USAUVER S09E03 - UNALI KUTI?

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 31 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 607

  • @PiksyMalawi
    @PiksyMalawi  7 місяців тому +185

    Please remember to subscribe and share to show support
    Thank you ❤

    • @Didogama
      @Didogama 7 місяців тому

      Tapaunga kaule angauzo🫡

    • @brightwankhama5962
      @brightwankhama5962 7 місяців тому

      Ka nyimbo akamalila kumapetoko title bwaa😊

    • @Robbenkachulu-lm8ls
      @Robbenkachulu-lm8ls 7 місяців тому +1

      Angozo the fame song chonde ikani pa Spotify

    • @PhilimoniEphraim
      @PhilimoniEphraim 7 місяців тому

      🔥🔥🔥

    • @MikaNamwada
      @MikaNamwada 7 місяців тому +2

      Angozo I think it could be better if you put English lyrics at the bottom of the video.. that's my suggestion

  • @ChinsisiMaomba
    @ChinsisiMaomba 7 місяців тому +88

    Team Sangie let's gather here🔥🔥

  • @godfreyguwa5805
    @godfreyguwa5805 7 місяців тому +41

    Koma Sangie has good choice of words and the way she articulates them...😂😂😂

  • @DoricaChimzimu
    @DoricaChimzimu 7 місяців тому +17

    Team Emmie lets gather here,,and showing some love to her❤❤❤❤❤❤

  • @mwaisambani1849
    @mwaisambani1849 7 місяців тому +3

    Ndamva kukoma ndisaname this is wow 👌 ndipo ndaseka kwabasi

  • @SangieOfficial
    @SangieOfficial 7 місяців тому +32

    Ama mwafika pokugwa ndi mowa?😂😂😂

    • @PiksyMalawi
      @PiksyMalawi  7 місяців тому +2

      Wapita uyu 😂

    • @mwaisambani1849
      @mwaisambani1849 7 місяців тому

      😂😂😂😂 guys mwandimvetsa kukoma ❤❤❤

    • @MarthaMtalika-mv2il
      @MarthaMtalika-mv2il 7 місяців тому

      Ndpo tudikila aulule mwini mwanatu

    • @TamandaniMakunje-oo1nc
      @TamandaniMakunje-oo1nc 7 місяців тому

      I love you ❤ndinamutuma sulu kuti akuze ndizagudumuka uja ndine❤❤❤❤

    • @Aaron-MW
      @Aaron-MW 7 місяців тому

      Anamuyambisa dala😂😂

  • @GraceRichard-s6q
    @GraceRichard-s6q 7 місяців тому +108

    Friends of Gani let's gather here😅😅🔥🔥🔥🔥

  • @SmilingFarmhouse-tf5ct
    @SmilingFarmhouse-tf5ct 7 місяців тому +12

    Gani is real acter and he deserves much respect

  • @SilvaJoe-c6z
    @SilvaJoe-c6z 7 місяців тому +11

    I enjoy streaming your content guys❤ I always follow you
    this one is very educative one, guys don't teach your wife kumwa mowa please, otherwise one day mudzadandaule ndinu

  • @limbanimsatilomo3592
    @limbanimsatilomo3592 7 місяців тому +19

    Ganizani is a natural entertainer🔥. This season is fire tackling different Malawian current scenarios

  • @KondwaniKaduya
    @KondwaniKaduya 7 місяців тому +2

    Komatu ka mwana akaka mwakatenga kuti kachenjeresa bwanji 😂😂😂😂😂

  • @CARLOLYNCHIKALO
    @CARLOLYNCHIKALO 7 місяців тому +2

    Aunt p...... Ndithire tsabola kodi ndiwozi 🤣🤣🤣

  • @Tanishamsowoya
    @Tanishamsowoya 4 місяці тому

    Koma sangie amandiwanza mene umayakhulila mmmj😂😂😂 pena kamwano e!

