UTM YABWERA POYERA LERO NDIPO YAYANKHULA KUTI IPANGITSA CONVENTION PA 17 NOVEMBER

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 51

  • @ShadreckSabwera
    @ShadreckSabwera 14 днів тому

    We are together UTM vote yanga SKC my strength

  • @TamikaKaponya
    @TamikaKaponya 17 днів тому +4

    UTM is an idea yes...big up guys,tili nanu nanu...Osaopa Osatopa osafooka,

  • @Drmuhammadchiwona
    @Drmuhammadchiwona 17 днів тому +1

    Zipani ziwilizi dpp--- and utm eeeee ndi akatundu

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg 17 днів тому +5

    Izi ndye zezeni osati za manganya mwana woyipa kwambili mtima

  • @maggiendala664
    @maggiendala664 17 днів тому

    ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️UTM go go go🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼 this is it go up go Up 💪💪💪✅This is my part.❤🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e 17 днів тому +1

    ❤❤❤❤lyi nde UTM yomwe ndikuyidziwa osat zathiko

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 17 днів тому

    We have big brains 🧠 this Utm

  • @JuvenileDebwe-bv8ow
    @JuvenileDebwe-bv8ow 17 днів тому

    We will follow real UTM where ever you go not zinazija

  • @RaphaelKweve-u5s
    @RaphaelKweve-u5s 17 днів тому

    Utm forever ❤

  • @paulinemtachi466
    @paulinemtachi466 17 днів тому

    Anjawala osasiya kukonda chipani tili Nanu pambuyo🔥🔥

  • @user-lk8kj9zv6x
    @user-lk8kj9zv6x 17 днів тому

    Go go go UTM together we can make it we are together

  • @AnthonyChirwa-t4g
    @AnthonyChirwa-t4g 17 днів тому

    iyi ndiye utm imene ife timayiziwa zathikozo ndizadyela za mthela kuwili manganya phaka kwambili

  • @user-dw9zi6bo3o
    @user-dw9zi6bo3o 17 днів тому

    Lests keep the fire, Chilima died while fighting for the just cause and we have a responsibility to carry his shared vision for Malawi forward

  • @evalisterphiri8435
    @evalisterphiri8435 17 днів тому

    My party, UTM moto!!!!!!!

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 17 днів тому +1

    Ndi Ambuye zonse ndizotheka. United we stand.

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 16 днів тому

    Michael Usi ndi ufulu wako kusapota MCP (=chipani cha ufiti, chakupha, chamanyi). Koma kunamizira kuti ndiwe wa UTM ndi ukanyimbi (=uchiphwisi).

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 17 днів тому

    I respect this guy 🙏🙏

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 17 днів тому

    Vakutuka vilekeke waphlire banyamata , kutuka nkhunandi mu utm

  • @GoldenNamanguya-q9u
    @GoldenNamanguya-q9u 17 днів тому

    Akuvotelani azungu amene mukuwawuzawo

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v 17 днів тому +3

    Mukakamusankha Manganya ziwani kuti Utm ibwereranso ku mgwirizano ndi MCP chikangawa party

  • @beatricenkhoma1109
    @beatricenkhoma1109 17 днів тому

    We are together 💪💪💪💪osaopa, osafoka,osatopa

  • @greymitomoni4047
    @greymitomoni4047 17 днів тому

    UTM motto🔥🔥🔥🔥.

  • @HarryNtanga
    @HarryNtanga 17 днів тому

    UTM Chipani changa, Osaopa, osatopa, Osafooka 💪

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 17 днів тому

    UTM my party ❤❤❤❤

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 17 днів тому

    Mayi wathu mama Kaliyati,Bambo wathu Kambala, Anjawala chonde gwiranani manja ndipo musalore asatana kuti akusokoneni yang'anani kwa Ambuye akutsogolereni muzonse akanyimbiwa akuyesa kufuna kuthetsa UTM koma mzimu wa SKC ulinanu nthawi zonse.Manganya ndi yudasi usamuzolowera akupwetekani

  • @robinmathandalizwe
    @robinmathandalizwe 17 днів тому

    ❤❤❤❤

  • @LukasiGawamadzi
    @LukasiGawamadzi 17 днів тому

    Nice one

  • @user-ln5hw7dn9g
    @user-ln5hw7dn9g 17 днів тому

    UTM my party

  • @StevenFombe
    @StevenFombe 17 днів тому

    Ican smell money moving among ...

  • @JanetNthondowa
    @JanetNthondowa 17 днів тому

    Amen

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h 17 днів тому

    Welcome ❤❤

  • @user-jc9gy9ou3v
    @user-jc9gy9ou3v 17 днів тому

    Good 💪

  • @WatsonMsukwa-y5i
    @WatsonMsukwa-y5i 17 днів тому

    Ok

  • @user-zo4ox7bn6s
    @user-zo4ox7bn6s 17 днів тому

    Kubwera ngati coming

  • @chinomwephiri1183
    @chinomwephiri1183 17 днів тому

    Idea

  • @fredgabrielnyangulu
    @fredgabrielnyangulu 17 днів тому

    Paja Makosana imazapoira pena pake

  • @MayesoGwedeza
    @MayesoGwedeza 17 днів тому

    🎉🎉🎉🎉

  • @SELEMANJAMESB
    @SELEMANJAMESB 16 днів тому

    amalawi mudakhala bwanji tayambani ndi chichewa kut muthu wakunuziave koyambirila so mukangoyamba ndi chizugu muthu wakumuzi amangotseka osavelaso or mubwele ndi chichewa kumapeto iye amakhal kut wayamba nchito

  • @user-io2uw2me9f
    @user-io2uw2me9f 17 днів тому

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @AndrewChirombo
    @AndrewChirombo 17 днів тому

    Kanyimbo kamene kamanveka pansi pansipo musazayikenso kamabowesa

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 17 днів тому

    Timadikira zimenezi Kaliati

  • @Violet-wf9pf
    @Violet-wf9pf 17 днів тому

    Mgwirizano ukufunika zipani ngati UDF, UTM komanso AFORD, please osati ndi DPP nayonso mudzavutika nayi chonde, once bitten twice shy

  • @user-wm4bt3so2i
    @user-wm4bt3so2i 17 днів тому

    Osaopa osafooka osatopa

  • @SamboMaria
    @SamboMaria 17 днів тому

    Tili pambuyo panu

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 17 днів тому

    Zipani pano zonse utm dpp ndi zina agwilizane apange chimozi amuchose chilangawa pamozi ndi manganya mwana oyipa kwambi athu amewa ndi athu amagazi koma zuzika pano kwambili mulungu athana nawo pompano

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 17 днів тому

      Dpp inatipanga chipongwe ife a udf sitingaloleso kt itipangeso chipongwe dpp ife a udf sitidzayiwala

  • @RemaniNkhoma
    @RemaniNkhoma 17 днів тому

    Koma prz gyz osayerekeza kuti mupangeso mgwirzano ndi mcp uko ndikuputsa ngat mukufuna kupanga mgwirzano pangani ndi DPP prz gyz kusogoroku boma rizakhara ranu tikuvankhani zoti akugureni musavomere Apolo ndiye kuti mukuzigurisa ng'onazi ndizoyipa zizakudyanisoni

  • @emmanuelmuyilaa
    @emmanuelmuyilaa 17 днів тому

    ❤❤❤❤