Phungu Joseph Nkasa-Munthu Wamulungu Kudya Gondolosi Ndi Chiswa B

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 42

  • @WinnieMaxwell
    @WinnieMaxwell 17 днів тому +1

    Zoonadi zake , ndipo kothawira ndi kwa Yesu yekha ma nyasa

  • @KasuzaSteve
    @KasuzaSteve 5 місяців тому +1

    Music of the year big up mr nkasa kungo ngalula bas

  • @ngolekakondwani
    @ngolekakondwani 6 місяців тому +1

    Nkasa apapa timati wabwela osawona mbali nice massage

  • @GeorgeSungani-fn3kp
    @GeorgeSungani-fn3kp Місяць тому +1

    Kodi iwe ndiye timve ziti pamenepa

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 5 місяців тому

    Azimai ambili akulela ana azibusa😂😂😂 Chakwela wamwaza ana mmidzimu

  • @JenniferThomas-m4l
    @JenniferThomas-m4l 6 місяців тому +1

    Nkasa tulusanso Ina munthu wa mkulu mgwilizano uja aphanako

  • @NoahKamwendo-io6vg
    @NoahKamwendo-io6vg 6 місяців тому

    Muthu wopephera akutafuna gondolosi wa muwisi kunyambita chiswa b kubwila tseke tseke ungoziwa kuti wopephera wa chinyengo ayi zikomo😄😄😄😄

  • @giftelesoni
    @giftelesoni 3 місяці тому

    currently in SA but still listening in 2024

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 6 місяців тому

    Ndi chiswa B mr chikangawa ndie kulonjezakodi ndie amakuziwadi km kuti akwanilise ndie eeee zimenezo ndie amakanikadi 😂😂😂😂 km nkasa yaa khuku zopanda manyazi zimenezo basi km kugwesa ndalama daily ndie kumene akukuziwana basi .

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 6 місяців тому

    Chakwela ndiwachifwamba anapha chilima kuti azilamulilabe kupanda manyazi,
    Iwe amene uzavotele Chakwela iwe ndiwe watsoka kwambili ndikupemphela kuti Chakwelayi azaphekonso wachibale wako,
    Anthu Mapension sakulandila

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 6 місяців тому

    Phungu wathu ife osauka ❤

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 6 місяців тому

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 phungu waosauka

  • @KanthuSankalah
    @KanthuSankalah 6 місяців тому

    Number one nkasa

  • @AlfredSolomon-o4h
    @AlfredSolomon-o4h 5 місяців тому

    I like this song buda

  • @owennyama3643
    @owennyama3643 26 днів тому

    koma ankolo mfundo mulinazo inuyo eeeh

  • @MavutoJackson-j3v
    @MavutoJackson-j3v 5 місяців тому

    Nkasa ndi dolo kunena mosalambalala

  • @princelonje7833
    @princelonje7833 6 місяців тому

    Eishhhh Malawi wavuta

  • @NoelMasala-i9g
    @NoelMasala-i9g 18 днів тому

    Nkasa sadzatheka

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 6 місяців тому

    Zoona nkasa iweyo ndi Muthu wankulu 😂😂😂😂😂

  • @EllaMohango-qd1pg
    @EllaMohango-qd1pg 6 місяців тому +1

    Ku ng,alula kkkk

  • @ferraoreino2441
    @ferraoreino2441 6 місяців тому

    Chiswa kkkkk....zonsezi ndi achakwerawa basi

  • @Freedomchennl47
    @Freedomchennl47 4 місяці тому

    kkkk hee kma nkasa

  • @humphreysidie4747
    @humphreysidie4747 5 місяців тому

    Mwana wayimba bwino, u were ukatenge Galimoto 😅

  • @Creslevison-vj2sl
    @Creslevison-vj2sl 6 місяців тому

    Aaaa yes munthu wamkhulu

  • @comradechimbayo3167
    @comradechimbayo3167 5 місяців тому

    Inuyo ndi big...

  • @NoahKamwendo-io6vg
    @NoahKamwendo-io6vg 6 місяців тому

    Yemwe anatsitsila mpweya Malawi anali wamkulu matako fungo silitha mpaka pano

  • @melodymsopole8603
    @melodymsopole8603 3 місяці тому

    🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 uyu anabwera kuzakhala

  • @DivalaKaphaka
    @DivalaKaphaka 6 місяців тому

    Zowona iz

  • @FloraMafken
    @FloraMafken 6 місяців тому +1

    Chiswa chani a mkasa 😂😂😂😂

    • @EamonChikanda
      @EamonChikanda 6 місяців тому

      Chiswa B 😂😂😂😂
      Wachidziwa eti ? 🙈

  • @OusmanDavie
    @OusmanDavie 6 місяців тому

    Munthu wankulu kwambiri mkasa

  • @giftelesoni
    @giftelesoni 3 місяці тому

    I can't see my comment here

  • @AhmadNicks
    @AhmadNicks 6 місяців тому

    Lucias banda

  • @prophetgiftelijah1805
    @prophetgiftelijah1805 6 місяців тому

    Koma nkasa kk

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga 6 місяців тому

    Komaakasa kkkkkk

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 5 місяців тому

    😂😂😂😂❤❤❤❤

  • @eloimaiwa1321
    @eloimaiwa1321 5 місяців тому

    😂😂😂😂😂

  • @GreyJecky
    @GreyJecky 6 місяців тому

    😂😂😂😂😂

  • @geniuselectrical
    @geniuselectrical 6 місяців тому

    Kkkkkkkkkkk