ZIKUTI BWANJI ZAMA PASSPORT ?

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 19

  • @mathiusbizinesi2482
    @mathiusbizinesi2482 6 місяців тому +1

    Awesome thanks

  • @user-vp3ph1ig9f
    @user-vp3ph1ig9f 6 місяців тому

    ADPP anakanika kale palibe.wabwino

  • @mustapheryousuf7718
    @mustapheryousuf7718 5 місяців тому

    Peter ndi munthu wabwino kusiyana ndi galu uyuyu Peter anamanga chipatala kumangochi

  • @arafatMtyala-bo8ev
    @arafatMtyala-bo8ev 6 місяців тому +2

    Omwe akulensa mademowo akuyenela akutumulidwe, a president sakupangitsa misokhano asayambe manyi amenewo ma DC chonde

    • @ZelinaKisswell
      @ZelinaKisswell 6 місяців тому

      ATI awaopseza ma DC KT amene ataloleze ma demo amuchosa ntchito😢 nde akuopa

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 6 місяців тому

    A Steve Kondwa Banda ine ndikuyamikileni maka maka pa nkhani yobelekena, a Malawi sitikuganiza za tsogolo la ana athu ndi dziko lathu. Anthu amene ali mbuli ndi amenenso akubeleka ana ambiri omwe sangawasamalire. Shame! Mwaniyankhulila bwino malume.

  • @oscarnamirecah5386
    @oscarnamirecah5386 6 місяців тому

    😂😂😂😂😂😂chikhale nanu chibagela

  • @omarlux3434
    @omarlux3434 6 місяців тому

    koma mutifikisile uthenga wangawu manvanizo anga ndimaona ngati ayambe kutulusa athu amene analangssa pano zaka ziwili sinatulukebe athane nawo achaka chatha athane anawo azisata chocbo paka apanowo asayambe walelo pomwe wina pano zaka ziwile akudikilila

  • @romsa4590
    @romsa4590 6 місяців тому +1

  • @RhodaKalumbi
    @RhodaKalumbi 6 місяців тому

    Kkkkkkkk chipongwe nane ndipitisa changa akandigaisile

    • @MariamCassm
      @MariamCassm 6 місяців тому

      😊😊😊😊😊

  • @MasegoModukanele-xg2hj
    @MasegoModukanele-xg2hj 6 місяців тому

    Mukusowa astivi tikusoweka choonadi chokhachokha

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 6 місяців тому

    Zoona ndithu anyamata inuyo

  • @lyiemax
    @lyiemax 6 місяців тому

    Mwina quotation yake anapeleka ya zidina zosaotcha

  • @user-vp3ph1ig9f
    @user-vp3ph1ig9f 6 місяців тому

    Kuba amalawi

  • @RodgersBaluti
    @RodgersBaluti 6 місяців тому

    Koma a DPP akut chani

  • @HildatoweraMhango-et4mz
    @HildatoweraMhango-et4mz 6 місяців тому

    Iwowo akupanga misonkhano kulibe maso kupatsilana kapena namondwe ndipo zikhale achokedi ndi chimwendo ndi kunkuyu

  • @user-lc3sw8iz2g
    @user-lc3sw8iz2g 6 місяців тому

    Ma Contractor alibe vuto. Koma opeleka tchito.
    Mu pange life style audit kwa a Procurement ndi Ma Engineers.
    Malamulo okhwima alipo. kale.
    Koma sagwira tchito.

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr 6 місяців тому

      President akufunika mudzikomuno ndingati Kamuzu or Bingu Ankhaza chifukwa amalawi tingasinthe machitidwe athu akatangale, tikaona ma buildings amene anamanga kamuzu, misewu, zipatala zina zikanali mwalamwalatu and enawa amangoti ayi anali wankhaza look now! Ine ndiye ndimati bola dzikoli alitenge ma China or azungu kuti amalawi tisinthe machitidwe ndimaganizidwe athu. Cooking oil, fertilizer, sugar, chimanga, soap, school funds etc zinali zophweka koma lero ayi zikomo, zimitengo ngati taliguritsa dziko lathuli, kumangonamizdwa ndiazipulezidenti Akubawa fotseki