Azungu Abwerenso - Dziko Talikanika

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 3 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 111

  • @geckojt3918
    @geckojt3918 7 днів тому +4

    I agree with u on this issue, Bro

    • @munikabambe7625
      @munikabambe7625 4 дні тому

      Ngati ophunzilawo anathawa nkumachemelela kwa eni.. 😂😂.. Tili
      PA moto

  • @AbdulYusuf-j3t
    @AbdulYusuf-j3t 8 днів тому +1

    Yes for sure kulibwino azungu abwele ndithu alamulile

  • @holtzalexander8967
    @holtzalexander8967 8 днів тому +1

    Lero ndavetsetsa kukula kwaphunoko mulinso ubongo 😂 ndiwe dolo katatu🔥🔥

  • @christophershankmunthali7567
    @christophershankmunthali7567 8 днів тому +2

    Good example pa thyolo pompa ku estate ya tea, people are very serious kumakampani ya azungu ndipo zinthu zikuyenda mu line😂

  • @dalisoulphiri3094
    @dalisoulphiri3094 7 днів тому +2

    Ati yankhulani ngati mmalawi 😂😂😂😂😂 komatu apa ineyo ndavotela nfundo zomwe ukuyankhulazi ase, chabe kuti munthu atenge ndi kugwiritsa ntchito nfundo izizi ndiye mmalawi eeeee nzovuta man

  • @shattamoxy2393
    @shattamoxy2393 7 днів тому

    That's True Bro,,,We need to call back Angelezi ...Anthu Okudafe Zatilaka Ndithu.

  • @UdabwaAxse
    @UdabwaAxse День тому

    Amene ujadi ndi kapolo

  • @hamissimdoka9665
    @hamissimdoka9665 День тому

    I a gree with u 100% brother man zoona zimenezo, ma resources Ali pweee but let's go and see development nothing. Only stupid of leadership

  • @graciouskamwendo1873
    @graciouskamwendo1873 7 днів тому +1

    Tikufunikadi azungu abwereso

  • @KossimasiMaluwa
    @KossimasiMaluwa 8 днів тому

    Achimwene bingu Dziko lija analitenga bwino koma muchita kumupha kod iweyo kukolegi unapitakuja umakataniko tulusa lusolako tiwone osamangolongolora

  • @alicemalika677
    @alicemalika677 День тому

    Choka iwe azungu achiyami

  • @chisomokuipa7069
    @chisomokuipa7069 8 днів тому +1

    Azungu dziko ili analibe nalo ntchito amkangolitenga ngati kumunda kwawo

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 6 днів тому +1

    I agree. Azungu abwerenso.

  • @patricktaibu4874
    @patricktaibu4874 8 днів тому +1

    John Chilembwe sanapange phuma azungu amapanga sankho, John Chilembwe anamwalira 1915 azungu omweo ndi amene amalamulira ziko mpaka Kamuzu anatenga ziko bwanji nthawi yonsei samapanga chitukuko?osanamizira Chilembwe azungu ndi asankho.

  • @MasausoHopuson
    @MasausoHopuson 7 днів тому +1

    Umayakhula chilungamo aise

  • @chigomezuchigumbuliluwenac624
    @chigomezuchigumbuliluwenac624 7 днів тому +1

    Anthu omwe akuwononga dziko ili ndi azungu omwewo, Dont ever make a mistake kuti nzungu nde akhoza kutitukula, ndi ameneyo amapngisa kuti zizitivutika.
    The pin us down mwachibisila, kuti pasa ngongole zoti zimatilephela kubwenza coz of unrealistic debt interest.
    Nzungu amatipangisa devide and rule, kutipangisa kuti tiziziona ngat ndife olephela. Iyayi vuto ndi nzungu yomweyo

    • @rangersonngirazi6741
      @rangersonngirazi6741 6 днів тому

      Amapanga zimenezo coz tikuzilamilira tokha. Koma kubwera iwowo kumapanga they will boost the economy

    • @chigomezuchigumbuliluwenac624
      @chigomezuchigumbuliluwenac624 6 днів тому +1

      @ they cant. Azungu amathandiza pomwe iwowo akupezapo phindu 100 times phindu lanu. Its all systemic, if African shud be autonomous economically, for example tizigulisa miyala yantengo wapatali mitengo yomwe tufuna azungu sangasangalale amafuna azigula motchipa kenako azizatigulisaso ifeo modula. Africa is systematically left the way it is so that izipeleke raw resources with no value added at a cheap price so that azizipeza motchipa. Mavutowa siatokha ngochita kupasidwa. Musapusisike kuti ndife olephela patokha.

