Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Nkasa always amakwera cholamula ndichifukwa chake amakhala akumenyedwa
Nkasa ndi nkasa tipasire uthenga tiripano ife kumvera morefire 🔥🔥🔥
This is great mr nkasa
Mwakwana achikulile kumeneko ndekuyimba
Umakwana Munthu wamkulu keep fire 🔥 burning
Mkasa inuyo u deserve flowers while u still alive ❤❤😂😂
Wow this is beautifully song ❤️❤️ umakwna
That's a great song bro keep it up
ndimawona ngati nkasa anatha ,ayi ndithu phungu ndi phungu ❤
Well done elder Mkasa,auze akuona ngati AMalawi opusa
Mkasa is a GOAT...he has talent man
Mtondo! I like your flow... Unique...
Legend 🎉 Mkasa nyimbo waigabadza
Please subscribe and share the video
Mr phungu am full time your fan from Zambia, but I need the song called Moyo wachikale
I love this word amene anawononga dziko lathu anali mukulu matako😂😂😂🙌🙌🙌
Ine apo pandiwaza pa Tsogoleri wa mulungu akutafuna gondolosi kkkkkkkk, kukomzekera chani ? Koma akapolo ambuye amasiku ano
Iweyo eeh ai ndi macna apa kuswakuswa bsi palibe wabwino, zoona tizingoyang'ana komweko bsi
Ulemu wanu landilani mr🙏
❤❤❤❤😊 more fire 🔥 Fire 🔥 Fire 🔥 mpungu
Osaopaaa
Good one
Aaaa pa Mkasa Ambuye anakodza, Mulungu azikusamalirani nakupasanibe nzeru zakuya, palibe chosatha mafungo woipawo azachoka tsiku lake ndi limodzi wosadandaula Ambuye akuwona zonsezi, komanso wosamaiwala kuti Mulungu salakwisa amapereka chimene wapempha nthawi zonse akumatipasa chimene tikufuna ndithu. Atsogoleri onsewa timachita kuwafuna eeetu
Big brother keep it up
Great song respect to big man nada
Best song❤
nkasa ulemu wanu 🤗
He is one of the greatest men ,and the prophet
Muli kachilungamo kowawa munyimbo iyi
Mumakwana akulu
Ndikatundu mkasa auzeni atsogoleli autsilu ameneyo
Mkasa Moto !!!!!!!! Tokosa ndithu
anthu tikuzikupizabe mpaka pano😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Mbambande, Bola kwa pharaoh, timadya mavwembe
This is a great hit Bro. Litman from Zambia love this 😅
Thank you so my boss please subscribe
👍👍👍👍👍👍👍
Chilungamo chiikbidwe amaneyo ndi phungu
Mr kasa timaona ngati munathatu koma nyimbo iyiyi landilani ulemu
Big up bro from SA
😂😂😂😂😂nkasa amatha kuyimba
That's true and true phungu
Man mwapha nyimbo iyiii❤❤❤❤
AaaaA phungu Josephy mkasa mukunena zoona amalawi tilibe kothawira tithawire kwa yesu basi
respect big boss
Ndimayesa ya nyuwanitu
Me nkasa more!!!!!!
Nkasa umatha😂
Double salute mkasa
Umakwanila bro.
Waa mbuya mkasa wayimba bwino kwambili
Umakwana kasa
True Phungu Joseph Nkasa is now talking
Nyimbo ya bwino kwambiri.Tili mu ma tsiku otsiriza. Tivomereze dziko likupita kwao ili.Palibe amene adzakonze dzikoli koma Mwini Mulungu yekha basi.
