ZIPANI ZOTSUTSA ZIKAMVA IZI ZIKUTIPO CHANI?

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 42

  • @MerryMphande
    @MerryMphande 3 дні тому +2

    Nanga Smartmatic ndiya chani ? Ife tigwilitsila machine omwe tinagwilizana 2019

  • @AbdulMalik-o7n1q
    @AbdulMalik-o7n1q 3 дні тому +2

    Mudaphela dala chilima mumadziwa kuti zama shin ndi dolo lelo mwatasa

  • @AntonioNicoAntonio-ph1um
    @AntonioNicoAntonio-ph1um 3 дні тому +1

    Anabelo udzipatse ulemu wekha pakunva kulira Kwa Malawi ungotura bas udindo zisanafike poipa

  • @SkylerBlessingManyenje
    @SkylerBlessingManyenje 3 дні тому +3

    Kodi iyeyu akukakamila chani? Asatikwane anthu akuvutikatu kunjaku.

  • @bornface4786
    @bornface4786 3 дні тому +1

    Who brought the ideas of using smart matic😅

  • @DavieChiyepa-e5v
    @DavieChiyepa-e5v 3 дні тому +2

    Mayi amenewa akuyitenga MEC ngati ndi grocery ya kwawo akulongosola ngati anabadwila konko Ku MEC mayi amenewa azitenge bwino

  • @InnocentNitamanMilanzi
    @InnocentNitamanMilanzi 3 дні тому +2

    Pomwe anthu osusa amavomereza samadziwa kuti chinthuchi chimakhala chitavoteredwa kale komanso zichitochito za mec ndizimene xachititsa kuti anthu awatulukire kuti ndi a mcp apapa musalimbane ndi xipani zosutsa tikuvutika ndife monga mzika zokhunzika tithana nazo tokha chifukwa tikuvutika kwambiri ndi ifeyo

  • @DONRONMNYEMBE-i8u
    @DONRONMNYEMBE-i8u 3 дні тому +1

    😂😂😂 Mai simukufunikira mu mec ndi katunduyo

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 3 дні тому +2

    Like father like son (mwana mbuu make mbuuu eeetu)

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 3 дні тому +1

    TAYANKHULA ALIYESE MBONI MUNO MALAWI ZA MASHINI KUTI IFE ZIKA ZADZIKO SITIKUFUNA CHISANKHO CHOWERENGA NDI MACHINI IKUCHULUKA ZERU IFESO TICHULUKA ZERU

  • @DONRONMNYEMBE-i8u
    @DONRONMNYEMBE-i8u 3 дні тому +1

    Olo makinao ataotchedwa ndi ndalama za a Malawi
    Mwaba zochuluka bwaji anthufe tikuti ayi

  • @swadikimbwana7680
    @swadikimbwana7680 3 дні тому +1

    Machine amenewa people has lost confidence

  • @eliaskachali-xn2ve
    @eliaskachali-xn2ve 3 дні тому +2

    Chisilu cha muzimayi Anabel,chifukwa nichani ukukana Ku Thula pansi udindo? Ndiposo chifukwa chani mukukana kuzawele nga mavoti pa Manuel?

  • @benjaminjobo3525
    @benjaminjobo3525 3 дні тому +1

    Pali zinthu Zina zikamachitika zimamvetsa chisoni for example munthu mayeso a standard 1 then nkuloledwa kukayamba 2.Do you think standard 2 ukakhoza ? MEC yalephera kuyendatsa kalembera oyamba pano ayamba stage 2 it doesn't make sense at all. Tionana mawa,🙃🙃🙃🙃

  • @jackalview7491
    @jackalview7491 3 дні тому +1

    Iwe bwanji Mwana wa John Tembo ukukakamila izo dziko silako ,abambo ako anapha anthu ambiri mudziko llino

  • @swadikimbwana7680
    @swadikimbwana7680 3 дні тому +1

    Kodi Mai chimene mukakanilira kumeneku ndi chiyani pls understand. and hear the voice of the people .pls tulani pansi udindo

  • @BensonJere-i9k
    @BensonJere-i9k 3 дні тому +1

    Kodi chinthu anthu akati ayi,,, iweyo ukuti yes chifukwa chani? Ndalama zogulirazo zinali zako? Tanena kuti machine ayi,,, waonamo ubwino otani iweyo?

