COMRADE NTANYIWA - GEORGE CHAPONDA NGATI WAKULA SIILA UDINDO ANYAMATA ATHANE NDI NDIBOMALI

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 27 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 137

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 7 днів тому +9

    Koma Chiwanda chalowa Dziko la Malawi hmmmm sindikuchimvesa.
    Brother Mtanyiwa you are trying your best as the Chosen one.
    Stay safe ✊✊
    Stay blessed 🙏🙏 and protected.
    Never give Up Mchimwene keep moving and fighting for the better Malawi.
    Chakwera Why torturing Malawians.

  • @IqrahSikweya-wm5mn
    @IqrahSikweya-wm5mn 7 днів тому +6

    Anabelo zoona kuluza moyo chifukwa cha udindo zoona😢😢 Mzimayi uyu matsiku omwalira amuyandikira

  • @ShownMboma
    @ShownMboma 6 днів тому +2

    Comrad matiyimilisa God save you❤❤

  • @EnochSamuel-o5e
    @EnochSamuel-o5e 7 днів тому +4

    I wonder where she get her courage😥
    Uyutu akunama Jane Ansa anasankhidwira pa Msewu Kodi...??

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 7 днів тому +3

    Ndilipo zooonadi abale tikuvutika nde chikangawa adzawineso dzikoli lidzakhala masanza ntanyiwa mukunena zooona💔💔💔💔

  • @AkimumusaMusaakimu
    @AkimumusaMusaakimu 7 днів тому +4

    ❤❤❤❤umatiimilila comrad ntanyiwa

  • @FelixGuta
    @FelixGuta 7 днів тому +2

    You're right my brother

  • @wedsonnyirongo5166
    @wedsonnyirongo5166 7 днів тому +3

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥....him....osawaopa guys this is our country ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 6 днів тому +1

    Comrade big up. The opposition parties in Malawi are dead.
    Useless

  • @ChawingaMwaseteza
    @ChawingaMwaseteza 7 днів тому +4

    Mayesa munatiwuza kuti,Semantic imeneyi sizagwila ntchito ngati mungazakhale muli moyo..ndiye lelo mukutiso akangovomeleza basi aluza,,tiwuzeni xowona comrade

    • @MandalaChaona
      @MandalaChaona 7 днів тому

      Eya ananena but he needs support sakufuna Kuti Opposition ndi Amalawi tingokhala Bas, Koma tizimupasa mphamvu thru action.

  • @GraceKalombola
    @GraceKalombola 6 днів тому

    Eish ,,,God protect you where ever you go. Mukuyesetsa kwambiri koma anthuwo ndiomwe alibe mtima omvesetsa ndikuvomeleza chifukwa zawo ndazibale awo zilipabwino Amtalimanja tulani pansi udindowo

  • @esthermkwapatira1693
    @esthermkwapatira1693 5 днів тому

    Ndipo mr ntanyiwa mwatirankhurira tikunzuzika ku south Africa masamba omwe timalima kuno bonya,akut ayenda Monday ndee kaa tiona tiona kut atichita zotani chifukwa or tibwerere kumalw mabvuto tikulima kuno kunzuzika koma tirowera kuti😢😢😢ma paper tiwatenga kut geni ya bonya tanaposi kuno timaseza kumakuwa tanaposi makomo timaguritsa kachipukutu,koma kut tithandze kumudz anthu akagure baketi rachimamga malw okoma uja rero alikut ambuye ndalira kwainu mokuwa dziko lapansi tirowera kut ku School sitinapite kubwera ku south Africa ntchto zikusowa amalw tachulukana penapaliponse tikulima kumadmba malipiro banchi yampiru kukaguritsa akut ma pepala tirowera kut ambuye😢😢😢😢

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 7 днів тому +2

    We are fed up with this leadership.

  • @ChanceZambika
    @ChanceZambika 7 днів тому +3

    Umakwanaa ❤❤❤

  • @MaggieJsinkaika
    @MaggieJsinkaika 6 днів тому

    Mumakwana ntanyiwa umatiimilil❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @AbdulJohn-t7l
    @AbdulJohn-t7l 6 днів тому +1

    Malawi ikuwopsa kuposa mkango tikudikila kulandila ma holiday next month koma sitipita ku Malawi malinga ndi momwe dziko lathu lili azisogoleli mwatiwonongela dziko lathu chifukwa Cha dyela lanu

