I have never seen a robot president like this one. This country is under His excellency Richard Chimwendo Banda. The real president is in deep sleep 😴😴
Wawa history is best teacher davite adapha goliati ndi chida chaching ono A uopossition chida chogonjesela Satan's ndi penphero chofunika ndikupanphela pamene tikupita ku zisankho basi
Koma gayz chakwera zimene akuyambisazi ziko lino apanisa kuti anthu amayiko Ina Ngati ife tipange oganazi tibwerese ankhondo Kaya wamva iwe chikangawa zimene ukupanga iwe ok
Ufulu tinagulitsa Ku MCP mavuto Awa tinawayamba tokha 😂😂😂 Palibe olimba mtima Ngati Chilima he was demonstrating against his own president while him was a vice president enawa zamavuto anthu alive nawo ntchito 😢😢😢
Apa aku opposition asamale chifukwa ngakhale nthawi yolengeza za ma vote akabera ali mubowa pazavuta kuti alande Bomali mmanja mwa mcp. Maloya a ku opposition sakuwoneka lero akufuna adzabwere zitawonongeka ? Iiiii kma Malawi wathu wokoma akupita kuti?
I have never seen a robot president like this one. This country is under His excellency Richard Chimwendo Banda. The real president is in deep sleep 😴😴
Wawa history is best teacher davite adapha goliati ndi chida chaching ono
A uopossition chida chogonjesela Satan's ndi penphero chofunika ndikupanphela pamene tikupita ku zisankho basi
Tinkangokuva kuti mcp idali yankhaza, apa tatsimikizadi ndizoona, ithink its enough know chipanichi 2025 chikuzathera pompo basi
Even me ndimkangomva kuti MCP ndiyouma mtima ngt mwala
Apapa bansi .MCP kummwera Asazapangiseso Sonkhano... Aliyese akhare ndi home Ground yake ..Ziwawa sizizata ayi
Ndipo asadzayerekeze kubwera ku mpoto adzachimina.
A Malawi ufulu tinaugulitsa ku m c p komano tikuziwa kuti mcp ndi chipani cha nkhaza
Biyeni anatipitisa kwa pilato
Anatipititsa ku ng'ona ku nyawu
Apa democracy kulibe we are still in one party system
komatu zikuchitikazi timenyanatu tokhatokha sopano yamanja guys mcp munguliputalitu ndi soka inuyo musaone ngati muli pa mwamba
Anthu amailawa kma chikumbumtima Chokha mudzikhala nacho popeza sikaletu lija nanu munkachita zionetsero 😢
Kod tikati mademo ndi chani? Malawi sitikudziwa nthandauzo la ma demo
Ndadulano malire MCP kumwela kuno isazapangiseso msokhano
Osati msonkhano okha ngakhale zina zili zonse zopanga MCP zosadzachitike kumwera. Obwerera makani adzapite mtembo popita kwawo.
Izi ndi zimene Timothy Ntambo anafuna kuti a Malawi akumane nazo.
Ndipo Mutharika asadzakhululukire mtambo ndi anzake
Kd a DPP alibe ma bawusa?
Aaaaa awawa akufunika kuwawonetsaso Kaya , ma bawusa a DPP tatulukirani
Go to Thyolo and make demos there, , this is LLs kuchimake Kwa MCP
Wa mcp asadzapangitseso msonkhano kulikose kumanthamangitsa osanyengerela
Mesa munkafuna mcp ndi zimenezo Malawi back to 1 pate
KOMA KU MALAWIKO ARMY ILIPO KAPENA YIDATHA?
idatha
Why are they violating our rights vto demonstrate eish koma abale. God is watching this
Amphakawa aturuke atikwana namiwa motoooooooo
azipani otsutsa nawonso azipezeka asamangodikira mabungwe ndife anthu wamba nthawi ikuwandikira tionana kutsogolo
Never giver up
Kodi osusa boma wose alikuti osawopa osatopa A malawi please
Koma mwati sinkhondo imeneyi
Kazikalimani alomwe ulesi basi,. tiyeni kumunda mukuchedwa ndi zopanda pake izi ndi za ziii mvula.yagwa. kalimeni
ANAMIWA NDI A MANTHA SERIOUS SANAONEKE NKOMWE
Akupusitsa zisiru Namiwa
Basi kumtima mbeee ndi zinenezi. We want peace we don't want problems
A police zoona mwapisila mmatumba kuwonerera zikwanje zoona?
