KWAYAKA MOTO KU MALAWI! ANTHU AWA APEKELEKA MASIKU 14 KWA CHAKWERA ~~ NGATI SAPANGA IZI IWO ATELE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 19 вер 2024
  • KWAYAKA MOTO KU MALAWI! ANTHU AWA APEKELEKA MASIKU 14 KWA CHAKWERA ~~ NGATI SAPANGA IZI IWO ATELE
    Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
    Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
    Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
    #MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

КОМЕНТАРІ • 143

  • @PetrusTlhokwane
    @PetrusTlhokwane 5 годин тому +7

    Namiwa ndi Office yanu pitilizani kupanga chilungamo mupaka Mulungu ationese chimene chinapha azibale athu zikomo kwambiri

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 5 годин тому +5

    Chakwera ndi azinzake a MCP akutitora kwambiri ngati dziko

  • @ThomsonChipwele
    @ThomsonChipwele 4 години тому +4

    Amenewo ndiye mau mr namiwa timakunyadilani

  • @MlaziJames
    @MlaziJames 5 годин тому +5

    Chakwara achoka chikangawa

  • @arnoldchikopa2611
    @arnoldchikopa2611 4 години тому +4

    Rip SKC

  • @LloydLuwis
    @LloydLuwis 4 години тому +2

    Powerful massage

  • @Elson-cf1gy
    @Elson-cf1gy Годину тому +1

    Chilungamo chiyende ngati madzi❤ from cape town

  • @jennyx6914
    @jennyx6914 27 хвилин тому +1

    bon kalindo please join hands with nsmiwa and lead malawian kuoanga ma demonstratiin atule pansi udindo

  • @TamalaMwamlima-gk5im
    @TamalaMwamlima-gk5im 5 годин тому +3

    Zoona tidakalira Abale athu ife

  • @user-vh1cq5gs5u
    @user-vh1cq5gs5u 4 години тому +3

    Ma demonstration akhale oti asiye pasi udindo.

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x 4 години тому +1

    That's good well done

  • @MarriamBakalie
    @MarriamBakalie 4 години тому +4

    Gear 2 ipondeni fader Mr Namiwa ❤❤

  • @ChisomoMachowa
    @ChisomoMachowa 3 хвилини тому

    Loud and clear!!!!!

  • @FebbieNjewa-g3k
    @FebbieNjewa-g3k 3 години тому +1

    Well done Mr namiwa,, keep it up

    • @LameckBanda-gk6ri
      @LameckBanda-gk6ri 45 хвилин тому

      Namiwa ,born kalindo ,mtanyiwa JB ,bakili muluzi TV ose ndi alomwe ,akumenyera kampeni mulomwe nzawo peter muntharika,koma adziwe kuti Malawi sikumuntha kwa muntharika

  • @NoluvuyoMatutu
    @NoluvuyoMatutu 2 години тому

    powerful 💪 Mr Namiwa

  • @user-ol1hf7ru1v
    @user-ol1hf7ru1v 5 годин тому +2

    Pamenepo mwadza ndithu

  • @HaleemaAllie
    @HaleemaAllie 5 годин тому +2

    Mr namiwa tikukudalulani pamozi ndigululanu mukamayangula zamakape amewa

  • @rhodahjere8747
    @rhodahjere8747 3 години тому

    Great job Mr Nam

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Годину тому

    Mr M Namiwa mmmmh Ambuye akutetedzeni ndithu mumatiimilira ulemu wanu 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🙍

  • @VitumbikoKaunga
    @VitumbikoKaunga Годину тому

    Good point

  • @YAMIEKAMANENGWA
    @YAMIEKAMANENGWA 47 хвилин тому

    Mr Namiwa mulungu akhale Nanu kulikonse mungapite, pitilizan kutumikira amalawi .