  • @PatumaCassim
    @PatumaCassim 6 днів тому

    Ndakuiiimikiran manja mr ntanyiwa ..... anthu tikuvutika kuno chifukwa chothawa dziko lathu sisilibwno 😢😢😢ukapezaso ka ndalama movuta momo kakuthera kumiza kut anthu agule chakudya kuopa kut makolo Afa ndi njala 😢😢😢😢 mayiiii malawi ikupita kut chakwera iwe undiyakhe wamva 😢😢😢

  • @nthandozamantungwakhumalo1507
    @nthandozamantungwakhumalo1507 6 днів тому

    ndipo live Ntanyiwa iweyo umanena zoonadi amalawi akuvutika ku south Africa ndi akut akugulisa poison 😢😢😢😢 kunena matemba

  • @ShinglaiAli-be3yn
    @ShinglaiAli-be3yn 6 днів тому

    Ibrahim Traore can you adopt Malawi please 🥺🥺🥺🙏

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 6 днів тому

    Mina khe,, am tired with chakwera government,, every day problems, problems until when.. Us Malawians we're really suffering here in SA because we can't do anything. Police, police everywhere

  • @PhillipChisanu-k3r
    @PhillipChisanu-k3r 6 днів тому

    George Chaponda Plz! Plz! Plz! Wake up, you have to organize the team for Demos.Plz

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 7 днів тому +1

    Inu a chaponda Ku opposition parliament mukugona..mayi WA Ku mulanje ija amayenera kukhala wankulu WA opposition

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 6 днів тому

    Anabel akumawuzidwa zochita ndi order from above, Koma choti mudziwe Mulungu alipo kunja kuno amasintha nyengo m'mene akufunira

  • @LameckNgoma-f7k
    @LameckNgoma-f7k 6 днів тому

    You Tube is my best.

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 7 днів тому +1

    Ine ndi wa dpp koma mr chaponda mukugona

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 7 днів тому +2

    JENI ASA KODI ANACHITSEDWA NDINDANI JENI ASA ANAMUCHOTSA NDI CHAKWERA NDIYE KODI IWE ANABEL NDIWE NDANI

  • @JonaSato-j8e
    @JonaSato-j8e 6 днів тому

    God be with you mr ❤❤❤❤

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc 6 днів тому

    Amene akut zunza lerowa azayiwone ndende anthu amenewa

  • @hastingskayange
    @hastingskayange 6 днів тому

    Zofinika mademo ku Blantyre Mzuzu ndi mmadela onse kuti Mai mtalimanja ,mpesi atule pasi maudindo awondi smartmatic machine sitikufuna ndipo isangwilitsidwe ntchito... stupid MEC and NRB.

  • @stevietungama9775
    @stevietungama9775 6 днів тому

    Comrade ntanyiwa paja munati muzalowa mu system ya smartmatic nkuisokoneza plan imene ija isalephereke coz a opposition Sali serious

  • @EmmanuelSambani
    @EmmanuelSambani 5 днів тому

    Anabel tikufuna tikuuze kuti Jean Ansa nayeso anasakhidwa mwandondomeko koma zinatheka anatula pansi udindo zamveka.

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 7 днів тому

    Comrade ntanyiwa paliponse mmalawi muno pali mavuto kunena kwaiwe palibe ciliconse cikutheka.cokakamilaco cimeneco cawoneselatu kuti cisakho icici palibe ca mzeru.Ndizomwe ndimanenazo kuti ngati smart matic sicoka pali mavuto.pac bungweli ndi la mcp osati a malawi ai mbuzi za anthu, zisilu palibe comwe akucita ife tipange zoti zitithandize.comrade kobili angonyengela panopa ithyoke ithyoke dzikawoneka ku msewu komko.

  • @BilliatManuel
    @BilliatManuel 7 днів тому +4

    Eer koma mzimai uyuyu watitopetsa mwava iwe ukuona ngat jen answer uja adadziika yakha pa mpando? Bwanji anadzichepetsa nkutula pasi udindo ndye iweo ndiwe yani opusa iwe

  • @GetrudeBanda-sd1yf
    @GetrudeBanda-sd1yf 7 днів тому

    Zoona Antanyiwa atiuze a opostion ngati sakufuna kutipulumusa kuti tisakhe wina wa pa dela inuyo or kalindo

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 6 днів тому

    Well spoken

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 7 днів тому

    Yhis is so pathetic..Mr ntanyiwa is really concerned while thos Government is selfish and stealing.May God judge this evil act.

