NTHAWI ZIWIRI ZOMWE JOAB CHAKHAZA ANAOPHYEZA ANTHU PA TV

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 14 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 85

  • @Lydia-t4b
    @Lydia-t4b 17 днів тому +8

    Very true Sir. Zinthu zingaopse motani but somebody must do it. God bless you for a good job of serving your country

  • @JawaduShafie
    @JawaduShafie 12 днів тому +1

    May the Almighty never allow my body to be taken to mortuary when I die Aameen 🙏

  • @PaulMalemba-pp8hk
    @PaulMalemba-pp8hk 13 днів тому +1

    Joab upole moto😂😂😂😂 funso mpaka "mumadzinamiza chani" pomuyeza munthu aaaaaaa.
    Iwe ndi mbambande 😅😅😅

  • @EzekielBanda-r7r
    @EzekielBanda-r7r 3 дні тому

    Koma Joab tchito mukuyigwila congrats

  • @theodorabanda
    @theodorabanda 18 днів тому +2

    Popempha ma gloves thumbs up, coz interviewee anayenera kukuthandizani kuti mubvale moyenera ndi Malo munaliwo.

  • @ianjanga2053
    @ianjanga2053 10 днів тому +2

    Angotchula mitengo ya Njoka aliphee 😂😂

  • @WisdomMwale-j9h
    @WisdomMwale-j9h 13 днів тому +1

    Ma bzy ndee Aliko!🙌

    • @peterchipala1822
      @peterchipala1822 12 днів тому

      Ndipo eeee man ndichimozimozi kupha munthutu ntchito zina 😂😂

  • @JussabRobert
    @JussabRobert 18 днів тому +1

    Mmmmm komatu ntchito zosezi ndizoopsya kwambiri 🙆🙆

  • @katenyalayanayla2040
    @katenyalayanayla2040 18 днів тому +2

    Koma kuchipatala kuja iiii💔😭

  • @chisomotamanga1696
    @chisomotamanga1696 9 днів тому

    Somebody must do it and let somebody be me. 😊

  • @JohnLingilirani-m8d
    @JohnLingilirani-m8d 18 днів тому

    Big man Supayi from Mtuwakale Lilongwe

  • @peterrompwa5731
    @peterrompwa5731 11 днів тому +1

    Joabu ndi wa chibwana Iwe kkkk

  • @motivation2779
    @motivation2779 14 днів тому

    Ati kucheza bade😂😂😂 tilembeni ntchito

  • @REBECCAKABATI
    @REBECCAKABATI 17 днів тому +1

    Eeeee koma Joabu mmm mpaka kugwira njoka 😮

  • @JustinWBanda
    @JustinWBanda 18 днів тому

    😂😂😂😂😂😂 ine joab 🙌🏼🙌🏼🙌🏼🙌🏼🙌🏼

  • @GertrudePhiri-u8t
    @GertrudePhiri-u8t День тому

    Ai zikomo maka kuzanjokazo

  • @Essi-i2e
    @Essi-i2e 16 днів тому

    😂😂😂😂😂 Joab upole sure osasewera ndi moyo 😂😂😂😂

  • @FladielMwase
    @FladielMwase 17 днів тому +1

    Mmmmmmmm koma joab umakwana kwambiri ❤❤❤❤

  • @IbrahimSiraj-u6j
    @IbrahimSiraj-u6j 6 днів тому

    Kkkkkkkkkkkk katundu tigawana abwana osadanda

  • @BlessingsTembenu
    @BlessingsTembenu 18 днів тому +2

    Kkkkk Koma Joab iweyo ayise,katundu tigawana ikani nkhosi njoka😂😂😂

  • @HappyMsukwa-j1q
    @HappyMsukwa-j1q 17 днів тому

    Tigawanadi ika nkosi njokayo😂😂🤣

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 3 дні тому

    Joab uzafera zaeni

  • @FolonessMambo
    @FolonessMambo Годину тому

    Dziko lapansi kukuchitika zinthu.

  • @giftlisimba6628
    @giftlisimba6628 17 днів тому

    Courage

  • @SayidiMisessa-x6y
    @SayidiMisessa-x6y 13 днів тому +3

    Izi nde nkhaza ndithu chodulira mutu wamunthu omwalira nchiyani ? Chikalirecho akatero sakhalaso ndimoyo aaaaa 😢😢😢

  • @nitafraphael2362
    @nitafraphael2362 18 днів тому

    Joab God bless your Job surely 🙏 🙌

  • @jameslweya-eo1uj
    @jameslweya-eo1uj 18 днів тому

    Joab , kugwira njoka

  • @HenryMikithayo
    @HenryMikithayo 18 днів тому +2

    Mmmm guys koma nowadays internet itionetsa zinthu zosaoneka ndithu mpaka kumakadula ubongo wamunthu iiiii nawe chakhaza interview inayi ayi ndithu

    • @Lydia-t4b
      @Lydia-t4b 17 днів тому

      Yatani interview timayenera tiziziwa zenizeni kumene

  • @JoeKhoma
    @JoeKhoma 17 днів тому

    Joab wationesa kulimba mtima 😂😂😂 coz pa tchito zonsezo Pali yabwino

  • @lysonmanda-ri6od
    @lysonmanda-ri6od 5 днів тому

    Life is hard

  • @PrinceFoster-x9x
    @PrinceFoster-x9x 18 днів тому

    Komat a job muzakayakha kwamulungu zimene mumapangainu khaza kuthupi muzikozeka wakumoto

