Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Omwe timafila sangie bwelani tikhale malo amodzi
akt ine millitary sindingapepese
Ndipo ndichi vibe
Koma Hyphen can act with confidence and serious 😂😂😂😂😂😂😂😂 I love it
The part I liked
Sangie is good at acting
True
I always say the same nane. She's great
She's Dope Indeed
I was about to type the same.
very exceptionalindered
Friends of Ganizani let's gather hear ❤
❤
Neighbour wa mtebe nd doloso hvy🔥🔥💯
Ndipo zowona
It's Emmie and her Ben 10 for me 😂😂😂 crew yonse ndinu madolo ❤
Izi akupanga Sangie ndi Ganizani kudana ndi m’bale wa Piksy zinandichitikirapo ndikukhala ndi mkozi yanga, a very bad experience I don’t wish anyone to go through 😢😢😢
Gani ndi sister wake tsiku lina adzaphulitsa bomba mnyumba mwa ngozomu
Koma sangie ndi obheba💞
EEEE MAMA G ALEROYU
Uyu anabwera
Ndipo kwambiri,being black and beautiful❤
Tonde, neba wa abusa; voice yake really fits for that one batchala in most yards.
Amatha
On point nice observation kkkk
@@NelsonMumbulu-mq5ob m'bale wanga iwe
Sangie apite ku mushroom shade she's too good
Who's watching because of Ngozo and Patricia?😂
Koma Gani ndi sister wake eee 😂😂😂😂 smoko. Ndinu mtundu wanji was anthu 😅
Wow ine khawa chipere🤗Keep it up guys❤️Mpali yachimalawi
Usampepese inenso sindngampepese koma Patricia nd Gani mmakwana 😂 neba wamasuka koma abusa nthandizeni 😂 anthu amaendadi awiriawiri kkkk Gani wada bwa . Keep the fire burning guys 💪🔥
Koma i admire relationship ya gani ndi sister wakeyu ndi fire eeh😂😂😂🙌
Ngati eni eni et?
Kungolowelera nkhani yosaidziwa.....😂😂😂😂
Sangie is too good...
Tizi fusana mchizungu uwu nde mwano of the year 😮😮😮😅 a Gun pwiiiii
Patricia nd moto keep up guys good work
Patricia pa chiwongolelo one body one soul amandiuza kuti ndipange verify 😂😂😂😂😂😂😂😂
Munthu ngati sangakangane ndi ine mu "English " Waluza🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Kam'busa kachinyengo in Patricia's voice😂
sangie is one of the reasons why I watch usauver😂😂
😂😂😂gani ati ndiwe maskin-tu😂😂usauver is my favourite 😍 ❤❤
Watching from mwineriwa vg mulanje Sangie kumulalatira munthu oswalakwa eee😂😂😂😂😢😢
koma sangie eeeeeeeeeee, nde kuli hyphen kuyankhula with khoffffffffffffi
Koma mnyumba mwa Ngauzo muzaphulika bomba day 1😂😂
Nice one Koma dry head mutu ouma😂😂😂
Albert yatenga lehu🤣🤣🤣
Ndaona chocho😂
Kom sangie umatha kom ndimafuna nyimboyo guys please
Ati azatchola nyumba😂😂 Patricia is dramatic ah
Koma sangie ada iwe nd dolo 🎉🎉
Sangie akuti nayenso ndi Army😂😂😂😂😂
Sangie🎉 😅😅😅 Ati zinthu zambiri zitha kupezeka zachitika
Gani ndi 🐐
Patricial and Ganizani muzioneka kwambili u guys makes it gud recieve ur 🌹
Sangie to the world.Mbambande 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥Best episode
Nice stuff!💙🔥💯
Iyiyi yandikomera hvyy mmmm....u guys u just wow,,,,improvement ya boh hvyy.... this is professional
Sangie ndidolo heavy ❤❤❤❤
Muli boh guys keep it up
Keep on fire burning magaye YoooooooooYou rock guys 🔥🔥🔥🔥🔥
Saggie you are too good at this
Koma Gan adha akut amathu
Great job guys❤
Usauver is my favorite ❤
I love this
Sangie you will kill us with laughter one day
😂😂😂😂😂 sangie ujayooooo ndi vibe
😂🤣 😂Sangie. Eshh kungofikila chorus.. Nkhani yosaidziwa "umbava "😂 🤣 Iwe ndi more bwanji😂
One body one soul😅😅😅😅 man munomo?😅😅😅😅😅 Patricia umandiwaza🎉🎉
😂😂😂😂
Sangie shiiii kkkk. Ndeno mwat makampanie oika ma shandiyiliyao ndachna genie wo 😮 kkkk. Here we goo!!