  • @JamesYusufu-m4r
    @JamesYusufu-m4r 7 днів тому +1

    akuti amalawi tinafela chizungu cha achakwela. za ziiiii. usagoleli alibe

  • @Chilekafarai
    @Chilekafarai 7 днів тому +1

    koma wanena ngamo olo akwiye

  • @paulnkhata9421
    @paulnkhata9421 7 днів тому

    Izi nzoona

  • @hydra_mw
    @hydra_mw 8 днів тому +1

    You have a great point kma😂😂 I don't think the white men, especially Americans can refuse

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 6 днів тому

    Kkkkk vuto ndiloti azungu sanatisiye akumenya nkhondo yakabisalila

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 7 днів тому

    Inu wonama vuto ndi katangale wosati zomwe mukubwebwetazo munthu ngati chidina😂😂😂😂

  • @takondwajamesdickson7917
    @takondwajamesdickson7917 4 дні тому

    Inensotu kapolo ndinagwirizana naye mtangomvera muja

  • @JamesYusufu-m4r
    @JamesYusufu-m4r 7 днів тому

    ndichocho. apa nanje tikulamulidwa.ndigule wakulu. kungokhala chamba

  • @Shepherd342
    @Shepherd342 8 днів тому

    I agree with you km tigoligulis for good bx aliyes atenga gawo lake

  • @ackimChiumia
    @ackimChiumia 8 днів тому +1

    Koma Morton watokota za nzeru chiyambireni,

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 8 днів тому +1

    Chakwera chinyini chamake

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l 7 днів тому

    Ineso ndugwilizananazo,dzakudadzi manyi too much.umbanva,kunyengana,komaso kupanda nzeru

  • @DamianoYohane
    @DamianoYohane 8 днів тому

    Ndakhala ndikumanena izi for long time

  • @AliNtolera
    @AliNtolera 7 днів тому

    Mulekeni fisi uyu sabeleka umuna wadzadza ku ubongo akapungule

  • @MorganBanda-oc2jx
    @MorganBanda-oc2jx 6 днів тому

    Kurephera zoona anthu akuda talepheradi kulmulirana tokha tokha koma chokhacho choyitana makosana mukuwanenawo ndthu or kumtundu kwanu amorton sangagwirizane nazo and kumeneko nde kuduka mutuko.

  • @stephenkbanda598
    @stephenkbanda598 7 днів тому

    Pena pake ndizoona ku Zambia atangotenga Boma vice president mzungu uja Ndalama yawo yinasintha mpaka kukhalanso ndi mphamvu kumalimbana ndi Dollar 💵.

  • @jeremiahmemmanuel9988
    @jeremiahmemmanuel9988 7 днів тому

    Yes chilembwe anatilakwira kwambili

  • @ChimzyWesley
    @ChimzyWesley 7 днів тому

    This is facts munthu wamkulu

  • @HELWIDZY
    @HELWIDZY 7 днів тому

    People don't know kut chimanga tikulimachi its because of azungu ndipo chipanda azungu bwezi tili ma bush men

  • @Bigboydre600
    @Bigboydre600 8 днів тому +2

    Izizi ndizowona ngat utayike hate comment yangayi naweso pathako Pako we have all failed 😑

  • @PixyPililaniNyonizendah
    @PixyPililaniNyonizendah 8 днів тому

    Mwadumba unenesko tuu akulo

  • @ShafiAli-my2fi
    @ShafiAli-my2fi 8 днів тому +1

    Ufulu uposa zonse

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 8 днів тому

    Palibe,mzungu amene atabwele kulamulila ameneyo ndiye ndingamudule mutu.ifeyo,tithane,ndi chindele chilipochi Tanzania ikuchita bwino amene atisogolelawa,alibe zelu.azungu,kuba ndiye president amaba ku zera mwa zungu.africa,si ziko la azungu apo mwanama.olo,baibulo likuti kwao kwa azungu kuthandaudza,kuti,pali malile.

