ZAULULIKA// Dan Lu waulura zinsinsi zina zomwe zikuchitika mu music industry ya ku Malawi.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 вер 2024
  • Factory265 caught up with legendary artist Dan Lu to shed more light on what has prompted him to start thinking of quitting music.

КОМЕНТАРІ • 76

  • @user-ro1pl7rv7z
    @user-ro1pl7rv7z 18 днів тому +3

    😢😢😢Ehhhhh Sorry ajangu nambo basi ngayiw^enga mmwejo amdala basii, ngadandaula

  • @sharrifgwape7169
    @sharrifgwape7169 18 днів тому +8

    Ndale ndizomwe zimakupha oyimbanu ma supporter a mcp sangakukondeni big siyani ndale ukhale oimba basi

  • @AlexBeluka
    @AlexBeluka 18 днів тому +2

    Kaya zako izo! Kaya zako izo, uziupezaaa uziupeza

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 14 днів тому +2

    MCP ndi ufiti weniweni komanso osaphunzira ndipo anapha Chilima

  • @Frankkabotolo
    @Frankkabotolo 18 днів тому +2

    I love Dan's old songs koma zomwe akutimba pano zotukwanazi mmmm

  • @nedsonchanache7822
    @nedsonchanache7822 18 днів тому +8

    Zangowavuta awa avomereze.... Time comes time goes

  • @user-ih3qe8ho3v
    @user-ih3qe8ho3v 14 днів тому +1

    Dan Lu old song was very fantastic but now mmmmmh whow bad😢

  • @tenexchikumba
    @tenexchikumba 18 днів тому +2

    Big artist, don't be discouraged

  • @chancymakuluni8818
    @chancymakuluni8818 17 днів тому +3

    A Danlu vuto loyamba ndi kuyimba zotikwana mmmm kungova imene ija mmmm ayi.
    Chachiwiri kuyimba za ndale zimapangitsa kuluza fans.

  • @MonicaBvumbwe
    @MonicaBvumbwe 18 днів тому +3

    Mmm dan ifetu timakukondani mwalekelanj kuimba music 😔

  • @FloraZoto-b8s
    @FloraZoto-b8s 17 днів тому +2

    Ndamuvesa sakufuna zausatana

  • @CalorynerHolla-yh9be
    @CalorynerHolla-yh9be 17 днів тому +1

    Napman anadandauulapo nkhani imeneyi kuponderezana

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 18 днів тому +2

    Real fact

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 18 днів тому +1

    do like what aba'le do.makape asakudyere work with local DJs, youtube bloggers tidzivera ifeyo

  • @officemoyenda-rj2hz
    @officemoyenda-rj2hz 18 днів тому +5

    Sanasiye but he is contemplating to : because the industry is now a non regulated mixed bag

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr 18 днів тому +3

    Kumatchula mwachindunji Dan,,kagulu ka athu asataniki ndiwe odala bro,kuzindikira zakumidima ndikutheka anamupasa poison aja ndi asatanic .

  • @AUFIMADENGU
    @AUFIMADENGU 18 днів тому +1

    WACHIYAWO WANGALUSA BRASA.MATIVESA KUKOMA

  • @shukurajaaffarie-cr2nm
    @shukurajaaffarie-cr2nm 18 днів тому +1

    Ndakuvetsetsa mwana wakwathi

  • @MCLoudZeka
    @MCLoudZeka 12 днів тому

    nyimbo zako azikavera. ndi APM ife ai

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 18 днів тому +2

    umachulutsa kutukwana nyimbo zanu brother inde pumani 😅😅😅😅 ine ndiye nyimbo zako phone Mwanga mulibe

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe 18 днів тому +2

    Ati group of people not groups of people ,tazingoyankhulani chichewa abale

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 18 днів тому +1

    Zimavuta kumavomelezah koma wakuluwa zawabvuta ndithu avomeleze

  • @SEEJSHJEFFREY
    @SEEJSHJEFFREY 18 днів тому +4

    Things are changing each and every day...Dan akanangokhala mu industry yake osati kuona za ena chifukwa sangasinthe zinthu zomwe oyimba apano akupanga

