ANTHU ENA GULU LA NGONI NDI MDF YALOWELERAPO PAMADEMO OMWE AKUCHITIKA KOMA SINKHONDO IYI🥺

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 1 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 137

  • @MalickMkweche
    @MalickMkweche 18 днів тому +4

    Never give up ziko ndilathu ili anatipasa ekha mulungu silachakwera ayi

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 18 днів тому +3

    Nthawi ya asilikali.yolanda dziko lija ndiimeneyi

  • @MemoryZiyaya
    @MemoryZiyaya 18 днів тому +2

    Dziko lathu lasochera .. maguwa asatana achulukitsa now.. Ambuye atithandize ndithu 😢😢

    • @jimmywhitecollins
      @jimmywhitecollins 17 днів тому

      @@MemoryZiyaya koma ulamulilo wachisilikali mumaziwa kapena mumangomva

  • @JulietMrsAndrea
    @JulietMrsAndrea 18 днів тому +3

    Ambuye akudaliseni azathu mukuvitika mukuvutikila Malawi yose

  • @WatsonSimwaka
    @WatsonSimwaka 6 днів тому

    Ngat zilizoona zot MDF ilowererapo nipereka Excellent distinction ku malawi army

  • @masoyaonamunkhondya9074
    @masoyaonamunkhondya9074 18 днів тому +3

    Anthu a mulungu ,MDF ,dzikomo kwambiri tiyeni tiyende limodzi kukonza dziko lathu. MCP leadership has totally loose direction to run the country, Malawi.

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 18 днів тому +2

    Ndipo ......timaziwa kuti Biyeni...anachita ku mphedwa....ndi Ànthu amene anali mu ndege come out.....chilugamo ku mtundu wa Malawi....yebo. mu Mukulu

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 18 днів тому

    Timanena nthawi zomse kuti mdf ndi t
    Yaife a malawi, Abale ndife tili mmuzimu tikuvutika sikuti iwowo akusangalatsidwa ndi ulamuliro wa cikangawawu ai ndicifukwa ndikuti mcp ngati sasamala dzikoli tiligawanapo.dzikomo a silikali athu potipatsa citetezo osati zisilu za ku area 30, yolamu ndi mbuzi zizacezi asiyeni tithana nawo.bravo MDF

  • @Malawinews24-7
    @Malawinews24-7  18 днів тому +4

    Osatukwana guys tonse ndi amalawi ndife amodzi, kma osayiwala kupanga subscribe, like and comment.

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 18 днів тому

    May the Almighty God bless you and be with us all Malawians.Amen

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni 18 днів тому

    Amalawi kuyakhula number one kumakulowa paground ndikalindo ekha . Bwanji kundolola Chakwera akutembenuzeni bsi

  • @AdamMakala
    @AdamMakala 18 днів тому +1

    Chisale ndi mamuna❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson 18 днів тому +2

    Alemekezeke A MDF ndipo awa kwapule zedi akawapeza anyamata a zikwange wa awathibule zedi ngakhale a police amenewa kuwa kwapula zedi

  • @LimbikaniChirwa
    @LimbikaniChirwa 18 днів тому

    Ndiye kodi mademowo achitika mawa ndiye ngati mawasachitika ndiye asilikaliwo abwela kuzatani

  • @ChisomoSaiti
    @ChisomoSaiti 18 днів тому +1

    Ife tikufuna Richard amene akudzitamayo iyeyo mesa akufuna chisale

  • @Zebron-kg2qz
    @Zebron-kg2qz 18 днів тому +2

    Military yogulidwa ndichakwera kunabwera madzuro mumawa analikuti?? 🤔🤔 Ndawona kuti anthu aliphe akugulitsa Malawi 2 pin

