Koma ndizoyenera kupanga brame nduna ziwili zokha. Aaaa ku mcp kulibe wina wamzeru kuposa mzake. Ndi boma la anthu osaganiza basi. Minister of finance komanso president, onse zawavuta
Angavotere mcp ndi utm mitu sigwira chifukwa mavuto osewa tikukumana nawo adabwera chifukwa cha Chilima adafunisisa kukhala msogoleli wa ziko pano bwezi Ali president ku dpp koma kunyoza ndi kusava pano alikuti adamudya
Pepani Kaya ndinu wamamuno Kaya wamkazi chonde Mulungu analenga munthu aliyense ndichifanizo cha Mulungu, mudziyankhula mfundo osati kutukwana mwa phunzo mulandira temberero. Ine si wa MCP koma kutukwana kwanu mpaka munthu wakufa. Chonde sinthani mayankhulidwe oterewo.
Akut anthu akusangalala mulungu sangakondwe Kut anthu ena azivutoka tsogoleli azikonda anthu ose poti ose ndi amalaw mosatengera ntundu not kukondwera ndeno inu amene mukusangalala ndi boma lachakwera mudziwe Kut anzanu akuvutika musamalitse pamenepo mukamayamikira chakwera poti mukukhuta
@@tingamasi106 Lucifer iwe, ngati Mai ako anabelekapo mbuzi ndi kwanu komweko. Anthu ongodziwa kutukwana pa social media phindu lake ndi chani kutuwa muli mbuuu
Well said,,, Chilungamo kuchiswa zeni zeni Ochewa.
Boma lochitsa manyazi kulephela kusamala anthu ake
Boma lagubuduzika basi😂 APM MY VOTE
Tikafika APa ndiye kuti mzimu wa Chilima Ndi Anthu 8 yakwiya sikubweza Maganizo m mbuyo ayi boma la MCP ulendo basi APM my vote 💃💃💃💃💃💃
Munanyanya kuthamanga ndi dzilombo kulanda boma aziwona kkk Apm my vote💙💙💙 kazikambilanani kkkkkk
Tandigulitsen timaduwati😂😂😂 nice blue
Ritchard Chimwendo alibe mzeru komaso umunthu
😅😅😅😅😅😂😂😂😂 malawi anakoza kkkk america nayoso atimana ma ARV 😂😂😂
Kufa kulipo 🤣🤣🤣
apeka mayina a subsidyRichard ndi Samuel... anthu amewa agwetsa boma😂😂🙌
😅😅😅 kwaoli, kwavunda😜😜😜
Munthu wanzeru sangavotere Chakwera chifukwa ndimunthu opepera amangovomereza maganizo a nzungu. Nzungu Akati mugwetse kwacha iye kuvomera kuiwala kuti dziko muno simapanga katundu ogulitsa kunja ndizi katundu kukwera daily. Tikuvutika ndi njala chifukwa feteleza sakupezeka mopweka. Chakwera sangatukule dziko
Nyau zafatsa2😂😂😂😂😂
APM waku State House, confirmed by Malawian cameras💙💙💙💙💪🏿💪🏿💪🏿💪🏿💪🏿💪🏿💪🏿
@@RiteRoderick I really agree with you my brother.
Wapsadi wakustate house 🏡
Koma ndizoyenera kupanga brame nduna ziwili zokha. Aaaa ku mcp kulibe wina wamzeru kuposa mzake. Ndi boma la anthu osaganiza basi. Minister of finance komanso president, onse zawavuta
Akuti aziunike government ngati boma😂😂😂😂
ndimasaka comment iyi😂😂😂mtima wanga wazizila
ine ndine m 'chewa...ndipo zomwe boma ili likupanga ndi 0 pa 10
Yakwiya ndi mizimu😮😮
Malawian cameras ❤❤ munali pomwepo kodi kkkkk anthuwa anadekhatu 😂😂😂
@YasinterKapinga 🤣🤣🤣
I love u Malawi Cameras 😂
Kkkkk koma ndaseka chakwela sazava mafuta kulibe akupita kokapanga za mages zosephan mcp mulipo
Ukakhala niwana amapasa umagona chagada kuti Wana oyamweko.
Angavotere mcp ndi utm mitu sigwira chifukwa mavuto osewa tikukumana nawo adabwera chifukwa cha Chilima adafunisisa kukhala msogoleli wa ziko pano bwezi Ali president ku dpp koma kunyoza ndi kusava pano alikuti adamudya
Chikangawa pa ulendo basi. Akwiye akwiyeee 😅😅😅😅😅
Welcome. Malawian camera 📸
This should now be Malawian Eyes ....Cameras yachepa😂😂
Ine chewa km nunena zoona ineyo boma suluyenda bwino yayi tere😢
God bless Malawi.