  • @cassimmtambo968
    @cassimmtambo968 2 години тому

    Ulemu wanu namiwa ❤

  • @MiracleDamiano
    @MiracleDamiano 5 годин тому +1

    Tiyeni Tiyeni asatizolowere Bambo otembereledwa chikangawa yi

  • @YamikanChirwa
    @YamikanChirwa Годину тому

    🎉🎉 nkhanii niyoona

  • @jeanbotomani9081
    @jeanbotomani9081 2 години тому

    Big up Namiwa

  • @PromiseSaidi
    @PromiseSaidi 3 години тому +1

    Makamaka kugwirana manja ndi kalondo

  • @BoscoJosaya-u3r
    @BoscoJosaya-u3r 3 години тому

    Yes ayankhe ndithu

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Годину тому

    Mademo omweo ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @DICKSONJACOB-g4l
    @DICKSONJACOB-g4l Годину тому

    Thank u umakwana

  • @ChilekaMoyenda
    @ChilekaMoyenda 16 хвилин тому

    ❤❤ umakwana malume

  • @user-vh1cq5gs5u
    @user-vh1cq5gs5u 4 години тому +1

    Ai chakwela asiye pasi udindo kuti afufuzidwe bwinobwo za ifa imeneyi

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Годину тому

    Paja Chakwera akuti sawopsyezedwa iye sanva za anthu

  • @MjombaMoosa
    @MjombaMoosa 2 години тому

    Ine ndili okwiya kwambiri ndi chipani Cha Mr chikangawa ndi m c p nkhondotu iyi akuyiyambayi😢😢😢

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo Годину тому

    Big up 🔥🔥

  • @cynthiandekhakatundu6890
    @cynthiandekhakatundu6890 Годину тому

    Behind you !!

  • @bandachawanangwa6437
    @bandachawanangwa6437 2 години тому

    Ukunena zoona. Ndikudabwa kuti tikungokhala! Chakwera akudziwapo kanthu.

  • @CadTafa2
    @CadTafa2 4 години тому +4

    Uramurilo uwu ndiwa 1940 wachakwera

  • @ChristinaSimwaka
    @ChristinaSimwaka 4 години тому +1

    Çhikangawa achke

  • @MphatsoIshmaeladam
    @MphatsoIshmaeladam 3 години тому

    100% chilungamo tikuchifuna ife tatopa ndi ulamuliro wa chikangawa that is the point

  • @MphatsoIshmaeladam
    @MphatsoIshmaeladam 3 години тому +1

    Ndipo zithunzi za skc tili nazo ndipo chinawavula zovala ndi tayi munthu kusala ali mbulanda tichidziwe chifukwa taona ndege zikugwa koma si ya skc aaaa chikangawa wakupha

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 2 години тому

    Naniwa adaika kale mutu pa njanji samaopa kufa ndiolimba mtima go ahead namiwa.

  • @YamikanChirwa
    @YamikanChirwa Годину тому

    Kd chilima unafadi km zimanivutabe kuvetsa ishiiii😢😢

  • @NoluvuyoMatutu
    @NoluvuyoMatutu 2 години тому

    km aah pure awaaa mulungu awaone 😭😭😭😭

  • @HgghddYfgdfdd
    @HgghddYfgdfdd 2 години тому

    Zoona bwana

  • @mbelengamavuto2517
    @mbelengamavuto2517 3 години тому +1

    Ndipo so masiku 14 achuluka kumafunika kupanda mademo Ali kuunga asabweleso

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 2 години тому

    ❤❤❤❤

  • @SophieLupiya
    @SophieLupiya 5 годин тому +1

    Zoona

  • @BrianAmos-s2k
    @BrianAmos-s2k 43 хвилини тому

    Wamurder by phalombe muzik

  • @Standwell78
    @Standwell78 2 години тому

    Born kanindo please join them

  • @PatriciaAlomwe-oz8wc
    @PatriciaAlomwe-oz8wc 2 години тому

    Ifwanthamureni fada!!!!!!!

  • @BandaLega
    @BandaLega 2 години тому

    Rip skc mmmmm chakwera uyankhe ife tikulira mpaka pano sitimavetsa

  • @AndrewjemesJemes
    @AndrewjemesJemes 2 години тому

    Namiwa osafoka

  • @allanlouis6235
    @allanlouis6235 4 години тому

    Please work on you background music

  • @AtupeleChitenje
    @AtupeleChitenje 4 години тому +1

    Komanso akubanja asakhale chete please

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 3 години тому

      Koma ndipodi akuma banja akhala chete kwambiri. Akuwugwira bwanji mtima akuma banja. Akudekha kwambiri akuma banja oferedwawa.

