Ndipo akangomanga wina Ku Ndirande Ndix boys yasani Moto kuwathibula a Police wo . Apo biiii akamange Kaye AKAZIKWANJE. Weldone Comrade Mtanyiwa Big up never give Up fight for the better Malawi . Kumawayalusa basi anthu Oyipa amenewa. Chikangawa serial killer -- Chakwera
First come first save apolisi wo ndi amisala kapena zopanda zeru ayamba bwanji kumunga anthu aku ndirande kusiya azikwanje amene anayamba kuchita chipongwe ndindane poti zapolisi zakumalawi or jombo yikhale yakutha sizinena kathu ndi inde bwana
Dziko likutsogoleredwa ndi anthu osadziwa kanthu. Dziko Lili mmanja mwa mbuli, President mmutu mulibe kanthu, President akumalamulidwa ndi nduna zake, pomwe ndunazo ndi mbava komanso mahule
Comrade Ntanyiwa 😂😂😂😂😂more fire boma lovetsa chisoni.
Antanyiwa tauzen agalu amenewa
Ndipo akangomanga wina Ku Ndirande Ndix boys yasani Moto kuwathibula a Police wo .
Apo biiii akamange Kaye AKAZIKWANJE.
Weldone Comrade Mtanyiwa
Big up never give Up fight for the better Malawi .
Kumawayalusa basi anthu Oyipa amenewa.
Chikangawa serial killer -- Chakwera
First come first save apolisi wo ndi amisala kapena zopanda zeru ayamba bwanji kumunga anthu aku ndirande kusiya azikwanje amene anayamba kuchita chipongwe ndindane poti zapolisi zakumalawi or jombo yikhale yakutha sizinena kathu ndi inde bwana
Dziko likutsogoleredwa ndi anthu osadziwa kanthu. Dziko Lili mmanja mwa mbuli, President mmutu mulibe kanthu, President akumalamulidwa ndi nduna zake, pomwe ndunazo ndi mbava komanso mahule
Tingomenyanna Bass better than ever live on Malawi shinkangawaw sinkwanje sonka sonka mwallankwa sibagella 🇿🇦🇿🇦👊 mtanyiwa imeneyo ndi nyonyoooooo
Awuze ntanyiwa mcp ndi zisilu aaaah! Cikangawa zimenezi ukawuze amako ku kasiya. Ku ndilande kuno tagwilizana kale kuti akangobwela kuno sitisiyana mcp kuno sitikuifuna.Tinadziwa kuti mafumu amene aja anatumidwa ndicifukwa tinanena kuti cihana sapepesa mumuze cimwendo kuti tithana nae ifenso tinafa kwambiri
Zoona keep up brother he must not eat uchi na forget!!
Akamange kaye azikwanje aja ku Lilongwe, apolice musapite dala anthu akundirande mukaona zakudya, Mcp chimene ndaona ikufuna kubweretsa nkhondo
miyala yambili musunge Ku ndilandeko muyende mosayang.ana nkhope ya galu wina aliyese
Comrade Ntanyiwa you are the best one
Mumange a zikwanje Kaye .then Ndirande
Kkkkkk kondwani ndi chitsiru, kwambiri ndipo sazawinaso olo mpando wa u mp
Awuzen mr ntanyiwa
Mbambande comrade ntanyiwa
Mr Comrade
CIA Agent Comrade Ntanyiwa 😂😂
Akuona ngati ndi witika
A Ntanyiwa koma mukanawachenjewa anthu ngati mwaona choipa chomwe chingachitike.
Inu mukuimira a Malawi osati aliyense koma sitikufuna kuti titaye anthu enanso
Ine ndimadabwa kuti mademo awa, aloledwa mosavuta bwanji? Kani Namiwa is a sell-out? Ndamutaya
MCP imadziwa kupha basi kuyendetsa dziko zero
Sanamalize kuba mesa
Kod a president akutani? Angoti duu ngati sakuwona zinthu komwe zikulowera?
Koma ine nkuona ngati anthu Ali mbomawa nzeru alibe
Mukufuna chisokonozo muchenjere mwanva a police musamare guys muvurara iweso mkuku zopusa ukudzinva ndarama zakubazo mutibere ndarama zathu zamisokho mutikwatireso ana iwe iwe iwe usamare witika pano natash ukuziva unaliri ndani iweyo nkuku zopusa wanva
Zomvetsa chisoni ndi boma ili nawoso a police m'malo moteteza anthu akuonjeza khanza zosakhala bwino
Malawi ili mmanja mwasatana Chakwera
Zoonadi akayambe kumanga anthu omwe analepheretsa ma Demo ku Lilongwe aja
Umakwana mntanyiwa yam phalombe
Boma ili silabwino,boma lotsogozedwa ndi wa satanic mavuto ake ngomwewa
Komuledi atanyiwa tauzeni anyaniwo
Boma ili lamakape
𝙒𝙚 𝙡𝙤𝙫𝙚 𝙮𝙤𝙪 𝙗𝙧𝙤𝙩𝙝𝙚𝙧 𝙉𝙩𝙖𝙣𝙮𝙞𝙬𝙖