    • @JOHNNKHATA-dn3gw
      @JOHNNKHATA-dn3gw 8 днів тому

      Inu mwamwetsa inu 😂

    • @FranciscoTisungebanda
      @FranciscoTisungebanda 7 днів тому

      Moti Tanzania mufananize ndimalawi? Tanzania ndidziko lalikulu malawi athakulowamo time's times , Tanzania ili ndi doko, migodi ndi mbwelekete ili mu top ten yamayiko omwe kuli migodi yochuluka pomwe malawi imadalila ulimi okha, and alimi nawo mmafuna muziwagula zinthu motchipa zomwe zakhala zikuwagwesa ulesi

    • @HarrisonMwanga-xy4sc
      @HarrisonMwanga-xy4sc 7 днів тому

      @FranciscoTisungebanda man malawi tili nazo koma chifukwa cha azitsogoleli okubawa, malawi ndi yolemela koopya, capital hill ijayo pasi paja ndi maini, ntcheu yoseyi ndi maini,koma kuba,tikunena pano,ndi manena za malile a Tanzania ndi Mozambique anthu akufa chifukwa cha zigawenga zobvala mask ngati zikunyamula zikwanje zija,ndi chifukwa ndikuti kwathu kuno tisabvomeledze,chitidwe umenewo,uchitike chifukwa cha azitsogoleli opanda chilungamo ngati tili nawo panowa

  • @KondwanNtotela
    @KondwanNtotela 7 днів тому

    Palibepo Cha zeru

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 6 днів тому

    Mumufunse Denis mahata akuwuzani

  • @Ziz_Wani
    @Ziz_Wani 8 днів тому

    after kutsegula maso kukacha, choyamba kuganiza chimakhala chigololo😂

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 7 днів тому

    Anaferiya anafeliya.

  • @jesuit579
    @jesuit579 7 днів тому

    a Morton nanunxo ndiye ayi2.... who's is behind Africa's poverty..mmexa ndi Nzunhu yemweyo

    • @mwai19
      @mwai19 7 днів тому

      Iyayi, poverty yaku Africa ndi tokha chifukwa chakaganizidwe kathu. Vuto la anthu okuda ndi limenelo, we always try to find someone to blame for our poverty or stupidity.

  • @DavieMisomali
    @DavieMisomali 8 днів тому

    Ferteliza atipangile Boma Ku south àñth7 amalima amalima zika ngati zika amazimangila madenn

  • @RobertJohn-nj2re
    @RobertJohn-nj2re 8 днів тому +1

    Palibe kukwiya apa zativuta akudafe

  • @dysongosten-sg9rh
    @dysongosten-sg9rh 8 днів тому

    Morton ndi dolo heavy zafika poti boma likumatichinda daily

  • @slesterchabwera3508
    @slesterchabwera3508 7 днів тому

    Ma pan Africanist mbodzole zenizeni

  • @kondwaninamathanganelson2794
    @kondwaninamathanganelson2794 6 днів тому

    thats true, ndakhalandikunena zimenezi

  • @governormoses4037
    @governormoses4037 7 днів тому

    Ukunena zoona

  • @leveltrapper4322
    @leveltrapper4322 7 днів тому

    Ndpo zativutadiii mmmm

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 6 днів тому

    Uwone mumene anamuphela bingu ndi mangufuli

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 9 годин тому

    Ndipo live

  • @michaelkachiwalajr6381
    @michaelkachiwalajr6381 7 днів тому +1

    Apa ndakutuluka ndivideo iyiyi wandilankhulalira mwaumbuli

    • @AllHandsOnEveryThing
      @AllHandsOnEveryThing 7 днів тому

      😂😂😂😂Ndidolo wa mbuli uyu. zoti africa amaipanga criple everytime we try to rise azungu omwewo through world bank sangaganize😂😂 azunguwo akumusekelera chakwera zomwe skupanga

  • @Benty_Pro
    @Benty_Pro 8 днів тому

    izizi zandikomela

  • @LucksonMaduna-t6y
    @LucksonMaduna-t6y 8 днів тому

    Agree with you.