Kumazikupizabe ndi fungo😂😂😂😂
Yaaah tafikadi kubagamoyo
Bwana tisaname mwati ikanpamoto palibe chifukwa kuti sitose tinga pindule ndiyinu koma apapa zafika kuiguputi
Nice
That's is true Mr phungu
Koma Nkasa ndi mphangala pa nyimbo
That's true phungu ❤
Komatu Phungu 😅 mpaka mneneri kunyambita chiswa B 😂
True phungu
NKASA NDI NKASA NDIPO SAZATHEKA KUIMBA MOPANDA KUPANDA KUBISA AI🎉🎉🎉🎉🎉
Mphungu ndi phungu.atsogoleri a chakwera bodza basi ndi chilima wao
Tell them ,remind them time has gone
😂❤nice
This man l like so much
Nkhassa iapa muaimba nhymbo
FUNGO LOSAMVA PEREFIMU😅😅😅
Mbuzi zawathu ngati chakwera
Umakwana mkasa
Bigili man mumatiimilila
Strong song akuva anve
Azibambo 🎉🎉🎉🎉
Mkasa😂😂😂😂😂
Thamps up nkasa
Katswiri pamayimbidwe😂
May soul Rest In Peace ur Exerence
Mwapha❤❤
Zikomo kwambili
Please amene amatipasila mauthenga ngati awawa aziyesetsa kubwela ndi chichewa chomveka bwino 👏!
Phokotso lachule silingalephelese mdipiti wa njovu kumwa madzi?kkkkkkk
Koma phungu😂😂😂
Machine
Mumaita🔥🔥🔥🔥
❤
Tikapuma ku mwamba ndthu 😢
Mkaza kumuyimba satana chalwera ndi chilima
Iyi ndiye ngamo
Umakwana
Respect to phungu wa a mphwai.
Yah that's true
Thank you so much 💓
Mkasa zoonadi ndimaesa kut sukudziwa anthu akulira
Maiku osiliza kwa iweyo ife tidakalipo
Mulunzi channel Anthu olemera omwe anapita ndimadzi
Awa ndi akatundu osasewera nawo
Nothing but the truth 😮😮
Zoona
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Amene anaphwisira Malawi ngwamkulu matako. Fungo losamva pelefiyumu.Enjoying from Maputo.😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Inu ndipungud
Mukunena zoona
Amalazwi munthu osavinidwa osamuika panpandoso
Kodi simurha kulemba?
Phungu nkasa ulemu wanu
Mumakwana man
Mumakwanila broo
Nkasa always amakwera cholamula ndichifukwa chake amakhala akumenyedwa
Nkasa ndi nkasa tipasire uthenga tiripano ife kumvera morefire 🔥🔥🔥
This is great mr nkasa
Mwakwana achikulile kumeneko ndekuyimba
Umakwana Munthu wamkulu keep fire 🔥 burning
Mkasa inuyo u deserve flowers while u still alive ❤❤😂😂
Wow this is beautifully song ❤️❤️ umakwna
That's a great song bro keep
it up
ndimawona ngati nkasa anatha ,ayi ndithu phungu ndi phungu ❤
Well done elder Mkasa,auze akuona ngati AMalawi opusa
Mkasa is a GOAT...he has talent man
Mtondo! I like your flow... Unique...
Legend 🎉 Mkasa nyimbo waigabadza
Please subscribe and share the video
Mr phungu am full time your fan from Zambia, but I need the song called Moyo wachikale
I love this word amene anawononga dziko lathu anali mukulu matako😂😂😂🙌🙌🙌
Ine apo pandiwaza pa Tsogoleri wa mulungu akutafuna gondolosi kkkkkkkk, kukomzekera chani ? Koma akapolo ambuye amasiku ano
Iweyo eeh ai ndi macna apa kuswakuswa bsi palibe wabwino, zoona tizingoyang'ana komweko bsi
Ulemu wanu landilani mr🙏
❤❤❤❤😊 more fire 🔥 Fire 🔥 Fire 🔥 mpungu
Osaopaaa
Good one
Aaaa pa Mkasa Ambuye anakodza, Mulungu azikusamalirani nakupasanibe nzeru zakuya, palibe chosatha mafungo woipawo azachoka tsiku lake ndi limodzi wosadandaula Ambuye akuwona zonsezi, komanso wosamaiwala kuti Mulungu salakwisa amapereka chimene wapempha nthawi zonse akumatipasa chimene tikufuna ndithu. Atsogoleri onsewa timachita kuwafuna eeetu
Big brother keep it up
Great song respect to big man nada
Best song❤
nkasa ulemu wanu 🤗
He is one of the greatest men ,and the prophet
Muli kachilungamo kowawa munyimbo iyi
Mumakwana akulu
Ndikatundu mkasa auzeni atsogoleli autsilu ameneyo
Mkasa Moto !!!!!!!! Tokosa ndithu
anthu tikuzikupizabe mpaka pano😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Mbambande, Bola kwa pharaoh, timadya mavwembe
This is a great hit Bro. Litman from Zambia love this 😅
Thank you so my boss please subscribe
👍👍👍👍👍👍👍
Chilungamo chiikbidwe amaneyo ndi phungu
Mr kasa timaona ngati munathatu koma nyimbo iyiyi landilani ulemu
Big up bro from SA
😂😂😂😂😂nkasa amatha kuyimba
That's true and true phungu
Man mwapha nyimbo iyiii❤❤❤❤
AaaaA phungu Josephy mkasa mukunena zoona amalawi tilibe kothawira tithawire kwa yesu basi
respect big boss
Ndimayesa ya nyuwanitu
Me nkasa more!!!!!!