Chakwera, Manganya, Kumkuyu Chimwendo,Zikhale Hmm Musaiware Kuti Mphamvu Zingachuluke Sungazifinye chithupya kunsana !!! Komaso chinauluka chinatera ndipo security murinayoyo muzakhara muribe, Muzandikumbukira Muri mmanja mwa wathu kusowa okutetezani sure 🤔🤔🤔
Avichita bwino vibwelele mma kwawo mademo mademo achaniso? Akufuna kumangopezelapo mwayi omaba katundu wa eni vithamangitseni
Akapangile ku Blantyre
Basitu pafikapa mademo tizingopangira kwathu komkuno ku blantyre kwaeniko zativuta basii mapeto ake tiphedwa ambiri zikalata tizikasiya kwa DC Blantyre kapena iyayi tingoligawaba dzikoli basiiii nane ndatopa ndichilungamo tsopano ndisamafinyike dziko lakwathu lomwe😭😭😭😭
Koma zomakachita odi kwa DC ndizongowapatsa matama kudzimva kumeneko. Adzingopanga mademowo
Osawarora kuchita mademo enawa ndakuba
Kodi malume anga solder chisare anali pat sindinawaone azibwera tizikhara nawo mwina mantha nkumathako""
Koma gayz chakwera zimene akuyambisazi ziko lino apanisa kuti anthu amayiko Ina Ngati ife tipange oganazi tibwerese ankhondo Kaya wamva iwe chikangawa zimene ukupanga iwe ok
Inu mumakonda kutimiza zinthu sothi ena atimiza kare musamatitele bundle 😅😅😅😅😅😅 iyaaa
Yes I'm here with u bro aaaaa amandipsetsa mtima bwanji
Mwatsara pang'ono kuchoka agalu inu mwatikwana
Ngati chilima anganve munzimu wake achitepo kanthu
Kodindekuti dzikolino asilikali aribe dzipopolo. Coz Chigawenga kachipha silingakhale vuto
Ambuyee imvani kulira Kwanthu musatiyang'anire, kumbali
Mmmmmm dziko silikuyenda bwino ambuye atichitire chifundo
Ufulu tinagulitsa Ku MCP mavuto Awa tinawayamba tokha 😂😂😂
Palibe olimba mtima Ngati Chilima he was demonstrating against his own president while him was a vice president enawa zamavuto anthu alive nawo ntchito 😢😢😢
Ma Demo mumangofuna kudzaba ku Lilongwe next let's go to Zomba why Lilongwe
A malawi anzanga, apapa boma ili pomatitumizira anthu azikwanjewa likutanthauza kuti ife tikulakwisa pomakonzekera peaceful demonstrations monga momwe linkanenera poyamba paja. Apapa nzofunika kuti tikamabweranso pamseu tisabwerenso ndi azimayi koma tibwere amuna tokhatokha nafe ndizikwanje zathu ready for heavy violence, ndipo pazakhale kuphana basi, ndipo izi ife tizipanga achonganso.
AMBUYE TICHITIRENI CHIFUNDO MALAWI ALI M'MANJA MWASATANA
Dzimenezo si zingasinthe kanthu
Mcp izipanga misokhano kulilongwe Koko kwinaku akabwela azigendedwa
Ngati akuwuza anyamata azikwanje ku mmwera asadzapangitse msonkhano ,azikunthidwa,nanga si akukana za mtendere ,zikusonyezeratu kuti bomali likupanga zonyasa
PANO AMALAŴI TIKULIRA MOTERE " SAULOS CHILIMA IWE. UNATIPELEKA IFE KWA MKANGO LAZARUS CHAKWERAYU..OGO !! IFE A MALAWI KUĹORA UKU
This contributes to poor leadership, koditu zikakhala kwa wina zimakhala zophweka,stupid government and leadership
Koma mpaka anthu kumatulutsa zikwanje apolice ali pompo dziko lathu layipadi tilibe chitetezo
Mufera za eni inu. Za ziiiiiiiiiiiiiii
Koma who are these people who wear mask
Iyiyi ndikuona kuti ndi nkhondo iyi
Dziko la malawi lafika pa uchisiru ndith
Inu a mcp kodi mumaziwona chani kodi? Dzikoli silanutu anyani Inu, kuyendetsa dziko simutha agalu Inu mukungoti zudza anyani inu
Namiwa alikuti apa kikikiikiki
Nyekhwe ijatu ndimeneyi yangoyamba
Umtola nkhaniyo zomwe amayankhulazo sizimanvekatu wa Ku luntha tv
Zimayamba nchocho, mapeto ake ndi nkhondo
ndipo kungoponya bom pamenepo mkuthana nao azikwanjewa boma lomvesa chisoni loganizitsa molakwika mulungu akuona koma?