  • @MackThom-y9e
    @MackThom-y9e 8 днів тому

    Akanabwelad nde zkanatipagila bwino esh

  • @NgeyasjuWadeya
    @NgeyasjuWadeya 8 днів тому

    Sitinapange phuma vuto ndiamene amatilamulira dyera ndi kudzikonda

    • @apatsaphanga9252
      @apatsaphanga9252 8 днів тому

      zeru zomwe akunena baghayazo osati dyera kumalawi udyako chani

    • @NgeyasjuWadeya
      @NgeyasjuWadeya 8 днів тому

      @apatsaphanga9252 zoziyenereza zilipo koma vuto ndiutsogoleri Bingu anali mzungu????

    • @FranciscoTisungebanda
      @FranciscoTisungebanda 7 днів тому

      ​@@NgeyasjuWadeya Bingu anasiya chani chanzeru? mesa ndiamodzi analiononga dzikoli?

  • @AbdulAzeezChapita
    @AbdulAzeezChapita 7 днів тому

    Come with solutions ma history sangasinthe zinthu zinachitika zinantha

  • @Indianaderick
    @Indianaderick 8 днів тому

    I agree with you broh

  • @MrMagombo
    @MrMagombo 7 днів тому

    Achimwene how can you call munthu okuti amatitenga zitsilu kubwela kumagwira nafe tchito?
    We are sabotaged. Mwadzionera pasi.

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 8 днів тому

    Iwe nawe walandi ndalama

  • @hamissimdoka9665
    @hamissimdoka9665 День тому

    For example south Africa, it was admired country go and see today only high hackers thy urine any where, killings robber's shaa ,is dangerous to be in south Africa than to be in the national park, where there's lions and other dangerous animals

  • @handsomenkonde2552
    @handsomenkonde2552 8 днів тому

    Kkkkk ndipo Talephela
    Kungokhala ndi Ufulu koma Zopoila zen zen

  • @emmaculatemenzeiwa
    @emmaculatemenzeiwa 8 днів тому

    Thats very true

  • @GonaMkuphe
    @GonaMkuphe 8 днів тому

    Pamtumbo pako ndi azungu omwewo

  • @moxanderYe-zv9zs
    @moxanderYe-zv9zs 8 днів тому

    Morton,, military. Rule ikufunika,,, asilikali atenge boma

  • @SteynMaduka
    @SteynMaduka 8 днів тому

    Iwenso nde kunamapo apa

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 8 днів тому

    Mzungu ndi chisilu

  • @stevenoah4578
    @stevenoah4578 7 днів тому

    Wakwithu syndrome 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @kamozankhoswe6492
    @kamozankhoswe6492 8 днів тому

    Bro last time you said we need a ruthless leader mesa. mwasinthaso? 😅😅

  • @Bernprosper
    @Bernprosper 8 днів тому +1

    Ndili pano kuzapanga translate chichewa comments 😂

  • @MIKEMWALE-y8s
    @MIKEMWALE-y8s 7 днів тому

    Can you please explain....kulikanika and how Zimbabwe and south Africa were developed by white people....

  • @governormoses4037
    @governormoses4037 7 днів тому

    Tiyeni tiwa itane osati nthata zanjarazi tiyeni tiyesekoso rusher ngati American yavuta

  • @ZamuZamu-ud5ro
    @ZamuZamu-ud5ro 7 днів тому

    Motoni mzeru zako ndizopelewela , suziwa chomwe ukufuna komaso ukuti dziko lomwe kuli munthu wakuda palibe chikuenda ndiye monga inuyo ma graduate mungakanike kuona chomwe chikuchitika samu yophweka kuisova mukufuna muonese ngati zovuta bwanji? Inuyo simukuona kuti sikulephela kwa munthu wa kuda koma system yomwe tinapasidwa komaso inuyo mukamakhala ndikuphuzila kwanuko mumati Africa kuli dziko lomwe linalandila ufulu? Mhhh koma anthu ophuzila enanu not nonse koma ka 70% ndinu anthu osazindikila koma chifukwa chamapepala anu mumazipusisa kuti ndinu madolo koma muli ogona ophuzila osegukaso maso alipo koma ndiochepa 30%. Mwachisazi inuyo mumaziwa kuti azungu anamupha John Chilembwe inuso mukuti John anapanga changu kuthamangisa azungu , koma azungu ake ati poti azunguwo ndi John Chilembwe anayamba kuchoka padziko pano ndi John ndiye ndimadabwa inu anthu ophuzilanu bwanji mumasakha kuona zinthu mozondoka. Adah inuyo mudakali mu dark koma muzimva kuti gemu mumaionela patali koma ndinu abodza komaso munthu osabwelesa chitukuko dziko mwake.

