Nkhomi is the black mamba in English. Only that some of the stories were just exaggerated but the fact is that it can stand on half of it's body. Komanso it's so fast and deadly.....
komano panjoka ya nsongoyo tabwerani ku phalombe lake chirwa marsh udzapange ma research akowo tione ngati ungabwelere kwanu wamoyo especially in nkholonje hill. ifensotu taziona, those njokazo are still in there, it can not fly though, but it travels at a very high speed in trees or grasses and when you are cornered up you can not escape.and when it bites you cant run more than 100m away before you die, ndi njoka ija yoti imakusaka yokha other than izi zomathawa zikaona anthuzi
Morton i love your channel❤
Koma Pena Morton umapulumusa anthu woti amafuna kuzimangilira😂😂😂
😂😂😂😂that made us the way we're today
Nde kuli ya ayao at amamusilika nkazi 😂😂 kukakamilana at kukanika kuchoka 😅😅😅 koma ungamvetu kukoma
😂😂😂😂yoseka olumalayo nde tinkaopadi
Aah kuneno sunapiteko iwee zimenezo ziliko zinjoka zoopya chonchozo
Ya nguluka siunaikambe tu😂😂, komaso ya mphenzi yo iweyo ukunama. Ubwere ku ntcheu ku tsangano, amatumiza time ya dzuwa.
Nkhani ya ku karonga, yochosana mafupayo ndayimva 2023 yomweyi 😂😂😂😂 ndipo ndinakhulupilira coz munthu amandiuzayo eeeeeee ndiwachabe. Anthu ku karongako mpaka amalephera kumufunsa ngongole amamuwopa. Ndi munthu wakuchifumu kumeneko ndithu 😂😂😂😂😂😂😂
Sapitwa yokhayo usaphwekese ohoooo
Ndimafuna audio ya bwana kapolo anamubifa chilembwe ija
Akuti osadyera mpeni ungadwale chibayo😅
@@osygmultimedia9854 hahaha za ziiiiii
Am in neno now. Komwe kumapezeka mphenziko is just few kilometers away, usaphwekese.
😂😂😂 kale
Akuti amakoma koopsa 😂😂😂😂
ameneyu ndi galu kwabasi🤣🤣🤣🤣
Koma ase kumeneko ndye kuli security kathithi paliponse ma CCTV?
Real old lies...ndazikonda...kkkkk I was looking to see manyi anjovu kuti ndidzaone maungu akupsa...
😂😂😂😂😂😂pano nsima inasiya kupezeka mu phiri la mulanje, devaluation yanyanya😂😂😂😂
😂
Nkhomi is the black mamba in English. Only that some of the stories were just exaggerated but the fact is that it can stand on half of it's body. Komanso it's so fast and deadly.....
@@fumukumwenda9824 black mamba can't do that. That's the cobra.
😅😅😅 eeeh
Chi nde chimbutuma ndithu
Kkkk
komano panjoka ya nsongoyo tabwerani ku phalombe lake chirwa marsh udzapange ma research akowo tione ngati ungabwelere kwanu wamoyo especially in nkholonje hill. ifensotu taziona, those njokazo are still in there, it can not fly though, but it travels at a very high speed in trees or grasses and when you are cornered up you can not escape.and when it bites you cant run more than 100m away before you die, ndi njoka ija yoti imakusaka yokha other than izi zomathawa zikaona anthuzi
@@fabianomussa vuto ndiloti muli captured ndi ma myths. Mwaziona kuti picture ili kuti? Inaphako ndani? Zitayeni izi achimwene muli ndi phone pano
😂😂😂
Kkkkkkkkk