Phungu ndi woimba kwambiri,ngakhale zili nyimbo zakale komabe his songs still make sense today, bible linalembedwa kalaekale komabe likutembenuza mitima anthu lero
Big up Nkasa ❤ I love ur Songs but Malawi is the problem to vote MCP.Nkasa since start music 🎼 gave US message but when to to vote u do Sam mistake. 😂😂😂😂
Nkasa is the one of musician advisor in the country of malawi.....kp it up🤝
I like the songs sung by phungu. I do encouraged 🎉
Phungu ndi woimba kwambiri,ngakhale zili nyimbo zakale komabe his songs still make sense today, bible linalembedwa kalaekale komabe likutembenuza mitima anthu lero
Mwalowa mmalo mwa soldier ndinuyo sopano😊
Phungu's sagacity is indeed from God. He is musician. Brother Nkasa keep on entertaining beloved Malawians.🎉😂
Ndipo chakwera ambuye MULUNGU akuone munthu kuipa mtima ngat imfa eee ndipo chakwera wamuonga Malawi
Legend we love your music
WANUNKHADI MALAWI 🇲🇼 MR NKASA GOD BLESS YOU
What a song.. Big up Nkasa. Sugar Ali pa 3700 now.. Malawi wanukhadi
Gosto de escutar mensagens deste musico
Chakwera adzivere yekha uthenga wabho Mr Nkasa
Koma Nkasa umayiponyeradi kwakuya, ❤woyimba koma uyu
I like this guy too much amaganiza movuta kwambili na nyimo iyi siyandale koma ngamo bsi kuswakuswa sakugawa ma sweet I like once again i like it.
Mfumu kapena kt paramount ya mzeru phungu wa chilonwe ku Zomba Malawian,go ahead phungu
I love this song. You've said it all Phungu
Nice mr mkasa sakumva a poster
Phungu Mulungu apitilize kukupatsa. nzeru zochuluka kuti upitilize kutisangalatsa more fire
Big man kuzatulukila sopano ndi waduka ndi Malawi ndizona simukunama ayiii God bless you always
keep it up mr mkasa god bless u malawi know is destroyed
This man is very creative I'm telling you.mr nkasa more love to you sir
Wanukha malawi🙏🙏 may God bless you my fadah ❤❤❤❤
Big mutchuleni munthuyo kkkkkk mumakwana ndinu prophet
Big up mr Nkasa nice song
Davide mbewe woyeeeeeeeee
Big up phungu,we like your music
Nice song keep it up
Big up my brother,that's Joseph Nkasa whom I know 100,,%
Umakwanira mkasa big up
Nice tune big up nkhasa
I like this song very much the meaning is still elevant &power😂
Very nice song❤
This guy iiiiiiii born for his country
Mr Chakwera please tamvani kulira kwa Malawi
Mr chakwera please Malawi akuvutika kwambili tavani kulila kwa anthu
I like his music it's straight and true
nice song tinenereni basi
Ndiye kuti mavuto a dziko la malawi ndi ogonera. Chifukwatu pomwe ena akuona ngati nyimbo iyi ndi yatsopano koma ayi ndithu ndi zaka za kumbuyo
Big up Nkasa ❤ I love ur Songs but Malawi is the problem to vote MCP.Nkasa since start music 🎼 gave US message but when to to vote u do Sam mistake.