Km malawi eee
Timakamati a Mcp mukavoterana ku dambwe tikulakwisa
Zitsilu za anthu a MCP ,achita kudya ndalama zingati amenewa? Akhaula chaka cha mawa palibe amene akawavotere amfiti amenewa eeeeeee
Zisawawe chifukwa zili kwaiwo amalawi mademo odekha
Like
Makolo anga anandilangiza kut mwana wanga usazavotele mcp ine kusamva
Boma loyendetsedwa ndi abusa ....ayi zikomo
MCP osayisekerera kubwera ku mwera
Mvuto chakwela wakupha akufuna kupha amalawi onse, apolice pano ndi mcp sakupanga zokomela amalawi, ndie mblo yako chakwela ndi apolice akowo,
Awine ma vote muchilungamo osati zobela ai
Mcp
Áyi. Zikomo. Ulemu. Wanu. Mcp
Zamasewera eti,
Mwaiona m c p
Koma kuli anthu osowa zochita kunja kuno, teere
Apa aku opposition asamale chifukwa ngakhale nthawi yolengeza za ma vote akabera ali mubowa pazavuta kuti alande Bomali mmanja mwa mcp. Maloya a ku opposition sakuwoneka lero akufuna adzabwere zitawonongeka ? Iiiii kma Malawi wathu wokoma akupita kuti?
Tulani pasi udindo
Pajatu apolisi aku Malawi ambili ndi a std 8
Mziko ili mmanja mwa agalu
jean claude van damm
Ambuye mubwera liti ??
Olo muletse ma demo simudzawinaso
Ndipo sipang'ono
ZIKOMO KWAMBIRI CHILIMA
Mcp musayende kumwera kapena kumpoto tikumenyani
Chakwera tizakunyathera
Zosayenda bwino
Osamakapangira ku thyolo bwanji aaaamutikwane
Boma ndilomweli sitikusintha
😢😢😢 dzko lija tnapasa Satana
Boma ndilomweri alomwe mubwerela kwanu
Mumanama Koko Ku Thyolo Kuno ayi fokoso,
Akupangani bwino, mukusowa zochita inu, munayamba ndinu ku Ndirande kugenda Kunkuyu. Akudulani makosi kumeneko, Lilongwe moto
Chani palibe
Vuto achinyamata ndinu amene munagulitsa ufulu ku mcp lero mwaziona
Hy
CHIBWANA ETI ? MADEMO ALEPHEREKERENJI ? ANTHU TATOPA NDIKUZUNZA ZIMENE APOĹSI NDI AZIKWSNJEWA AKUCHITA IFE ÞTOPA NAWO A CHAKWERA. NKHANZA ZAOZI ? IWO WO MUNTĤU MMODZI YEKHA ANGAZUNZE MALAWI YENSE .? AYI .MACITIZENS ASALOLE MADEMO AKHALEBE BASI
eeeh malawi salibwino
Agaru mesa inu mwathangitsa kunyuyu
Mcp yaponda anthu kangati kuno ku Lilongwe ndipo akumwera awagenda kangati? Mmmmmh kumazitsata musanalembe apa MCP ndiyankhazadi kusamva ife 😢
Amalawi tidzadziwa zochita next year awo AA supatali
Pilato pachiongolero,,,mulungu tithandizeni
Kodi. a Kabambe mukuyesa.ngati.dziko amatenga ndi ma Demo? 2019 anthu.amapanga.ma.Demo chifukwa anali ndimfundo zomveka zoti DPP ibabera mavoti ndipo anapezekadi olakwa ku court zomwe zinapangitsa.kuti tivotenso, amene akukutumaniyo akulakwa dikirani 2025 yafika kale tiyeni tikavote