  • @StellaCharmer
    @StellaCharmer 17 днів тому +1

    Sinyimbo zonse zomwe amatukwana

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 16 днів тому +1

    Mmesa wachiyawo wangalutsa Sono. Zikuti bwanji

  • @michaelnazimera7231
    @michaelnazimera7231 15 днів тому +1

    Inu mumatha bro kuyimba osafooka ai

  • @JamihFernandoSimao
    @JamihFernandoSimao 18 днів тому +1

    Awa alibe nzeru

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 18 днів тому

    Uwetu ayao uwetu wamanyi ❤❤❤

  • @jowiemhango5058
    @jowiemhango5058 17 днів тому +1

    Muli ndi anger tu phiri. Inuyo osaimba mangelengelewo bwanj anthu akonde???? Umadzimva iwe

  • @KennethObvious
    @KennethObvious 13 днів тому

    It is true broh akulemekeza chibwana

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 13 днів тому

    Ndi zoona big... Pano music mmm mwalowa zina

  • @PRINCE_COOL78
    @PRINCE_COOL78 12 днів тому

    Anthu anakutuluka dan since unaimba nyimbo yotukwana ija ukuphunzitsa chani kwaachinyata manager wakoyo anatolia bwanji kuimba zopusazo

  • @EvenessBwanaisa
    @EvenessBwanaisa 16 днів тому +1

    Dan Lu umatha anthu gerous basi

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 18 днів тому +2

    Musamapange comment ngati mukulankhulana ndi Dan Lu😂😂😂page yitu siya Dan Lu awa angopangapo post nkhaniyi

  • @AmadumtungasudiSudimtungaamadu
    @AmadumtungasudiSudimtungaamadu 14 днів тому

    Mumatha ndpo tlip ambr okhala kumbar yanu zandaleazitengele ku music aaaa sbwn😢😢

  • @Zied-u2k
    @Zied-u2k 13 днів тому

    Pano zimene mkuyimba ana ama 2 pin ife ndi mbola kuli anatu kuno akiphulisa music

  • @jowiemhango5058
    @jowiemhango5058 17 днів тому +1

    Ingobonani phiri mudziimbila mulungu basi

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no 17 днів тому +1

    Dan lu , iwe shupi usafalitse kacholombo kako , nyimbo yokoma usasiye kuyimba

  • @RiazKalimbuka
    @RiazKalimbuka 17 днів тому +1

    Anatha awa thawi yake inatha

  • @ModesterWilliam-g7z
    @ModesterWilliam-g7z 10 днів тому

    Wati samafuna zopusa

  • @user-dh3gr2cg4o
    @user-dh3gr2cg4o 11 днів тому

    Inuyo mumantha kuimba

  • @MCLoudZeka
    @MCLoudZeka 12 днів тому

    vuto ndiwekha azikuvera APM

  • @MosesSolomoni
    @MosesSolomoni 18 днів тому +1

    Oimba kungoyamba ndale anthu amaku tulula bas apapa amukonde dan lu ndi a DPP bas azipani enawa sangamukonde Dan Lu tsogolo loimba waliononga ekha ndiwe oimba wabwino nyimbo za ndizokoma km mawanga a DPP wobasi ndamene awononga zinthu sorry bro

  • @JulietGunde
    @JulietGunde 12 днів тому

    Nkhani yavuta ndindalama😂 koma to be honest Dan Lu kalekale muja umaimba nyimbo za dzeru hvy

  • @ianchapotela8773
    @ianchapotela8773 18 днів тому +1

    zavuta ku mpanje

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 18 днів тому

    Hmmm ndamumvetsa Dan, that's what happens in music industry, and nzapakanthawi. In other words, muli satana mu music,

  • @InnocentChisale-fo5di
    @InnocentChisale-fo5di 18 днів тому +1

    Zomereza unatha basi vuto munalowa ndale ndizomwe zinakitsitsa aise

  • @user-ju9lg5pg5g
    @user-ju9lg5pg5g 18 днів тому

    Kuimba ngati kuli Mbali yake sangasiye Koma ngati isali Mbali yake Asiya komaso politics ndiyoipa amapha luso la oyimba chifukwa kuyimba umafunika uzosangalatsa anthu onse ndiye ukapita Ku politics zimavuta Kuti zitero chifukwa Mbali yomwe iwe Uli pankhani ya politics ndikomwe anthu amakusapota kwinako ayi so oyimba Aku Malawi musamalowe kwambili kumeneku luso limantha chinsazo ndi mkasa komaso tikapita kuzambia organise family nthawi ya edigar Lungu anatheratu chifukwa anali Mbali inayi panopa sindikunkhulupilia ngati anthu ambiliachipani cholamula angavere nyimbo Za Dan Lu

