikuyakheni😅😅😅😅

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Місяць тому

      ​@@ibrahimchalimba5985😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @MaggieMuhone-r7m
    @MaggieMuhone-r7m Місяць тому

    Kkkkkkk Kkkkkkk Kkkkkkk nda kunyadilani

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Місяць тому

    Amalawi chakwera tinamuvotera tokha ndeno chaka chamawa tizamuvotereso chakwera ine nizamuvoteraso chakwera azawineso chakwera ndipo azapheso anthu ambiri ni vula yachigumula.makamaka azayambireso kumwera kupha anthu ni vula kusi kwa nyanja kuribe magazi

  • @mzondinkosi1151
    @mzondinkosi1151 Місяць тому

    The problem with you is that you think you are very wise. You are not.

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o Місяць тому

    For what reason za zii chimdala iwe

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o Місяць тому

    Tamulandira kwambiri ife a kumpoto ndiposo timamukonda so who r u Mr lwara chitsiru Cha munthu iwe

  • @BrightonEnockEnock
    @BrightonEnockEnock Місяць тому

    Iwes ndi galu bwanji

  • @RaphaelHara-tr9iy
    @RaphaelHara-tr9iy Місяць тому

    Ziko lakwanthu ndilabwino koma inu mukukakamiza chakwera akwiye mupesaa anthu ambiri anamwalira nthawi ya bingu kumupoto asilikali akwanthu ndiabwino koma akati kwiye ife nthawa from lilongwe to muzuzu thanwi yapayoniya zina mukamanena kape iwe you must balance ubwinondikuyipa koma kafukufu uyende bwino cheni cheni chiziwike after that tijaje munthu muzapetsa anthu kape iwe

  • @LameckBanda-ph2nh
    @LameckBanda-ph2nh Місяць тому

    Mukunena zowona akawoneko komwe kunagwa ndege

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Місяць тому

    Apite chakwera akaoneko kumene kunagwera ndege