My opinion is strategy ya mcp is to make southern region parties to fight so that mavote azakhale ogawanikana to weaken Dpp votes.. A usi atumidwa ndi mcp to devide utm... Just imagine mpungwempungwe uli kumwera kokhatu not central region.. Anthu asamale
Anyamata atokota sakufuna kusewera phada wa miyendo iwiri🤣🤣
Musayembekele kuti achitetezo akhonza kuteteza anthu, Iwo amateteza aboma chifukwa ndikumene amapeza ya ufa
Mudzilankhula zonse chifukwa a mcp including a Kunkuyu ndamene amatuma anyamata a kwa msundwe, ndipo a Kunkuyu simunati mudzawona zenizeni
Why chakwera is ignoring Malawians koma inu 😢 ,anakuika pa mpando ndi ndani? God intervene please ,
Achakwera akuopa
Munalekeranji kumanga a ku Lilongwe munamanga anthu aku nsanje nchisankho chimenechi chikubwera bwanji
Komano asala awiri Namanjekethe ndi chikangawa nawo tiwagende
Tikhala bata asogoleli oganiza modothawa atachoka
My opinion is strategy ya mcp is to make southern region parties to fight so that mavote azakhale ogawanikana to weaken Dpp votes.. A usi atumidwa ndi mcp to devide utm... Just imagine mpungwempungwe uli kumwera kokhatu not central region.. Anthu asamale
Welcome guyz
Pepani tiyikeko mulomo nthawi yimene Boma amati likuramuraro ndiye nthawi yowonetsa chikonde ndi wanthu kuwaudza za ziwawa chonde mu Boma loramura ine ziwawa ayi tonse ndi amalawi palibe kumenyana ayi koma amayambatu ndi bwanawo kutulusa ndarama ya zikwanji akuti chitetedzo chikure eeeesh basi anthu adadzolowerano pano kuli konse zikwanji olo minyara ndiye mtima ziiiiii anyamata akugwira ntchito akuti ok
Ataliwo nd ausilu tizagenda
😂nanuso a times you open your mouth chifukwa CHOTI agendedwa nda Kunkuyu koma dzanja munali chete