Chakwera akuziwa kuti aluza. Amalawi sakufuna MCP again.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 28 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 84

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 11 днів тому +6

    His exllence professor Peter muthalika
    The president of the republic of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 2025 general election ,,
    My fellow malawians , don't ever repeat any single mistake to vote mcp again ,
    Let's vote professor to continue give us development in this country .
    Zovuta sizimalephela boma lililonse koma mcp yationjeza .

  • @AdamuKasimu-x5o
    @AdamuKasimu-x5o 8 днів тому +1

    Wanyuwan sitikumufuna atinamizanso ngat chikangawa tukufuna peter atiombole kwanako azinzabwera enawo

  • @DannyKalumbaWaBanda-q7o
    @DannyKalumbaWaBanda-q7o 11 днів тому +7

    Nyimbo ikhale Grace chinga moffat,wayalura

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 11 днів тому +6

    Muzeni chakwera yo amazitenga ngati iyeyo ndiwolenga dzuwa,wayiwala kuti ali pamenepo, ndi mavoti athu,.a Malawi 🇲🇼

  • @EthelKspito
    @EthelKspito 11 днів тому +9

    Ndpo munamubela udindo Peter professor timuikaso ameneyu we love him ,his is a humble man ndpo amatha kukhala bwino ndi anthu amakolidya inu nkamapitani kwanu kukasiya uko

    • @EvansEgra
      @EvansEgra 10 днів тому

      Inu ,mukuona ngati ma banja anthu a lubino aja munapha, anayiwala?

    • @EthelKspito
      @EthelKspito 10 днів тому

      @EvansEgra akanakhala kuti a DPP amapha ma alubino kd akanaleka Ku magwidwa amene amaphawo mesa anali a MCP WO amapha cholinga chofuna kuipisa mbili ya a dpp mene ya lusila MCP pano akanakhala kuti a dpp amapanga aahh mesa anthu alikundende kd ya ma lubino yo ndye kampan ya MCP kd kd or ma rubinowo kuti muwafuse pano kuti kd utsogoleliu muona bwanji sangakumbukile za bwino zomwe amaziona mu ulamulilo wa peter. if you got evidence kuti a dpp amapha alibino you can go to police kut emwe anapangidwa zimenezoyo amangidwe but simukumpezela choipa Peter live Peter alone we love him ndpo chikondi chake paifeyo simungachichose ayi or mukanfuse lero chilima akuwuzan kuti nachita mwano ndi munthu wa bwino kukazipachika mavuto

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 11 днів тому +7

    100 percent komanso adamusiyira 1billion dollars kaya adakwelera ndenge

  • @MisheckChinjala
    @MisheckChinjala 11 днів тому +4

    Point taken my brother ❤

  • @GiftGift-d6u
    @GiftGift-d6u 11 днів тому +3

    Captain, big ups...

  • @StandwellNjoka
    @StandwellNjoka 11 днів тому +4

    Ndipo munthu ameneyu ndi mfiti yoopsya, ma dollars wapangira ma transport okwera ndege,galu ameneyu dziko kulisokoneza

  • @IbrahimRamzy-s9i
    @IbrahimRamzy-s9i 11 днів тому +3

    Noted big man, ndipo munena zoona,DPP my vote❤

  • @UmaliMmussa
    @UmaliMmussa 11 днів тому +3

    On the point

  • @ToneyPicksse
    @ToneyPicksse 9 днів тому

    Ok Chabwino bola inu mwauzidwa kale komano enafe tikudikirila Kwa mulungu ☝️ chifukwa ndiyekhayo azawelutsa sozatila zamu September ☝️

  • @FreddieKanyerere-u2z
    @FreddieKanyerere-u2z 10 днів тому

    Comrade that's 💯💪🔥🔥.

  • @SelinaMasangwi
    @SelinaMasangwi 11 днів тому +3

    Exactly

  • @EthelKspito
    @EthelKspito 11 днів тому +4

    Kd uyu ndi ndani mau akewa akhalangt abwandetu who know this man

    • @LeyvanSamuel-pe5tc
      @LeyvanSamuel-pe5tc 11 днів тому +3

      Uyu ndi captain bones amang'alura mwachabe😅

    • @EthelKspito
      @EthelKspito 11 днів тому +1

      @LeyvanSamuel-pe5tc oohh km NDE amayakhuladitu km zili bwino

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole 11 днів тому +3

      Mkatundu comrade bone amangoswa zilungamo akuseka 😂❤

  • @GwedezaBusuman
    @GwedezaBusuman 11 днів тому +2

    Mukunama sitikufuna kubwera mbuyo inuyo bwanji sanakumangeni akumangidwa akuba musaganize tivotera mthundu wamunthu muiware zimenezo

  • @stallionJames-u8r
    @stallionJames-u8r 11 днів тому +3

    Amen amen

  • @Chack..chifunro
    @Chack..chifunro 10 днів тому

    auzen baba DPP my vote andu okuba

  • @BenjaminNkhata-c4b
    @BenjaminNkhata-c4b 10 днів тому

    🖐point of order sir.