  • @ChimwemwePhiso
    @ChimwemwePhiso 49 хвилин тому

    Chikangawa wapita ku us

  • @KingDavedNkhata
    @KingDavedNkhata 2 години тому

    Zinthu izidzi Chakwera ndi agalu azinzakewa atipedzelera kwambiri sinanga chinanga sakuopa chilichonse wayambira mabungwe, zipani zotsutsa amipingo ndi zipembedzo a Malawi Eni akewo nde nyanyi chifukwa angoyang'anidwa akamapanga zoputsa zakezo
    Coz tamupatsa mphamvu zonse watansa malamulo nde angowasintha Ngati am'nyumba mwake
    Koma tonse tikagwirana ndikumanga chimodzi Kanyimbi ameneyu idzakha mbiri Kuti adalipo pharaoh
    Serious

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q Годину тому

    Kenako athamanga ndi chithumba cha ndalama kenako munva ziwonetsero zija sitipanganso

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 12 хвилин тому

    guys nkhani ndimeneyi atsogoleri amalawi dzikoli alitola kwambili pasakhaleso kusekerera anthu opusawa

  • @ElliottBelon
    @ElliottBelon 4 години тому

    Timenyeren nkhondo mr namiwa

  • @PollyLysonLutepo
    @PollyLysonLutepo Годину тому

    Koma nkhani ya 14 days 21 days inayambapo ndi kale. Koma palibe chomwe chikuchitika.
    Khalani anthu ochita osati olankhula okha.

  • @BladesBullets-pu5uw
    @BladesBullets-pu5uw 3 години тому

    Akakuphani ndi bread zonsezo musiya kulankhula, nanga amzathuwa ndalama yaboma siiyi ikuthera kugulira anthuyi.

  • @TimbasonPhiri
    @TimbasonPhiri 7 хвилин тому

    bwana aNamiwa pangani zomwezo ife amalawi tikulila

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 3 години тому

    Awuzeni chilungamo awuzeni chilungamo chidutse muchilungamo

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 4 години тому

    Namiwa ukumanyako ku chikangawa? Dege yikawa ya chakwera? Lindilani Germany namwe ,

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma 2 години тому

    Niwopenga awa akuwa namiza ninkhala ya dpp ija

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 4 години тому

    Va ziii ivo

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer Годину тому

    Rest in peace bhiyeni ngt bodza eeeesh

  • @wisekanyinji5377
    @wisekanyinji5377 2 години тому

    Chilungamo chiyende ngati madzi, mcp njakupha ndani sakudziwa? Mcp imapha

  • @FunnyDimSum-hk1so
    @FunnyDimSum-hk1so 16 хвилин тому

    Ndipo live chomwe akuziwa kuyenda yenda kuba ndarara kumapitira maiko akuja athu akudya chitedzi

  • @MussaRafael-d4q
    @MussaRafael-d4q 2 години тому

    Esh Anamiwa mukundilankulila bwino bwanji

  • @Alice-z7t4z
    @Alice-z7t4z 59 хвилин тому

    14 dyz yachuluka kwambiri mr Namiwa chikangawa must goooo

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu8384 2 години тому

    MCP ndi chipani Cha kupha ndikale

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 2 години тому

    Kulila talila..Pano tidziwe choona

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie Годину тому

    Kodi 7 days yomwe munamupatsa chimwendo Banda uja zili pati?

  • @NgeyasjuWadeya
    @NgeyasjuWadeya 4 години тому

    Lilo dziko Lina sindikukayika konse awa pochoka ku UNGA anangofikira ku court dziko akulamulira asilikali, koma poti ku Malawi kumangodzivetsa chisoni. Komatu kunena chilungamo mafunso akufunsidwa ndioveka ndipo onse okhudzidwa akazivera sindikukayika amatuluka mamina ndithu

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 48 хвилин тому

    Apa palibe zobisa anatiphera chilima achakwera.chipani cha mcp ndichowophya chamagazi .

  • @WelemuSayizi
    @WelemuSayizi 2 години тому

    Ndipo 1983 kunalibe anthu ambili wophunzilanso anali wochepa ndiye matamawo akuyambira pati

  • @AtupeleChitenje
    @AtupeleChitenje 4 години тому

    Musasiyile pomwepa bwana😢

  • @BacklinebwanaliBwanali
    @BacklinebwanaliBwanali 4 години тому

    Zoona zoona

  • @JOHNOlesmasCosmas
    @JOHNOlesmasCosmas Годину тому

    Akumveka ngat wa Bakili muluzi TV 😂😂😂
    Koma I support you Mr.Namiwa

  • @giftbanda7690
    @giftbanda7690 16 хвилин тому

    Nvuto amalawi fe Mantha too much 😅😅😅😅

  • @SurathAnnubi
    @SurathAnnubi 4 години тому

    Ndipo zoonadi ngati sakuyakha chomwe anamuphela chilima ifeso timupha tidulakhoso komaso uyu Richard chimwendo tidula khosi

