Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
This guy is smart ,,.. my first time kumva his speech
I see this man is very intergent n mature in politics
UTM ili ndi mizwanya, komabe Kabambe ndi amene atawine ndipo aKambala ndi aNtumbuka adzamupange support kuti UTM ipitirire kukhala yamphamvu.
Uyu ndi waku dabwenso eti,osayelekeza kumusakha u president wa UTM
Manganya is not such type of person to work with
Mphuno salota::mukanadziwa simukana sankha Usi
Kambala my vote
Olo brian banda waziwa kuti wakumana nazo
Mugwire tchito ndi KabambeMumuphure Malawi pa Moto
Kambaka ngwaboza uyu
Ngakhale kuti khothi, ukamafotokoza chilungamo sumavutika konse kuyankha mafunso. Tithokoze, chilungamo chayenda ngati madzi on Times Exclusive.
Engineer kambala machine
Wazake saopa kulankhula~uwuzeni zoona biggy!
Panyo pamako. Why are you hating Dr Dalitso Kabambe.
Nkhani yake iti bwana...?
Zoona akuba ndi ambiri::ens choncho akonzekela kuti abe chipani
Mfundo za bwino zomveka
Mmuzeni bwino Usi
Ngati utm ili yako ndiye ife tikuti izivotera wekha.
Ameneyutu
Ephraim wayandikana ndi mafano mulekeni...
Palije cha zelu, chipani chakutondeka ichi
#1
engineer
This guy is smart ,,.. my first time kumva his speech
I see this man is very intergent n mature in politics
UTM ili ndi mizwanya, komabe Kabambe ndi amene atawine ndipo aKambala ndi aNtumbuka adzamupange support kuti UTM ipitirire kukhala yamphamvu.
Uyu ndi waku dabwenso eti,osayelekeza kumusakha u president wa UTM
Manganya is not such type of person to work with
Mphuno salota::mukanadziwa simukana sankha Usi
Kambala my vote
Olo brian banda waziwa kuti wakumana nazo
Mugwire tchito ndi Kabambe
Mumuphure Malawi pa Moto