  • @FrancisGama-qb7ze
    @FrancisGama-qb7ze 18 днів тому +2

    MDF alandire ulemu kwambri apolice nd zsilu iyaa

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 18 днів тому +2

    Good job MDF

  • @JosephNambazo
    @JosephNambazo 18 днів тому

    Good job MDF for loving your country Malawiay God bless you all

  • @WatsonSimwaka
    @WatsonSimwaka 6 днів тому

    MDF hurry up work independently transparency tulukilan plz zisanafike poyipa anthu afapo nizikwanje b4 it is too late wonesan professional yanu 👮👮👮

  • @Miles-d8g
    @Miles-d8g 18 днів тому +2

    MDF ndi boma palokha koma chikangawa sakudziwa good news

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 5 днів тому

    Ngati mdf yalowelelapo ndie kuti zili bwino chakwera out

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni 18 днів тому +1

    Muno mulibe chitetezo or Dc mulibe mbavha yochedwa DC

  • @JessieMbewe
    @JessieMbewe 18 днів тому +2

    Mulungu aliko kunja kuno athufe tikuvutika kwambiri mamidzimu mabvuto kwambiri athu akugona ndi njala

  • @MtewaMtewa-j4g
    @MtewaMtewa-j4g 17 днів тому

    Mukamamva kudzetsa chisokonezo mdziko ndi uku,kukomza ufulu wophwanyika kusokoneza Malawi wa mtendere

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni 18 днів тому +1

    Dc ndiwakunyumba kwachakwera fiti

  • @AcramJuma-lr6np
    @AcramJuma-lr6np 18 днів тому +2

    Pamenepo zachita bwino a police ndizitsiru za anthu

  • @SherifaG.Mlelemba
    @SherifaG.Mlelemba 18 днів тому +1

    Moyo wamagazi,autsuke etii!? 🤔🤔🤔🤔 😂😂😂😂

  • @BillyBentryMunthali
    @BillyBentryMunthali 4 дні тому

    Ndiwe wa bodza galu iwe, mademo tinapanga kale nthawi ya pitala

  • @GERALDCHRISMNJONDOBANDA
    @GERALDCHRISMNJONDOBANDA 17 днів тому

    Mukifuna mukhetse mwazi kuteroko 😢 ndale za ku Africa...eeeish 😢😢😢

    • @fredsemu7136
      @fredsemu7136 17 днів тому

      Osaiwala MCP inakhesazo mwazi ndiye mwazi uwu upambana chani onsw ndi mwazi

  • @Zebron-kg2qz
    @Zebron-kg2qz 18 днів тому +1

    Kkkkkkkkk asikali AA MDF MANTHA

  • @Chaphera-hd5kq
    @Chaphera-hd5kq 18 днів тому +1

    Muli ndi mbali ,sitikunkuvani

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 18 днів тому +1

    Ulemu wanu MDF tiyeni tinware ntchito limodzi tikoze Malawi

  • @alibwana4452
    @alibwana4452 18 днів тому

    Zikomo kwambiri MDF 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 ife tili manja mwanu

  • @osmanmdala-uh7xw
    @osmanmdala-uh7xw 18 днів тому +3

    😂😂😂kodi kani kulinso Ngoni military? Ponyani acc yanu chifukwa pafunika ndalama kuti ikhale ya mphamvu mmodzi mwa a Malawi osonkha ndine....

  • @EstherBonga
    @EstherBonga 18 днів тому

    Our God is always a winner

  • @GiftGamphula-z5x
    @GiftGamphula-z5x 17 днів тому

    Kod mdziko muno muliso ngoni military eeesh zachilendo izi kaya anthu adyeranu vula yagwa wakumunda mukadya mademo next year

  • @DanielGanizani-h8r
    @DanielGanizani-h8r 2 дні тому

    Umbuli sizinthu MDF sunaiziwebe mpaka lelo?kwanu nkuti iwe?akutuma? MDF inaphedwa yonse asala ndi olanda makala ndikulondera nkhalango

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 18 днів тому

    Tithoke a MDF, 100% zikwanje zichoke pa msewu.

