BAKILI MULUZI TV TEAM IKUYENELA KULANDILA MAULEMU AWO NDITHU PAZOMWE ACHITA LERO ADZIDZIMUSA A POLIC

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 3 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 79

  • @Christianmaya-lw2pp
    @Christianmaya-lw2pp 13 днів тому +5

    Bakili muluzi tv silengeza za boza it the only Chanel pple trust ndi kuziwa zobisika

  • @Happ2y
    @Happ2y 20 днів тому +9

    Bakili muluzi TV big history is the best teacher

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 20 днів тому +1

    History is the best teacher.....Bakili muluzi tv woyeeeee ur number 1❤

  • @gracechiumia7103
    @gracechiumia7103 16 днів тому +2

    Bakili muluzi tv ndi fana wa look sharp

  • @RodgersAbina
    @RodgersAbina 19 днів тому +4

    Pano ndinafika poti ngat osamvera bakili muluzi TV tulo osabwera

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 12 днів тому +1

    Ndipo ineyo itrust BAKILI MULUZI and Limpopo fm

  • @MwaiPhiri-g5u
    @MwaiPhiri-g5u 20 днів тому +3

    Bmtv respect wako basi
    Umakwana

  • @TasiyanaChinula
    @TasiyanaChinula 20 днів тому

    That part of kusamupeza wogwidwayo kkkkk
    Zangondikomera......😂😂😂😂😂

  • @YasmeenYalabi-b2c
    @YasmeenYalabi-b2c 20 днів тому

    History is the best teacher Bakili Muluzi ndi pangolin wathu

  • @khasimMusa-d3w
    @khasimMusa-d3w 20 днів тому +2

    Bakili muluzi tv Nd Muthu wankulu kwambili

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 19 днів тому

    Number one bakili mluzi TV ❤❤❤

  • @GodfreyKamphiripiri
    @GodfreyKamphiripiri 20 днів тому

    History is best teacher bakili muluzi TV

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 19 днів тому

    Bakili muluzi tv history is the best teacher

  • @OmarJumah-i3f
    @OmarJumah-i3f 18 днів тому +3

    Bakili Muluzi TV, ndimkhatheya

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 18 днів тому +1

    MaSavage, ndumbuli😄

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 20 днів тому +1

    Ulemu wako Bakili Muluzi TV ndpo pa jeneza yanga popita kumanda pazalembedwa Bakili Muluzi TV

  • @AnnastasiaChakwiya
    @AnnastasiaChakwiya 19 днів тому

    Bakili TV ndi bambande ❤❤❤❤❤

  • @AARONCHISUKAMZION-we3vp
    @AARONCHISUKAMZION-we3vp 20 днів тому

    @HISTORY IS THE BEST TEACHER.😂😂😂😂 , GO BAKILI TV GO

  • @ChimwemweSauka
    @ChimwemweSauka 20 днів тому

    Welcome brother bakili muluzi tv

  • @alfredgoba-mb8bz
    @alfredgoba-mb8bz 20 днів тому

    Inuyo bro matimilira ulema wanu❤❤❤

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 20 днів тому

    Thanks bakili tv

  • @SolomonShaibuh
    @SolomonShaibuh 20 днів тому

    History is the best teacher

  • @YusufMoyo
    @YusufMoyo 20 днів тому +1

    Mulungu wathu ndiwazatheka bwanji agwidwa sanati

  • @EMMARKKALIAPA
    @EMMARKKALIAPA 15 днів тому

    Timu vote le Bakili muluzi tv 📺

  • @AnaLourencokan
    @AnaLourencokan 20 днів тому

    Bravo..Brav0

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 20 днів тому +7

    Broh wapereka malangizo aulere achinyamata pezani zina zochita andale amakutaya ngt tishu

    • @clubjunta
      @clubjunta  20 днів тому

      Thanks very much boss

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 19 днів тому +2

    Bakili muluzi tv ndi wathu wathu uja samalankhura zaboza ai aja ndi akatundi

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 20 днів тому +1

    Asatana,akupha.mulungu awalanga

  • @MussaZamesi-rs8nm
    @MussaZamesi-rs8nm 20 днів тому

    Wawo ❤❤

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 16 днів тому

    Btv best tv ever ❤❤❤❤❤

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 20 днів тому

    God bless u sir

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 20 днів тому

    Mugwidwa simunati Mulungu wakuyalutsanitu azikhale ng, oma ntchito zanu zayipa Mulungu akulangeni mwapadera dera ndithu

  • @JamesSinyolo
    @JamesSinyolo 20 днів тому +2

    Sanayankhulepo zabodza uyu

  • @GileyaMataye
    @GileyaMataye 9 днів тому

    Umatha ase chilungamo chiyende ngat madzi

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera 17 днів тому

    BM T my first choice.