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 11 днів тому +3

    Kkkk makolija boma lamupulumukadi inu ndizomwe ndanena dzulo kuti anthu afune, asafune dpp ikutenga boma dzifukwa zina ndizimenezi, Aliyense mmalawi muno akuti nthawi ya APM dzinthu dzimatchipa komanso kunali ufulu opanga mademo ndi dzinthu zina, kuphatikizapo zambiri zimene mcp sikufikapo olo kota.Ndipo ndizoonadi kuti kampeni ya APM simvuta chifukwa anthu ntchito zake akudzidziwa kale.Dpp imapanga zimene munthu wakumudzi akufuna.

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 11 днів тому +3

    Point

  • @StevenKay-p4c
    @StevenKay-p4c 11 днів тому +2

    Ndipo Mulungu sangaloreso kut awa alamulireso, moyo ukulimba kwambiri pano eeeh🙌

    • @maryphiri2409
      @maryphiri2409 11 днів тому +1

      @@StevenKay-p4c Mulungu adzalola bwino bwino kuti alamulilenso Chakwera Nanga iwe ndiwe ndani ungalamulile Mulungu

    • @EvansEgra
      @EvansEgra 10 днів тому

      Ukuona ngati Dpp yakoyo idzidzagawa ndalama? Aaaaaaaaaaaa

    • @StevenKay-p4c
      @StevenKay-p4c 10 днів тому

      @EvansEgra Muziwerenga musanapange comment, patchulidwa chipani apa? Tapitani azikakutumani nchere ana odyetsedwa inu simungadziwe mavuto

  • @maryphiri2409
    @maryphiri2409 11 днів тому +2

    Kodi inu muzatsitsa mtengo Muka wina kodi nthawi yaka Kamuzu zinthu zinali zotani inu anthu osamphunzila simumvesa zinthu

    • @EvansEgra
      @EvansEgra 10 днів тому

      Wopusa awo, angatsitse mafuta amenewo? Muli ndi dzitsime inuyo? Mungopusitsa wopusa kaletu

  • @cmsanyama200
    @cmsanyama200 11 днів тому +1

    Nyimbo yake tsono ikhale ya EarlSixteen waku Jamaica yoti Rise up Oh you kings and queens.

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 11 днів тому +2

    Zikomo kwambiri abraz anga

  • @AlexanderYovatiKhumalo
    @AlexanderYovatiKhumalo 11 днів тому +1

    Sitikuyenda ndi mmene zinalili ayi, tikuyenda ndi nyengo osanamiza anthu kuti Suger adzachipa ayi mukhale ngati opemphera bukhu la Timoteo akusiyanitsa mmene zili lero ndi masiku akutsolo suer anali 600 inde koma sangabwelele pa mtengo umenewo tiuze a Malawi zoona osanamiza a Malawi chifukwa cha njala ya udindo ayi panopa olimbika kugwila ntchito kukacha akupindula dzala lende kudikila wina akupatse mayankho ndi wekha kudya bwino needs working.

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 11 днів тому +1

    Busa wafegi yekha mekanika wafegi iyeyu akuziwa kupha anthu kuwatumizira vula sataniki chakwera waonekeratu pambarambanda tikufuna pita ife

  • @FlorenceBanda-w5s
    @FlorenceBanda-w5s 11 днів тому

    DPP❤❤❤❤

  • @ChikhaondIssah
    @ChikhaondIssah 9 днів тому

    chakwela mbozi yamunthu😂😂😂

  • @Mosa-b6g
    @Mosa-b6g 11 днів тому +3

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @jackalview7491
    @jackalview7491 10 днів тому

    Jessie kabwila akuti boma ndilomweli,zopusa izo kabwila

  • @GwedezaBusuman
    @GwedezaBusuman 11 днів тому +1

    Adadiwo chimene mukuwafunira tikuchiziwa mukufuna muzinsaba kamasinza muofesi

  • @BenjaminNkhata-c4b
    @BenjaminNkhata-c4b 10 днів тому

    He failed to take care of Malawi.anyamule mphasa abwere mwakwao basi

  • @jamesmlungu8042
    @jamesmlungu8042 11 днів тому +1

    september 2025 ndiye mutadzayankhule mau anuwa osati pano chifukwa chomwe wakoza mulengi ine ndi inu sitikudziwa

  • @HestingsEdward
    @HestingsEdward 11 днів тому +1

    Muzibwera bwera bwana timava kukoma ndi mau amphauvu

  • @VeroMpanda
    @VeroMpanda 11 днів тому +1

    Mbusa wa fege

  • @DanielJuwawo-s5n
    @DanielJuwawo-s5n 11 днів тому +2

    Ndipo akudziwa

  • @MailosGamaliel
    @MailosGamaliel 9 днів тому

    Amen and Amen

  • @LastonBensonLungu
    @LastonBensonLungu 10 днів тому

    Galu iwee machesi umagula ndalama zingati nthawi ya Kamuzu?
    Unakwera chifukwa chiani nthawi ya DDP?
    Chabodza kauze ma tenants ako.
    Ife sungatinamize.