  • @Rasheedissa-f3q
    @Rasheedissa-f3q 3 дні тому +1

    DPP utm afood UDF pp mangani umodsi shosani MCP 2025 please

  • @LastonMmanga-r2u
    @LastonMmanga-r2u 3 дні тому +1

    Vuto machine wo anawajudura ndichifukwa sitikufunso and m'ntalimanja wakhalira manyi PA mpando ndichifukwa akuchita makani😢😢😢Xiiiiiiiiiiiiiiiiim

  • @SaidiMilaji-dk8sr
    @SaidiMilaji-dk8sr 3 дні тому

    Amayiwa tikuwafuna as anuwake misokho astipangile zo chita machine ameneyo ife ayi iyu apite pa radio timuuze zochita machine awa ife ayi amalawi munatiuuza?

  • @marthansaliwa7732
    @marthansaliwa7732 3 дні тому +1

    Komanso iwe anabelo unavomereza kuti chi smasmatic machine anadzetsa chipolowe ku mayiko ena. Ife sitikuchifuna chida chimenechi. Ma representative anali atapatsidwa ndalama

  • @InnocentKavalo
    @InnocentKavalo 3 дні тому +1

    Mene munkakagula munali gulu komano zokuti makinawo amagwilisaso njila yobela ndiamene pakaikisa

  • @VictormitomoniMitomoni
    @VictormitomoniMitomoni День тому

    Sitilola machn amenewa

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 3 дні тому

    mawa kuyendedwe basi awawa zikhoza kutheka kuti ufiti ulimo ndithu

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 3 дні тому

    Komatu mayiyu ali ndikukamwa kosololoka ngati kasongo.

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 3 дні тому +1

    Otsatula udindo

  • @MweneibuIbula
    @MweneibuIbula 3 дні тому +1

    Kunyasa ndi mtima omwee chimenecho

  • @InnocentNitamanMilanzi
    @InnocentNitamanMilanzi 3 дні тому

    Ndalama zomwa zinagulilidwazo zinachokera kunyini kwakoko hule iwe mesa ndimisonkho yathu imeneyo iwetu ukunama akuthawitsa nthawi yovota isanakwane

  • @SaidiMilaji-dk8sr
    @SaidiMilaji-dk8sr 3 дні тому

    Mamaanzanuwa akuwakana machinewa chifukwa ndioyipa

  • @ElizabethAlick-e6b
    @ElizabethAlick-e6b 3 дні тому

    Iwe ana kunyera mwana ukudziwa ?' anthu akufa ndinjara iwe ukukamira machine ndichoringa CHOTI chakwela kapena chikangawa wakoyo adzawineso. Chikharirenicho ana akufa ndi njara umadziwa kunya mwana iwe? Ndani angasangarare ndi uramurilo wachakwera?

  • @HaroldChadza
    @HaroldChadza 3 дні тому +1

    Mhu 🤣 ufit chani 👆

  • @chifundochiwaula998
    @chifundochiwaula998 3 дні тому

    Uyu akufuna kukhuudwitsa amalawi azipaniwo timavotera ndifeyo inuyo Munvere ife chimenecho ayi sitikuchifuna

  • @MweneibuIbula
    @MweneibuIbula 3 дні тому

    Kodi chisilu chimenechi cha anable zenazi ungapake tembo chilibe ntchito zina kapena chikufuna chibwelese nkhondo dziko muno chimenechi

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 3 дні тому

    PANYINI PAKO CHOKA NDI PLAN YOBERA MAVOTI YA MALAWIAN

  • @eliaskachali-xn2ve
    @eliaskachali-xn2ve 3 дні тому +1

    Thula pansi udindo mwalephera inu a mcp

  • @YusufMoyo
    @YusufMoyo 3 дні тому

    Mayi iwe ufiti eti

  • @MoosaSidrick
    @MoosaSidrick 3 дні тому

    Panyini pako iwe anabel chitsilu galu iwe uzaona iweyo kutsogoloko ok

  • @CharlesjeremiahNyirenda
    @CharlesjeremiahNyirenda 3 дні тому

    Nyemba yako kikwa ngat mboli ya John tembo

  • @AckimMalidard
    @AckimMalidard 3 дні тому

    Panyero pako hule

  • @MweneibuIbula
    @MweneibuIbula 3 дні тому +1

    Kunyasa ndi mtima omwee chimenecho