BRIAN BANDA KUWERENGA NKHANI ZA LERO PA 8 NDIPO AKUTI IZI NDIZIMENE ZITACHITIKE MAWA DZIKO MUNO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 8 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 20

  • @elsontmsukwa4356
    @elsontmsukwa4356 5 годин тому +4

    It was good program I think zitamatero zikhoza kumasitha zinthu dziko lathu

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 6 годин тому +6

    Tiyeni tikayipase 🔥🔥 mawa guys

  • @NathanGadamika
    @NathanGadamika 6 годин тому +3

    Tikaipatse Moto tonse tituluke osaopa osafooka

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 5 годин тому +1

    More fire comrade osaopa osatopa osafooka chakwera wakwana sakufunikaso kuyendesa dziko pano warephera kuyendesa dziko ungotuluka basi chimene ukukakamira ndi chani mcp warephera kuyendesa dziko basi

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 6 годин тому +1

    Ashumba avutika pano kumaura chifukwa chazopusa ngati zimenezo

  • @robsonmapeto1911
    @robsonmapeto1911 5 годин тому +1

    Vuto too much corruption ku judiciary ndipo sizingathe
    Pa list ya Satter anamangidwapo ndi angatii out of 87

  • @MaryMputi
    @MaryMputi 5 годин тому

    Chilungamo ndiye chikusowa muma khoti tithandizeni anthu amakondera Kwa amene Ali ndi ndalama opanda libe naye ntchito zikomo

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 6 годин тому

    Mec iyenera kulemekeza amalawi poti ndi amene anawalemba ntchito. Osati kuti mec izikhala ndi mphamvu ngati kuti mec yo ndiyimene inalemba ntchito amalawi

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 3 години тому

    Is that white man a spy....
    Kumalawi kwachuluka mbuzi.....

  • @McshonWilliam
    @McshonWilliam 5 годин тому +1

    😂😂😂😂😂😂😂😂Mademo pat

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 6 годин тому

    Tiyeni mawa ku mademo.
    Apolice majaji alikondera kwambiri achuma ndalama zawo zimawanthandiza koma amphawi ndi amene amakhala kundende koma apolice ndi majaji aziwe kuti kumwamba kuli Mulungu wamoyo akuwona

  • @GidionLufani
    @GidionLufani 6 годин тому

    Jimenez ndiye zopusa athu Akuma ndinjala inu mukuseweletsa ndalama pazamasewela

  • @EdsonMahamudu-px6ug
    @EdsonMahamudu-px6ug 6 годин тому

    Simunajambule bwino mwaziya mbila pakati.

  • @Milanzi-nb5fv
    @Milanzi-nb5fv 4 години тому

    Mupempheko za nsewu wa neno osamangochezako kumeneko

  • @HawaSadiki-u9d
    @HawaSadiki-u9d 6 годин тому

    Vuto mumadikira kuti anthu apedze vuto mmalo momangothandidza Mai jb mulungu akudaliseni

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l 3 години тому

    Sizingatheke,🐓tambala akunzonzoola too much,audzikondera

  • @jennyx6914
    @jennyx6914 6 годин тому

    no truth is in malawi at all

  • @AtanasioGuifite
    @AtanasioGuifite 6 годин тому

    Eeeeeeeeee