DALITSO KABAMBE NAYE WAFIKA KU MA DEMO NDIPO WAYANKHULA IZI AKUTI UTHENGA UWU UPITE KWA CHAKWERA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 26 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 271

  • @IBRAHIMCHIPASULA
    @IBRAHIMCHIPASULA День тому +58

    Dr Kabambe is a real leader. If we want change, this man is a change. I salute you Mr president, your actions speak louder than words. Long live Dr Kabambe. My fellow Malawians, let's love our country by voting for this man who is not scared but to die with Malawians, DR DALITSO KABAMBE.

  • @jogechawa6192
    @jogechawa6192 День тому +42

    I'm definitely voting for Kabambe he has SKC qualities

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale День тому +20

    Kabambe my Vote ...May the spirit of Chilima guide you my President ❤❤❤
    I have all the reasons to convince my fellow youth and my family members to vote for you ❤

  • @KampilaAllie
    @KampilaAllie День тому +15

    Congratulation dalitso kabambe keep it up ❤

  • @ChikondiMasebo
    @ChikondiMasebo День тому +27

    Mkulu wa a police atule pansi udindo chifukwa akugwilitsidwa ntchito ndi mcp achoke.

  • @fanymatchumbuza6125
    @fanymatchumbuza6125 День тому +2

    We always pray for Dk .God should always protect him .He is our hope .am now encouraged tu vote.DK yu have ma vote

  • @LinlyMathewe
    @LinlyMathewe День тому +5

    Dr Kabambe 2025 boma UTM my vote ❤❤❤❤

  • @EnerstBanda-m4s
    @EnerstBanda-m4s День тому +1

    Wandikumbutsa Chilima Dr Kabambe more fire my president osaopa osatopa osafooka osaphethira

  • @RuthTimothyChirwa
    @RuthTimothyChirwa День тому +3

    Congratulations my big brother Dr dalitso k ❤❤😂😂😂🎉

  • @johnngambi8018
    @johnngambi8018 День тому +1

    Long live Mr. Kabambe
    Long live UTM
    Viva Malawi

  • @ChikwengaTaelo
    @ChikwengaTaelo День тому +1

    Congratulation Mr kabambe fire!!!!!!!!!!

  • @MicksonPakhota-j1q
    @MicksonPakhota-j1q День тому +2

    We are behind you Dr kabambe, more fire🔥🔥🔥

  • @KampingoJere
    @KampingoJere День тому +4

    Wow kabambe my vote

  • @AnaJakson
    @AnaJakson День тому +3

    Tikuwona ngati a dpp ali ndi manda utm yoooo❤

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 23 години тому

    Osaopa, osatopa osafoooka. Bravo Kabambe.

  • @MigarChancy
    @MigarChancy День тому +2

    Big up Dr Kabambe my vote ❤❤

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 День тому +11

    Kabambe moto buuuu osaopa osafooka osatopa

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses День тому +2

    Kutha kwa chipani kumakhala chonchi, mcp uwu ndi ulendo basi alephera kuwatumikila amalawi. Ndipo kuchoka kwa chakwera pa upresident kuzakhala kuchitisa manyazi.

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 День тому +14

    Kabambe mumene wafikila ku mademo zaonesa kuti ndiyemwe azalamulila boma 2025 wina afune asafune

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift День тому +1

    Abuye mulungu mukumurekeraji chakwera kt azitizuza?

  • @EnockMvula
    @EnockMvula День тому +2

    koma chakwera abare murungu amurange ndithu ziko ramarawi kufika size iyiii yooooo

  • @SarahsKitchenMW
    @SarahsKitchenMW День тому +6

    Kabambe 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🥳

  • @Maxielyie
    @Maxielyie День тому +2

    Big up Kabambe, I'm keeping your vote

  • @EllenNgona
    @EllenNgona День тому +4

    ❤ kabambe moto guys 🎉🎉🎉🎉

  • @MikeLodzi
    @MikeLodzi День тому +7

    kaya mutikhapa koma 2025 chakwera ng'oooooo suzawina aise iwe pita kima batile kwakoko

