Movie mbambande kwambiri. Muli boh guys. Takukondani heavy. Mungochepesa kuonetsa malo amodzimodzi for instance ndinaona ka mkazi ka business kaja kakukonza katundu mu shop mwake muja zomwe tinachitika nthawi yaitali. Mukumatenga nthawi kumuonesa munthu malo amodzi kwambiri things like those. Its like you are just buying time
Mmmmm guys this is WOW! Iyiyi guys mwagwira. Camera yabho,, voice yabho pofunika kuyitsatsa pa Mikoz cz ndi movie ya classic km anthu sakuyidziwa chabe. By the way keep up guys i love Malawian movie ❤️❤️
Iliboh heavy, only problem, ikutenga Nthawi pa malo amodzi try to fasten it, and yesesani kupeza ma camera 4 o 5 muzitenga ma angle onse not camera izingooneka pa malo amodzimodzi Nthawi yaitali osasuntha .. can't wait part 2 ibwere fast..
Storyline is okay, theme song is lit but it has a lot to be worked on starting from the acting itself, lack of creativity, the production, the director and producer of the movie wasn't serious. The movie is too long with very little content. Anyway nice trial, keep on pushing
Thanks boss is the work of one-man operation nde mukuziwa kale nkhani yaikulu ndi chiyambi chilichonse I was working alone nde Eeeee but thanks for collection I gonna prove it.
Movie ili bwino, zoyenera kukonza konzani monga nthawi, nyimbo ikumatalika,komanso ikumachedwa pa chinthu chimodzi,but all in all zili bwino ndithu i hope next Movie it will be on🎉🔥 🔥
its a nice movie komaso yophuzisa i like it mwayesesa ❤ but the scene was too long ikutiphuzisa zambil komaso kumapetoko mukanaongezerako nkazi uja ataziwa kut mzake wamupanga betrayal koma 100% its perfect keep it up
Ilibwino kwambiri ambiri zomwe anena ndizofunika kuzisata ngati ka translate musimo English ndikupeza ma camera ambiri komanso 2 mukamajambula titha kuzakuthandizani direction

Thanks boss tikodza zimenezo
Mwaiyamba bwino kwambili big up proud of you guys ipitilizen koma musalekele pomwepai
Titelo ndinthu
Muli mwala guys
Muliboh koma mukumachedwapo kwambir pa part imozi
Mmmmm guys this is WOW! Iyiyi guys mwagwira. Camera yabho,, voice yabho pofunika kuyitsatsa pa Mikoz cz ndi movie ya classic km anthu sakuyidziwa chabe. By the way keep up guys i love Malawian movie ❤️❤️
Thanks bro for your encouragement and support
Mwana wakwathu Doreen ndasangalala nditakuona in this movie 😊 Keep up the good work
Zina umangowona waziyamba live form South Africa
That's nice nice movie that's the way to go
Keep it up
Thanks for watching
From my comment. This is another good must watch Malawian movie. You guys are all artists.. Continue being creative
Thanks a lot much appreciated
Malawi Music industry has improved greatly but I hope they will keep on improving to attain the highest peak
Iliboh heavy, only problem, ikutenga Nthawi pa malo amodzi try to fasten it, and yesesani kupeza ma camera 4 o 5 muzitenga ma angle onse not camera izingooneka pa malo amodzimodzi Nthawi yaitali osasuntha .. can't wait part 2 ibwere fast..
Thanks boss tikodza zimenezo
True ndiyayitali kwambiri
Wonderful!! Keep it up guys!! Proud of you. We need more of these from our own land!!
Keep it up the good work 💪💪🇲🇼🇲🇼
Keep fire 🔥🔥🔥🔥🔥 bening ma guys film yi ili bho kwambiri ukamaionera ngati isathe
Wawa taiyambatu the scene ija
Nyc local production!!!! keep the fire burning 🔥 🔥 🔥
Wow guys this is so nice i can't wait for part 2 guys is already out not wow well done
Coming soon
Indeed Keep it up guys this is great for our nation
Thanks
Awww🥰🥰the movie it's nice 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Keep it up guys good work
Thanks so much
Awwwww guys..... This movie is just wowww😮
Hello guys this is amazing for sure
Keep going😂😂😂😂
Thank you so much 😁
Welcome
Ilibwino km mukumakhazikika kwambili
This is beautiful guys ,I really love it keep it up 🎉
I like it so much🥳🥳keep the fire burning🔥🔥
It's good but mudakayipanga in 1hr 30 minutes ...munachulutsa zochitika in between the actual action
Oky boss takumvani next time
Nice acting by all members.... komaso amene anapanga compose nyimboyo anaitha ...
movie ili bwino ,. komano muziyesesa kuti mukakhala pamalo aphokoso chonde muziphako mphokosolo monga ngati lama galimoto ..mphepo ..ana kumamveka ngatiso muli nawo limozi ayi ...