  • @EmmanuelKapichi
    @EmmanuelKapichi 6 днів тому

    Opposition yomwe mukuyinenayo mmesa mmesa ndiyomwe ija munayithamangisa mm'boma ija... Asiyeni a mcp atifinye mmesa tinawafuna... A dpp khalani chete choncho.
    Inuyo omenyera ma ufulu do something mmesa ndinu munachosa dpp ndiye apa muzitikwana

  • @TimexKaufa
    @TimexKaufa 7 днів тому

    Ntanyiwa ngati Ntabel akukana pasakhale kuvuta ife tikufuna kubwera ku Malawi . TIKUFUNA PETER AWINE

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 7 днів тому +1

    A dpp udf pdp aford utm lef nonsenu mukugona kod mwapasidwa ndalama?

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera 7 днів тому

    Annabel Mtalimanja must go she is apupet of MCP.

  • @MattinGold-l9w
    @MattinGold-l9w 6 днів тому

    Chakwela ndi nduna Zake onse alibe nzeru zitsilu zokha zokha mbava za anthu

  • @VicentMalopa
    @VicentMalopa 6 днів тому

    I SECOND YOU BRAVO KEEP THE FIRE
    PAC IS USELESS

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 6 днів тому

    Zikuoneka kuti dzikoli ndiku Lilongwe ndipo eni ndi a Chewa.
    Achewa akuchita zomwe akufuna tonse mkukhumata,akuletsa ma Demo mmene akufunira ndipo sizikuthekadi.
    MCP ikuenda ndi zikwanje popanda omangidwa.
    Thats why akuti ndi Achewa ndi 15million

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 6 днів тому

    Chaponda akugona heavy

  • @mgarachimsybwoy
    @mgarachimsybwoy 6 днів тому

    GOD HELP US

  • @DamianoYohane
    @DamianoYohane 6 днів тому

    And kalamulo aka komati injunction ka mademo kumaletsedwa aaaaaaaa komaso izi zomati kumakambirana nthawi young kuchita mademo sizabwino ayi

  • @OwenchangnyaMkandawire
    @OwenchangnyaMkandawire 6 днів тому

    Ineyo mkatolika mwenimweni.ndakhala ndikunenakuti anthu mumaopa mikhanjo.ansembe,mabishops ndizitsiru za anthu.mwaona nokha tsopano.mukhaula chifukwa chokunamizani ndi ukhristu.

  • @johnnyirenda5848
    @johnnyirenda5848 7 днів тому

    msartmatic Tizagwiritse 2030 tizachidziwe kaye 2025 manual Basi Zikakanika Kuvutatu adikile nthawi. Chachilendo Pali anwayi kuchiona Atsoka Chachilendocho Sabgachione Basi ndiyekuti nthawi imeneyo Yadutsapo Basi
    Its a matter of time ler them wait.

  • @HamzahMiles
    @HamzahMiles 7 днів тому +1

    Kodi asing'ang'a amene mumazimenya pa mtima aja, mesa ntchito ndi iyi, yosowesa anabelo, chakwera,Banda and kamajekete

    • @ColetteMalunga
      @ColetteMalunga 7 днів тому +1

      Kkkkkkk amangodziwa kulodza anthu osalakwa kuti alandidwe amuna. Asing'anga odziwa mankhwala adatha 😂😂😂😂😂

    • @HamzahMiles
      @HamzahMiles 6 днів тому

      @ColetteMalunga nda Galu ndithu

  • @BrightonChidzalo
    @BrightonChidzalo 6 днів тому

    Nhanyiwa apack ndipo ndiathu overall chisoni kwambili kodi nfhawi yapita ija athu amene aja alikut abale mukulolelad matching azagwile Natchitoches amalawi mwadya ndalama zochuluka koma Ana abale and mwakonda iiiiiii

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson 7 днів тому

    Amalawi malodza sagawana inu munthu wa mkazi asatipusise Ayi and this time Mademo everyone must get prepared must bring anything to defend himself.isati nyase MCP ndi mwana Tembo.and I don't know why Chakwela. Is still president after mgwilizano unatha auzeni comrade agalu awa apposition sakuva malanginzo anu.bwanji osawa uza anthu onse owasatila kuti tiyeni tonse tichite Mademo coward all opposition leaders im sick and tired with this so called leaders all are usless and don't know what they stand they must just quit and leave Malawians alon mukutipwetesa ife masapotazi

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 7 днів тому

    Ndipo mayi wandikwiyisa kwambiri atha kundiyakhulisa pambali ndimwano umene akunena komaso kuzikonda mitumbwa ndiye kuchoka ku chitipa mupaka ku sanje mutali manja ndiye ali ndizeru. Chimene tipange chisakho apange ku lilongwe komweko kumwera ku mpoto asabwere