  • @yohanepbamusi
    @yohanepbamusi 7 місяців тому

    This is nice ever
    Usauver munadza Angozo Patricia♨️♨️

  • @GiftmphaaThindwa
    @GiftmphaaThindwa Місяць тому

    Ka sangie mkachiwandatu 😂😂
    Liwiro lokatseka pagate ngt munthu othawa atapexeka red hundred on cheating 🤣🤣🤣

  • @MikaNamwada
    @MikaNamwada 7 місяців тому +2

    Gani iweyo ndi one ase 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @InnocentJames-d3l
    @InnocentJames-d3l 2 місяці тому

    Mesa mwati abwerere komwe anari Angozo😂😂😂😂

  • @ChimwemweJere-f5z
    @ChimwemweJere-f5z 7 місяців тому +5

    Atsogoleri ndi m'mutu mwanu ngati chalk🤣🤣🤣🤣🤣iweyo ndi mimba ngati chigubu🙌🙌

  • @BisalomuChiutsi-du8ot
    @BisalomuChiutsi-du8ot 7 місяців тому +1

    That soundtrack is vibe...I'm need of a song please

  • @TsuzenThomas
    @TsuzenThomas 7 місяців тому +1

    Koma Ganizan ati chips n plain chimabwera nd chicken yopanda nsuzi 😂😂😂😂
    Chenkope kuchenjeretsa 😂😂
    Mr n Mrs Ngozo kwachema 😂😂😂mmatha gyz simupala + abusa 🔥🔥

  • @SundayScova
    @SundayScova 7 місяців тому

    😂😂😂Ngouzo muothelatu dzuwa nawo ABUSA mukufuna tea 😅😅😅 mukhaulatu

  • @EmmanuelMoyo-hy5ni
    @EmmanuelMoyo-hy5ni 7 місяців тому

    Koma bodza ili ndi ngozo ,,keep it up guys

  • @mikeilahmendes1643
    @mikeilahmendes1643 7 місяців тому

    Abusa😂 nawoso ndimunthu apume pa dzuwa anthu sakuoneka ngati ndi public holiday

  • @trynessmwenda4950
    @trynessmwenda4950 7 місяців тому

    Eh nyimbo yakuapetoyi tittle nchani makosana🔥🔥🔥🔥

  • @ivyfrankie-jf2eq
    @ivyfrankie-jf2eq 7 місяців тому +1

    More fire guys season iyi mwabwera🔥🔥🔥

  • @Gracendau-d3l
    @Gracendau-d3l 7 місяців тому

    Koma Patricia 😂😂 umakwana,,,,Albert mkazi usamugonese panja unaziyamba wekha😂😂😂😂

  • @jozBouy265
    @jozBouy265 7 місяців тому +2

    This time ma guy mwabwela ndi fire🔥🔥🔥

  • @macleanmalilizopangana2712
    @macleanmalilizopangana2712 7 місяців тому +17

    Unandiyambisa shisha , mowa Mesa ndiwe

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 5 місяців тому

    😅😅😅😅😅😅😅 afotokozedi apanga nthawi yayitali bwanji

  • @violetnthala6183
    @violetnthala6183 7 місяців тому

    Paja munati muzipanga zimodzitu...mamie aledzela kuno😅😅😅

  • @LucyZimbiri
    @LucyZimbiri 5 місяців тому

    Thumbs up 👍for Gani ... ichichi chili ndi natural talent

  • @tatendermwawa3051
    @tatendermwawa3051 7 місяців тому

    😂😂😂 Mwafika poyankhana Kuti tikudziwana kkkk kkkkk... Nyimbo ikhare ya Driemo yomwe ija hahaha

  • @TiyamikeMituka
    @TiyamikeMituka 6 місяців тому +1

    Ifeso timafuna kasisi ngati kanu koma gani osangosungila sisilo bwa😂

  • @georgesiwale8127
    @georgesiwale8127 7 місяців тому

    Gan koma adhaaa!!! Eti obwino wake wayamba ndikuthesa njala chifukwa chiwapasa phwanya 😂😂😂😂

  • @FrahaTelaviv
    @FrahaTelaviv 5 місяців тому

    No or hug 😂😂..... next time 😅 ..... waguru lathu ameneyo 😂

  • @BlklilSis
    @BlklilSis 7 місяців тому

    Koma kamwana aka🤣🤣🤣. Ati kungotembeniza 6 to 9 eish....