😂😂😂😂
eeeemkasa ndi katundu mumalosera zoooona
Ndipo inu zachabetu kwathu komwe ngati ndife obwela mhh
Akupaseni galimoto chondechonde😅😅😅😅
Komabe zina zikusapotabe kusangalala kuti anthu akuvutika
Etieti zomvetsa chisoni Ku Malawi
Song with a massage❤
Mr Mp indeed things are tough,covid,and Ukraine war are not a good excuse
Nkasa koma pano ali ku Chikangawa awa dyera apa zina kuseri zina awa
Beautiful song
"galimoto yomwe yaononga nsewu yomweyo singakoze, pakufunika katapila adzakonze"
Wanunkhadi Nyasaland Maka nthawi ino eeeeeeeeeee
Nice keep it up
Nkasa nthawi zonse amalangiza, komanso kunena chilungamo angokhara osaganiza bwino ndi atsogoleli wo🤔🤔
Mukasa umakwana❤
Mafuno abwno Apte kwa Joseph mkasa,phungu mfumu yacikhalidwe pamaimbidwe amadziko amzeru kwambiri
Mayo dziko langa
Boni kalindo ndi atupele Muluzi akhonza kusintha zinthu tiese amenewa
Upole moto kkk
Ndiye umbuli
Atupele ndi Peter Muthalika
Ñice song
Nyimbo iyii muli uthenga 😢😢😢
Awuze phungu anthu opanda chfundowa,adyera
Mkunena chakwela was ma trip uyu Kodi?
😢😢😢😢 nyimbo iyi inali vumbulutso
Inu ndi nyatwa Mr mkasa
Atupele muluzi azakoza dziko❤
Eeeh this guy dyela too much like father like son, koma ngati akuganiza atupele and chilima waiphonya
Welcom Nkasa kp it up chinyimbo cha heavy Malawi is on for sale koma ndiye wanunkhirathu
Nice
Kkkkkkkkkkk kuimbatu ndikumeneku
Ndithawira kuti 😢😢😢 passport ndi license atseka Malawi watha basi
Nkasa umakwana chakwera has to understand the message
Auze Zions wanunkha
Zoona big
🔥🔥🔥
Amkasa 5000 ilipo gaileni number yanu ndikuthokozeni
Nkasa ndi akamuna
Apadi ofunika D 7 ikonze Malawi
Mumakwana big
Soldier wake uti angamake ndi nkasayo,? Nkasa ndi nkhani zina
Legend
Malawi wanukhadi mukuziwakale
Ndi choncho phungu
Eddie longwe Dada general 2025
Kkkkk mutchuleni timuziwe
Nyimbo yabwera muthaw yake
Mkasa ndiwe mulosi ndipo ulosi wako ndiwolondola
Zoo na big
Double salute mkasa
Tokota nkasa,koma nsaku musiye asauka yekha ndi mowa wake,zolinga ndi zofuna
Ndi mommo phungu
❤❤❤
Phungu umakwana
Kutseri kwake kuja kuli satanic lomwe limatengaponso oimbawo powapereka nsembe oimbawo asakudziwa,nde mudziwe zimenezi ,nde pochita zinthu khalani ochenjera .
Koma ndiye wanuknkhadi Malawi lazaro wanunkhitsa Malawi
IZI tinasankha tokha timati tiyese achinyamata komanso opemphera lero ndi izi. APM amadziwa ndipo anatiuza kuti ngati tikufuna mavuto tivotere CHAKWERA koma ngati tikufuna zabwinobe bola DPP koma ife tinasankha kuvutika ndi anthu amulungu komanso wachinyamata oganiza bhooo.Lero mavuto okhawokha.
A malawi kuvutika chifkwa cha vote yao ai zikomo
Usinda
Amalawi tili pamoto
😂😂😂😂😂Chakwera wanunkhisadi Malawi mfiti ameneyi zedi ya MCP
😅😅😮😢
@@nkopedafter831 😃😃😃Nthakati yoopsa zedi tiigwetsa Chaka chammawa ibwelere kumakalima maganyu😃😃
Mapasaport ayamba kutuluka pamtengo wa 14500
Ndipo zoonaditu
Malawi is on the market
😢😢😢
Timadabwa kuti otiyankhulira aja alikuti
Ndeno nyimbo zako ngat menezi ungapeze 10k views...anzako akulemelelatu zomwe zija iwe busy zandale...fokol
Zovuta
Kkkkk