BON KALINDO LERO WACHISAMBWADZA CHIPANI CHOMWE CHABADWA DZULO |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 26 кві 2024

КОМЕНТАРІ • 60

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni День тому +1

    Akunena zoona kalindo

  • @CharlesMulikhiwa
    @CharlesMulikhiwa 11 годин тому

    Alibeso ndalama anaba xochepa bolatu ma guys a sattal Ali ndi kanthu

  • @JimukarimuAdini
    @JimukarimuAdini 5 днів тому

    Msiyeni kalindo ayankhule nanunso ngati pali zoyankhula yankhulani ife tilipano kumva zoyankhulidwa zina zilizonse palibe apye mtima ndi kuyankhula basi ife tisitsunga mawuwo

  • @user-oe1lg4xo7w
    @user-oe1lg4xo7w 12 днів тому +1

    Timakunyadira Bon the Dc ndiwe diso la dziko la malawi ndiwe chiwomba nkhanga usazafe kalindooooooo! The Dc

  • @user-vl8uw8mc3u
    @user-vl8uw8mc3u 12 днів тому +1

    Nankhumwa ndi mwana.akulephela kupeza dzina la chipani chawo😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @CharlesMulikhiwa
    @CharlesMulikhiwa 11 годин тому

    Aise akumsngatu ndi ma dictator akupha uona

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 11 днів тому

    Good message Mr bon Kalindo

  • @user-rc3ze2oi7u
    @user-rc3ze2oi7u 12 днів тому +4

    Amalawi zonse tikuona zipani zoyambika CHIFUKWA CHA nkwiyo tikuziziwa osadandaula ayi ife tikavotera dpp basi komaso chakwera asaiwale mau amene ananena oti azakhesa mwazi chakwera akazangowina 2025 anthu sitizalola ai chakwera wazunza Amalawi kwambiri 🎉🎉🎉🎉🎉🎉Amalawi tisagone ai tipemphere zolimba kwambiri kuti Satan ameneyi achoke basi 🎉🎉🎉

    • @blessingsmimu5236
      @blessingsmimu5236 12 днів тому

      😊kupemphera ndekusakhale kolekeza cos mwazi nde uzakhesedwa ,mulungu atipqngire chifundo koma😭

    • @user-vu9es6nz3k
      @user-vu9es6nz3k 9 днів тому

      Mukunama DPP siyingawine anthu adatopanayo misewu yozila Chaka chimozi watha ndizimene mukufuna yiwalani take mau anga chipani chikufunika abweze Kwa bakili mwini wake ndiye bakili ananena kale kuti mcp yikalowa mu Boma basi Palibe chipani chingachose mcp

  • @user-lw9su5om5z
    @user-lw9su5om5z 12 днів тому

    Ngat nankhumwa akulephera kupeka dzina la chipan chake nde angayendetse bwanj dziko 😂😂😂

  • @TressLuka
    @TressLuka 7 днів тому

    Akukambatu ngamoo. MCP ndi akamberembere basi. Akufuna aphe democracy 😢😢

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 8 днів тому

    Chipani cha Mtundu wanji chopanda intelligence????

  • @user-yk9lx7xd1i
    @user-yk9lx7xd1i День тому

    Vuto ndiogulidwayo

  • @JustinPhiri-kq2bb
    @JustinPhiri-kq2bb 12 днів тому

    Chipani munthu sapanga form yekha ayi.this party is well organized ,

  • @sandramkaligida1163
    @sandramkaligida1163 5 днів тому

    Kuwina ndi kuwina basi

  • @andrewBwanaisa
    @andrewBwanaisa 10 днів тому +1

    Ndi mwana uyu ndipo ndi kape

  • @macleanmachamo
    @macleanmachamo 5 днів тому

    Kape uyu

  • @MussaManyero
    @MussaManyero 12 днів тому

    Bwana DC mumatiimilila

  • @user-pj3rf4rn9w
    @user-pj3rf4rn9w 9 днів тому

    Koma kalindo ndiwandare ine amandinyasa kwambili bora masewero omwe aja

  • @user-dd1qq5xq1k
    @user-dd1qq5xq1k 11 днів тому

    Nankhumwa munthu osokoneza,Sudzakhala nsugoleli ku malawi. A mcp adzingokugwilisa ntchito basi.

  • @JamesSpondo
    @JamesSpondo 11 днів тому

    😅😅😅😂😂😂Ati malawi isazathe kwachuluka ma drama

  • @clivemhango6183
    @clivemhango6183 9 днів тому

    Penapake kalindo nakhala ngati wakhuta mbwanda, kanundu mukati.