  • @ReadsonChisaga
    @ReadsonChisaga 11 днів тому +2

    Chakwera anachita kulanda.

  • @CliftonPhiri-m8v
    @CliftonPhiri-m8v 10 днів тому

    Iyeyo akuziwa koma akungowopa milandu,koma zoti sangawine he knows

  • @Adam-u9x8m
    @Adam-u9x8m 11 днів тому +1

    😂😂😂😂 yakupulumuka boma ndani?😂😂

  • @Patricia-l7m6u
    @Patricia-l7m6u 11 днів тому +2

    Malawi moto

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi 11 днів тому +1

    Feteleza kuchaka 18k kuvika 135k mapwala anu

  • @GeraldChilundu-e3v
    @GeraldChilundu-e3v 11 днів тому +2

    Audzeni chilungamo adziwe

  • @MakawaPartrick
    @MakawaPartrick 11 днів тому +2

    😂😂😂😂😂Awatu bzawabvuta

  • @voicedumathindwa
    @voicedumathindwa 11 днів тому +2

    Inuyo mumandisangalasa kwambili ulemu wanu bg mn🎉

  • @LastonBensonLungu
    @LastonBensonLungu 10 днів тому

    Or Peter waloyo abwerenso iyeyo ndie adzatani?

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 11 днів тому

    🔥🔥🔥🔥

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs 11 днів тому +2

    ❤❤❤❤❤😂😂😂😂😂

  • @ehinsupport3217
    @ehinsupport3217 11 днів тому +1

    Dpp never again rubish

    • @EvansEgra
      @EvansEgra 10 днів тому

      Rubbish too much, amasautsa mitundu ya ma Alubino awo, bwanji panopa sìzikuchitikanso? Achina Chisale apha ma alubino awo dzitsiru

  • @MayesoBikefa
    @MayesoBikefa 11 днів тому +1

    Zoonadi big mukunena mau amphavu

  • @PackstanGanizani
    @PackstanGanizani 11 днів тому

    Ukunama iwey wanva kd tikkamba khani za kusayenda bwino zithu mdziko kunaymba lero Inu mukunama boma ndilomweli bc

  • @JaneBanda-ht4ve
    @JaneBanda-ht4ve 10 днів тому

    Kodi nthawi imene Bakili Muluzi ankatenga boma zimene mukunenazo zinali bwanji? Nanga mmene amatuluka mitengo ya zinthu inali chimodzimodzi? Dziko lonse lapansi zinthu zadula. Wina afune asafune CHAKWERA AWINANSO
    pa 16 September chaka chino

  • @EmmanuelChavula-y3f
    @EmmanuelChavula-y3f 10 днів тому

    My vote go to DPP

  • @LimzeySande-b9n
    @LimzeySande-b9n 11 днів тому +1

    Chirungamo ichi Big

  • @PetroMatias-j9l
    @PetroMatias-j9l 11 днів тому +2

    Mmatha

  • @collengoma6542
    @collengoma6542 11 днів тому

    utsogoleri wa chakwera ndiwa pansi pa nyanja asatana palibe chomwe angawachitire amalawi chabwino chifukwa kwa satana kulibe chabwino Peter muntharika was chosen by God while chakwera chosen by satan

  • @MarthaBrino
    @MarthaBrino 11 днів тому +1

    😂

  • @EnifarSeleman
    @EnifarSeleman 11 днів тому +1

    Ndi abwanda awa

  • @chimzymhashieroo4180
    @chimzymhashieroo4180 10 днів тому

    Bwana kuyakhulatu uku

  • @GwedezaBusuman
    @GwedezaBusuman 11 днів тому

    Mcp dpp utm palibe wabwino pamenepo enawo anatinamiza tisidya katatu pa tsiku angakhale atsamariya reloli mukunamainu

  • @ElickBanda
    @ElickBanda 11 днів тому

    Zoonat zomwe akuyakhula nkulu ameneyu

  • @LastonBensonLungu
    @LastonBensonLungu 10 днів тому

    Ukawerenge Bible Ku Timoteo wamva?
    Zamasiku otsiiiza ukamva

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr 11 днів тому

    auxen

  • @KaumaNtora
    @KaumaNtora 11 днів тому

    😂😂😂😂😂😂🎉

  • @PiliraniStephano
    @PiliraniStephano 10 днів тому

    Live😂😂😂😂😂

  • @CeciliaNthenda
    @CeciliaNthenda 6 днів тому

    😂😂😂😂😂

  • @JosterLeman
    @JosterLeman 10 днів тому

    Mbambande

  • @EdwardMagaleta
    @EdwardMagaleta 11 днів тому

    Mulungu akuone zonse