Kumtumbo kwanu agalu a MCP mwatiwonongela dziko
Lero si mawa, tidzikhala anthu okondana. Denis Mahata, chonde azungulireni anthu ku Dowa.
😆😆❤️🙏🏾.
Achewa sitikondwa oro pag ono
Zaziii umbuli eti UTM my vote ❤❤❤❤
Simmene kuliri 😂😂😂😂😂😂❤
Macadet azako ameneo ndipo dpp singabweleleso muboma
Uyanya wena😮
Umuuze Chikangawa wakoyo mbolo yake mkadzi wake misempha mikono ngati nyani.Afumu akwanu mbolo yawo ngati ndi akadzi nyini yawo komanso abambo ako machende awo ndipo ngati anamwalira ndikutukwana mafupa awo mandamo
Pepani Kaya ndinu wamamuno Kaya wamkazi chonde Mulungu analenga munthu aliyense ndichifanizo cha Mulungu, mudziyankhula mfundo osati kutukwana mwa phunzo mulandira temberero. Ine si wa MCP koma kutukwana kwanu mpaka munthu wakufa. Chonde sinthani mayankhulidwe oterewo.
Akut anthu akusangalala mulungu sangakondwe Kut anthu ena azivutoka tsogoleli azikonda anthu ose poti ose ndi amalaw mosatengera ntundu not kukondwera ndeno inu amene mukusangalala ndi boma lachakwera mudziwe Kut anzanu akuvutika musamalitse pamenepo mukamayamikira chakwera poti mukukhuta
HlS exllent professor Peter muthalika
The president of the republic of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 2025 to 2030
Sianthu akudowa bodza velani koyambirilako anthuwo achita kusintha voice
Musatinamizile ife kuno olo zitavutanwanji sitingavotele dpp
UTM my vote
Dpp boma basi izi ayi ndinthu
Kumwela akusangalala ,bodza achewa mukutimphimba maso,ulamuliro uwu unthelamo popanda chochitika kuno,akt kuli Neef,tikungomva kt anthu akulandila ,kuli fetelizer wamakopon kuli ziii chimanga chikumasula pano kma ndi chofiila kusowa fertilizer,chitukuko china chilichonse kulibe,zonsezo zikuchitika komweko chigawo chapakati mau mbomi tili nao,apatu musat akapanda kusmala agwa,kd asamala chani nthawi yao yantha kale ,awat agwa kale kwatsala nditsikulo kt likwanilisidwe bas.,Achakwela akwela mumtengo akuona ngt pansiipa palibe mame
Ndiye mwati government ngati boma?
Mungoti ku dowa wisachula dera limene akuchokera zabodza mumasowa zokamba
,mcp,ngakhale,asemphane,zochita,samayambitsa,,,,,chipani,china,km,kum,mwelako,mpaka,zikwana,,10,zipani,mcp,ilikomwekoso,,,tionetsane,chaka,chakachino,
BOMA la MCP lagwa bwasi Chakwela anamudyesa buluzi amangolamulilidwa ndi Chimwendo mpaka kugwesa MCP
Wise man Chimwendo yo?? Ngati kuli munthu wa MCP yemwe akupusitsa Chakwera ndi Chimwendo.
Munkati boma ndilomweli lero mwagwila chiphwisi ku Dowa. Ndale za MCP zauchitsilu basi.
Malawian Cameras❤❤❤❤
Achewa ndi ozikondadi nonse poti mumangofela kuti uyu mngwatu😂
Inu musavere ameneyo kadet wa dpp dowa singavotere dpp mchewa sangasithe muwone koti mukapangire kampeni inu mukuchedwa
Zilibwino kwambiri kuti izizi akuyankhulawa ndiachaeniake a MCp komaso ku base ya mcp-yomweyo😢 uyu atiphauyu iiii
Malawian Camera anali pomwepo koma anthuwo samamuona Malawian Camera ndi twinie brother wa Mose uja wa Baibulo znse zikhale poyera
😂😂😂😂
Blues basi chakwera akagwele
Mwakochana ma cadets nokha nokha apa, zopusa
I like Malawi camera 🤳😂😂😂😂
Government ngati Boma
Ku mmwera kwake kuti anthu akusangalala? Ifenso kuno ayi
Kuma amalawi tisazaerekezeso ku vote vinyau
Kkkkkk mukamapanga zinthu muziyiwerenga kut anthu adziwe kut sizoopanga
MCP iwinira kubwera not kuti zama voti..anthu amenewo akupanga ma plan obera
Adadii oyeee 2025 akutenga boma basi mufune musafune koma simuthawa??