Ati anthu andichenjelera zikhala ndekha😂😂😂😂😂 sangie
Amathu kumukana ganizani katatu ngati mmene petulo anankanira yesu
😂😂 Gani waziona,ati mwana wamasikini
Eti eti Kodi ndi aja anali ndi chibwezi ndi sisoko eti 😂😂
Ndipo sisoko wasowatu
At least you have extended the time guys, we appreciate ❤
Who's watching it right now 😊😮
Mi😊
@@user-jg2ow9ul8x nice my favorite is sangie
🖐️
@@Alefa-vd7ww watching it from where me lilongwe 23
Me
Can't wait for another part ❤
Sangie ndi dolo❤❤❤
agani nda matiyasi malo mokwatira muli busy kushishana pakhomo lamwana ngati sangie
keep it up guys zilibwino
Ma guy inuyo mumandiwaza heavy
Am so addicted with this movie
Bestie too continue kuipatsa fire😂😂😂😂
Sangie is really good 😊
Anthu amayendad awiriii awiriiii 😂😂 kma Gan , abusa kkkkkk winayo akut simungakangane muchingerez
Ili bho sangie 🎉❤❤
Best usova
Watching from Johannesburg
10/10 series
Will always like sangie❤🥳🥳🔥is a good one
I swear sangie is the best
Mumachedwa kutulusa ,😢😢and then ma 2 min min sibhoo muzitolere
where is part 2? this comedy is very very impressive.
Ati Gani akupemphelele zalowa masanje ndithu
Nice one keep it up
😘💪 So beautiful movies
Emmmmie ndi vibe inu
Hehehe koma yeah akuti za barzo zimandibwelelabwelela kukhosi koma ndaseka😅😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂
Nice one❤
Amathu anakonza kkkj
Mtebe mpaka ukufuna ndalama 😂
Can't wait
can't wait
😂😂😂😂😂😂😂koma ma guy ati nakumwesa wine kamozi😂😂
Mwamuna ndi mwamuna safuna nkazi azipanga zobalalika..hyphen wakwiya
Team Hyphen manja m'mwamba
About to watch
Malachi yemweyo abusa😅😅
Sangie nawe iiiiii😂😂😂❤❤❤❤
Sangie akuti iyeso Ndi army
😂😂koma ndaseka Emmie akuti kwathu sitimayikitsa ma Buble koma timayikitsa ma ShanDaria
Mumatha guys🔥🔥🔥
Koma gan ndi pat😂😂😂 ati moyo waumbanda😂😂😂
I love the confidence of hyphen ....