  • @ConeriasPhiri
    @ConeriasPhiri 15 днів тому

    Akufuna angopuma awa

  • @PreciousMangulama-l4i
    @PreciousMangulama-l4i 16 днів тому

    Mr lufani musatisiye musakwiye musa foke tihansizeni tima phuzila zambili kwainu

  • @LanjessYehuru-f1o
    @LanjessYehuru-f1o 18 днів тому

    Sanachite bwino kugwa mphwayi ndi artist wankulu anakakhala azingokankha

  • @DesireNkosi-p6b
    @DesireNkosi-p6b 18 днів тому

    Malawi

  • @UmaliDickson
    @UmaliDickson День тому

    hhhhhhhh koma kumalawi anthu mukuvutika bwanji ife pheee achina DKY olo kudyera mnkhwani

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 17 днів тому

    Dan ife timakunyadila kuyambila kale

  • @AmadumtungasudiSudimtungaamadu
    @AmadumtungasudiSudimtungaamadu 14 днів тому

    Kuzolower kupondelezana bc malawi🤪🤪🤪🤪

  • @EliyaYakobe-bg6jb
    @EliyaYakobe-bg6jb 18 днів тому

    mmmmm

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 18 днів тому

    Siyani mwalimbana nako kulimbana wabwino 😅😅

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 18 днів тому

    Vuto kutukwana kwako mnyimbo so athu anakutuluka

  • @user-ju9lg5pg5g
    @user-ju9lg5pg5g 18 днів тому

    Anyama ambili amene zikuwayendera bwino pano Kuti muone samalowa Dale bwinaso amene abwera pa mbuyo pake komaso pankhani ya nyimbo omvera ndiamene amanena Kuti ndiyabwino osati oyiyimba ndiye anthu akusankha kumvera zimene mukuziwona ngati akumangokuwazo komaso chinthu China Malawi samafuna munthu oyankhula kwambili

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 16 днів тому

    Siya kuyimba zandale iwe pamtumbo pako

  • @SEEJSHJEFFREY
    @SEEJSHJEFFREY 18 днів тому

    Game yathinatu....😅

  • @MayimunaZuber
    @MayimunaZuber 14 днів тому

    Zabwino zonse brother musiyedi kuyimba mwapanga chisankho chabwino

  • @user-ju9lg5pg5g
    @user-ju9lg5pg5g 18 днів тому

    Komaso Ku Malawi tili ndi vuto poyamba munthu zinthu zikamamuyendera timkati ndiwonkhwima pano tasintha tikuti satanic ok!!! Zikatero one ndimangokumbukila nyimbo ya fuko ya Malawi Kuti amene anayimba nyimbo imeneyi anaziwona ndipo anapangadi kafukufuku kumuziwa bwino mmalawi mmalawi samafuna kumuwona mzake zikumuyendera ayi, chikwa chakuti nthawi zambili sitimaziwa anthu Anja Kuti adutsa motani mwachinsazo sent nthawi Ina anali ndi interview amafotokoza mmene anayambila ena sangankhulupire Koma ine ndinankhulupila chifukwa ndimkamuwona zikuchita so let's put satanic pambali enawa adutsa mwambili ndipo akumana ndizambili Kuti afike pamenepo

  • @isaacmikondo
    @isaacmikondo 18 днів тому

    olo wa satanic pano ali mmaluzii😅😅

    • @chekiamaabdul5083
      @chekiamaabdul5083 18 днів тому +1

      Ndiye ukhale kutali ndi Mulungu uzikhalaso mmaluzi aaaaa hell is waiting as well

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 18 днів тому +1

    Dan luuuu akunena zoona anyamata ambiri ayamba satanic anthu ambiri sakuchuka pa okha

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 18 днів тому

    Awopa mcp kumupha