Bakili Muluzi TV, the best of the best channels, dziko likudziwa dzinthu zobisika , pitilizani bwana ,makutu athu ali kwainu May you live long , only God must protect you from the present thugs ,crodiles , and tyrants who were once like humble creatures , now they have rebelled against Malawi citizens. God is still living.
For the next generation yet unborn , whenever you come across this comment, just know that we were once alive this day to witness this masterpiece. Bakili tv, salute 🎉❤
I have heard your analysis but let everyone know this " IF You SALE YOUR brother THE BUYER has no REASON TO Trust You. Let us wait for the other tragedies.
Manganya apapokha nde watiwonjeza komano asanyadire mwayi ili ndiziko pachichewa amati chawona nzako chapita mawa chili kwayiwe the best bakılı muluzi tv 🎉🎉🎉 watching from Mozambique never give up BG brother tili pano kukusatiran basi
Komaso iwe iwe zikhale ngoma pamodzi ndi chakwela wakoyo mukeretu kulimbana ndi atola nkhani chilima mwapha nde mukufunaso chani Kwa atola nkhani bvuto Yako iwe zikhale ngoma pamodzi ndi chakwela wakoyo umburi unakura zinthu mwazidziwila ku ukulu
Did you see Joe Biden akupambuka pa podium Dday ceremony? He is poo and Gill mkazi wache took him away chif ananyera pamb pa Macron wakufa France ataima pambuyo pake, tsono bibilo linayamba kununkha pambuyo pake, Joe Biden kubibs ndithu osati artificial intelligence zeni zeni pushing faeces three times, watch the Dday ceremony you will see him pooping. Koma za manyazi ku USA.
@@raytavares2256 kkkk komaso Biden nde eeeh akumupha nawo ma jokes on TikTok kkk ,nde kuno u can't potray jokes on politicians?? Even the British monarchy thy are making fun of Charles who is a king
The best TV in southern Africa I support you brother God bless you all the time
Iwe uzasiya mbili ❤ muziko latulino ukaza mwalila 😢
Timakukondan mn ❤❤
Always with you bakili muluzi TV ❤
I love Bakili muluzi tv ❤ watching from Israel kumunda
I can't believe am loving this channel so badly 😂
Mcp anthu oipa kwambiri amalawi takambilana kudzachotsa boma loipali
May God protect BAKILI MULUZI TV......
Please 🙏
Loud and clear ✔️✔️✔️✔️✔️
Keep opening our eyes
I like this one bakil muluz tv mumatiyimilil
Bakili Muluzi TV, the best of the best channels, dziko likudziwa dzinthu zobisika , pitilizani bwana ,makutu athu ali kwainu
May you live long , only God must protect you from the present thugs ,crodiles , and tyrants who were once like humble creatures , now they have rebelled against Malawi citizens. God is still living.
Thanks brother for your best work and please take care
nanga atanimaka akuchika mu boma coming 2025 we are not going to allow mcp to continue us a ruling party we are sick and tired
Bakili muluzi tv, munthu okonda ziko lake God bless you
Watching from state house Malawi 🇲🇼
I like ur video our, activists
Powerful voice brother man 💪💯
Thanks boss
We have been waiting for this
Analyse the Utm status
Be safe my brother wherever you are, we rely on you
May Allah taallah protect Bakili Muluzi TV and all freedom fighter
Aaaah sungapeze bakili muluzi tv
For the next generation yet unborn , whenever you come across this comment, just know that we were once alive this day to witness this masterpiece. Bakili tv, salute 🎉❤
I have heard your analysis but let everyone know this " IF You SALE YOUR brother THE BUYER has no REASON TO Trust You.
Let us wait for the other tragedies.
Inu ndi machine fada Angelo akukuyanganira ndikukufunhatira
Much appreciate elder ❤❤❤
Money of match bakili muluzi l❤
ine or dziko lose likonde chakwera koma ine ndekha never because i know that chakwera is evil president than kamuzu banda
Sure
The man of the fact I salute bro talking without a fear😝😝😝🤫🤫
We love you boss man.
