I remember my girl chikond anapitq kulilongwe kuxool ndinamudikira kwa chaka km osabweq then ndinapangq za passport ndikuvaya theba apa ndinangotsala ndiminsozi mmaso mwanga😢😢😢😢😢 ndipo guys mu moyowu timqdutsa mwambiri
Nditayimva penapake ndinkawona ngati yatuluka kumene n I searched it online n I discovered that it was released 1 yr ago... It's on repeat, it's ahit song that deserves 1M+ views cuz it's concept is splendid
Ndimawerenga ma comments omwe anthu mwalemba onse ndi olimbikitsa zomwe zimpangitse mfanayu ku phusha hvy keep the fire burning 🔥 ♥️ 👌 👍 uli bho hvy please don't loose the track keep going one day you will tell the story
I can relate 😋😋😋 anyway big up boss.its a song that base on real Life situation
Ineyo nyimbo ngat izizi nde ndimazifila koopsa,,, iwe ndi dolo🔥🔥
Ase nyimbo iyiyi ndainva lero koma ili pa repeat❤❤
Inenso Bwanawe
Same here
Ineso imandiwaza
he kill it
Iyi nyimbo ikukuza mizimu it slaps hard ase💪💪🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Ndabwera after winawake waidikula kwambiri ku chigwiri,ndat let me search, nice tune bro.
Anytime wen your online like my comments its my dosage every moment
😢😢
😅😅😅😅😅 mpaka dosage
@@CatherineMbeye oky dear
Keep it up bro uzabowoleza one day
mpaka ndawonera katatu😩🙌 this is real muzik
Pa lilongwepo pakanakhala Jubeki ambiri tikanalirq
😂😂muuzeni ayimbeso
At first I thought it's Elli njunchi 😅eeeh luso chiksy more🔥🔥🔥
Me too😂 all this time I was like it's Eli
Tilipo ambiri😂
@@SiyabongaKunkumbira apa tadziwa bas😂
Ndipo ineso I thought its Eli njuch
@@edithbonongwe5529 😂😂😂😂😂 same WhatsApp group mamie
Chiko ku Jon, ubwela liti ku Jon
Amazing song I love it
this guy needs an award 👏 what a delicious song, keep pon gwaan
Road to million🎉🎉🎉
You rock boss.. This song mmmm makes me think crazy..
Beautiful song,based on reality
Ichichii ineyoo chimandiswa mtimaaa
av been confusing with Elli njuchi...bt uli bho🎉🎉
Ndaikonda nyimboy❤
Wow 😊 , wat a wonderful theme! I've found in this song !
Mubwera liti Ku Lilongwee,, umatha ayise being a young musician like you
I love this song
This track is lit man........................... U got the ENERGY
Kanyimbo akaka nkoyenera award koma ❤
My boy is from Malawian but this is making myself soul
Everything in this song is kept simple...yet so poetic and so nice.. love the vocals lots...
thank you so much
From mzimba boooom....🥁🔥
And I like this song❤
Ine repeat yosayamba lero ❤❤❤ nice song
Chinyimbo chaphwedwa ichi.. big up guy
Kukupeza ayise nkanakumwetsa fanta ,umatha
Adatchona ku jon amuna aine kosapita ndi mapazi😢its hitting differently😢❤
Ayse uli ndi voice and u can sing mmmmmmmmmmmmm keep the fire burning ❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉😅
Waswa ase big up
Ichch ndchgayo cha sound. Respect
Mwapha iyi mjomba aaaaaa nkk ikudikila zazikulu kuchokela kwa inu
Koma iyi anapha❤
Nyimbo iyi unapha chiksy
Wow what a song I really like it keep it up bro
This song imandikhuza ine 😢 big up chiksy
Man muli ndi luso. Mukapeza mwayi wa Manager muyesese kuphusha.
U deserve an award ❤ I love yr song but I dnt understand yr language ❤watching from Zimbabwe ❤🎉
I thought it was done by Eli Njuchi seriously. I even searched Eli Njuchi Kuilongwe
Even me I thought is Eli njuchi,nyc vibe
Exactly ineso
I thought it's Eli njuchi too😹😩
Nyimbo beautifully
Am from Zambia Lusaka this song ili dope... Komwee ku LILONGWE kwa msinje😂😂
Nyimbo iyi munapha madala Very Nice💥💣
Its first time to listen to this guy but the talent is there big up brother ❤
Aaaaah nthaw yonseyi mmati anayimba ndi Eli Njuchi, This is nice mweeee🥳🥳
Wabwela bredarh kuzatipasa zimwemwe Moyo kwathu umakwana 🔥🔥🔥🔥
Good composition raw talent
Nyimbo mbambandee....keep it up man muli ndi luso
Ineyo ndaika kale repeat
IMENEYI NDIYE NDI FIRE 🔥🔥🔥🔥 YANDIKHUDZATU 😢😢 CHONDE TIPHUNZILEPO APA TIBWELELE TISANGOLONJEZA CHONDE
Kwambiri osalola kuti wina adzikudandaula mmoyo
Muli lusoo umumuu🔥🔥🔥🔥.