  • @BrightLuciano
    @BrightLuciano 6 днів тому

    Palibe yomwe ndingagwile

  • @AhamaduJRAminie
    @AhamaduJRAminie 18 днів тому

    Ayi zkm is not easy to make ndalama 😅😅😅

  • @jameskachime2975
    @jameskachime2975 7 днів тому

    Aku mortuary akundionekela mwa ufiti 😮

  • @Martha-x8z
    @Martha-x8z 11 днів тому

    Joab ndifunsile funso ili,,ndinamva kuti Asprin amapanga kuchokera ku ubongo wamunthu yemwe wachita ngozi,,,in short onse omwalira pangozi amawachotsa ubongo for asprin

    • @pempheromulepa9281
      @pempheromulepa9281 7 днів тому

      Not true. Pharmacognosy ya aspirin is from reactions that's chemistry. It's through combination of elements to make acid. That's why aspirin in chemistry is called ASA. ASA is acid form

  • @bensonmaluwa
    @bensonmaluwa 10 днів тому

    Joab uzigwirako brake ndi njoka iyi

  • @kingssalema3364
    @kingssalema3364 18 днів тому +1

    Kkkkkkk,
    Owoooo? Amazinamiza chan? Kkkkk

  • @williamfriday5323
    @williamfriday5323 16 днів тому

    Kkkkkk tiwoneko njokayo

  • @HamiltonwaNamuwah
    @HamiltonwaNamuwah 11 днів тому

    Ishii koma Joab

  • @ArnoldNosheHBandaBanda-r4z
    @ArnoldNosheHBandaBanda-r4z 11 днів тому

    Wanjokayu sayenera kukwera bus azaphetsa anthu

  • @martinettebredell3537
    @martinettebredell3537 18 днів тому

    Koma Eee mitembo imaziwonera 😂😂😂😂😂

  • @WisdomMwale-j9h
    @WisdomMwale-j9h 13 днів тому

    🙌

  • @JaneKadzuwa
    @JaneKadzuwa 18 днів тому

    Koma chowetera nsato ndichani abale?

  • @ELIDAMISOMALI
    @ELIDAMISOMALI 17 днів тому

    Ndili ndi mafunso ochuluka nthawi yachepa kucheza naye munthu ameneyi

  • @coastersRob
    @coastersRob 18 днів тому

    Ndibwera ndizafusileko ntchito basi chifukwa eeeee ndiyabwino kumazacheka anthu amwano kwambiri

  • @AubreyWiskes
    @AubreyWiskes 18 днів тому +1

    Ayi zikomo

  • @FreedahKandoje
    @FreedahKandoje 18 днів тому

    Mmmmm ayi zikomo

  • @HamuzahRoben
    @HamuzahRoben 18 днів тому

    Tchito zake zimenezo ndimakuchedweselaso malipilo eeee

  • @ThokoMsonkho-hy4uc
    @ThokoMsonkho-hy4uc 18 днів тому

    Yandisangalasa ndiya bizinezi ya njoka.

  • @PromiseChanza-q9j
    @PromiseChanza-q9j 18 днів тому

    5:53 mmmm komatu

  • @GodfreyMzembe-b3n
    @GodfreyMzembe-b3n 18 днів тому

    Joab a kupanga so mantha

  • @REBECCAKABATI
    @REBECCAKABATI 18 днів тому

    Eeee ntchito zodzipeleka kwatoto moyo

  • @tamalangoma2765
    @tamalangoma2765 18 днів тому

    🤣🤣🤣 koma ntchito zinazi kkkkkk

  • @HenzoniceMW
    @HenzoniceMW 17 днів тому

    Asaaaah

  • @nyondoandrews1621
    @nyondoandrews1621 18 днів тому +1

    Ziliko ziliko

  • @BlessingsMcnight
    @BlessingsMcnight 18 днів тому

    Khani idzi zoophya zedi

  • @JaneNgwira-d7t
    @JaneNgwira-d7t 13 днів тому

    Katunduu

  • @ELIDAMISOMALI
    @ELIDAMISOMALI 17 днів тому

    Koma mutu kumautero inu iii kumontchale

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu8384 18 днів тому

    Eeeee koma ndee

  • @EvansKasoloka
    @EvansKasoloka 15 днів тому

    Wachibwana iwe

  • @EnertChidwala
    @EnertChidwala 18 днів тому

    Amakwama

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 18 днів тому +1

    Koma eeeeee

  • @GiftJuwah
    @GiftJuwah 18 днів тому

    Mmmm

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska 17 днів тому

    😢😂😂mgawane katundu

  • @LynessNyando
    @LynessNyando 15 днів тому

    Iiiiii komatu

  • @YouthfocusGroup
    @YouthfocusGroup 18 днів тому

    😂

  • @Anthonymendos
    @Anthonymendos 18 днів тому

    Anthu olimba mtima, ukatero umakadya chakudya, osanyasidwa, mbole zako, ntchito zonsezi, kukasankha zodula anthu

  • @CharlesMatope-xg6ln
    @CharlesMatope-xg6ln 18 днів тому

    😂😂😂Mwaigwira ndithu

  • @AllanMumba-b9q
    @AllanMumba-b9q 18 днів тому

    But this interview iiish

  • @RasheedkanyengaMatress-vs7hn
    @RasheedkanyengaMatress-vs7hn 12 днів тому

    Uku ndikuzuz mtembo serious oipa ndi amene amapitis mtemb kt azikaupanga zoipaz