anakupasa ndalama galu iwe zaka kuchuluka chitukuko chake ndikukhala namuntekenya ameyu ada ngati wasowa zokamba usamabwelese nyasizakozo pamenepo pantumbo pako
Chawezi ndi wa MCP uyu palibe chachilendo apa ndi chani kodi Njanjizo anamanga ndi ndani zinthu zoti ena akungopitiliza a Chawezi musayankhule motha mau ai ingoyamikani kuti zinthu zili bwino basi osati kuyankhula mopusa ai
ADMARC = Agricultural Development & Marketing Corporation. This organization has made us poor by limiting Farming improvement and prices on Agricultural Products. MCP built ADMARC to suppress Farming growth. MCP isn't Malawian. When are we going to wake up...???
❤❤❤❤❤
I love this program
thanks for sharing this video!
Zikomo kwambiri Chakwera, Mulungu akudaluse
😂😂😂😂Ndaikonda kwambili program yi
Mbambande chief
Ndaikonda kwambiri programme imeneyi
Aaaa panyopako
iwenso ndi wandale
komatu CHAWEZI SIMUKUWONEKA BWINO...KU MBC KUJA TU..MUNKASANGALALA😂😂😂😂
anakupasa ndalama galu iwe zaka kuchuluka chitukuko chake ndikukhala namuntekenya ameyu ada ngati wasowa zokamba usamabwelese nyasizakozo pamenepo pantumbo pako
chawezi ali TUUUUUUUUU...aaaaahhh....ukuvutikatu aise😂😂😂😂😂😂
Or atakhala wa mcp koma amanena momwe zikuyendela. Mumafuna azinama kapena
Evn ku zikiti amati kumakhala bwino ndi anthu ndima nebaz kumakhala nao bwino coz iweyo zikakuvuta amayamba kkuthandiza ndi neba yo
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
Fact
Chawezi ndi wa MCP uyu palibe chachilendo apa ndi chani kodi Njanjizo anamanga ndi ndani zinthu zoti ena akungopitiliza a Chawezi musayankhule motha mau ai ingoyamikani kuti zinthu zili bwino basi osati kuyankhula mopusa ai
Inu mukudziwa kt anamanga ndi ndan?? Osat inuyo pot sindinu a mcp ndichifukwa chake mukutelo
ADMARC = Agricultural Development & Marketing Corporation. This organization has made us poor by limiting Farming improvement and prices on Agricultural Products. MCP built ADMARC to suppress Farming growth. MCP isn't Malawian. When are we going to wake up...???
CCB mumasulira nokha kwinako I don't have a lawyer
Umakha adha,,,,,,,facts
Program imeneyi amene amapanga sponsorship ndi boma la mcp ndichifukwa chake zonse zikukambidwa zikumakhala zabomali basi nonsense government
Zofunikira
Chipani cha magazi
Okay mafuta abwela alipa ndalama zingati sopano 😂😂
Paja kachilungamo kamabaya 😂😂
Eee zowona zake
Yawa ndi A mcp program imeneyi ikubola osanama zokambidwa apa zikumakhala zachipani cha mcp basi
Koma ngat sakutchipa zopanda ntchito
A ma Propaganda inu