Dolo kwambiri 🔥 🔥
Big up bro ❤❤❤
Anthu amatha kuyimba iiii 🙌💯
Chikooo 😅😂ubwela liti Ku Lilongwe, Super super
Ndaionda kwambiri 😊😊
I remember my girl chikond anapitq kulilongwe kuxool ndinamudikira kwa chaka km osabweq then ndinapangq za passport ndikuvaya theba apa ndinangotsala ndiminsozi mmaso mwanga😢😢😢😢😢 ndipo guys mu moyowu timqdutsa mwambiri
Ngt mwationatu zomwe zatichikira😢ku lilongwe kwandlanda mamuna ine😢
Sorry dear Sanali wako
@@chiksymw l believe so😥🙌
Kkkkk🤣🤣🤣
😂😂
Nyimbo zofunika zizi_hitter 1 million views zija ndi izizi..big up bro
Eli njuchi + Driemo 🔥🔥🔥🔥
Ngat waimbila inetu years ago achibwenzi atapita ku Lilongwe mkumapanga zake 😂😂 nice song bro
Eshii iyi yatithera kopalatu ❤❤❤❤❤
Iwe ndi dolo anse❤❤❤
I have missed my chiko so much.
Nyimbo iyiyi nde unangoyimbira inetu.❤❤
Nyimbo yovinika komanso yoti ukhonza kukhetsa nsozi
Why did I just start loving this music😢
In love with this❤
Ili pa repeat 🔥🔥
Iwe nde wabwera bho
Nyimbo iyi ndimavera or 10 time a day ❤🔥🔥🔥
This is what we call music. Nice one. Keep it up
Ngati nditumize vn cz I'm 😢 nyimbo iyiyi ndichi vibe
Mphamvu brother 💪🔥
You are a talented person brother continue with your heart making good teachings around the world.
Ukali my brother apa ntchito mwagwira bro🔥🔥
Ada awawa akadakhala nd zina bohboh nyimboyi ikadavuta kuposa mmene ndkuganizira..... Keep it up buddy.. God blessed u will your carrier
Muziti akanakhala asataniki inakavuta nyimboyi koma akungoyimba basi
Aise ndili capetown kma ndangoyivela ada ena ake atayika mu galimoto yanga kma yili pa repeat
Sanamutenge ma satanic so it's difficult kuti atchuke
ndizoonadi man
Kanyimbo Ka bho
Nyimbo iyitu ikuzunza mizimu mmakwalalamu moti azimayi akuyika pa repeat komanso makolo Ali khumakhuma kuganizila
Kulilongwe on 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Keep going my bro 💯🎶🏆💖
Umatha iweyo❤
There is potential in you big up bro umakwapula sound hvy massive
Zabwino sitichita ku penta ukundinvetsa kukoma,ziri bwino
I thought nyimbo ndiya ELI, 🔥🔥🔥🔥
Bomba 💣 💣 💣. God bless your great talent, dear. You have gold🎉
I don't mind repeating this song, it's perfect and I love it ♥️
Man u hv talent
Wishing you all the best to grow in music industry
Nditayimva penapake ndinkawona ngati yatuluka kumene n I searched it online n I discovered that it was released 1 yr ago... It's on repeat, it's ahit song that deserves 1M+ views cuz it's concept is splendid
you are a star afana. sound ya bho heavy !!!!!!!! ndipo these are real life events zomwe zikuchitika ndithu.
This is great song. It lacks recognition from the public
Concept, voice on point
On Repeat 🔁 you killed it bro
My guy you were called to minister HIS WORD through Gospel music. Thank you for this song 🙏🙏
U gat skill bro...keep it 100
Welcome my home boy,Appreciate to you mbambande song and video
Chiksy big up, full of senses this song mwapha
You are so talented brother 🎉🎉 i really like this song ❤❤
Ndimawerenga ma comments omwe anthu mwalemba onse ndi olimbikitsa zomwe zimpangitse mfanayu ku phusha hvy keep the fire burning 🔥 ♥️ 👌 👍 uli bho hvy please don't loose the track keep going one day you will tell the story
Mchimwene hit more fire🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Nyimbo ikuveledwa iyi 🙌🔥
Love❤ from 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