  • @robertkalima874
    @robertkalima874 7 днів тому

    Akulu boma silingatekeseke ndi inu. Sukugona tulo ndiwe

  • @atusayeMtalama
    @atusayeMtalama 12 днів тому

    Akalindo aliyense ali ndimaganizo ake ake sionse ali aDPP ulindi manta tipitiliza mpaka 2030

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 12 днів тому +1

    No chance for Mcp again

  • @user-kr1kg5hy9l
    @user-kr1kg5hy9l 8 днів тому

    umakwana DC

  • @user-gh6qm5ze3b
    @user-gh6qm5ze3b 12 днів тому

    Ife kupoto Munthali ndiye ayi anatinamiza mbombora

  • @InnocentDaveson
    @InnocentDaveson 10 днів тому

    Akunenadi zowona zipani zichenjele ndithu

  • @user-ot6lt8iy8f
    @user-ot6lt8iy8f 12 днів тому

    Chakwela ndioipa ntima ngat kambuku akufuna kupitiriza kusokoneza malawi bas

  • @ChisomoChikafa-dd3sj
    @ChisomoChikafa-dd3sj 9 днів тому

    Kalindo lengeza kuti walowa dpp osatinamiza. Umati atani atawathamangitsa ku dpp. Dpp yatha basi mwathetsa nokha zitsiru inu. Mulila 2025 simunati. Kalindo watch out.

  • @FabianoNgozo
    @FabianoNgozo 12 днів тому

    Ndizoona mcp si kugona tiro ndi dpp

  • @user-rm8jd9mu8r
    @user-rm8jd9mu8r 12 днів тому

    Bon mukasowa zolankhula muzikhala phee...how can u say there is plan yothetsa dzina la dpp?

  • @user-nc4vi1jt5g
    @user-nc4vi1jt5g 12 днів тому

    Kodi akalindo mwalowa bpp

  • @jonathanmunthali8500
    @jonathanmunthali8500 12 днів тому

    Awa ndi amisala p d p zanzawo izi akutani zawavuta

  • @FosterChilumba
    @FosterChilumba 12 днів тому

    Mulungu sinsuwani wake wa munthu dzanja likalemba lalemba Babylon is falling apart

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 12 днів тому

    Odana ndi bon ndi nsawi

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r 12 днів тому

    Nankhumwa walakwaso chiyani achisilu akalindo pangani zanu gwape uyu

  • @user-lp2sd7lt8b
    @user-lp2sd7lt8b 12 днів тому

    Kalindo ndiopenga. Mwawathamangitsa apa ayambitsa chipani chawo alakwitsaso. Pompano mumati angoyambitsa chipani chawo

  • @blesstonphiri
    @blesstonphiri 12 днів тому

    Amatha kalindo palibenso

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 12 днів тому

    Inutso opanda zelu ndithu peter mukumulankhulilayo,yemwe uja,anakumangani,mutaulula,kuti amapha ma alubino,ndipo mutoziwako,komwe amakagulitsa,mafupa uja?sitimaiwalatu,uyu, nankhumwa ali ndi ufulu,ndi joker yemwe amadikila Anthu,uja ndiyetu,ameneyi.a kalindo zelu mudzikhala nazo.dpp, kuwina sidzalamulila malawi.iweyo,usalodzedwe kubwela ku phalombe kumazalankhula,zonunkha.

  • @OwenKachipapa
    @OwenKachipapa 8 днів тому

    The headless chicken

  • @macleanmachamo
    @macleanmachamo 5 днів тому

    PDP woyee

  • @ValueSibande
    @ValueSibande 12 днів тому

    We need DPP back

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w 12 днів тому +2

    Whether you want or not Dpp 2025 boma

  • @user-nc4vi1jt5g
    @user-nc4vi1jt5g 12 днів тому

    Akalindo ndinu chitsilu mulinditsanje mumagwlitsa ntchito anthuosauka mulindinsanje

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o 12 днів тому

    Bon kalindo ndiwe chitsiru kwambiri ndiposo iwe sungamenyane nane ndiwe mwana

  • @MmikeeMateyo-kj2pn
    @MmikeeMateyo-kj2pn 12 днів тому

    Bon tapangani zanu zoti zikuthandizeni

  • @user-ml2vw1dc9c
    @user-ml2vw1dc9c 12 днів тому

    Kalindo watha supu. Walowa DPP mwachisisi. Dairy kulalata ukutisokoneza mmalo moti tizigwila ntchito uxitha mwezi osayankhula

    • @user-mg9ie2pi3d
      @user-mg9ie2pi3d 12 днів тому

      😅😅

    • @robertkalima874
      @robertkalima874 7 днів тому

      @@user-mg9ie2pi3d Wamisala satopa. Mulekeni. Ngati chili chi ban chomwe wadya adzimbidwa nacho

  • @blessingsgeoffrey9414
    @blessingsgeoffrey9414 12 днів тому +1

    Akalindo bodza inuu AAA osamakula ayi

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r 12 днів тому

    Alowa yadpp kuti aziwapasa banzi

  • @macleanmachamo
    @macleanmachamo 5 днів тому

    Za adress usasochelese anthu bon address ndichitnthu chofunika kwambiri

  • @macleanmachamo
    @macleanmachamo 5 днів тому

    Nsanje boni kalindo

  • @kalimawandale7161
    @kalimawandale7161 5 днів тому

    Awa akupengatu

  • @user-kr1tf2tu7s
    @user-kr1tf2tu7s 12 днів тому

    Akulu awa ndi akhunyu che kalindo