Nkasa umatha😂
Double salute mkasa
Umakwanila bro.
Waa mbuya mkasa wayimba bwino kwambili
Umakwana kasa
True Phungu Joseph Nkasa is now talking
Nyimbo ya bwino kwambiri.
Tili mu ma tsiku otsiriza. Tivomereze dziko likupita kwao ili.
Palibe amene adzakonze dzikoli koma Mwini Mulungu yekha basi.
Kumazikupizabe ndi fungo😂😂😂😂
Yaaah tafikadi kubagamoyo
Bwana tisaname mwati ikanpamoto palibe chifukwa kuti sitose tinga pindule ndiyinu koma apapa zafika kuiguputi
Nice
That's is true Mr phungu
Koma Nkasa ndi mphangala pa nyimbo
That's true phungu ❤
Komatu Phungu 😅 mpaka mneneri kunyambita chiswa B 😂
True phungu
NKASA NDI NKASA NDIPO SAZATHEKA KUIMBA MOPANDA KUPANDA KUBISA AI🎉🎉🎉🎉🎉
Mphungu ndi phungu.atsogoleri a chakwera bodza basi ndi chilima wao
Tell them ,remind them time has gone
😂❤nice
This man l like so much
Nkhassa iapa muaimba nhymbo
FUNGO LOSAMVA PEREFIMU😅😅😅
Mbuzi zawathu ngati chakwera
Umakwana mkasa
Bigili man mumatiimilila
Strong song akuva anve
Azibambo 🎉🎉🎉🎉
Mkasa😂😂😂😂😂
Thamps up nkasa
Katswiri pamayimbidwe😂
May soul Rest In Peace ur Exerence
Mwapha❤❤
Zikomo kwambili
Please amene amatipasila mauthenga ngati awawa aziyesetsa kubwela ndi chichewa chomveka bwino 👏!
Phokotso lachule silingalephelese mdipiti wa njovu kumwa madzi?kkkkkkk
Koma phungu😂😂😂
Machine
Mumaita🔥🔥🔥🔥
❤
Tikapuma ku mwamba ndthu 😢
Mkaza kumuyimba satana chalwera ndi chilima
Iyi ndiye ngamo
Umakwana
Respect to phungu wa a mphwai.
Yah that's true
Thank you so much 💓
Mkasa zoonadi ndimaesa kut sukudziwa anthu akulira
Maiku osiliza kwa iweyo ife tidakalipo
Mulunzi channel Anthu olemera omwe anapita ndimadzi
Awa ndi akatundu osasewera nawo
Nothing but the truth 😮😮
Zoona
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Amene anaphwisira Malawi ngwamkulu matako. Fungo losamva pelefiyumu.
Enjoying from Maputo.
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Inu ndipungud
Mukunena zoona
Amalazwi munthu osavinidwa osamuika panpandoso
Kodi simurha kulemba?
Phungu nkasa ulemu wanu
Please subscribe and share the video
Mumakwana man
Mumakwanila broo
Nice