    • @ChisomoYosefe
      @ChisomoYosefe День тому +1

      exactly adzayenda chothawa galu ameneyu pamodzi ndi committee yake yonse

  • @LinlyNgala
    @LinlyNgala 50 хвилин тому

    Zikakuvotelani zikwanje zomwex, 2025 kabambe boma❤❤❤❤❤❤

  • @Staphelsavimbindhlovu
    @Staphelsavimbindhlovu День тому

    Hundred percent Mr kabambe may God protect u and guide u . We love you mr kabambe ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @GraceChikosa
    @GraceChikosa День тому +1

    Dalitso Kabambe mumatiimira inuyo ❤❤❤❤❤

  • @AlfredJuliusTemboh
    @AlfredJuliusTemboh День тому

    Dr Dalitso kabambe please you must go around the whole Malawi doing this. It's so encouraging to see you amongst your pipo. Chakwera is doing nothing to the Malawians and and these demonstrations were suppose to be of impiching Chakwera. Fight for the freedom of your country and I will surely support you

  • @RuthMkangala
    @RuthMkangala День тому +4

    Musiyeni kàbambe naye ndi munthu Ali ndi ufulu opanga nawo ma demonstration

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo День тому +10

    ALLAH mutetezeni kabambe coz waonetsa mtima okonda mbendera yake

  • @Spiderujay
    @Spiderujay День тому

    Chakwera mapwala ako😂😂

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 День тому +1

    Bravo Dr Kabambe

  • @tracybennie7783
    @tracybennie7783 День тому +1

    Tasangalala. Kwambili Mr. President

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 День тому

    Kabambe ndi Dolo komanso ndi ophubzira kwambiri than chakwera 2025 ✅

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn День тому +1

    Chakwera nayenso amapanganawo mademo Kabambe nayenso ndimunthu akuyenera kupanganawo

  • @AnnahZimba-v8i
    @AnnahZimba-v8i День тому

    Keep it up Mr kabambe

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence День тому +4

    Kabambe moreeeee fireeeeee 💪💪🚰🚰🚰

  • @JosephNambazo
    @JosephNambazo День тому

    Congratulations Dr Kabambe for showing that you are a true Malawian son

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo День тому +2

    KABAMBE MY VOTE.OSAOPA,OSATOPA,OSAFOOKA

  • @Eresia-z2i
    @Eresia-z2i День тому +3

    Congratulations Mr kabambe

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 День тому +4

    Zionetsero always zimakhala za ntendere koma a Police akayamba kuphulitsa tear gas anthu amayamba kubalalika mkuyamba zipolowe.

  • @CaloreenMphunda
    @CaloreenMphunda День тому +1

    Kabambe my vote❤❤❤❤

  • @AleCloset
    @AleCloset День тому +1

    Mtambo akanakhala Shasha akanabwera lero ku mademo

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya День тому

    Ndipo alanga nose wosokonezsnu mutha psiti iyaaa kufuna kulamulila dziko molanda 😢😢😢😢

    • @wadyazakealibemulandu
      @wadyazakealibemulandu День тому

      Chakwela mbuzi yamunthu amongoziwa kuyankhula chizungu nkhope ngati gweyani wenweni

  • @PhiriChiyambi
    @PhiriChiyambi День тому +4

    Kabambe woyee more fire my vote timafuna atsogoleli otelewa

  • @HappyMsukwa-j1q
    @HappyMsukwa-j1q День тому

    Kabambe 2025 Bomaaa!💥💥🥳💫

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507 День тому

    Well done elder Kabambe a true leader

  • @emmanueljelemani4203
    @emmanueljelemani4203 День тому +1

    Bravo Kabambe

  • @RodgersMwanakhu
    @RodgersMwanakhu День тому

    Ine vote yanga ndayiika pa kabambe

  • @AmoTiamo
    @AmoTiamo День тому +3

    Nanu opita ku mademo muzipita mutatenga petrol mu ma botolo agalasi akuchekuche kusakaniza ndi nchere ndi bomba payokha olo a police atha kuyamika okha