  • @HassanBanda-qo3ww
    @HassanBanda-qo3ww 7 місяців тому +1

    😂😂km Ganizani akut chips and plain

  • @Emmanuel2737-1t
    @Emmanuel2737-1t 7 місяців тому +1

    Ganizani eee ati chips and plain 😂😂😂😂😂😂 chips chimabwera ndi chicken yopanda nsuzi😂

  • @matfeomhango4898
    @matfeomhango4898 7 місяців тому +13

    Ngauzo uli pa moto ndi Sange😂
    Albert nde usamunyanyale mkazi mowa wamuphunzisa wekha 😅😅😅

  • @HEZEKIAHCHUNGA-ib2hi
    @HEZEKIAHCHUNGA-ib2hi 7 місяців тому

    Ndiye Gani mpaka kuuza alamu ako Kuti adzitenga awo ma key?🤣😂😂😂😂

  • @GraceKhonyo
    @GraceKhonyo 2 місяці тому

    Ati chipis and puleni kkkkkk koma guys ati chimakhala chanyama yopanda supu kkkkk

  • @ThomasNChinseu
    @ThomasNChinseu 3 місяці тому

    The play is very fantastic I enjoy very much

  • @eltonkasila4822
    @eltonkasila4822 7 місяців тому

    Hyphen kuwerenga manual ya ICAM.... Kwachemeratu!

  • @WilliamMpunga
    @WilliamMpunga 7 місяців тому

    Ganizani ndi munthu ozunguza anadya ndalama ya foundation siwoyenera kumupatsa ndalama ina😂😂😂❤

  • @elizahmaxwell5161
    @elizahmaxwell5161 7 місяців тому

    Eeeh na iyiyi guys mwabwera🤣🤣🙌🔥🔥

  • @SundayScova
    @SundayScova 7 місяців тому

    Koma gun Mumatha kucheza mukutifilisa😂😂

  • @kevinchipembere1137
    @kevinchipembere1137 7 місяців тому

    Ma guys amatha awa. Koma nyimbo yakumapetoyi nde ndaisaka sindiyipeza

  • @UwamahoroLucie
    @UwamahoroLucie 7 місяців тому

    😂😂😂 watching from Dubai hug paka kupepha km boys 😂

  • @jonaspatel6225
    @jonaspatel6225 7 місяців тому

    Shado uja osazamuphweketsa nkhani yama tease 🤣🤣🤣🤣

  • @MuhammadImraan-fs2ve
    @MuhammadImraan-fs2ve 7 місяців тому

    We really appreciate your effort guys.. Keep intertwining us.. May God take your project from strength to strength amen

  • @DoreenKambalame
    @DoreenKambalame 7 місяців тому

    Apatseni chopereka😂😂😂 atopa kudya mizimbe

  • @FatimaSaidi-o1q
    @FatimaSaidi-o1q 7 місяців тому

    Yoooo makwatila kwatila mwakwatila nazo zidakwatuu🤣🤣🤣

  • @benjaminbanda2534
    @benjaminbanda2534 7 місяців тому

    Kma mpaka kutembenuza 6 kukhala 9 kkkkk😂😂😂😂😂😂😂

  • @kaputoconrad9383
    @kaputoconrad9383 7 місяців тому +3

    Ati 30years in the game, koma sichinawineko still observing🤣🤣🤣🤣🤣

    • @BrightwaFane
      @BrightwaFane 7 місяців тому

      😂😂😂😂😂 chingawine chimenechijach pompous imeyo?