Yes we need this here in malawi
Storyline is okay, theme song is lit but it has a lot to be worked on starting from the acting itself, lack of creativity, the production, the director and producer of the movie wasn't serious. The movie is too long with very little content. Anyway nice trial, keep on pushing
Thanks boss is the work of one-man operation nde mukuziwa kale nkhani yaikulu ndi chiyambi chilichonse I was working alone nde Eeeee but thanks for collection I gonna prove it.
Malawian at the top, let's promote our self
It's nice but too long on one scene, it could be more nice even just an hour, the song was taking too long on the same action. Nice though, Keep it up
Thanks alot for your comment and support
Thanks alot SERIES iyamba pompano so osadanda
Stage play.
Apa a Malawi mwabweraa hozaa..this is nice kungot tym yachulukisaa 2hrs eeiishh. Next time zapangeni ka an hour basi
We are on a series so don't worry
Amazing guyz
Watching from mwineriwa vg mulanje
Ili bhoo kwambiri 💯
You're most welcome in movie industry keep it up.
Thanks
Ilibwno chni km guys nyimboyo Pena kumaimitsako mmmm ikuchuluka ndinyimbo
Good one
Much respect guys 🔥
This movie tells the reality of life nowadays
Nice movie part 2 please ❤❤
Very nice
wow!!
Wachibwenziyutu eeee amaupha
Movie ili bwino, zoyenera kukonza konzani monga nthawi, nyimbo ikumatalika,komanso ikumachedwa pa chinthu chimodzi,but all in all zili bwino ndithu i hope next Movie it will be on🎉🔥 🔥
Thanks alot tikodza ndinthu
its a nice movie komaso yophuzisa i like it mwayesesa ❤ but the scene was too long ikutiphuzisa zambil komaso kumapetoko mukanaongezerako nkazi uja ataziwa kut mzake wamupanga betrayal koma 100% its perfect keep it up
Much appreciated
this is nice ❣
Nice❤❤❤❤❤❤❤
Nice one bro
Thanks 🔥
Film ilibwino ndiyophunaitsa,ndipo ikikhala ngati zikuchitikadi,ine yandisangalatsa msaname
Keep pushing guys 😅😅😅
Zamuvuta gaez
It's a nice movie keep it up malawians but content was little
Ilibwino kwambiri ambiri zomwe anena ndizofunika kuzisata ngati ka translate musimo English ndikupeza ma camera ambiri komanso 2 mukamajambula titha kuzakuthandizani direction
What a nice movieeeee
Nice movie. The scenes were too long but keep it up
Thanks
Ndimaona ngati nkazi wake azimusatila mmbuyo kt akawapezelele akupasana ndalama, nde mission ikalepheleke😅
Komno nxt tm adawaa azabweleke mpasha yabho ndihandsome adawaa angofunika mpasha bs
Takumvani boss kkkkkk
Dis is lit! 🇲🇼
Nice ❤❤
Keep it up
zili bwino ndatitu, nde wina ndisamuve apa
Gud one guys
Wow guyz
Ilibho move yi koma vuto malo ambiri akuchuluka sound komanso camera man
Takumvani thanks
Nice movie
Chi move chili bho ichi
Makwana guys
Pena mau sakuveka guys onetsetsani kuti chose chikhale mumalo mwake
Zamveka boss tikodza
Frimuyi silibo mwambiri simukuveka komaso nyimboyo ikumachedwa
Nice movie but ma scene akumatalika kwambiri..koma zilibwino kwambiri. keep it up
Thanks boss pompano tikutulusa series
@@AlexanderMphalasa635 I HAVE SUBSCRIBED
Tamaphuzirani kuremekeza mkazi wanu osamatanganidwa ndi mahurewa
Wanna come back here nzamalize
Kumwembe anayamba kupanga drama ?😂😂😂😂😂😅😅😅
We are good in acting but malawi dziko kumangoneka ngati kumanda Eshiii
Kkkkkk komadi dziko life adha
Nyc
Nice gayz
Munthu ukuupanga dala za chisawawa nde uzidandaula kuti anthu akuona motani mmmmmmh azibambo sometimes srs ndiyofunika
Kkkkk mwaonansotu
❤
Aa muli khenge tikudikira part 2
Nice movie ❤
Storyline zilibwino but muli ma scene ena omwe sali necessary
Sound ndi ma video akusiyana pena
Nice movie but next time try to use English language please
😂😂😂😂
Prt2
Love it
mukuyenera kutulutsa part2,zilibwino
Nice
Keep it up 💪, but it's toooo long
Nyimbo ikumatenga nthawi yaitali
Mwat tikhale Malo amozi ndi aphoto zilikotu ziliko
Following
Nyimbo or movie? Too much music
Exactly
Tikudikila part 2
Tikudikila 2
Ili bwino koma editing try to make it as fast as you can ikumakhazikika kwambiri pa chinthu chimodzi
Kodi next part ilibe???
Ayi sitinajambule
Good job
Nice movies
Nice indeed
Thanks!
Ili khenge
J