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 18 днів тому

    God bless all mdf🙏🙏🙏🙏

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 18 днів тому

    Thanks MDF amalawi tilipamoto

  • @MtewaMtewa-j4g
    @MtewaMtewa-j4g 17 днів тому

    Amtambotu ndamzanu ndinuyo ofuna kusokoneza Malawi

  • @HolmanDazah
    @HolmanDazah 18 днів тому

    Ya bonga madodana, izani madoda. Ife kumambwe/ Bhiyeni

  • @TisopeMkozo-h8t
    @TisopeMkozo-h8t 18 днів тому

    Good job mdf

  • @GivenMvula-k5k
    @GivenMvula-k5k 18 днів тому +2

    Kodi anthu mungofokoza simukuonesa ma video bwanji

  • @AnyuxyJulias
    @AnyuxyJulias 18 днів тому

    Inu ndinu aboza nde madhemo bwanji sanachitike pankhondo sipamafunika ulemu

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 18 днів тому

    Chiwawa abweletsa ndi a. D. P. P. Achikwanje adalamula anthu aziphana ndie mukudabwa chiyani

  • @CalistoRichard-it8ot
    @CalistoRichard-it8ot 18 днів тому

    Mdf ndiwoyima paokha,ndipo ndikuziwa kt msundwe siphulaka2

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 18 днів тому

    Bafuwethu asiyeni soke,niwayasabana?asiwasabi siyawafuna.amandla,awethu, power to the people of malawi nation.masilwe,nabo,madoda.

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 18 днів тому +1

    Zikomo big man mcp ikutibwezelatso ku chipani chimodzi uchisilu dzedi amalawi mamvuto awa tidzikana 1992 1993 tinatsankha DEMOCRACY uyu chakwela ndi mbudzi dzizakezi dzimakana DEMOCRACY nde akufuna tibwelele chipani chimodzi awa agalu kwabasi

    • @JaneMapazi-ex6bb
      @JaneMapazi-ex6bb 18 днів тому

      Chokani Inu chiani cha banja, kagweleni uko, pitani ku court ko. Koma anthu akunn5cheu ndinu otengeka, anakuchitilaniko chani a dpp? A biyeni anafa ndi zizimba mumufunse anjella ndi kaliati

  • @NaomieBanda-t6g
    @NaomieBanda-t6g 17 днів тому

    Zabodazo izi mademo analikuti

  • @CharlesChilembwe-x3o
    @CharlesChilembwe-x3o 18 днів тому

    Aaaaaa chakwera sim’busa

  • @DavidJabesi-r1h
    @DavidJabesi-r1h 18 днів тому

    Mau mau bwana.

  • @ChikupizgaKajawaMkandawire
    @ChikupizgaKajawaMkandawire 15 днів тому

    Kodi a mdf akhanakhala kuti akuteteza zopusa zanuzo mukanathawa??

  • @JohnBishoza-t6m
    @JohnBishoza-t6m 18 днів тому +1

    A Malawi azanga,ine ndakhala ndikuzifunsa Kuti a MDF,akuwawopa anyamata azikwanjewa?

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f 18 днів тому +1

    Zaziiii

  • @DallaCass
    @DallaCass 18 днів тому

    Nic

  • @SteveKamwendo-wi8to
    @SteveKamwendo-wi8to 16 днів тому

    Mwayamba kunama

  • @JohnmjigoMalinda
    @JohnmjigoMalinda 18 днів тому +2

    MDF kumeneko ndiye kukhala chakwera wajaira soon take this government over to you

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 18 днів тому

    Mukunena zoona big man

    • @Malawinews24-7
      @Malawinews24-7  18 днів тому

      Yes ndipo nkhaniso akuti ili ku khoti pano kuti khoti ligamule kut mademo apitilire zambili zikubwera.