  • @ellensaka5883
    @ellensaka5883 7 місяців тому

    😂😂nnaziwa ine kuti ngozoo waishosha now see😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
    Komano mpakana sign ya dzungu eeee💔💔😝😝😝🙌🏼

  • @colletamtawali9793
    @colletamtawali9793 7 місяців тому

    😂😂😂😂 ati ifeso timafuna katsitsi ngati kanuko

  • @trevornthanie2685
    @trevornthanie2685 7 місяців тому

    Tikunva nanu kukoma guyz,,,Looking forward to the next episodes!
    Gan unabwera kuzakhala iwey 😂😂😂

  • @FrancisKamwendo-k7j
    @FrancisKamwendo-k7j 7 місяців тому

    😂😂😂 mwabwera gyz at mimba ngat chigubu

  • @RabeccaChafulumira
    @RabeccaChafulumira 7 місяців тому

    Koma patricia ndi deal ati mwandi blocker🤣🤣🤣🤣

  • @matfeomhango4898
    @matfeomhango4898 7 місяців тому

    Chips and plain 😂😂😂 guys mukundikomola ndi phwete😂😂

  • @lusungumsiska6628
    @lusungumsiska6628 7 місяців тому +1

    😂😂😂😂aleka kukhala ndi sugar yo bwanji

  • @EllenChambwinja
    @EllenChambwinja 7 місяців тому

    Koma ine 😂😂😂😂😂😂 ati sangatipange chipongwe nyama tidya tonse😅😅😅😅😅

  • @mswatizumalizwe4
    @mswatizumalizwe4 7 місяців тому

    Angachoke tsiku la nyama uja... Kodi mwati si ya lero??

  • @giftsiliuka6287
    @giftsiliuka6287 7 місяців тому

    Ashado lero nde mwayaka motoo mpaka ndikusowetsani 😂😂😂

  • @fragathama7988
    @fragathama7988 5 місяців тому

    Koma ganizani ndi dolo 🔥🔥

  • @YammieKaunda
    @YammieKaunda 7 місяців тому

    chimabwela ndi chicken yopanda nsunzi🤣

  • @ChimwemweThumba
    @ChimwemweThumba Місяць тому

    Mwabwera ma guys 🎉

  • @OmarPaul-qm2ki
    @OmarPaul-qm2ki 7 місяців тому

    😂😂😂😂😂Akuti mutu ngat choko kkkkk😂

  • @GanizaniBalon-ie2oq
    @GanizaniBalon-ie2oq 7 місяців тому

    Atitu akangotuluka gan asadzabweleso😂😂😂

  • @PRISCAMAKHANGA
    @PRISCAMAKHANGA 7 місяців тому

    Hyphen mkazi wako analikali chidakwa paja Edo anati anamuonakotu 😅😅😅 wamasuna galu pachain

  • @colletamtawali9793
    @colletamtawali9793 7 місяців тому

    Ati amajijilika tsiku la nyama 😂😂😂😂❤❤❤

  • @wanangwamlauzi7740
    @wanangwamlauzi7740 6 місяців тому

    Hyphen Mkazi munaphunzitsa nokha mowa😂😂

  • @thomasmatuta
    @thomasmatuta 7 місяців тому

    Ati 16 kungotembenuza 6 kukhala 9😅😅 anyamata enaso😂😂

  • @colsonsamuelnyeza9667
    @colsonsamuelnyeza9667 7 місяців тому

    Gani akuti ifesotu timafunatu ka tsitsi ngati kanuko 😅😅😅

  • @chimwemwemoyo9374
    @chimwemwemoyo9374 6 місяців тому +1

    Im i the only one that waits for the ep to pile and binge them? ❤❤

  • @Robbenkachulu-lm8ls
    @Robbenkachulu-lm8ls 7 місяців тому +1

    Hahaha ada comic yosachita kupanga force

  • @dd.y3524
    @dd.y3524 7 місяців тому +1

    Happy New Year, Shado! Ndiwe dolo nkope😂😂😂

  • @faluqmayere
    @faluqmayere 7 місяців тому

    😂😂😂😂eeeh actors inuyo ndi mbambande

  • @shupikayintuwaluwa-5899
    @shupikayintuwaluwa-5899 7 місяців тому

    Mmakwana a pipo inu! Albert mavuto sautheran kkkkkkk

  • @capalotGonlit-ui6cb
    @capalotGonlit-ui6cb 7 місяців тому

    Iziso agula chiphaliwali wakoyo ,zikuonekaso zokhoma bwanj chonsecho ndipa list😅😅