Iyi nde tiponyer pakuyatu😊
Sangie ndi WA Army sapepesa adafa kwambiri lol 😂
The last part though 😂
Tili pano 🎉❤
I think it just needs subtitles
Sangie umandiwaza nsaname
Kkkk ati moyo wawumbanda kkkkk atii simunthyola nyumbayiii
Komat ganizan ali srs za xool
Omwe timafila sangie bwelani tikhale malo amodzi
akt ine millitary sindingapepese
Ndipo ndichi vibe
Koma Hyphen can act with confidence and serious 😂😂😂😂😂😂😂😂 I love it
The part I liked
Sangie is good at acting
True
I always say the same nane. She's great
She's Dope Indeed
I was about to type the same.
very exceptional
indered
Friends of Ganizani let's gather hear ❤
❤
Neighbour wa mtebe nd doloso hvy🔥🔥💯
Ndipo zowona
It's Emmie and her Ben 10 for me 😂😂😂 crew yonse ndinu madolo ❤
Izi akupanga Sangie ndi Ganizani kudana ndi m’bale wa Piksy zinandichitikirapo ndikukhala ndi mkozi yanga, a very bad experience I don’t wish anyone to go through 😢😢😢
Gani ndi sister wake tsiku lina adzaphulitsa bomba mnyumba mwa ngozomu
Koma sangie ndi obheba💞
EEEE MAMA G ALEROYU
Uyu anabwera
Ndipo kwambiri,being black and beautiful❤
Tonde, neba wa abusa; voice yake really fits for that one batchala in most yards.
Amatha
On point nice observation kkkk
@@NelsonMumbulu-mq5ob m'bale wanga iwe
Sangie apite ku mushroom shade she's too good
Who's watching because of Ngozo and Patricia?😂
Koma Gani ndi sister wake eee 😂😂😂😂 smoko. Ndinu mtundu wanji was anthu 😅
Wow ine khawa chipere🤗Keep it up guys❤️Mpali yachimalawi
Usampepese inenso sindngampepese koma Patricia nd Gani mmakwana 😂 neba wamasuka koma abusa nthandizeni 😂 anthu amaendadi awiriawiri kkkk Gani wada bwa . Keep the fire burning guys 💪🔥
Koma i admire relationship ya gani ndi sister wakeyu ndi fire eeh😂😂😂🙌
Ngati eni eni et?
Kungolowelera nkhani yosaidziwa.....😂😂😂😂
Sangie is too good...
Tizi fusana mchizungu uwu nde mwano of the year 😮😮😮😅 a Gun pwiiiii
Patricia nd moto keep up guys good work
Patricia pa chiwongolelo one body one soul amandiuza kuti ndipange verify 😂😂😂😂😂😂😂😂
Munthu ngati sangakangane ndi ine mu "English " Waluza🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Kam'busa kachinyengo in Patricia's voice😂
sangie is one of the reasons why I watch usauver😂😂
😂😂😂gani ati ndiwe maskin-tu😂😂usauver is my favourite 😍 ❤❤
Watching from mwineriwa vg mulanje Sangie kumulalatira munthu oswalakwa eee😂😂😂😂😢😢
koma sangie eeeeeeeeeee, nde kuli hyphen kuyankhula with khoffffffffffffi
Koma mnyumba mwa Ngauzo muzaphulika bomba day 1😂😂
Nice one Koma dry head mutu ouma😂😂😂
Albert yatenga lehu🤣🤣🤣
Ndaona chocho😂
Kom sangie umatha kom ndimafuna nyimboyo guys please
Ati azatchola nyumba😂😂 Patricia is dramatic ah
Koma sangie ada iwe nd dolo 🎉🎉
Sangie akuti nayenso ndi Army😂😂😂😂😂
Sangie🎉 😅😅😅 Ati zinthu zambiri zitha kupezeka zachitika
Gani ndi 🐐
Patricial and Ganizani muzioneka kwambili u guys makes it gud recieve ur 🌹
Sangie to the world.
Mbambande 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Best episode
Nice stuff!💙🔥💯
Iyiyi yandikomera hvyy mmmm....u guys u just wow,,,,improvement ya boh hvyy.... this is professional
Sangie ndidolo heavy ❤❤❤❤
Muli boh guys keep it up
Keep on fire burning magaye
Yooooooooo
You rock guys 🔥🔥🔥🔥🔥