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 7 днів тому

    Ukuku kuiputa nkhondo straight, ameneyu yu aonesedwa shuwa

  • @Yusuf-j6c
    @Yusuf-j6c 6 днів тому

    We need actions please 🙏

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 7 днів тому

    Iwe chitsiru cha Munthu, Jane ather anachita. Apa zimene ukuganiza iwe sizinachitike ukuopa chani zikazachitika Court lizalamulaso

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 7 днів тому

    Koma atura pansi udindo crocodile chi hure chimenechi ndi chikangawa wakeyo zonsezi zisiya pansi udindo

  • @ShareefKalima
    @ShareefKalima 7 днів тому

    Nkhan ndi yot M.C.P. yikuwopa Manuel chifukwa akuziwa kut Manuel sangawine komanso kod Malawi si wa M.C.P Ayi. NKHAN NDI YOT CHAKWELA AFUSIDWE CHAKA CHA M'MAWA.AFIKE WINA PAMENEPO

  • @AdamuBenard
    @AdamuBenard 6 днів тому

    Yess

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 6 днів тому

    SIXTEEN TRILLIONYO AKUNGOLWSTILIRA AZIMAI NDI KUPANGILA ZIBWENZI AWA A MCP WA .TATOPA NAO PANO

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 7 днів тому

    Congress yaonetsa kuti ndi madolo ikungodods ZIPANI ma CSO left right and centre 🤣🤣🤣

  • @MlaziJames
    @MlaziJames 7 днів тому

    Please Please guys mademo more fire chakwara atule pansi udindo please osavotenso basi

  • @PeterRabson-z3w
    @PeterRabson-z3w 7 днів тому

    Chaponda akugona bola sameer kapena Mary navisha akanakhala leader of opposition osati Dalai amamuyamikira gotani hera dzana zanziii

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 6 днів тому

    KUTI IWO AKHALENSO MAPULEZIDENT ATSOGOLERI ENA A ZIPANI ZOTSUTSA MCP IKUNGOWAPHA PA ZONDEGE OLO KUWAKHAPA NDI ZIKWANJE OLO KUWAPHA POWAPATSA ZINDALAMA ZANKHANI NKHANI KUTI ASATEKESEKE KUFULUKUTA KUCHITA MADEMO OLO KUNENERA KUTI SMARTEMETEC MACHINE AYI KUGWIRITSA NTCHITO POVOTA .

  • @KettieNathaya
    @KettieNathaya 7 днів тому

    Ayi iye sanayambe ndiye kugwila ntchito ayi kunali Janne Assa iye ndi ndani ameneyo

  • @youmad9087
    @youmad9087 6 днів тому

    Hahahaha...chamudzadzila ndani chaulele

  • @BrunoChakukuma
    @BrunoChakukuma 7 днів тому

    Chakwera anakupasa yakumbuyo😂😂😂

  • @julygabrieltv9093
    @julygabrieltv9093 7 днів тому

    May God bless you

  • @LovemoreJeremia
    @LovemoreJeremia 6 днів тому

    Ku opposition kuli anthu okula mtima kwambili

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 7 днів тому

    Pither muthalika alindi umuthu kmaso president wabwino kom chakwera ndichimundu choyipa moyo

  • @AlexanderBilliat
    @AlexanderBilliat 7 днів тому +1

    Mademo achitike basi guys tikawalekerela anthuwa tizavutikaso Zaka Zina zokwana 5 ndipo tizalira kuposa momwe tivutikila pano

  • @SamukLungu
    @SamukLungu 7 днів тому

    Ife sitiziwakuremba nanga makometi athu azipitakuti?

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 6 днів тому

    Ntanyiwa ndiwaboza zana amat sazabera mavoti ngakhale agwirise ntchito sysmartic relo akut a oposition azaluza akulu inu tinve ziti

  • @JamesYusufu-m4r
    @JamesYusufu-m4r 5 днів тому

    anthu tazukani chakwela anagwil8zana ndibushili. akufuna magazi.bass akapeza magazi akondwela basi sichina akufuna magazi a mcp

  • @MpasulavisaSonjo
    @MpasulavisaSonjo 7 днів тому

    No connection between MEC and Fuel.