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya День тому

    Aaaa iweso uyu ndiwa DPP asakupusitse ai ndipo anyela sanati tingopempha moyo tidzathana ku msew komko ngati mungalimbe inuyo alomwe fwetseke

  • @prettytambala5687
    @prettytambala5687 День тому

    Akabambe akuvinitsa manja, anathamanga awa😅😅

  • @StevenDastan-f5y
    @StevenDastan-f5y День тому +1

    Bravo Dr kabamba

  • @JogaJoseph
    @JogaJoseph День тому

    Kabambe is best ever SKC friend not fiti manganya

  • @phyzixoscar7003
    @phyzixoscar7003 День тому +1

    Mr Kabambe ndiwofansa koma Chakwela waonjedza ine nyau basi sindidzavalaso ngakhale ndi chikwalidwe chanthu

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 День тому

    Munthu ungafike ku college, university ndikukhala ogona?

  • @ManyatwakoMalopa
    @ManyatwakoMalopa День тому

    Ndiye mukulira chani! Simunati ma demo anu muona kopangira

  • @MartinMajola
    @MartinMajola День тому

    Kabambe next president

  • @ElinesevitaGondwe-cq7tn
    @ElinesevitaGondwe-cq7tn День тому

    Big up mwayambabwino

  • @LinlyNgala
    @LinlyNgala 52 хвилини тому

    Mcp mulila, munjenjemela zenizeni, ndipo muona kovalila simunati 😂😂😂😂😂😂, mukuziotchela CV muli chetee,

  • @peterthawi
    @peterthawi 18 годин тому

    kabambe akhoza kuwina mtown..koma kumudzi anthu saakumudxiwa ahyi

  • @JerieWytonTengani
    @JerieWytonTengani День тому

    DC wa ku Lilongwe achosedwe ntchito ndi osokoneza

  • @DouglasDimingu
    @DouglasDimingu День тому +2

    Chomwe timafuna amalawi sitikhala sure. We don't know what we want malawians sitichedwa kuiwala

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 День тому

    Chakwera please tula pasi udindo

  • @isaacthawani5442
    @isaacthawani5442 День тому

    Panopa dani wanthu ndi wa police ndipo sitikunyegerelani muzipanga matama anuwoo mukakhala ndi sitsilu zizanu za kwa Sundwezo koma ife tizikupezani Manyumba Mwanu modzi modzi munya muona

  • @JohnmjigoMalinda
    @JohnmjigoMalinda День тому

    Ndipo ndiye aliladi chikangawa chakwera ndichisiru kwambiri tsogoleri olemphera

  • @MussahBusiness
    @MussahBusiness День тому

    kom kuno kumala eeeee kuvuta 2025 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @EmmanuelKiwale-n5u
    @EmmanuelKiwale-n5u День тому

    Kabambe my vote

  • @DanNzima
    @DanNzima День тому +1

    Dk 🔥🔥🔥💪

  • @JonaSato-j8e
    @JonaSato-j8e День тому

    Kabambe❤❤❤

  • @JosephChimaliro-ju9px
    @JosephChimaliro-ju9px День тому

    Dk my vote,I can't vote for silly people. In a democratic state, citizens are allowed to express there views on issues affecting them negatively.So let me teach you something,demonstrations acts as eye opener to leaders on areas to improve.

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim День тому

    Dr kambambe nafeso bwanji mutipezele zikwanje

  • @binalisaidi7617
    @binalisaidi7617 День тому

    Wabwela. ........ Thawi ndiyomwei........ Ndikuvotela

  • @AleCloset
    @AleCloset День тому

    Mzimai onyasa nkhope wa police uja atule pansi udindo...