  • @innocentnkonga8392
    @innocentnkonga8392 5 місяців тому

    Tsiku la nyama sitimachoka😂😂😂😂

  • @iamcrakie
    @iamcrakie 5 місяців тому

    Ndi mmutu mwanu ngati chalk 🤣😭

  • @wenfridamuhura-tb1wd
    @wenfridamuhura-tb1wd 7 місяців тому

    ATI mwapanga nthawi yaitali bwanj?🤣🤣🤣sangie

  • @JoelBanda-u8z
    @JoelBanda-u8z 7 місяців тому

    Eh km che Mkope ndikatundu😂

  • @katheychikoko4678
    @katheychikoko4678 7 місяців тому

    Whats the title of the song 😢

  • @blessingsmunthali9202
    @blessingsmunthali9202 7 місяців тому

    😂😂😂 mtipweteka maguy 🔥🔥

  • @ChifundoJeffrey
    @ChifundoJeffrey 7 місяців тому +1

    😂😂😂😂Hyphen unamuphunzitsatu wekha nkaziyo😂😂😂

  • @MphatsoLisimba-bb8yf
    @MphatsoLisimba-bb8yf 7 місяців тому

    Tambawali sasowa zoyankha , moti ungovutika ndikufunsa funsa2 pamenepa

  • @ashraffmidu7837
    @ashraffmidu7837 7 місяців тому

    What Gani and his sister does" it just reminds me what i used to do when i visit my sisters's place🤣

  • @stevenyakobe7730
    @stevenyakobe7730 7 місяців тому

    Kungofikira 1---100 brah 😂😂😂😂😂😂🎉❤

  • @OliveaMapanga
    @OliveaMapanga 7 місяців тому

    Km a shadow kkkkk nkope inuyo mumakwana 😂😂😂😂😂

  • @GodrineGerman
    @GodrineGerman 5 місяців тому

    Maltious ndi handsome no cap 🤣 ati ma rasta .... Gani koma

  • @NorahNote415
    @NorahNote415 7 місяців тому

    Patricia my favourite eeeeeh ine ndie umandwaza

  • @awaliwilliam6472
    @awaliwilliam6472 7 місяців тому

    Ati penapake malo moti mulange Muthu wina mapezeka mulanga ine bale wanu

    • @PatriceSubili
      @PatriceSubili 7 місяців тому

      Ndipo mmabanjamu zikuchitika

  • @InnohLukah.1998
    @InnohLukah.1998 7 місяців тому

    Ndakwera Aunt P lero😂😂😂

  • @yourrecruiter9753
    @yourrecruiter9753 7 місяців тому

    😂😂😂mkazi mwamphunzitsa nokha mukudabwaso 😂

  • @TrizaKalimmawa
    @TrizaKalimmawa 7 місяців тому +1

    Ati chips and plain chimabwera Ndi chicken yopanda nsuzi🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @ireenbottoman8120
    @ireenbottoman8120 7 місяців тому

    Unandiyambitsa shisha mowa mesa ndiwe😂😂😂 Albert wabalalika

  • @yamikanikadyeleni4128
    @yamikanikadyeleni4128 7 місяців тому

    Ati ndiwa chamba 😂😂😂

  • @akuzikemalindi105
    @akuzikemalindi105 7 місяців тому

    Kakundiwaza ndi ka "Aunty P"🤣🥳🥳