NDE MWATI THOKO KATIMBA NDI TAMIA JA ANADYELANA CHANI KUTI ZIFIKE POTERE?...ANTHU APWETEKANA AWA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 19 вер 2024
  • NDE MWATI THOKO KATIMBA NDI TAMIA JA ANADYELANA CHANI KUTI ZIFIKE POTERE?...ANTHU APWETEKANA AWA
    Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
    Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
    Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
    #MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

КОМЕНТАРІ • 33

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 6 годин тому +2

    A Tania anthu akupangani chipongwe samalani

  • @MaryJefry
    @MaryJefry 6 годин тому +3

    Mmm naweso tamia pora moto chakukhunzapo ndichani or 5hundred ukuishurayo nindarama imeneyo aaaa asisi inu mukusaka pofera

  • @MustafaRobert
    @MustafaRobert 2 години тому +1

    Bola Tamia unaba 8 million nanga 5 hundred thousand aaaa

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 7 годин тому +2

    Point of correction Tamia , 500 thousand ndi price kwamunthu amene angamugwile Thoco ,
    Sangathawe just because of 500 thousand is not enough money to run away

    • @MamaTheo-sm3dr
      @MamaTheo-sm3dr 2 години тому +1

      Ndipo akut kwamene atamupeza apasidwa 500,000 km ndalama zomwe wathawanazozo sizikuziwika😊

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 7 годин тому +2

    Vambula ntchito vakuyambana namwe

  • @CourageSydney
    @CourageSydney 5 годин тому +1

    Kusowa zochita amalawi moti muzipeza maganyu😂😂

  • @EmmanuelNgamuti
    @EmmanuelNgamuti 3 години тому +1

    So Money involved is half a million & reward for accurate infor is half a million again? U missed the point come get the right information!

  • @JusticeFriday-q1j
    @JusticeFriday-q1j 2 години тому +1

    Nanuso K 500,000 ndikachani kut muthu akathawe kuchezakukavuta osamaipisirana mbiri please

  • @chikaonekarh
    @chikaonekarh 8 годин тому +1

    Basi

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 8 годин тому +1

    Kodi ku top ten kwa anthu olemela kuja mesa thoko katimbaso alokomko
    Ndiye zitheka bwanji kuthawa ndi 500,000. Aaaa

    • @maxmundiwa6613
      @maxmundiwa6613 6 годин тому +1

      Zangosokonezeka,
      Sikuti akuti wathawa ndi 500 000 koma munthu odandaulayo akuti emwe angapereke information ya komwe kuli Katimba azapasidwa chiona maso Cha 500k

  • @MaryJefry
    @MaryJefry 6 годин тому

    Ulibize iwe kupanga zaanthu bwanji osapanga zoti zikuthandize mmmm

  • @jennyx6914
    @jennyx6914 5 хвилин тому

    ine ndiye tamia amandibowa ma audios ake ndomangowadutsa uhuke basi

  • @LestoneChigwedezeni
    @LestoneChigwedezeni 7 годин тому

    Bas ingokwatiranan nanga simwafanana zochitika

  • @GeorgeKambwiri-xr9ri
    @GeorgeKambwiri-xr9ri 7 годин тому +1

    Muruuuu

  • @user-ii9ch7oz8n
    @user-ii9ch7oz8n 4 години тому +1

    Zazii

  • @LenoMvula
    @LenoMvula 4 години тому

    Inu zipangani zanu zija mwasowa zonena zopusa

  • @MartinNgoma-tp2jk
    @MartinNgoma-tp2jk 5 годин тому

    Kodi simuziwa kuti Tamia ja akupangandalama ndimapoints

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 2 хвилини тому

    More fire TJ😂😂😂

  • @AishaChipande
    @AishaChipande 4 години тому

    Inu pangani zanu sithawi yopanga zamunthu iyi muzakhumudwa anthu omweo akukupangani chipongwe ili ndi dziko ndiwe mwana ochepa kwambiri ndiye poyakhula uziziwa kt dziko ndiloipa

  • @Blessmkotma
    @Blessmkotma 7 годин тому

    500000 bas aah akumunamizila thoko ndi wolemela

  • @DamaliceWamalanguluko
    @DamaliceWamalanguluko 2 години тому

    Kamsikana kokongola kasafere za eni zisiyani zimenezo ndi dzikoli mufa mudakali ana

  • @JafaliChiwimbi
    @JafaliChiwimbi 5 годин тому

    Komatu iwe watopa ndi moyo wako kufuna kuchuka kumeneko

  • @EdwardZuze-r7w
    @EdwardZuze-r7w 5 годин тому

    zopoira izi

  • @giftgama1325
    @giftgama1325 3 години тому

    Zaziiiiii

  • @SelemanIssahAhmad
    @SelemanIssahAhmad 2 години тому

    😂😂😂 koma ma background wa mmmh

  • @PeaceSakaike
    @PeaceSakaike 3 години тому

    Mmmm mmmmm ay wayamba chipogwe mmmmm

  • @MussaMsoma
    @MussaMsoma 4 години тому

    ❤❤😂

  • @SelemanIssahAhmad
    @SelemanIssahAhmad 2 години тому

    Voice 😂😂😂😂

  • @FlechaChipeta
    @FlechaChipeta 2 години тому

    😂😂😂

  • @alickmphalasa5167
    @alickmphalasa5167 3 години тому

    😂😂😂😂😂