  • @MalawianCamera
    @MalawianCamera 17 днів тому +1

    • @clubjunta
      @clubjunta  17 днів тому +1

      Zoona fada mumakwanila

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera 17 днів тому

      @clubjunta Ndakuona fada umakwana 👌✊

    • @clubjunta
      @clubjunta  17 днів тому +1

      Tiyeni ku UTM kuli kanthu lero

  • @WalleniMapulango
    @WalleniMapulango 17 днів тому

    ❤❤❤ndizoona

  • @ThokoMsonkho-hy4uc
    @ThokoMsonkho-hy4uc 20 днів тому +1

    BAKILI MULUZI tv sananenepo bodza,akanena zimakhara zoona zimenezo ndipo ija yakuti Chakwera wadwala stroke ndizoona

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 20 днів тому

    Salute

  • @fahadmilanzi
    @fahadmilanzi 18 днів тому +1

    Chisale ekhawo ndiye musayambe munyanaye

  • @IshmaelNesta-rb8dx
    @IshmaelNesta-rb8dx 20 днів тому +1

    BMTV IJA OSAZAIPHWEKESA🎉🎉

  • @ChicoBanda-kq7py
    @ChicoBanda-kq7py 20 днів тому

    Zikomo big man

  • @franktsoka
    @franktsoka 20 днів тому

    Solute 😅

  • @JumaJonas-d2x
    @JumaJonas-d2x 12 днів тому

    Bambende tv

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 17 днів тому

    Indeeeeee bwantasa zokha-zokha

  • @jesusminded3033
    @jesusminded3033 20 днів тому

    Viva BKMTV

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 19 днів тому +1

    Ndimmene ilili boma la mcp tikamanena uyu otuwa mmutuyi jessy chabwila akuti tikunama.mcp ikufuna nkhondo mmalaw muno simwaona? Tiwathokoze mabausa a ford agwila tcito ya boh pitilizani.Dj munyanane umakwana, kuyambila zikhale ng'oma, chabwila,wadowado,yolamu, mkukuyu ndi cikangawa nonsenu pa zisilu painu muuzane ndipo amanu akanadziwa mimba zanu akanangotaya mukutionongela dzikoli.

  • @FunnyKalimwayi
    @FunnyKalimwayi 14 днів тому

    achule

  • @RajabAssan
    @RajabAssan 20 днів тому

    Amakwanila bm tv

  • @blessingssaiti
    @blessingssaiti 20 днів тому

    Inu anthu akufera 100,000 adya masiku angat

  • @AbdullahMatolah
    @AbdullahMatolah 20 днів тому

    Osaopa

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 19 днів тому

    Apolice athu ali nivuto amagwiratsidwa ndi a mcp aziwe kuti izapita kusogolo muzanong'oneza London

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 20 днів тому

    Bakili Muluzi TV ndiyoopsa zedi guys eeeeeeee katundu

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev 20 днів тому

    Ndipo live ulemu wake

  • @BlessingsSeleman
    @BlessingsSeleman 19 днів тому

    Komaso analakwisa akanaocha bs ena apezelepo phumzilo

  • @MagieJames
    @MagieJames 20 днів тому

    Makwanira ulemu wanu

  • @VictormitomoniMitomoni
    @VictormitomoniMitomoni 17 днів тому

    Umakwana

  • @Thokozanikawanga
    @Thokozanikawanga 20 днів тому

    Zabodza basi nkungofuna kungotnchukirapo mbuli za anthu in a dpp

    • @JanuaryGwere
      @JanuaryGwere 19 днів тому +1

      Tiwuze zoona iweyo

    • @blandinabonaventure
      @blandinabonaventure 17 днів тому +1

      Mbuli ndiwe otsutsa zilizonse

    • @MfipaKapwera
      @MfipaKapwera 17 днів тому +1

      Thokozani Kawanga ndiwe mbuzi yamanokusi ngatiwuli wa Chikangawa Congress party ndizakozimenezo.

  • @mailos.laisoni7001
    @mailos.laisoni7001 20 днів тому

    Osamupha bwanji

  • @LawrenceSilver-h8n
    @LawrenceSilver-h8n 20 днів тому

    Zokut iweso upange TV yako ayi ungotokota zamzako😮😮😮😮

    • @clubjunta
      @clubjunta  17 днів тому

      I do have that's why ULI panopa Club Junta it's a big brand

  • @Thokozanikawanga
    @Thokozanikawanga 20 днів тому

    Wangosowa zochita iwe

    • @MfipaKapwera
      @MfipaKapwera 17 днів тому

      Wuzafa ndiwuchitsilu uyahlanya wena.

  • @DeanFrancisco-o9v
    @DeanFrancisco-o9v 17 днів тому

    Sekulu

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 19 днів тому

    Tikalowa boma ife a DPP tizabwezeretsa muofesi onse aboma zigawo zonse ni maboma muofesi

  • @usherjamson174
    @usherjamson174 20 днів тому

    History is the best teacher

  • @HarrySinoya
    @HarrySinoya 20 днів тому

    Salute

  • @RichardNgomba
    @RichardNgomba 17 днів тому

    Umakwana