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 2 години тому

    Ma deadline sakuopaso

  • @DysonTummiesSajiwa
    @DysonTummiesSajiwa 31 хвилина тому

    Dzikapangani ma demo ife tilibe nazo ntchito chifukwa sikut adzadzukaso ayi wapita ameneyo

  • @EnerstBanda-m4s
    @EnerstBanda-m4s Годину тому

    Nanga anamuvula zovala Chilima ndi ndani mpakana lamba?nanga emwe analoleza kuti Ndege iwuluke kuli nyengo yosakhala bwino ndani? Nanga munthu anamuletsa Richard Chimwendo kuti asakwere nawo ndani? Nanga emwe anamuuza president yo ndi ndani kuti Ndege inafika ku Mzuzu

  • @NgeyasjuWadeya
    @NgeyasjuWadeya 4 години тому

    Ife sitidikiratu 2025 kuti akathyaliwa achoke m'boma, mcp dziwani ichi Malawi siopusa palibeso ndale apa nkhani ndi mwazi wa anthu apa.

  • @AchiwaNikisya
    @AchiwaNikisya Годину тому

    Zoona anene bwino

  • @Eddie-b9f
    @Eddie-b9f 2 години тому

    Osaopa. 😅😅

  • @Jivason
    @Jivason 2 години тому

    Ndipo ndizoona chakwela akudziwapo kathu za imfa ya chilima satana chakwela

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 3 години тому

    Zikomo kwambiri bambo namiwa chenjani giya2 tiri pambuyo panu wawa.

  • @lazaruschitsamba8394
    @lazaruschitsamba8394 5 годин тому +2

    ummmm uyu ndiwa opposition ndamuona tsopano

    • @MiracleDamiano
      @MiracleDamiano 5 годин тому

      Ndye????😏😏😏

    • @Alexsaaa365
      @Alexsaaa365 5 годин тому

      Bon kalindo NDIwa opposition nsooo mmmm ife tifuna chilungamo

    • @GladysndilimbiraBonongwe-g6c
      @GladysndilimbiraBonongwe-g6c 5 годин тому +1

      Umafuna azisekerera zoipazi

    • @user-ol1hf7ru1v
      @user-ol1hf7ru1v 5 годин тому

      Nde umafuna afufuze ndani poti opposition nde angapange

    • @CHARLESMASINA-xx5kt
      @CHARLESMASINA-xx5kt 5 годин тому

      Wa opposition kuti chani...why are you hating the truth.....be there for the truth not for favours..... these guys are standing for the truth so whats wrong with that

  • @KalongaWhy
    @KalongaWhy 4 години тому

    Komadi pangan zomwezo kuthamanga bas

  • @PatriciaAlomwe-oz8wc
    @PatriciaAlomwe-oz8wc 2 години тому

    Auzen amalaw timulowele fasting ya estere ameneyi adwale khate

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 4 години тому

    Mulungu akutsogolele big chilungamo chofunika akutizolowela achakwela kwambili kutiwa kokhalila kutulukila kukamwa

  • @RichesMuyaya
    @RichesMuyaya 3 години тому

    Cided ilibe mphamvu payokha, ichite mgwirizano ndi mabungwe akukulu.

  • @giftsululu4274
    @giftsululu4274 4 години тому

    Kom bvuto LA anamiwa MA press briefing anu nsitinaonepo itabala zipatso

  • @LameckBanda-gk6ri
    @LameckBanda-gk6ri 37 хвилин тому

    Choti mudziwe anamiwa ndi mutharika pangani ndinuyo kafukufukuyo osati ena paja ndinu madolo aza ndenge nde ife tikuvera or mupitenawo ku mzuzu muka pangireko kampeni agogo anuwo paja nde alomwe anzanu

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 3 години тому

    Komaso adawuxandani kuti athu wose anali mundegemo afa anadxiwa bwanji?

  • @Paworo-h5r
    @Paworo-h5r 4 години тому

    Mubweletse zoti inuyo mwafufuza otsati zawukalizo ngati kuli akukutumani sizipindula izi. tiyamba kukutsikani muli be fundo zothandidza amalawi

  • @arnoldchikopa2611
    @arnoldchikopa2611 4 години тому

    Uyuyu ndi dolo