BON KALINDO & JACOB AT DISASTER COMMEMORATION
Вставка
- Опубліковано 15 вер 2024
- Bon Kalindo and Jacob performing at National Commemoration of the International Day for Disaster reduction in Chikwawa on 18th October 2015 at Bodza primary school. YONECO took part in the event through its displays, Cultural Troupe performance and YFM live coverage of the event.
watching WINIKO live was one of my biggest highlights of visiting Malawi what a talent what a guy ....salute to JAKOBO
Yes
Nyooo ndi 1 ❤
kodi zovala browse zija sunasiye eti umakwana kona🙌🙌
Hello phungu nkasa ndimazikonda nyimbo
Kmt Amakwana
Jakobo
The DC
Bambo nyoooo ndi 1
winiko anankhoza
Winiko umakwinala ase , ukazafa ndizakudandaula.
mabulauzi koma ndezimamumkhala
Mutu wa winikowo eeeeee😂😂😂😂😂😂😂
Winiko😂
Zili bho
Malawi wanga ine kumva kukoma winiko ndi deal eeee kkkk
Kkkkk otiimilira wathu wa ku Malawi sazathekaso wa brauseyu kkkkk
Kkkkkkkk ikaona matako okuda kma Winiko anakonza
Zosangalasa kwabasi bambo Nyoooo kkkkkk
Winiko ndi more
❤
Izeki and jakob
Malawi alomwe anayitukula
Kwambiri amwene
Ndichani?
Koma guy's
Koma winiko ndi drama lokwanila kwambila
D C
Dangerous Child
winiko siuzathekaso big man wavalasi bhobho,
Anduna samulola kuti awuluke...???
Nc comedy
Pena ngati ndizingosekabe ndisasiye kkkkkkk
Koma apoletu winiko
ALOMWE SAZATHEKA
mwati bwanji KO'd alomwe
alomwe kulongolola
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Nzukulu wache wa m'bona umakwana,kkkkkk
😂😂😂😂😂😂. Anyoooo
Koma winiko
winiko ndiwe dolo basi
winiko suzathe ai kkkk
Chemandota
kkkkkkkk nyooooo!
8
👏👏🤣🤣
mbuyache
kkkk kutengera kukanidwa eti
kkkkkkkk km madoro
Kkkkkkkkkkk matako okuda koma winiko
Kkkkkkkkkk
😅😅😅
Kkkkkkkkkk 😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂
Ndimamukondela zomwe
kkkkkkkkk
kkkkkk
kkkkkkkkkkk chovala icho
Kkkkkkk kuuluka
Kkkkkkkkkk mlomwe wakwathu
matako akuda kkkkkkk
MULI BWANJI ANTHU NONSE NDINE BONI KASELEWA KUNO KU MULANJE NDAIMA PANO NDUFUNA KULIMBITSENI MITIMA YANU YOMWE YASASA KWIYO NDIKUTOPA NDI UMBAWI.NDAKHALA NDIKUFUNA CHITHANDIZO KWA NTHAWI YAYITALI KUFUNAFUNA NTHANDIZO KWA ANTHU OSIYANASIYANA KOMA ZOBWELERA ZAKE NDI KUMANGO LIRA BASI NDENO NDINAONASO POST YAMUNTHU WINA AKUKAMBA ZAMBIRI ZOKHUDZA GOGO NDEMBURE.KUTI ANAWATANDIZA NDENO KWAINEYO KUNALI KUYESA CHABE KOMASO MULUNGU ANAFUNA KUTI INEYO NTHAWI YANGA IKWANIRE KUDZELA KWA AGOGO NDEMBURE .KOTELEKO INEYO NDUFUNA KULIMBITSENI MITIMA YANUYOSO KUTI CHITHANDIZO CHILIPO KWA AGOGO AMENEYU NDINTHU KWA AMENE AKUFUNA NUMBER YAWO NDI IYI .( 0987702558)ZIKOMO.
Tapezani zochita Zina masiku obela athu siano ayi pita ukooooo😂😂😂😂😂