Always with you bakili muluzi
Keep on bro salute❤❤❤❤
The best tv malawi yonse ❤
Keep it up my man Mulungu akusungeni bwino zigevenga zaboma zizakumangeni
Iwe ndi one assy 💪💪
History is best teacher 🎉
Dzikhali ndimbuli kwambili sangapedze Muthu pa theba olo Ku Malawi komweko
May God protect Bakili Muluzi TV ...MCP must fall
Manganya apapokha nde watiwonjeza komano asanyadire mwayi ili ndiziko pachichewa amati chawona nzako chapita mawa chili kwayiwe the best bakılı muluzi tv 🎉🎉🎉 watching from Mozambique never give up BG brother tili pano kukusatiran basi
Zoona bro msiyen mawa chili pa iwe
Sidiki Mia, chilima kenako manganya
Today am first to comment ku Malawi kuno tingokhala poti mkobadwira
I agreed 😢
ndipo zoona zake
True
Mmmm mumakwana phiri timva zambiri kuchoka kwa inu
Thanks brother for news
We still crying in Malawi 🇲🇼 😢
Following u from Zambia
Thanks boss 🙏🙏🙏🙏🙏
Best ever tv almighty protect u till we change this gavernment
Manganya nde anali muthira kuwiri etiii 😢😢😢😢😢😢
Kuzangot chakwera waluza ku mw khondo basi sazalora kuluza olo pang'ono mavuto alipo 😭😭😭😭
Mukunena zoona
Tizaphane kumene
Ineyo I support what you are saying. This man will not agree at all
Ameneyi tidzapha ndimanjà akadzangokana pano athu akumutsiyadala coz adakali ndimphavu
Ine ndatsimikiza kuti ufiti kulibe,mmene dziko lamalwi likuzuzikira ndi chakwela,opanda mfiti ina nkuthana naye?mmmmm mulungu tichitileni chifundo
salute salute Bakili Muluzi tv mumakwana ndithu
Koma iweyo mumatiiimilila kwambiri thanks for that Boss ❤❤❤❤
Kulakwa kwambiri 🙌
We are following everything and we gonna know the truth for every action ,awuzen azikhale ng'oma machende awo
Wlcm brother we appreciate you ❤
Bakili TV number one
Nanga nyimbo ya spots imamvekachoncho
Waooooh anthu oipa
Ine ndili mu Sabata ,
Chakwerayi andilkwitsa😢😢
Happy Sabbath bro
Happy Sabbath
Asamuphe born kalindo,anthu amagazi mmanja.lero amanganya amupachika chilima,lero taona amanganya akuyankhula mfundo zosamveka.nthira kuwiri .God is watching you Manganya
Manganya uja ndi mbola ine ndinaona kale, ndi wa mcp.
Komaso iwe iwe zikhale ngoma pamodzi ndi chakwela wakoyo mukeretu kulimbana ndi atola nkhani chilima mwapha nde mukufunaso chani Kwa atola nkhani bvuto Yako iwe zikhale ngoma pamodzi ndi chakwela wakoyo umburi unakura zinthu mwazidziwila ku ukulu
Popanda inuyo abakili muluzi tv koma please please muzikhala osamala athuwa asaku pangini chipongwe please please mumati ziwitsa nkhani zochuluka but please samalilani
God be with you mn
I like this guy
Katakwe,,,, best TV ❤
Chakwera ndiwe munthu oipa zed
Human rights violation Lord please protect Mr Kalua and Mr Kalindo
Their voice is from the People
Best TV waing'alula
LONG LIVE BAKILI MULUZI TV 🎉🎉🎉🎉
Be safe wherever you are
AND MANY MORE YRS BROTHER YOU AR THE BEST
Abraza inuyo umandisangalasa kwambili pakhani zako zimaveka kwambili I love you so much my brother
Evil people, Ambuye amawasoya mpaka kapu yawo yamagazi idzadze zenizeni... What a land of blood Malawi has become... Crying for my beloved country
Zikomo BM Tv morefire
BAKILI MULUZI UNG'ALULA KWABASI KEEP IT UP
history is the best teacher❤❤❤❤
Always bamkili tv is the best ❤❤❤❤
I don't understand what is happening in my country 🤔🤔🤔🇲🇼🇲🇼🇲🇼
God ahead u my brother
Big up Bakili muluzi TV 📺 ❤
Bakili Muluzi TV landila ulemu wako ❤❤❤
Best Tv in malawi 🇲🇼 koma tikuopa kulakhulako kwambiri coz mmmmm
Zikhale ng'oma anakulira kumudzi ndipo ndiwachimidzi very much, kmso ndibulutu wa theee! Ana anjoka mcp
Ndipo kwambr tu
Kmas mboli yake zikhale
God bless you brother
😂😂😂😂😂 malume ajatu sing'alura uku moti eeeee malume mumakwana God be with you
Komatu ku American anthu thy make fun of their Presidents koma palibe amamangidwa
Did you see Joe Biden akupambuka pa podium Dday ceremony? He is poo and Gill mkazi wache took him away chif ananyera pamb pa Macron wakufa France ataima pambuyo pake, tsono bibilo linayamba kununkha pambuyo pake, Joe Biden kubibs ndithu osati artificial intelligence zeni zeni pushing faeces three times, watch the Dday ceremony you will see him pooping. Koma za manyazi ku USA.
@@raytavares2256 kkkk komaso Biden nde eeeh akumupha nawo ma jokes on TikTok kkk ,nde kuno u can't potray jokes on politicians?? Even the British monarchy thy are making fun of Charles who is a king
We are behind you brother
Peter muthalika anatukwanidwa😢😢izizi a Malawi ndizofuna wonena ndy akanena
😢 mulungu Inu akuendelen but what God is my favorite and goodness for all
My best Tv👍
Mcp ndiyoyipa kwambili
He is forgetting that malawi is a democracy country 🎉 I believe in you sir you always say History is a best teacher.
Never give up bro ❤
We love your channel bro
Koma kungoesa kukugwilani inuyo bwana tikagenda serious palibe kusekaso apapa angoesela,🤨🤨🤨
God protect Kamlepo kalua ndi Kalindo .
Big ulemu wanu my Allah continue to protect u
What's the way forward? Things are getting out of hand
God bless you
Times tv yati xiiiiii kuopa unyolo
yaboma imene ija
Good articulation
Best tv ever
Eish zoopsa kwabasi 😭😭😭😭May your soul Rest in peace Mr Saulos Chilima
God bless u ❤