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 7 днів тому

    Tisalekelere..zaka 5 zina nso ayi..apa Malawi tonse tiyeni tigwirane manja tiyende pamodzi

  • @MikeSymon-si8dw
    @MikeSymon-si8dw 7 днів тому

    Nothing is good 😢😢😢

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 7 днів тому

    Ndipo zoona kulekelera uchisiru uwuwu dziko li lisandukadi masanza straight

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f 7 днів тому

    Pitani ku court, koma uyu sakuchoka. Kkkkk

  • @StevenKupheka-k6b
    @StevenKupheka-k6b 6 днів тому

    Kod hule ameneyu ine amandinyasa heavy mwinanso anapakula kale beans wina

  • @MussaMajid-c2i
    @MussaMajid-c2i 6 днів тому

    Bwana awawa atichedwetsa tiyeni pa msewu

  • @jesuit579
    @jesuit579 7 днів тому

    Mmawa pa nsewu guys

  • @Fanie-i7z
    @Fanie-i7z 7 днів тому

    Mtambo ndi Kalindo sanamuike pa mpando Koma munakavota nokha anthu don't condemn these people.

  • @KalongaWhy
    @KalongaWhy 7 днів тому

    Komadi a opposition atiphetsa chifukwa ife timafuna a opposition koma akoti kuopsesedwa basi kungokhara ziii ndiyeti tiyeni timvomeleze kuti tisaka zote namapwala chakwera akaleso chifukwa amene tikwafunawo aliphee inu chakwera chipani chimozi cha MCP yokha namachende chakwera azuze anthu ma million azuzike kambu ka chikangawa kume kuli iwe mboli yako wanditopeka kwambiri

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 7 днів тому +3

    Zipolowe zikazayamba zikufunika kuzamuchita target Annabel ndi kumupha basi chifukwa atayambitse nkhondo m'malawi ndiyeyo,watitola kwambiri

  • @ChrissNanchinga
    @ChrissNanchinga 6 днів тому

    Umatha ntanyiwa

  • @PatumaCassim
    @PatumaCassim 6 днів тому

    Iiiiiiii koma mai mfiti imenei bwanji koma amauluka sure chifukwa chomwe akukakamila ndi Chan eeeee koma ali mai anga ndikanalorera kudana nawo koma mpaka atasiya pansi udindo eeeeeee ndagoma nae 😮

  • @LucyManda-y2l
    @LucyManda-y2l 5 днів тому

    Chipanda inu a Mthanyiwa ife sitikanadziwa kanthu kuti a mcp akubera koma Mulungu akupatseni moyo wautali.
    Kodi zipani zotsutsa, atsogoleri akugulaninso nanga bwanji mwangoti ziiiii bwanji?
    Kodi mcp ikufuna mdziko muna mukhala chipani chimodzi? Nanga bwanji sakulolerana ndi zipani zotsutsa. Thawi yapitayi Jane Answer anachotsedwa nanga Anabela akukakamira bwanji?

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 7 днів тому

    Makina achoke. Ndipo a malawi 🇲🇼 tonse tisalole machine awa zisatekhe izi olo pan'gono

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 7 днів тому

    Sakufuna manual chifukwa akufuna kubera poti anavota kale..mene dziko lirili apa a mcp akuopa chifukwa anthu sakuwafuna

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 6 днів тому

    Ntanyiwa ndiwe chitsiru chenicheni

  • @Mahamudu-q6b
    @Mahamudu-q6b 7 днів тому

    Wofunika timpitile kwawokonko tikampange mademo tikamuwotchere nyumba ndipamene angaziwe kuti amalawi akwiya🚪🏃💨

  • @JustinMakoka
    @JustinMakoka 7 днів тому

    Wauzeni akalindo ndi mtamboyo coz adaika mcp m'boma

  • @peterbyson6269
    @peterbyson6269 7 днів тому

    Koma amwene lero nde mwalankhuladi tikuvutika ku south Africa kuno ndithu

  • @YousufuDaitine
    @YousufuDaitine 7 днів тому

    ❤❤❤❤

  • @JoseJangiya
    @JoseJangiya 6 днів тому

    Mmayi ameneyu tingomusowetsa basi

  • @AshilafuKasongo
    @AshilafuKasongo 6 днів тому

    Mukufuna kukwezedwa udondo kuchoka pa anabelo kupita ku Anabela talimanja fiti yayikazi yowuma mtima mwina dzikoli likufunaka kulipelelera sembe kuti lipulumusidwe ine ndakhozeka kupelekera sembewo bola anthu apulumuke kuchilombo chimenechi

  • @pilirani3536
    @pilirani3536 7 днів тому

    Amayi ndipo akudzimva sakufuna kumva zodandaula anthu

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 7 днів тому

    Zooonadi aaaa akuti tola tsopano...

  • @Timothy1142
    @Timothy1142 7 днів тому +1

    Za ku area 49 zili pati za mimba

  • @JoseJangiya
    @JoseJangiya 6 днів тому

    Timakunyadilani mmatiyankhulila zikomo