    • @peterthawi
      @peterthawi 7 днів тому

      iwe kuluta ku china uko...uli kutchimbila vichi kuno😂😂😂😂😂

    • @mutafire
      @mutafire  6 днів тому

      Ifeyo tinali ngati inu kale...palibe book la neocolonialism ndi negritude literature limene sitinawerenge...ndipo funsa lanulo apo akuchita bwino Ku Asia akuyuza system yanji? Inuyo mabvuto onse ansala yake ndi mzungu...mwayiwala kuyang'ana munyumba. Ndi nyau izi you think mumgapange vaccine? Mapepala nde tili nawo...komanso reality 100%

  • @RuqmanSulymana
    @RuqmanSulymana 8 днів тому

    Zikunveka bwino,koma i dont agree,bola zitikanike tokha

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf 6 днів тому

    Muunikirenso zimene anthu a ku middle east akukomana nazo, chimene chija ndichikondi? Ndiye ife onenedwa anyanife bwanji?

  • @BensonBanda-f6e
    @BensonBanda-f6e 8 днів тому

    Kupusa

  • @MIKEMWALE-y8s
    @MIKEMWALE-y8s 7 днів тому

    Kuteleku mumati mukamakhala john chilebwe anakutulusani mu ukapolo you don't know white people. Its sad that this day and age kumumva munthu wachikuda kukhala ndimalingililo otele.

  • @sungananigondwe2807
    @sungananigondwe2807 7 днів тому

    Maganizo ako nane ndimaganizo zomwezo akwiye akwiye ngamo imawawa

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153 8 днів тому +3

    U dont know who support our poverty,u are ignorant on that one bro

    • @MVP-muzic
      @MVP-muzic 8 днів тому +1

      He is saying the truth. Who is funding our poverty???? Let's look at the countries that azungu akulqmulila, you can't compare with Malawi, the problem we have as blacks, we need to inreach ourselves and our families

    • @mwai19
      @mwai19 7 днів тому

      Vuto la munthu okuda ndi limeneli, we always look for someone to blame for our poverty or lack of seriousness in everything we do. If ena ake supports our poverty ndekuti amapanga support anaona ma loopholes that's why they utilized it. Tili ndi vuto tiyeni tivomeleze

    • @dada5934
      @dada5934 2 дні тому

      Morton you need to wise up and do your research. You are not allowed to change your curriculum, you're not allowed to mine without the prove of nzungu. The colonial system still stands tall than anything. Look how many assassination attempts Traore of Burkina Faso has survived.
      Any black leader serving his country gets a life threat or get assassinated. Iweo you need to wise up, pachakwera pokhapo nde wakhoza machende ake.
      Iweyo for praising azungu Panyapako adha

  • @Dee-h7c
    @Dee-h7c 8 днів тому

    Your Right✅️ bru

  • @victormsalawatha8415
    @victormsalawatha8415 7 днів тому

    Post iyiyi osaiyang'ana ndi mkwiyo muli zilungamo za phweee

  • @JOHNNKHATA-dn3gw
    @JOHNNKHATA-dn3gw 8 днів тому +1

    Wat the hell

  • @RichmondKondowe
    @RichmondKondowe 7 днів тому

    Haitians are beasts 😂

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf 6 днів тому

    Sindigwirizana ndi maganizo amenewo chifukwa mavuto onsewa ndi azungu omwewo. Onani zomwe akumuchitira Ibrahim Traore. Zikuonetseratu kuti amakondwera ndi akuda opondereza akuda anzao mpaka kumawapatsa mendulo za ulemu, eni wake mkumadabwa kuti akuyamikira zichani. Magufuli ndi Bingu anali oyipa Kodi?