The Court Of Malawi

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 вер 2024
  • subscribe, comment, like & share

КОМЕНТАРІ • 41

  • @Johnmsewu
    @Johnmsewu 15 днів тому

    Zangovuta abale chakwera wandikwana,.Maka moyo ophanawu ai

  • @AlinaChauluka
    @AlinaChauluka Рік тому +1

    Mukanati muzitero milandu iliyonse bwezi zilibwino koma mumapangira asauka okhaokha komanso mukulimbana ndizithu zomwe sizingathandize amalawi olopangono koma koma mulungu oziwa kulanga akulangeni ma judge nonse Malawi muno🙏

  • @Deajay-jn8cf
    @Deajay-jn8cf Рік тому

    Kkkkkkk koma kumalawi kulizinthu 😂😂😂chizungu ngat vizungu shame my pipokkkkkk

  • @tomothybanda9070
    @tomothybanda9070 2 роки тому +1

    Mukumanga osawuka mukusiya akuba Gold ndi misonkho ya amalawi why amalawi? Ziwani chomwe chinapangisa kuti akalowe kunkhalango ndinu amu boma no jobs. And magesi amangoyaka 2 hours mukuganiza kuti amphawi iwe tiphirachani mumakomboni? Yambani kumanga akuba mubomawo ndi ena then pezani njira zabwino zathandizia amphawi.

  • @stevemasuli8715
    @stevemasuli8715 Рік тому

    Uyu mumusiye. Chakwela ndi chilima ndinuyo munaba ndalama zambiri. Mulungu athane nanu

  • @AlbunoCement
    @AlbunoCement 25 днів тому

    Sibwino munthu amayiwala.abweze.foni

  • @AlinaChauluka
    @AlinaChauluka Рік тому +1

    Mzaziii basi mukusiya kulimbana ndimbamva zomwe zikuba ndalama za boma mmmmhh koma mulungu akulangeni ndithu

  • @LekeleniUledi
    @LekeleniUledi Місяць тому

    Mukuitha magay big up

  • @esthergweje4038
    @esthergweje4038 Рік тому

    Kkkkkk tiyeni tziyankhula chichewa apa zizungu si chathu ichi

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 24 дні тому

    Nkhalango mwamaliza maliza kugulitsa mitengo kwa olemela lero muli bzy nd mphawi

  • @frankkamunde4575
    @frankkamunde4575 2 роки тому

    Zopusa zeni zeni kusiya mbava zeni zeni zomwe zikuononga dzikoli kumakalimbana ndi munthu osauka ngati ameneyo azimbambo akulu akulu ngati inu mulibe manyazitu

  • @alexanderkaunda9554
    @alexanderkaunda9554 2 роки тому

    Chizungu mukuwuza ndani simuzatheka dziko losauka koma vizungu kkkkk

  • @chazembaunderson-dm2lu
    @chazembaunderson-dm2lu Рік тому

    Nonse akhoti pantumbopanu mukulimbana ndiwodula mtengo koma wokuba ndalama zambilimbili mboma mukumusiya mbuzi muzatipeza

  • @yusufjailos
    @yusufjailos Рік тому

    Onena chilungamo ndiye mukumanga chilungamocho asananene

  • @janetnpaul426
    @janetnpaul426 Рік тому

    Basi inu peya peya kupit kukaona pomwe padulidwa mitengo mulungu akukhululukileni akuba ali mbweee misokho yathu mukulimbana ndizopelelazo

  • @yusufjailos
    @yusufjailos Рік тому

    Boni yambomayo ndiye mbavayo kufuna kupaka phawiyo

  • @zaidiealifualifu9989
    @zaidiealifualifu9989 Рік тому

    Nde mukuvutikilanji ndi chizungu chosecho alipamenepo ndi anthu ot amava chichewa cholinga winayo akhale ndi mantha muwine likubwela tsiku muzuzayankha zimenezi

  • @trinitykalima1840
    @trinitykalima1840 Рік тому

    Ena akuba ma billion mulibe nawo ntchto kma kulimbana ndi mphw chifkwa cha mtengo umoz,inuyo ndi amuyaya? Enawa mukuwaponya Pat?

  • @jvpondan4332
    @jvpondan4332 Рік тому

    Á malawi mukufuna umukhale ngati nafni skúti tidzizungu izitu ndi zopusa með mukutizunzatu tikamasauka kukhala opanda chuma

  • @jafarilulanga6561
    @jafarilulanga6561 2 роки тому

    muthu oti akudya bwinobwino sangarowe muchele ndikumadula mitengo? kod simukwaona amene akudula ndalama za malawi za misongo simumamanga? koma odula mitengo nde eeee☠️☠️💀💀💀💀😭

  • @masterjailos3913
    @masterjailos3913 Рік тому

    Kupusa basi munaonapo mzungu akuyangura chichewa?

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 2 роки тому

    choyamba mukuyenera kudziwa kuti dziko lanthu ndilosawuka

  • @danielkhinguirossejuliasse1214

    Malawi dziko lotembereredwa kupondereza anthu osauka pamene aboma Akuba mabilioni aboma pamene munthu odura mtengo woti adyetse banja alake

  • @promise3693
    @promise3693 2 роки тому

    Kumamanga osauka kusia olemera popeza ndrama zao zuchitira umbon

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363

    Ndiye mwati milanduyu njowona kapena ndimacheza chabe?

  • @stainlukali620
    @stainlukali620 2 роки тому

    Zoputsa mkuvutitsa anthu osauka musiyaokuba.

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Рік тому

    Za ziiii.

  • @alephangoma2158
    @alephangoma2158 2 роки тому +2

    Y not arrest leston Lazaro chilima Joyce peter bingu in gravy yard

  • @AureumProtelligent
    @AureumProtelligent Рік тому

    Chichewarising🤣🤣🤣

  • @promise3693
    @promise3693 2 роки тому

    Ndinu opusa nose

  • @chazembaunderson-dm2lu
    @chazembaunderson-dm2lu Рік тому

    Agalu inu munthu akusowa ntchito mumati ndiana azidya chani agalu inu koma inu ndiye kumaba ndalama muzalangidwa mizimutu ikakwiya

  • @PatrickBello-kz5zm
    @PatrickBello-kz5zm 9 місяців тому

    Kupusa

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Рік тому

    Kodi ndi drama chani??

  • @chicoyonas4641
    @chicoyonas4641 2 роки тому

    Zachibwana 😠😠😠😠

  • @alexanderkaunda9554
    @alexanderkaunda9554 2 роки тому

    Yr fools

  • @masterjailos3913
    @masterjailos3913 Рік тому

    Amalawi English is not urs