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 18 днів тому

    Anthu achokakudeza kuntcheu dedza kithandizila zakumtumbozo mesa m, mati apolisi komaso asilikali kunalibe ndieno mukut. M. D. F, inatenga gawolanji

  • @Mbeta-q8v
    @Mbeta-q8v 18 днів тому +1

    Sizoba si emuva kwenu
    Be Ngoni military
    Njalo
    Payeeede

  • @AndreaphiriAndrea
    @AndreaphiriAndrea 18 днів тому

    Osangokambirana bwa

  • @DallaCass
    @DallaCass 18 днів тому

    🎉nic

  • @mustafakasende-z3h
    @mustafakasende-z3h 17 днів тому

    Chakwera ndi si presindent akadakhala president akadalankhulapo kathu ndi mbuzi

  • @ChikupizgaKajawaMkandawire
    @ChikupizgaKajawaMkandawire 15 днів тому

    Awuzeni anthu azikalembetsa uko osati zanuzo

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 17 днів тому

    Unaboza iwe

  • @benjaminmvuma-rk6mu
    @benjaminmvuma-rk6mu 18 днів тому

    Angoni ndiye chani kwaife

    • @AchinaKellz
      @AchinaKellz 18 днів тому

      Kkkkkkkk😂mbuzi zathawamiyara kkkkkkkkk ana ajoka

  • @AbdulJohn-t7l
    @AbdulJohn-t7l 18 днів тому

    Kodi munthu akanyozela malamulo a court zosatila zake ndi chani? Kodi malamulawa amagwila ntchito kwa amphawi okha

  • @RoseThindwa-w4c
    @RoseThindwa-w4c 17 днів тому

    Danke

  • @DallaCass
    @DallaCass 18 днів тому

    Ulemu ulemu ulemu

  • @GERALDCHRISMNJONDOBANDA
    @GERALDCHRISMNJONDOBANDA 17 днів тому

    Mpaka kuikapo MILITARY?😢

  • @CentTiger
    @CentTiger 18 днів тому

    Maliwi vivaaa

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza 18 днів тому

    🔥🔥🔥🔥

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 18 днів тому

    amandla ethu madoda🎉🎉🎉🎉

    • @jennyx6914
      @jennyx6914 18 днів тому

      is it isizulu or ngoni lunguage or what???
      kkkkkk

  • @ChikupizgaKajawaMkandawire
    @ChikupizgaKajawaMkandawire 15 днів тому

    Koma kunali kuthamanga kuthawa

  • @Ybm-o5y
    @Ybm-o5y 18 днів тому

    A galu amene aja athokoze kuti pipe yanga yatha machaka, ndinaphulisa mitu yawo,,,kudalira zikwanje

  • @AbdulAzizihYasin
    @AbdulAzizihYasin 18 днів тому +1

    Amandla wethu phakama Malawi phakama

  • @TakondwaSulani
    @TakondwaSulani 18 днів тому +1

    Mwayakhula zanzeru Mulungu akutsogolereni even David amamenyera ufulu wa ana a israel

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 17 днів тому

    Boma lolephera ngati ili silinaonekenso

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 18 днів тому

    Wabodza iwe

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 18 днів тому

    Kd mufuna chakwela asakhale ndi omutetezela nanga makadeti amadzatani tinawona ife

  • @MikeMwale-bw1xw
    @MikeMwale-bw1xw 18 днів тому +1

    Ngoni military nde itiyoso imeneyi?

    • @GoodsonjTime-m8m
      @GoodsonjTime-m8m 18 днів тому

      😂😂😂😂😂😂 zomwe ndikudabwa nanenso

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 18 днів тому

    Ife timadabwatu kuti kodi army yathu ili kuti?lero nde mwapezeka zikomo kwambiri gwirani ntchito Mulungu akutsogolereni

  • @PiterDzinkambani
    @PiterDzinkambani 18 днів тому

    Zabodza kulila otsutsa muladzi

  • @AliNtolera
    @AliNtolera 18 днів тому

    Zabodza izi

  • @MarryUnyolo
    @MarryUnyolo 18 днів тому

    Mcp ndi manyi okhaokha

  • @jimmywhitecollins
    @jimmywhitecollins 18 днів тому

    Kunalibe mdf uku. Kodi inu simunamve kuti biyeni anatuma kaliyati ndi anjella ndiye analakwisa chizimba zinawatenga okha