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya День тому

    Machende akeso kabambe mbavayi ingakhale ikulamulila dziko laku kuphwala kwakoko kamanyi iweyo ukutukwana chakwelawe ? Pitalayo pamtumbo pake dziko linamukanika kale machende okwinyikaw

  • @YaxedyAlast
    @YaxedyAlast День тому

    Kabambe more fire

  • @ChristonHilda
    @ChristonHilda День тому

    Osatopa osafokaaa mpakana atule pasi udindo

  • @MeniyaMikaya
    @MeniyaMikaya День тому

    Mcp singathe ndipo sidzatha ngati mmene inathela DPP ai mukunama inuyo mbuzi za anthu mtambo ndiwa xl sangabwele izi akudziwa kt tikumulakwila chakwela

  • @EvanceSungani-cv9jk
    @EvanceSungani-cv9jk День тому +1

    Kenako munva namalomba ndi anzake kulibe chonsecho akufuna kuwina zopusa team ya DPP ndyozikonda ,,kuzinva umunthu inuyo. ? Ma guys akupanga ma demo akumenyeraso ufulu wainu komaso ana anu ndizizukulu zanu what do you do kuonetsa kukhuzdwa monga nzika? Mulikaliki liki kutipemoha kut tikuvotelen koma nkhonda smukumenya nao? Kupusa

  • @KalooMotheliwa
    @KalooMotheliwa 15 годин тому

    Koma iwe bwanji sumafuna kukhutisidwa kuti anthu enaso ambiri ambiri akupheledwa ufulu akudziwa

  • @CassimMeleka
    @CassimMeleka День тому +1

    Malawi watonse mcp ikufuna kubwelesa msankho paziko lamalawi

  • @raphaelmuliya6362
    @raphaelmuliya6362 День тому +6

    ❤❤ Your indeed true son of nyasa

  • @HumpChisanga
    @HumpChisanga День тому

    Komatu a Malawi anzanga ndale zili apo koma Mayina atsogoleri athuwa Mukuwawona bwanji their names Means alot guys Just think about these names Dalitso Kabambe,Saulos Chilima & OUR CURRENT president Name Lazarus Chakwera & Check the meaning only the Surnames again u will notice something great.

  • @alfredyesaya9419
    @alfredyesaya9419 Годину тому

    Ndi ma vendor amenewo, simukuti munthu azichita odi

  • @PetroHerman-z5g
    @PetroHerman-z5g День тому +1

    Tikuthokozeni nonse a zipani zotsutsa atsogoleli amene munatengapo gawo pa mademo a pa 25/11/2024 kumeneko ndiye kugwilizana

  • @collinschipala611
    @collinschipala611 День тому +1

    Tachosan Ako timkufuna timuone ifeyo kabambeyo

  • @thatgirrroskrr3570
    @thatgirrroskrr3570 16 годин тому

    Ambuye mukatheni chakwela. Anthu anu ife tipeze mtendele

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete День тому

    Kabambe ndiye tamuona where is Peter munthalika inock chihana atupele 😢😢

    • @ElizaSalunda
      @ElizaSalunda День тому

      😢😢😢
      Mapresdent enawa mantha ngati makwangwara

  • @EnelessBanda-x5n
    @EnelessBanda-x5n День тому

    Akabambe mul ndichipan inu, munakhalapo mp inu aaaa ol galu atadikula sitingavotere inu

  • @IbrahimIsmael-h2w
    @IbrahimIsmael-h2w День тому

    Anabadwira Kuyudeya akufuna Kuti anthu asamachite mademo koma amàlawi sitilola zambwererazo

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt День тому

    Kabbe is good president wabwino foodom imeneyo abwerese mabausa awoso chakwera akufuna nkhondo siliyas

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h День тому +1

    Mwana ndi DPP

  • @NaomiKalulu
    @NaomiKalulu День тому

    Sitikuopa zikwanje ife 2025 tikusintha zinthu.

  • @Arafuledi
    @Arafuledi День тому +1

    Kood zose zikuchitikazi malawi defoc for Ali kt asilikali opusa asaziwa chito axawa amalanda boma ngati likupanga xopusa

  • @cynthiataulo5211
    @cynthiataulo5211 День тому

    Spirit ya SKC yalowa umu.

  • @Johnybegood260
    @Johnybegood260 День тому

    Nice move kabambe

  • @MikeChimpeni
    @MikeChimpeni День тому

    Kabambe oyeee!

  • @andreakalambula7723
    @andreakalambula7723 День тому

    wawa mr kabambe

  • @khumbotembo302
    @khumbotembo302 День тому +1

    Akupita asiyeni