,bodza,ilo,mwapangana,nokhanokha,musanamizile,anthi,akudowa,muwaonetse,taone,,,akulankhulao,akutumaniwo,akuphwetekesa,mcp,singatekeseke,ndizopusazo,komweko,kuno,ayi,zagalu,zanuzo,
ULENSO UNO KULIBE ZACHIZOLOWEZI
Kkkk koma mcp simugona nayo tulo. Mwagula wanthu kuti azinyoza mcp. Kkkkkk koma
Apm boma 💙💙💙💙🙌💙
UTM pa16 Sept chongii ✅
Mukunamizana Dowa yake itiyo inuyo ingodikilani September basi
iwe uliko wekha kusowa Kuno ukat dowa yake just bcoz iwe udya nawo achimwendowo ife tifele zimenezo?
Wawa😅😅😅
Boma ili palibe chomwe anganene achita azipita anthu okuba ndi kupha basi
Zinthi suzuyenda...
Kodi wina amatepa iwo asakudziwa kapena zochita ukoza 😂😂😂😂 chifukwatu nde adadekha
Tachita bwino anthu aku Dowa mulape
Malawian cameras 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Abu bweretsa fatireza 😅😅😅 nchewa ANAKONZA BOMA ili ndi logwaigwa osati inachita chibwana yagwakale iyi
Mukuiwala mbava zina izi Howa nkaka, kamajekete zikhale ng'oma n
Dowa wake uti?
Koditu pafika malawipa kudzavotera mcp ndikupanda nzeru
Siluyenda bwino ataaa
Aaaaaaaa kķkkkk ndakatulo kapena drama
Mumtumizire chimwendo
Achitsiru Inu mwasowa zotumiza eti
Ife tikamanena mumati tikun
ama apapa mwamva nokha DC ananenso kuti ku dowa anthu akumvutika mumaona ngati akunama, mwacidule mcp palibe ciliconse yacita kwa a malawi 0% .apapa basi yagwa chifukwa alibe nthawi yokoza dzinthu alephela zaka nde angakoze dzinthu menzi 4? Panopa adzingopakila APM akubwela.Takunyadilani anthu a ku dowa kumene chikangawa amati mkwawo mwachita bwino kudzimasula nyau zimenezi.
Mabodzaamenewo mcp yiwinaso yinua dpp mukumasowazokamba ndinumakape mukunya bomandilomweli sitikusitha
Pepani ife kummwera kuno sitikusangalala tikuzunzika osati masewera so ife timati bola anzathu kumeneko poti ndikwawo
Meangless I'm from Thyolo but I'm not a Dpp Supporter, so kukhala waku Dowa sizitanthauza kuti ndi wa Mcp
APM 💙💙💙
Ndigaile timaduwa ta blue ti
Dowa kuchipinda kwa chikangawa party
mukamachita,ndala,musamachulutse,bodza,kunamizila,anzanu,zoipa,dziko,lidapenya,,,,kuwanamizila,anthu,akudowa,kapena,kuwaona,kupusa,athu,akudowa
anthu amene amamwa ma ARVS basi zinthu zativuta chifukwa America yasiya kaye thandizo lake kodi apanga bwanji chakwera pamene kwawo ndikuba basi
Moses kumkuyu mukumuiwala ndi zikhale ng'oma
APM MY VOTE DPP WUY😅😅
CHAKWERA mukumva naye kuwawatu, olo mulembe ganyu achewa opepela nkumalankhula zopepelazo mungozinamiza. CHAKWERA awina ndi landslide ndipo mudzapita ku court simudzawina mulandu chifukwa MCP idzawina mwachilingamo osati Tippex wanu uja ai
Ndiwe mbuzi
ULENDO UNO KULIBE ZA CHIZOLOWEZI
@@tingamasi106 Lucifer iwe, ngati Mai ako anabelekapo mbuzi ndi kwanu komweko.
Anthu ongodziwa kutukwana pa social media phindu lake ndi chani kutuwa muli mbuuu
@@HaroonSaidi-jv3ek ubwino wake September 16 kwatsala miezi yochepa, omuvotela Chakwera akuchulukilabe🇲🇼✅🔥🔥🔥🔥🔥
Government ngati Boma yemweyo
Likugwaa
Dowa yayankhulatu.
Chimwendo akuzitenga ngati ndi yesu
He's defending his belly
Azanu zikoli amaliyendesa bwino kma inuyo yakwiya ndi mizimu ya kuchikangawa
Bodza Ili 😂😂😂
Koma simukunama
Boma ili silikusamara za kampen iyi ikupakuliratu ikagwa iwowo alibe khawa zawo zizakhara zatheka
Kulibeso chakwera kuwina
Anthu awa a MCP awononga dziko asawapatsa vote
Zopusa zeni zeni your playing drama
🔥🔥🔥🔥
KKKKKKKKKKKK.MCP..😂