  • @LobertSamuel
    @LobertSamuel 18 днів тому

    Ok

  • @WatsonSimwaka
    @WatsonSimwaka 6 днів тому

    Zomwe zuchtika chot muziwe mulungu akukuonani amene mukumazunza a malawi kukkhala ine nikutsogolera dziko sindingalephere kupereja ufulu kuwanthu kut asiyeni ayende apange mademowo koma mwantendere mwaumunthu komaso kuufulu wamunthu komaso moziwa kut kumwamba kuli yehova tisamayiwale chimenechi osat anthu achauta akhale azilira mmm agalatiya inu mmm ohoho

  • @paulbanda9638
    @paulbanda9638 18 днів тому

    I'm sick and tired of this, MCP must go, by any means

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 16 днів тому

    Tiye uko iwe mbuzi ya munthu

  • @Charles-v1j2p
    @Charles-v1j2p 18 днів тому

  • @JerieWytonTengani
    @JerieWytonTengani 18 днів тому

    Koma inu a pòlisi mukudziwa kuti ndinu Ana athu?Ndiye ife tizithamangisana ndi inu chifukwa cha Chakwera Pali mzeru?Ine ndkuti tetezani akuchita anthu akuchita ma demo osati chakwera.Ngati simukumva izi zako iwe.

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer 18 днів тому

    God bless you achitiseni manyaz ameneo

  • @felistasbunu9824
    @felistasbunu9824 18 днів тому

    1:19

  • @DanielChipasula
    @DanielChipasula 18 днів тому

    MUKUPUTA MIRANDUTU INUYO... MULI KUTI.. OSAMANAMIZA AMALAWI PA IZO MUKAMBA !! NDANI AKUKANIDWA KULEMBETSEDWA PA ZA MA ID. ALIYENSE ALIBE UFULU WOCHITA ZANUZO !! AMKINDO WA ANGONI ALIPOTI APA NDADUTSA PA MSIPE ... ANGONI MILITARY SIDAWAONE !! KODI IWEYO NDIWE NDANI WOSABWDRA POYERA ✍️✍️🌎

  • @BashiruAdamus
    @BashiruAdamus 18 днів тому

    MDF mwabwera apolice ndi mbuzi yachabe chabe

  • @AlickKapapa
    @AlickKapapa 18 днів тому +1

    Mesa mmati president apange commission of inquiry panu mkuti simkuyifuna kodi inu ndinu ofunthadi a DPP zigawenga eti.kodi mkufuna kuwopyeza Boma?or what ngati simkufuna vote then withdraw it Boma ndilomweli

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa 18 днів тому +2

      😂😂😂mutu wako sukugwira ntchito ndwe ndani kafukufuku akuchitika kuti? Anakanilanji kut ikhale ya live aaa kungoyankhulira kusowa umunthu kaganize kae

    • @WakisaGodfrey-y8h
      @WakisaGodfrey-y8h 18 днів тому

      Zaugalu basi mesa ndinu gulu la satanic inu machende amako

    • @KondananPetro
      @KondananPetro 18 днів тому

      Ndpo chmenecho ndchitsiru kwambiri kd wapasidwa zngat kanyimb iwe

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa 18 днів тому

      @@KondananPetro palibenso wadyapo kungoyankhura mozipopo

    • @KondananPetro
      @KondananPetro 18 днів тому

      @MillyKachepa Nde ndi kape azafera za eni

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 17 днів тому

    Machende anu ma cadet mboli zanu

    • @ChikupizgaKajawaMkandawire
      @ChikupizgaKajawaMkandawire 15 днів тому

      Kkkkkkkkk

    • @samdiverson9733
      @samdiverson9733 5 днів тому

      Kapolo iwe ukhalila kutukwana

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 5 днів тому

      @samdiverson9733 kapolo ndani pakati pa iwe ndine, munthu ovetsa ngati iwe kwanu anthu akudya chitedze chifukwa munazolowela kudya zakuba